Pagulupa wa mcp ndi wonder enawa amangosatila but no wonder this is kandodos TV but zoona chakwera ndiolephera ndipo whether you like it or not mcp ikupita thank you
@SheenahMwalabu-iz3pr14 күн бұрын
Olo mutayankhula bwanji, kulangiza bwanji, Chakwera sangasinthe ndi president wamwano ndioipa sinnaoneko eee. Ndinamukhulupilira koma ndinabetsa, bolanso tikanaika Chilima chifukwa amaoneka kuti zopusa safuna bwenzi zomamenyanazi anthu achipani cholamula kulibe 😢 ndezonse ndinthawi 2025 tiona chifukwa olo mulungu sakukondwa ndazo and l believe kuti malemu Sidik Mia bwenzi akusekelera izi
@user-ev6bi7jr7g13 күн бұрын
Musavutike ndikuyankhula a Malawi akudziwa chabwino ndi choipa ndipo chomwe agwiracho ndi chomwecho DPP woyeeeeee
@marryphili541913 күн бұрын
Ine mutanena bwanji za zoipa za DPP Koma ine ndikuwona Kuti DPP yinali bwino chifukwa fertilize wunali wosika , makhwara muzipatara analimo chimanga chinali palipose mapassport timawapeza kwina kulikose mosavuta Koma kubwera Kwa MCP moyo wolimba okhaokha angomba ndarama mopanda chisoni ndipo I like DPP
@Abdul-xk8dq14 күн бұрын
Koma inu simungathe kusiyanisa pa thawi ya dpp ndi ino tili ino?
@AleksaWilliams-qc6cn14 күн бұрын
Mwadya banzitu iiiii koma ndalama anakonza
@ziyamporoma37714 күн бұрын
Kodi anthu akanena zosakukomelani ndekuti adya banzi? Do you think 20 million tonsefe tingakhale ndi maganizo amodzi?
@AleksaWilliams-qc6cn14 күн бұрын
@@ziyamporoma377 mwadya
@TarPoor-ye9jx14 күн бұрын
Yes Malawi izi sizingapitise chisogolo dzkoli chkufunika Inu maguys pakanemapa musamaope mukuona kwanga Inuyo madolo mukuopa mcp kut munene chilungamo mukubweza mau kwambiri and mcp ikusaka bakili muluzi tv chifukwa chachlungamo chimene iyeuja amalankhula Malawi yonse kuli Bakili muluzi tv and Bon kalindo saopa munthu and Inu zoona Malo mot boma likhale likuona mavto amalawi akulimbana ndkusaka bakili muluzi tv pali dzeru tonse yalepera pazonse bas we need new leadership chakwela ,chilima ,mutharika sakufunika boma and nankhumwa too we don't want them you should tell them please
Mmmm awatu kubwera pa tv ndikusonyeza kulimba mtima
@user-fi2by2ui9o14 күн бұрын
Mukamatero za dpp zimandinyasa kwambiri sindimafuna kumamva Zina limeneli Peter olo bingu amandinyasanso ndi zimbava zowononga dziko chonde musamatchule zinthu zimenezi
@TarPoor-ye9jx14 күн бұрын
And we know kut zodiak, mbc and times media all zili pansi pa mcp does why you scared please try to tell people the Truth not just blaming dpp only what's about mcp
Achakwera sogolo alibe, peter muthalika sogolo walibe ... Let find someone to lead us these two mubusa ndi professor tiwataye uko atinamiza chani Poti both of them akhala pa mpando wa upresident for 5yrs but nothing did for the nation Wonse Kuba, nepotism very excellent... Palibe wina wowapotsa
@WitnessMpakula-cs1so13 күн бұрын
Hot current idatha ndi Brian banda
@user-lw9su5om5z13 күн бұрын
Munya muona bolan Dpp ili nd ma pictures abho ku mtundu wa amalawi
@WhiteRichard-cw2fo14 күн бұрын
Inu mwayamba kudya ndalama zachakwela iti
@user-un6qv6sj3h14 күн бұрын
Mulungu akudalitseni nonse chifukwa chowaunikira amalawi I love guys inudi simutenga mbali mumangonena chilungamo chokha basi
@user-fr4gb4bq6q13 күн бұрын
Zipumi zanu mbuzi za anthu mukuzitenga ngati ndinu opambana
Guys mwalunkhula chilungamo, we must never say DPP but Peter muthalika munalipo pamupanfo zinthu zinakukanikani ,,, MCP yilibe vuto, problem ndi Chakwera walephera kukoza dziko. These two people please Malawian don't worst our time to vote for them at least they must handover to another person to represent their parties
@CyprianoSandalamu14 күн бұрын
Mcp my vote, during the time of DPP party,we have been killed by DPP party mainly the cost of dry maize,their cost was k60 per kg,but now we are going to admarc to sell dry maize at K650 per kg.But those they are not farming,they cry.Don't cry ,go to field and do farming you will not regret.
@husseinsangala337411 күн бұрын
You are selling that price bcoz of the devaluation your MCP brought but you can't see
@DennisDonework14 күн бұрын
Charge mpaka 45,000. Ngati ndi thini la chimanga kapena izicharger. Or magesi kulibe
@samsonmtumbati485514 күн бұрын
Ndipo zoseketsa kwambiri
@AlickLayson14 күн бұрын
Zooona xzake
@user-si7po9sd5i14 күн бұрын
Kodi mumalimbana ndi dpp chifukwa chani,Kodi mwaiwala kuti mcp inapha anthu ambiri mu ulamuliro wao motsogozedwa ndi kamuzu Banda,timadziwatu kuti times ndi yakubanja kwa akamuzu,komaso timadziwa kuti ndinu anthu adyera komaso muli mkhwapa mwa mcp.
@mosespemba882213 күн бұрын
Umbuli uli ndiinunso 😂😂. You will hate MCP up to when? Mbuzi ya munthu,,
@user-si7po9sd5i12 күн бұрын
@@mosespemba8822 you have proven yourself of who you are,the nasty words always represent the real person.
@user-qp8kh2hj9o14 күн бұрын
Ndipo ngati kuli chipani cha manyi nde ndi DPP anyamata inu
@AdenaGuest14 күн бұрын
Achabe
@JafaliAkimu-ll1bf14 күн бұрын
vuto ku mcp kwachuluka mbutuma za anthu anyawu ndi mbuzi zosapita ku xool
@AlickLayson14 күн бұрын
47:05
@PatrickLucius-bl3te14 күн бұрын
Mufune musafune kaya ndinu a times kaya zodiac koma CHOTI muziwe ndichakuti nkhondo imeneyi Mulung aimenya ndiponso aimaliza yekha.kukanakhala kt peter anakakamila nthawi imene ija bwezi kuli nkhondo yoopsya .koma mulungu anamunong'oneza peter kt zisiye kaye lero anthu azindikila kt chakwela ndi chilima anatinamiza anthu ayambanso kumufuna peter Muthalika .Nkhondo iyi Mulungu aimaliza yekha
@alexmkolongo308914 күн бұрын
Mau amphamvu
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw14 күн бұрын
Pankuku wayakhula bwino
@user-cs5ss4rj7g14 күн бұрын
Zikulipana ndi dpp chifukwa mbuzi izi zikudya kwachakwela buli ndichakwela
@JafaliAkimu-ll1bf14 күн бұрын
chakwera ndi mbuzi ya munthu democras samaiwa kuti ndi chani vuto lili pamenepo or kungoti mcp ndi anthu ankhaza ndizitsiru
@user-bm5yg6zm3c14 күн бұрын
Izitu sizigwila ukamalemba utakwia umadumpha mau Ena 😂😂😂
@AdenaGuest14 күн бұрын
Anthioipamcp
@BiquitoniNsandamila14 күн бұрын
Sindikukaika kuti Nanunso mukudya nawo za chakwera
@tisuhmakhwah708514 күн бұрын
mcp
@jemasmasimbi810914 күн бұрын
mmm kupusa bas,,, ngat mulinshunga makwanu
@user-nj5vu8cd5l14 күн бұрын
Peter is musogolele wapha ma albinos ambiri, kuba ndi chisale, nepotism racist Peter galu. DPP yilibe vuto, problem ndi Peter muthalika ndi mudala woipa mutima kwambiri
@alexgweje861014 күн бұрын
Inu muli ndi umboni Kuti Peter amapha ma komanso Kuba???bwinotu musamatamike ndi kuyankhula nanga anthu akuphedwawa ndi munthalikanso