Рет қаралды 10,864
Ndidzam'dziwa
//When My Life-Work Is Ended (Fanny Crosby (1894))
//I shall know Him by the print of the nails in His hands
Lyrics:
Verse 1
Pamene nditatha ntchito zanga,
Nditaoloka tsidya la nyanja;
Chakufachitu chikadzabvala chosafanso;
Pompo ndidzam'dziwa Mombolo wanga
Chorus
Ndidzamdziwa (Yesuyo), Ndidzamdziwa (Yesuyo),
Podzaima pa mbali pakepo,
Ndidzamdziwa, ndidzipsera Yesuyo
Za misomali m’manja mwace.
Verse 2
Ee! ndidzakondwa pakuona okondedwawo
Omwe ndalekana nawo m’dzikolino;
Koma n’dzayamba ndaonana naye Yesuyo,
Wokondedwa wanga wopambanayo.
Verse 3
(Kupyolera) Kupyolera pa zipata (kupyola) kunka ku Mzindawo, (oooh)
Iye adzanditsogolera ine (iine),
Nyimbo nthawi zonse ndidzayimba ine mokondwa;
(Nditamuona) Nditamuona Mpulumutsi wanga.
Outro
Ndidzamdziwa, ndidzipsera Yesuyo
Za misomali m’manja mwace.
Za misomali m’manja mwace.
Za misomali m’manja mwace.
-----------------------------------------------------
Originally Written by: Fanny Crosby (1894)
Rearranged by: The Morning Star, Kawale, Lilongwe, Malawi
Audio Prod. by: Recall, Kuimba Mwamphamvu Studio
Video Prod. by: Hope Channel Malawi
-----------------------------------------------------
Share this video:
• Ndidzam'dziwa - The M...
Subscribe for more videos:
/ @themorningstar-mw
Audio Available on:
www.mpesamusic.com/songs/deta...
-----------------------------------------------------
Connect with us (subscribe and follow):
Facebook: / themorningstarsingersmw
Instagram: / themorningstar_mw
Whatsapp: whatsapp.com/channel/0029Va5V...
Spotify - spotify.link/EC6GyW0v3xb
E-mail:
themorningstarsingers@gmail.com