😅😅😅😅😅😅🙌ife timasinga mbusi ndiye kakolingo ndi chani😂😂😂. Big up mbazada 🔥🔥🔥
@girlmama26511 ай бұрын
Ndi nkhani ya banja osati chibwensi😂😂😂😂basi ntchito kuitana anthu munseu mandota😂😂😂
@preciousmwale3465 Жыл бұрын
Hahahahha koma kankhani ndi wa srs😂😂😂😂😂
@VeronicaFaston-no2no Жыл бұрын
Nice one big up bro
@kettiemituka5766 Жыл бұрын
Chemandota samalapatu paja daily ma scandal samamuthera. Akanawaula koma ndevuzo mwina ukhudzumuke🤣🤣
@saifullahalick407 Жыл бұрын
Chemandota, chemandota, chemandotaaaaa! How many times did I calls you? Futo lili ndi inu zikakuthekerani kamodzi mumangoganiza ngati tsiku lililonse zitheka choncho, aaaah! Kupepera kweni kweni.
@promisemakawa1556 Жыл бұрын
Chemandota ndinu patali, kulakwa kunakuyanjani😅😅, Award ndi yanunso
@TRIZAHBLAIR-hv5kx Жыл бұрын
Mwayamba kuyenda ndi mpen,,, 🤣🤣🤣🤣😂 nde mwati kamatewe
@Afropino1417 Жыл бұрын
Hahahahaha moto unandi 🔥🔥
@cassimbwanali34 Жыл бұрын
Kankhani serious nde amatenga Mandota umatha ase
@KHOOMJIFUMBENKHATA Жыл бұрын
Kkkk koma ma member awa mmakwana guys koma acter zimamuonekela yaaa kkkk
@frankkachigumba187 Жыл бұрын
😅😅😅😅 Nzanga mandota iwe musafera manja mwa akanganiii ziliyaziiii 😀😀😀😀 Nice koma
@aishaayatu8653 Жыл бұрын
Kkkk mpakana mpeni nkazi oti sanakuvomere
@fatsosmart4295 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 eeeeeeeee eeeeh inuyo si level ya munthu😂😂💔💔💔 ena aja akanangozinyanyalatu coz u're th best💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Pitilizan kutipanga entertain ifenso tipitiliza kukupangan support🔥🔥
@eliaschatha1615 Жыл бұрын
Lafisiyu chemandota ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@hamzahsm8240 Жыл бұрын
Number one Che mandota 2023 best comedian again
@MavutoTheu-fj4yw Жыл бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣 koma mandota anapanga mwasiya kuoopa akazi et 😂