Zilibwino akumudzi kwathu m' mbali mwa mtsinje wa Nathenje apo tinkadyerapo mbatata yosasenda kale ife tisakudziwa kuti pali ulaliki wathoo. Mwandisintha kwambiri ndi nyimbo maka maka yoyambayi. Andipatse mtima wopilira zonse zondipinga dziko lavuta ili. Masiku ano ndi gwira bango madzi angakutenge kikkkkkk Alleluya.
@simbayihamaundu3552 Жыл бұрын
Watched this from Lundazi Zambia 🇿🇲
@CharlesChilinde-zm9xo Жыл бұрын
So nice do good keep it Nanthenje women choir thank you as lot