Nkhani Masana | 31 December 2024

  Рет қаралды 13,135

Malawi News Update

Malawi News Update

Күн бұрын

Пікірлер: 29
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 17 күн бұрын
Ulibe manyazi iwe kunkuyu ndiwe galu kobasi ndi chakwela wakoyo 😢😢😢😢
@MaulanaIriyasa
@MaulanaIriyasa 17 күн бұрын
Akumkuyu ndi mbuzi kobasi ndi Chabwino chiti chomwe angaloze uyudi ndi Mr nkhumba ndithu momwe ananela bm TV
@YusufuUsumani
@YusufuUsumani 17 күн бұрын
Kukuyu ndiwe galu wachabechabe machendeako
@IreenMwachande
@IreenMwachande 17 күн бұрын
Koma mmmm mkukuyu mulungu akuyendere mwapadera ndithu mumalawi muno zinthu zomwe munthu amazifuna pamoyo watsiku ndi tsiku izi chakudya mankhwala chipatala zathu katundu wa unlimi akhale osika mtengo iweyo ukanene zinthu zoti munthu sangadye
@giftbanda7690
@giftbanda7690 17 күн бұрын
Musadabwe naye kunkuyu iye ndi Minister of Information Tu paja Nde sikuti angayakhule zokomela aliyese😅😅😅 akupanga zakuntchito kwake or inuyo simungawangoze Abwana anu
@MichaelMpeki
@MichaelMpeki 17 күн бұрын
Iweyo Kumkuyu sindikukumvetsa olo pang'ono, chifukwa zomwe mukuti mwachitazo ine ndiye sindikuziona. Mudangobwera kudzamvetsa ululu a Malawi basi. Ndalama sidayambe yagwa chonchi, katundu sidayambe wakwera mtengo ngati ulamuliro wanu. Mwachidule ndingonena kuti dziko lakukanikani.
@ManesKamtambo
@ManesKamtambo 17 күн бұрын
Akafike bwino
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 17 күн бұрын
Inudi akukuyu ndiachiailu mavuto mwabwelesa malawi ndiinu a mcp pano thumba la chimanga lili pa 70 000 ndiulamulilo wa dpp kunalibe zimenezi athu ini ngoipa kwambili
@JustinMakoka
@JustinMakoka 17 күн бұрын
Kumkuyu wakuba
@AubreyMacdonald-w7f
@AubreyMacdonald-w7f 17 күн бұрын
akukuyu samalakwise ai ayakha bwino km alomwe mwangozolowela kutumwana bas
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 17 күн бұрын
Ine simulomwe koma Kunkuyu ndi garu satana chsru ndpo ndpo ndpo umuuze kuti ndichsru Kunkuyu
@AgrihortSuppliers-s7m
@AgrihortSuppliers-s7m 17 күн бұрын
Kodi nkukuyu umakhala ufitiii kapena chain, kapena chilope chakukwana ,taendani mmidzimu anthu akufa .Tazikhalaniko ndi umulungu .ndalama zitsakutaiseni korona.
@RAJEEFFABDUL
@RAJEEFFABDUL 17 күн бұрын
Akumkuyu mulibe umunthu Kodiak mwapanga chani
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 17 күн бұрын
NYANSI NDI CHIFWAMBA OLO KAPILIKONI WODYOLA KWA CHAKWERA KUTI CHILIMA APHEDWE NDI LAZARUS CHAKWERA NDIPO.CHIKANGAWA ANAKWANIRITSA GANIZO LAKE LOIPA PA MOYO WA CHILIMA.MTSOGOLERI WA UTM.TSONO USI KUCHOTSEDWA KU UTM PALIBE BVUTO.NDIPO AYENERADI kumuchotsa
@StandwellNjoka
@StandwellNjoka 17 күн бұрын
Anene iyeyo zabwino zomwe zilipo ngati sikukonza ziwembu anthu akawazuzula
@jackalview7491
@jackalview7491 17 күн бұрын
Kunkuyu peleka black box
@AnthoniohMazengera
@AnthoniohMazengera 17 күн бұрын
Nduna yopanda zelu iyi akat chabwno zabwno zake zit apanga iwowa mavuto osewa zaz
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 17 күн бұрын
Chipumi cha kunkuyu hi ndiye chizindikilo cha kuyipa ntima ayamikile chani? Kuphedwa kwa chilima ndi anthu 8 aja kudya chitedze ndi nyika ayamikile kukwela kwa katundu ndi mwano omwe chakwela a alankhula za kuti tidzigulitsa matumba awili kugula feteleza chimanga chomwe tilibe ayamikile zimenezo?
@goodwellnyirenda651
@goodwellnyirenda651 17 күн бұрын
Kunkuyu machende ako
@petrokagona1708
@petrokagona1708 17 күн бұрын
Bwana kumkuyu chuma chake chiti chomwe chingapezeke ndikupindulira a Malawi? Mungotichedwetsapo apa. Palibe chabwino kwa common man. Zonsezo mukunenazo zidzangochitira ubwino inuyo osati a Malawi
@GeoffreyEllias-m9l
@GeoffreyEllias-m9l 17 күн бұрын
Mutu ngati panyero pako kunkuyu mboliyako.
@GitfIobodo
@GitfIobodo 17 күн бұрын
Kunkuyu pathako pamako
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 17 күн бұрын
Kunkuyu.ndi.galu
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 17 күн бұрын
BWANAWE MOSES KUNKUYU PAJATU INAKHALA MP WA KUCHILOBWE KUNO.KOMA UNACHITA CHIYANI CHOTUKULA KUCGILOBWE.? ZAKA ZAKO ZONSE 5 ZINALI ZERO PA 100% .IWEYO NDI PHALA BASI LOOANDA MCERE .KU MCP KO PALIBE CHOTHANDIZA UKUMUPATSA CHAKWERA NDI ZERO BASI.
@GoldenNamanguya-b1f
@GoldenNamanguya-b1f 17 күн бұрын
Mesa mumalakhula kuti mukalowa muzathesa mavuto onse
@RAJEEFFABDUL
@RAJEEFFABDUL 17 күн бұрын
Mulibe many axis poyakhula
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 17 күн бұрын
UNAKHALA NOT INAKHALA
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 17 күн бұрын
Iwe kumkuyu ndiwe chitsilu kwambiri padzana umkati mudzasitha zithu lerolino mukuyakhula mozemba chifukwa cha tsogoreli chakwela mbuzi ya tsogoreli devil's zitsilu
Izindaba zesiZulu @19H00 l 17 January 2025
23:01
SABC Izindaba
Рет қаралды 21 М.
Van Reenen Accident | Nquthu Funeral
10:00
AyandaMsweliTV
Рет қаралды 1 М.
Beat Ronaldo, Win $1,000,000
22:45
MrBeast
Рет қаралды 158 МЛН
IL'HAN - Qalqam | Official Music Video
03:17
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 700 М.
Cat mode and a glass of water #family #humor #fun
00:22
Kotiki_Z
Рет қаралды 42 МЛН
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН
Kagame Warn About Coup from Young People, Questioning UN Role in DRC,
16:44
Make Afrika Great
Рет қаралды 2,1 М.
Nkhani Mmawa | 18 JANUARY 2025
26:56
Malawi News Update
Рет қаралды 571
The CAPE COLOUREDS, the TRUE OWNERS of SOUTH AFRICA!!!
5:17
CPPBLTC
Рет қаралды 3,2 М.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BISHOP GILFORD MATONGA | 17 JANUARY 2025
57:50
Malawi News Update
Рет қаралды 9 М.
MK Party Treasurer General, Dr Thanti Mthanti resigns
8:20
SABC News
Рет қаралды 32 М.
ZIKUCHITIKA | 17 JANUARY 2025
1:07:54
Malawi News Update
Рет қаралды 2,4 М.
ANC tackles internal challenges, election losses
11:37
Newzroom Afrika
Рет қаралды 547
Nkhani Madzulo | 17 JANUARY 2025
22:55
Malawi News Update
Рет қаралды 675
Why is Israel accused of being an apartheid state? | Start Here
15:00
Al Jazeera English
Рет қаралды 250 М.
MDYANGU | 18 JANUARY 2025
26:08
Malawi News Update
Рет қаралды 11 М.
Beat Ronaldo, Win $1,000,000
22:45
MrBeast
Рет қаралды 158 МЛН