No Passport; Tsankho ku Lilongwe; Sugar wakwera

  Рет қаралды 29,818

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

Күн бұрын

Пікірлер: 135
@RiteRoderick
@RiteRoderick 6 ай бұрын
Chakwera ndi aliyense wa MCP Ambuye akukantheni konse muli inuko mukutidzuza koopsa zedi😢😢😢
@ApsChap
@ApsChap 6 ай бұрын
The only voiceful titan Malawi ever have Keep us always updated
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 6 ай бұрын
Chakwera watizuza mokwana, ndipo 2025 ndikutali kobasi.
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 6 ай бұрын
Anthu akummwerafe ndife ogona. ma office ambili asamutsa kupita kulilongwe tikungoyang,anira .lero migration inasekedwa kummwera koma tiliphee
@DanJoe-v6y
@DanJoe-v6y 24 күн бұрын
❤❤ uyuu atikwana president wanj uyuuu
@RobertoKapopo
@RobertoKapopo 6 ай бұрын
Charles nkhombeni ayesere kupanga ine adzafa osadwala
@JaneChimasula
@JaneChimasula 6 ай бұрын
koma abale mulungu atichitire chifundo atichonse mmanja mwa zigawengazi 😢
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 6 ай бұрын
Chakwera why? Ukuzunza amalawi kuba chilichose palibe chochitika pa utsogoleri wako Mulungu akukanthe iweyo ndithu
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
❤❤ inu ndi dolo history is best teacher 🤞
@PaulDaka-dc3re
@PaulDaka-dc3re 6 ай бұрын
Chakwera achoke inu!!!! Koma zitivuta izizi bwanji.
@christophermkhize1991
@christophermkhize1991 6 ай бұрын
Our best journalist ever
@kubengovender6996
@kubengovender6996 6 ай бұрын
More fire 🔥 !!! We need some more teachings brother man!!
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 6 ай бұрын
Nonse a MCP ndi msogoleli wanuyi akukantheni ndipo apeleke milili yochuluka ngat mmene anachitila kwa pharaoh ku Egypt.. Ndipo yaweh mumve ma pemphero a ana anufe. 😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@PatrickGonagona
@PatrickGonagona 6 ай бұрын
Nkhani yomvetsa.cisoni kwambiri, chakwera ndiwoipa mtima ndithu
@RoseChiphiri-ts8jx
@RoseChiphiri-ts8jx 6 ай бұрын
Watching from Israel
@shuraimuwamama2349
@shuraimuwamama2349 6 ай бұрын
A Munro ndikomwe akantera ku ugawenga ndi bibida wawoyo zamanyazi
@ashikalam8616
@ashikalam8616 6 ай бұрын
Boma lomvesa chisoni ili, mmitu muli mamina okha okha ,Go deeper sir ,achewa osaganiza awa.
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 6 ай бұрын
Eish this party mcp must go otherwise people will be tiered and use power to remove them and it will be blood shad guys we are watching my friend
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 6 ай бұрын
Zolandana malo ndikuma wopsezanazo ifeso tinaziwona,
@IqrahOmar-x6w
@IqrahOmar-x6w 6 ай бұрын
Koma bwana inuyo mulungu anakudalitsan
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 6 ай бұрын
Big up brother always with you
@OrackPhili
@OrackPhili 6 ай бұрын
We love you brother all the best
@sharifmussah5307
@sharifmussah5307 6 ай бұрын
Chitsilu cha president
@KenaniSanudie
@KenaniSanudie 6 ай бұрын
Mwawona guys m'mene zikukhalira 😢😢😢
@honourablesc97tv
@honourablesc97tv 6 ай бұрын
Wina ndiye azikati MCP Boma 2025 a usawi, olo atandipopera Doom mkamwa I will never vote for MCP 4 years iyi yandiwonetsera zilango personally
@tingo3155
@tingo3155 6 ай бұрын
That is how Nyau people live if your not part of Nyau they do hate you, apart Nyau ndi ufiti goes together
@MwenyeCheNsoma-gb2yz
@MwenyeCheNsoma-gb2yz 6 ай бұрын
Hope Mr. President His Excellency Lazarus Chakwera is following this man. A single a advise to Mr. President "samalani ndi anyamata amene akuzungulirani otherwise I personally love you Mr. President
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 6 ай бұрын
That's how idiots and un Godly and materialistic,lazy people speak
@PatrickowenKadammanja
@PatrickowenKadammanja 6 ай бұрын
Guys tiyeni pa table,tonse Alliance ikatha mcp mphavu zathanso chifukwa zipani zinazi mutonse Alliance tizipanga dicampaign,olo kuti chilima amulore kuyimilira mcp yathabe,kulibe kopulumukira achina suleman sangapulumutse popeza bwino computer ndiye chilima ,kodi mcp pano ndi doors uli ndi mphavu ndichani,dpp ikangokumbutsa mitengo ya katundu straight boma
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 6 ай бұрын
Apm my vote
@ElizahMadi
@ElizahMadi 6 ай бұрын
Zimayamba chonchi ,nkhondo siyiyamba ndi fumbi
@innocentchirombo2073
@innocentchirombo2073 6 ай бұрын
Ipondeni fadah ❤❤
@JohnChipeta-wg9cf
@JohnChipeta-wg9cf 6 ай бұрын
Anthuwa ndi abuli
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 6 ай бұрын
Pallibe chamu yaya pasi panthakayi
@LukaAron-el5qh
@LukaAron-el5qh 6 ай бұрын
Koma koma chakwera zoona nyasi zimenezi zikuchitika iweyo kukhala wantchito wathu koma kukapanga n Khanza zoterezi iwe kukhala busa kodi udali busa wanji
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 6 ай бұрын
Nonse azitsogoleli a mcp Mulungu akuyendereni, mukunzuza amalawi
@WedsonVinkhumbo-m2n
@WedsonVinkhumbo-m2n 6 ай бұрын
Mmmmm ambuye amukathe chakwela
@DonaldPonda-p2q
@DonaldPonda-p2q 6 ай бұрын
Chakwera malawi sanatuluke kuntumbo kwa monica kuti uzingopanga zomwe ukufuna pita sopano ukalamulire kuntumbo kwa mako
@farmupmalawi
@farmupmalawi 6 ай бұрын
😂😂😂😂
@promisegeorge5902
@promisegeorge5902 6 ай бұрын
Zoona zonse timanva kwa inu bro
@LawrenceMsango
@LawrenceMsango 6 ай бұрын
Koma zikuchitikazi ndichibwana zikoli lifika ponunkha
@HendryChiwezo
@HendryChiwezo 6 ай бұрын
Pena anthu akumwela amalakhula molokwa kodi mudamuva kalindo akamalakhula amafuna wina achite zina amationela kwambiri ngati zikutero ndizabwino😊
@ShadreckKaleso
@ShadreckKaleso 6 ай бұрын
Bg inu timasowa pokuikani mumatidziwitsa zinsisi zikuluzikulu😎
@CalvinKhumalombalule
@CalvinKhumalombalule 6 ай бұрын
Big Boss on time
@starlonJames-qr4xl
@starlonJames-qr4xl 6 ай бұрын
prz ndipepheko nkhani ngati zimenezi munthuwankulu mudziwatumoziko mamelecani cholinga azidziwa kt kumalawi kukuchitika zinthu zangat izi
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 6 ай бұрын
chakwera ndi gulu lake nywana ya mao
@FrancisKamwendo-k7j
@FrancisKamwendo-k7j 6 ай бұрын
Eya ndizowonad bakili muluz TV imakambad zowona ndipo izizi zikuchitikad
@Richardfolopes
@Richardfolopes 6 ай бұрын
Zovuta Malawi wanga
@marryphili5419
@marryphili5419 6 ай бұрын
Ndipo tikuwona kuchedwa 2025 tikufuna adadi abwerere muboma mwina sugar, fertilize , makhwara muzipatara ndi ma passport zingabaerereso muchimaki zamukanika chakwera ndi mwana Kwa basi anangolowa mu boma ndi cholinga chofuna kulemera basi osati kutukura dziko eish
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 6 ай бұрын
Malawi eish
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera 6 ай бұрын
Mabi amenewo ayelekeze kumupanga wachiyao tiwone ngati enawo sayenda wothamanga dzikomuno
@ThokoMaggie
@ThokoMaggie 5 ай бұрын
Mmmmm km chakwela mulungu amuone
@lloydjeremiah2250
@lloydjeremiah2250 6 ай бұрын
mmmm kma malawi wafika poola
@ChimwemweMnthali-l5n
@ChimwemweMnthali-l5n 6 ай бұрын
Azingidwe pa camping uyu
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 6 ай бұрын
Tinadzilakwisa tokha amalawi busa sangakhale plasident busa ntchito yake ndi ya church
@maulidisaidibugudadi4091
@maulidisaidibugudadi4091 6 ай бұрын
m'busa wa fake uyo
@BenissoneErnesto-eh6zs
@BenissoneErnesto-eh6zs 6 ай бұрын
The best bakılı muluzi tv zimene zikuchita boma lachakwera ngati tinalakwa kuwavotera aziwa ndimulungu koma chimene angaziwe Pazıko pano palibe chisatha watching from Mozambique koma kwathu ndikumulanje
@HopefulCoralReef-tx4vx
@HopefulCoralReef-tx4vx 6 ай бұрын
Zoona zake man nthawi izakwana
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga 6 ай бұрын
Ndimakunyadirani brother ❤
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 6 ай бұрын
Napamtumbo namachende namapwala amene akukweza zinthu.
@raytavares2256
@raytavares2256 6 ай бұрын
MCP woye boma labwino la his excellency president wamuyaya president Lazurus Chakwera wamuyaya wathu. Ifee kuno kunyadira president wathu ndipo NGWAZI wamuyaya president wachikondi ndipo wokonda anthu
@GeorgeMphale-n8q
@GeorgeMphale-n8q 6 ай бұрын
Ine ndidzamukhulupilila adzakambe za buleya lule ndi masambuka osati izi akukambazi
@MadaalaYare
@MadaalaYare 6 ай бұрын
Chakwela ndi fiti azawona 2025
@MemoryNkolesya
@MemoryNkolesya 6 ай бұрын
Tikumana nextyear September
@AndrewInnocent-he8gs
@AndrewInnocent-he8gs 6 ай бұрын
Ine ndalandidwaso ndi gululomweli ku mchesi mcp group
@MercyChipezayani
@MercyChipezayani 6 ай бұрын
Amalawi amene adakavota 2020 ada panga mistake yaikulu
@zeckbmalawi8017
@zeckbmalawi8017 6 ай бұрын
Our boss
@BonomaliIman
@BonomaliIman 6 ай бұрын
Ngati zilinchonche anyamata a MCP musamale mangochi ikudikila anyamata a MCP musadilidwa matumbo chakwera musamale in MH
@GiftHaward
@GiftHaward 5 ай бұрын
Boma la malawi likuganiza bwanji munthu uzichoka ku blantyre ku zomba ku mangochi kupita ku lilongwe kukapanga passport why malawi
@ShadreckKaleso
@ShadreckKaleso 6 ай бұрын
Cholandila katundu wa anthu ndichiyani Mulungu akukantheni inu athakati
@MisheckAselo
@MisheckAselo 6 ай бұрын
Mavuto adakalipo 2025 kuchedwa ndithu 🤔
@maulidisaidibugudadi4091
@maulidisaidibugudadi4091 6 ай бұрын
chakwera ngat ukutumidwa ni Benjamin Netanyahu akuphweteketsa
@HamzaAyame-ch3et
@HamzaAyame-ch3et 6 ай бұрын
Achakwera ayamba zamanyi
@abdullahibrahimbacqri3628
@abdullahibrahimbacqri3628 6 ай бұрын
Osewa azalandidwe chuma chawo chizabwerere boma anthuwa akutibera misokho ndithu
@JohnChipeta-wg9cf
@JohnChipeta-wg9cf 6 ай бұрын
Koma achakwera eeeeee ayi ndithu pepan tapota nanu
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 6 ай бұрын
Ndimakunyadila aisle
@abisalomchunga6695
@abisalomchunga6695 6 ай бұрын
Good work boss
@AleksaWilliams
@AleksaWilliams 6 ай бұрын
Mmmmmh likupita kt dzikoli
@isaacbwanali4699
@isaacbwanali4699 6 ай бұрын
Boma ili ndiye latikwanatu
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 6 ай бұрын
Good Message ❤
@isaacmidesa
@isaacmidesa 6 ай бұрын
Ndipotu nkhani yaku 25 yokhayo ndizoona palibepo zabodza apa
@RiteRoderick
@RiteRoderick 6 ай бұрын
APM my vote ❤❤❤❤❤❤
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 6 ай бұрын
💙💙💙💙💙
@user-Grant260
@user-Grant260 6 ай бұрын
Watching from Venezuela in Caracas 🇻🇪
@ceptermicray
@ceptermicray 6 ай бұрын
Nde ufuna ife titani?🤨
@user-Grant260
@user-Grant260 6 ай бұрын
@@ceptermicray Do you want an answer from me ?
@FrancisDay-br7xb
@FrancisDay-br7xb 6 ай бұрын
Amalawi tieni tikhale nao anao
@ephraimmagomondosoko2775
@ephraimmagomondosoko2775 6 ай бұрын
I'm sorry with this nyau regime 😢😢
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 6 ай бұрын
Asatana adzipita awa basi
@EnerstManess
@EnerstManess 6 ай бұрын
Koma nkhaza zanyanya abale kugula malo sichinthu chamasewela
@MoosaSame
@MoosaSame 6 ай бұрын
Chakwera n his government all them they're theaf
@Fatima-li5rg
@Fatima-li5rg 6 ай бұрын
Tangomuthilura tameki amalawi Inu ukudandawula
@AbdulrasheedSaddam
@AbdulrasheedSaddam 6 ай бұрын
Keep pushing bro...
@FrankBanda-c3e
@FrankBanda-c3e 6 ай бұрын
Mulungu amuwonjezere mtendere wosatha
@Dee-h7c
@Dee-h7c 6 ай бұрын
So sad 😢😢 our malawi
@GenialaChalera
@GenialaChalera 6 ай бұрын
Akulu muli ndi bodza
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 6 ай бұрын
Eeeeee koma boma ili liyambisa nkhondo ndithi
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 6 ай бұрын
Chakwela mbudzi ya Munthu
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 6 ай бұрын
chakwera maso ngati panyelo pa bakha
@jameschipula4475
@jameschipula4475 6 ай бұрын
From Johannesburg Kempton park
@timothychilwe5231
@timothychilwe5231 6 ай бұрын
Kodi asilikari alikuti osatenga boma
@usumanidaudi
@usumanidaudi 6 ай бұрын
Nangati yothamangisana asamare nawoso achewa zigawo zina za kumwera tizakhapa paja mangochi sigonja
@kantionsankhulani
@kantionsankhulani 6 ай бұрын
inu mudzangosowa ❤
@ChembeSolomon
@ChembeSolomon 6 ай бұрын
Never give up bro ❤
@rashidlamos3403
@rashidlamos3403 6 ай бұрын
Koma zovuta kwambili eeeeee
@Alabu-g6i
@Alabu-g6i 6 ай бұрын
Timakunyadila man kwambiri
@isaacschamatwa3596
@isaacschamatwa3596 6 ай бұрын
Mavuto ku Malawi adzavuta kuti athe
@kasupeowenpaul
@kasupeowenpaul 6 ай бұрын
Koma amalawi tinafasa mopusa sure
Chizolowezi cha namkholowa chinazulitsa mbatata. Good example from America
11:23
SILVESTER NAMIWA AJOINA NAWO PAMA DEMOSTRATIONS AMA LAWYER
52:02
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 14 М.
Real Man relocate to Remote Controlled Car 👨🏻➡️🚙🕹️ #builderc
00:24
Players vs Pitch 🤯
00:26
LE FOOT EN VIDÉO
Рет қаралды 112 МЛН
Julius Malema meets Botswana President Duma Boko at Inauguration.
5:12
Daily Updates ZA
Рет қаралды 66 М.
UNITED SHOWBIZ WITH EMPRESS GIFTY  09/11/24
UTV Ghana Online
Рет қаралды 4,1 М.
Passport Scandal; Bendulo-Gate; Bango-Gate. Kuba kwaphweka ndi Chakwera.
11:48