NKHANI IJA YAFIKA POVUTA KWAMBIRI🙌🙌🙌

  Рет қаралды 27,333

HOT 265

HOT 265

24 күн бұрын

Пікірлер: 370
@LovemoreSalima
@LovemoreSalima 23 күн бұрын
Mbuzi ya munthu iweso Ndi mbava. Mbudzii
@MisheckManners
@MisheckManners 23 күн бұрын
Nkhope zogulidwa izi...anthu osakonda dziko lanu inu😮
@YNOTGEORGE8
@YNOTGEORGE8 23 күн бұрын
Mukatero akupasani mabanzi....mwaba mwaba
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 23 күн бұрын
Inu mwalakwisa mukanakhala chete. Musikanayo kodi akumunamizila kuti magalimoto 20 alibe. Ngati magalimoto alinawo ayenera kutufuzidwa kumene zachokera. Sikaduka koma tiziwe. Mukakhala ndimoyo wotere kumalawi katangale sangathe zikuonesa poyera kuti chilipo chimene mwalandila. Ndichifukwa chani muku pondereza madandaulo azanu mwina mwatumidwa and mukukaniza ACB kuti ifufuze ndi zeru zimene mwabwera nazo mukuona kwanga please amalawi tisakhale ndimoyo wotere. Aliyese wosemphesa chilungamo chifukwa cha chiphuphu adzalangidwa
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 22 күн бұрын
Ndipo mulungu adzawalanga ndithu
@user-xf6hp3ik8r
@user-xf6hp3ik8r 23 күн бұрын
Kulankhula mwamphamvu akudziwa zowona. Mulungu awaunikile ndithu
@user-so7wg6ii5m
@user-so7wg6ii5m 23 күн бұрын
Mwagulidwa uko mudzibwera apa mudziyankhura zopusa zanu zi dzitsiru
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 23 күн бұрын
Ndipo anthu opusa awaaa zedi eeeeee afiti okhaokha
@JustinPhiri-kq2bb
@JustinPhiri-kq2bb 23 күн бұрын
mukudyanawo eti yafikatu ku mabungwe kunja
@WonderMinjale-bg6kd
@WonderMinjale-bg6kd 23 күн бұрын
Mbava iyi ayituma. Kuti ikile umboni kwa mbava zinzake. Chithyola ndi mwana wake onse ndi okuba amangidwe
@alexsumani6823
@alexsumani6823 23 күн бұрын
Anthu osowa zochita media team mukatero akupasani ya bundle,amasikini enieni
@user-zd9js7qx1i
@user-zd9js7qx1i 23 күн бұрын
Mukudya ndalama koma kathupi ngt khwangwala Edzi ikukuperesani inu
@IssakeMateyo
@IssakeMateyo 23 күн бұрын
Ameneyo khani yake ikuyenelatu chifukwa ndamene wapagitsa Malawi kusauka
@MalickDyton
@MalickDyton 22 күн бұрын
Nanuso achisilu mukatelo mwalandila Koma mumaganizila atuwosauka inuyo ukufuna muyanganile ufulu wamunthu mozi Kusiya maufulu awanthu
@mphatsojuliostandy4918
@mphatsojuliostandy4918 23 күн бұрын
Manyazi ulibe ,machende ako
@user-qb4pj5yy5b
@user-qb4pj5yy5b 22 күн бұрын
Achewa okhaokha awa, anganene chani, mumangidwa chaka chake nchamawachi
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 23 күн бұрын
A mbadwa zokhudzidwa ,nose manyi anu. Ndinu mukupangitsa dzikoli kusayenda bwino, mwapasidwa ndalama mukonekelatu
@MCDONALDTHENGENDE
@MCDONALDTHENGENDE 23 күн бұрын
Ngt mulungu wanga muli wa moyo , chitanaoni anthu akubawa ngt nkotheka thotholani mtundu onse ,,asoloke ndithu ....mukapanda kutero ana anu tikhala tikuvutikabe ndipo okhulupirirafe tichita manyazi Dear Lord , push these thieves
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 22 күн бұрын
Amen 🙏🙏❤
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m 22 күн бұрын
Muli Mbali yimodzi ndianthu akuba mbuzi dzaanthu
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly 23 күн бұрын
Iwe ndiwe chitsiru kwambiri Anthu momwe tikuvutikiramu akuba Kuba Kuba Kuba Kuba iweyo uli mdziko liti Tangotsala pang'ono MALAWI wathuyu anukha kwa iwe wakubawe. Ibani ndalamazo zidzakupulumutseni Mawa lino
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 20 күн бұрын
Agalu mwadya mabanzi Mukwonago ngati mungatiputsitse ife, mbuzi za mabo kunsi
@DennisDonework
@DennisDonework 23 күн бұрын
Iwe ndi galu akupasa zingati kuti utsuse tsika ameneyo sanagwilepo ntchito inailiyose. Machende ako wanva akupasi zingati kuti upange defending nkhaniyi
@HappyFlower-nu5rz
@HappyFlower-nu5rz 23 күн бұрын
😊
@JamesBanda-gx3re
@JamesBanda-gx3re 22 күн бұрын
Ameneyo ndiye m malawi
@user-yx9qz2lp5h
@user-yx9qz2lp5h 21 күн бұрын
Anthuwa.ndimbava.amangeni
@GiftNazira
@GiftNazira 23 күн бұрын
Mwatumidwa ndinthan iwe athonthwe tonthwe fank you man Machendeanu notse
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 23 күн бұрын
Sanjetu iyi ndipo nkhani iyi sangaluze chitholayo Ndalama ndi zake umboni mulibe ngakhaleso a Mwenye amachita zomwezo chuma ndikumilembesela mwana wake nkhani imeneyo mukaluza
@felixsaidi6715
@felixsaidi6715 23 күн бұрын
Osamayikira kumbuyo akubaa .maybe your one of them
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 22 күн бұрын
​@felixsaisdi6715 sure
@user-pu3sb2xw6z
@user-pu3sb2xw6z 22 күн бұрын
Mwasowa solangu cha mene alemba kalatho ndi amalawa thathopa ndinu okala ngathi amabungwu muli othetheza phafa sikhulu sikulu
@user-pw1kl3vo5d
@user-pw1kl3vo5d 23 күн бұрын
Inuso amabungwe mwayambaso kuukilana zaziii
@GrecianWyson
@GrecianWyson 23 күн бұрын
Ambuye athuwa akuona Ngati akamaba simukuwawona Koma maso anga ari painu ambuye.Athuwa Kuba anyanya ambuye mutithandize mdziko lathu lamalawi
@OliverNkhoma
@OliverNkhoma 23 күн бұрын
Zopanda nzeru ndiponso bungwe lanu siloyimira a Malawi lithetsedwe la anthu opanda nzeru
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 23 күн бұрын
Inu ndiye anthu amene mukufuna kuti ndalama zaboma zizibedwa mosadziwika
@aggogokina8992
@aggogokina8992 23 күн бұрын
Ukapanidwa ndi umphawi umajoina okuba kut udye nawo ndie ndi izi...
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 23 күн бұрын
Ooooihh kagulu kakuba Kajang ndikomwe kakhala aphaka
@olindamhondiwa8714
@olindamhondiwa8714 22 күн бұрын
Olo chityolayo wakupasani ndalama muli madzi munya
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 23 күн бұрын
Kkkk uchitsilu koma mene mwakulilamo kuyikila kumbuyo mbamva inetso ngati mwadya mabadzi ingokhani mutsatinyase apa
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 23 күн бұрын
Malata, agape khombe mbava zokhazokha iziiii Palibe chanzeru apa mbuzi iiii
@cosmasnkanda8193
@cosmasnkanda8193 23 күн бұрын
Paja nyimbo ija ikumati awa mbuzi anzao ajanso mbuzi onse mbuzi mbuzi mbuzi mbuzi😆
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z 23 күн бұрын
Mwalandila ndalama agalu nose kumeneko mapwala anu mboli zanu mwava
@user-zd5tq9bk9k
@user-zd5tq9bk9k 22 күн бұрын
Ku Malawi andale akuku gwilisani ntchito pogwesa chilungamo
@user-pw1kl3vo5d
@user-pw1kl3vo5d 23 күн бұрын
Ndiye Kuti Inu amabungwe mulibe upangili oimilila Malawi siilan anthu afundo Inu nonse amabungwe mwalandila baz
@user-ld7gw1zb5w
@user-ld7gw1zb5w 23 күн бұрын
Kmt anthu sanawalembele iwowo
@NebieKillion
@NebieKillion 22 күн бұрын
Kkk kma Ada inu Moti ameneyo anagulitsa mogo
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 23 күн бұрын
Akupatsani ndalama inu chithyolayo
@franciscomalola9735
@franciscomalola9735 21 күн бұрын
kuzolowera kuzunza a Malawi bc mbuziinu Loma anthu mukuona ,ndithu inu mulungu akulangeni ndithu ,ndipo tiona
@hendrixmwangata3452
@hendrixmwangata3452 22 күн бұрын
Malawi mammm mwadya zingati mabanzi
@kelvindickson
@kelvindickson 19 күн бұрын
Abambo inu mumuziwe yesu
@rashidadan2533
@rashidadan2533 23 күн бұрын
Not only chithyola banda , start from chakwela and all carbinet need check up
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 23 күн бұрын
Regina chithyola mulungu akulange ndipo udzafa imfa yowawa
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 23 күн бұрын
Ziwanda izi zopusa mene akuoneoa
@user-tl3sg5uf9w
@user-tl3sg5uf9w 22 күн бұрын
Chithyola ndalama ndi zake,nanunso ngati muli ndi ndalama gulani anu magalimoto,
@Silverkaunda-ig5lf
@Silverkaunda-ig5lf 23 күн бұрын
Mboli zanu
@FortyoneHarwa
@FortyoneHarwa 23 күн бұрын
Iwe Malaya ndinzakoyo msatiwopsedze ndinu dzisilu
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 23 күн бұрын
Abilly malata inu ndi akuzomba ndalama zisakupangeni kusekeleza zinthu chifukwa mukudya nawo
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 23 күн бұрын
Kodi inu ndichifukwa chiyani pamene adamangidwa marth chizuma simudalankhule chonchi chokani apa musatinyasepo chifukwa chakuti akupatsani ndalama komatu nawa likubwera mudzayankha zonse izi
@BostonGwazani-hl3bg
@BostonGwazani-hl3bg 23 күн бұрын
Alibe zelu amenewo
@adamkudzala186
@adamkudzala186 23 күн бұрын
Mbudzi za wanthu mwadya ma banzi
@kelvindickson
@kelvindickson 19 күн бұрын
Abambo inu nzelu kulibe akalembele kalata Kwa oona za kuulula chuma iye amagwila kuboma Mesa alembela acb ndicholinga choti afufuze za nkhani , abambo opusa
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 23 күн бұрын
Machende ako iwe Billy malata
@amiduclement2142
@amiduclement2142 23 күн бұрын
Ngati biry marata inu simungamenyere ufuru amarawi mwachepa
@rashiedmanjombe2255
@rashiedmanjombe2255 23 күн бұрын
Malawi sazatheka 😊😊
@anusahjenala1063
@anusahjenala1063 22 күн бұрын
Queen kapalamula wadya bread wa stork pamodzi ndinuyo nonse
@GiftNazira
@GiftNazira 23 күн бұрын
Mwagwirisana agalu iwe
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 23 күн бұрын
Mwagulidwa palibe chezeru chimene ukulankhula ndiwe chisiru
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 22 күн бұрын
Mutamulephela muthalika mwayamba izi amalata
@isaaczuze
@isaaczuze 12 күн бұрын
Kodi iwe malata chakukhuza pamenepa ndi chiyani Iweyo wandila ndalama ndalama kwa chithyola ....chithyola ndi munthu wokuba koopsa ...anaba ndalama za global fund iweyo ukuteteza okuba
@ZaidJafar-kk9be
@ZaidJafar-kk9be 22 күн бұрын
aaaaaaah ine ndimaona ngat uyankhula zanzelu ase machende akoso wava galuiwe
@lenzophiri
@lenzophiri 23 күн бұрын
Osatipusisa nkhondo iyi ndi ya mu MCP kulimbirana mpando wa ku chipani koma simunati muyalusana zowona kkkkk
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 23 күн бұрын
Akuba awa
@user-ob1wx4gf2h
@user-ob1wx4gf2h 23 күн бұрын
Ndrama ndiyoopsa kwabasi
@Imraanjafali
@Imraanjafali 23 күн бұрын
😂😂😂😂😂Inuso mulihulu lodya ndalama mwebwera pa intenent ngati sumunadye bwa
@PraisePhillip
@PraisePhillip 22 күн бұрын
Zosezi ulesi kusafuna kugwila ntchito machende anu nonse plus amene wakupasani ndalamayo
@CoulioZulu
@CoulioZulu 22 күн бұрын
Man ndiinu chitsilu kwambiri cz zomwe mukulankhulazo ndiye utsiluwo kay banzi mwasamwa nayo ife tatopa kuombera manja zazibwanatu
@user-vr5jn8sz5r
@user-vr5jn8sz5r 22 күн бұрын
Zopusa zimene ukuyakhulazo.
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 23 күн бұрын
Akuchita kuonekaratu kuti agulidwa. Zonse zomwe akukamba apa zochita kugwirizana kufuna kuphiphiritsa
@user-xz7jg2eu6r
@user-xz7jg2eu6r 23 күн бұрын
Koma dziko lapansi,ai zisomo, MULUNGU AKUKUONANI NDITHUTU MUKAMAPANGA ZANUZI
@user-jw5rx9ze8k
@user-jw5rx9ze8k 23 күн бұрын
Zidyani ndalamazo basi , dziko ndi lathu koma ndalama ndi zanu.
@FrankBaison
@FrankBaison 23 күн бұрын
Koma njara yamvuta pamalawi ganyu aziwawa😂😂😂 chithyora iwe ukupusitsa akuluakulu
@billalmayer5586
@billalmayer5586 23 күн бұрын
Iweyo ndi galu kwabas
@AllanChabwela
@AllanChabwela 23 күн бұрын
Zankutu,mwalandila ndalama uko ndiye muzikamba zabodza pano?
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 23 күн бұрын
Apumbwa aganyu
@HamzahJafali
@HamzahJafali 21 күн бұрын
Wangokula mutukoma zeru mulibe
@user-xx7mk3fw8v
@user-xx7mk3fw8v 22 күн бұрын
Nyero zanu
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b 22 күн бұрын
Kodi inu mwadya ndalama ingati kod😂😂😂😂
@hackwellkagolo6614
@hackwellkagolo6614 21 күн бұрын
Mkulu ameneyi akuchita kuonetsa mbali 3000%
@user-yi1po9kh2f
@user-yi1po9kh2f 23 күн бұрын
Basi mwamaliza zonunkhazo
@user-xn9ov2fn4i
@user-xn9ov2fn4i 23 күн бұрын
Ndipo Ngati mulungu ndimakhulupilira ine ndiwakufa ayi Zanu zilibwino Koma poti ndiwamoyo dikirani sikale 2025 muzalandila chilango choyenera khulupilirani ndikukambazi
@GiftNazira
@GiftNazira 23 күн бұрын
Notse machende anu dazilo ngati pwala
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 23 күн бұрын
Aaaaaaa osamaopseza mukuba inu anthu akinzidzika kwambiri
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 23 күн бұрын
Ine ndikaona magalasi mumaso ndimaganiza kuti timva zazeru koma ayi. 😂😂
@JailosShadreck
@JailosShadreck 23 күн бұрын
Inetu I thought ayakhula za nzeru. Kodi iwowo akusangalala pamene antu akuvutika ndalama angoba
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i 23 күн бұрын
Kodi inu ndi ma Lawyer???
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 23 күн бұрын
Ukatero watumidwa ndiboma eish koma akulu akulu
@RabsonMulumbe
@RabsonMulumbe 22 күн бұрын
Ife tizisekelera zopepela zikukambidwazi, anthu akuvutika mzikomu mpaka 20 mwana wazaka 24 mmmmm ACB ntchito ndiimeneyo
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo 23 күн бұрын
Iwe ndi chisilu ,mbudzi ya muthu
@user-wn2hm2dc8e
@user-wn2hm2dc8e 23 күн бұрын
Mxieew
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 23 күн бұрын
Makape inu mwalemphela kugwila Chilima
@user-dn6eg1xk7f
@user-dn6eg1xk7f 23 күн бұрын
ayi simukulakhula moveka mani nzeru mulibe fufuzani nkhani ya chisale ndi ameneyu
@HenryTruwa
@HenryTruwa 21 күн бұрын
koma iwe uli mu bagamoyo momuno😴 nyamako wamva ndi wa chifufu wakoyo🏹
@TrysonChimenya4-fm8nt
@TrysonChimenya4-fm8nt 23 күн бұрын
Afufuzidwe nsikanayo mofanana ndi pempho lomwe laikidwu Ku ACB Inu ambadwa kambani ya ma dollaziyo.
@user-ti8ds7iq8z
@user-ti8ds7iq8z 23 күн бұрын
Bakili muluzi tv woyeeee
@jaydee1236
@jaydee1236 23 күн бұрын
Zopoira kwambiri 🙌
@IqrahSikweya
@IqrahSikweya 21 күн бұрын
Galu wachabe chabe ameneu kwabasi
@philemontitusnkhoma7740
@philemontitusnkhoma7740 23 күн бұрын
Siinavute. Mwavuta ndi inu.
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 22 күн бұрын
Mbudzi ya munthu!!!
@FrancisStima-sc7zs
@FrancisStima-sc7zs 23 күн бұрын
Osasiya Kuti amufufuze bwanji mboloyo aise pakholo pa mako chisilu iwe et
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 31 М.
BON KALINDO/ KU MALAWI KUKULOWA ZIGAWENGA🙌🙌🙌
15:16
Они убрались очень быстро!
00:40
Аришнев
Рет қаралды 3,1 МЛН
Универ. 10 лет спустя - ВСЕ СЕРИИ ПОДРЯД
9:04:59
Комедии 2023
Рет қаралды 1,4 МЛН
ИРИНА КАЙРАТОВНА - АЙДАХАР (БЕКА) [MV]
02:51
ГОСТ ENTERTAINMENT
Рет қаралды 1,4 МЛН
Why You Should Always Help Others ❤️
00:40
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 110 МЛН
Wolfram Physics Project: A Discussion with Jim Gates
2:43:04
Wolfram
Рет қаралды 26 М.
ZOMWE ZIKUCHITIKA KU NTCHERU 🙌🙌
24:02
HOT 265
Рет қаралды 16 М.
MPHEPO ZINAYI: CHAKWERA AYIMANSO
48:18
Zodiak Malawi
Рет қаралды 37 М.
A Malawi Lyton Mangochi Musamukhulupilileso - Bon Kalindo
19:43
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 18 М.
Kasungu
2:20
MicroLoan Foundation
Рет қаралды 113 М.
BRIAN BANDA KUCHEZA NDI MAI KALIATI/ ZOMWE ZILI KU MALIRO
16:49
Они убрались очень быстро!
00:40
Аришнев
Рет қаралды 3,1 МЛН