NORMAN CHISALE LERO WAUGEYASO MTUDZU KU DPP RALLY IN LILONGWE, AWA NDI AKATUNDU OMANGA NDI MAWAYA

  Рет қаралды 34,008

AM TV MALAWI

AM TV MALAWI

Күн бұрын

Пікірлер: 68
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb 13 күн бұрын
Future minister of Defense, Honourable Chisale...
@dreetosh8502
@dreetosh8502 13 күн бұрын
We must Praised God almighty always in the name of Jesus Christ Amen
@RosinaPatel
@RosinaPatel 14 күн бұрын
APM my vote
@DoreenFriday-b3o
@DoreenFriday-b3o 14 күн бұрын
My vote
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 14 күн бұрын
APM MY VOTE 💙💙💙💙 ndpo palibeso peter yemweyo
@ALIEMUHAMMAD-yb4lr
@ALIEMUHAMMAD-yb4lr 11 күн бұрын
Chikangawa wagwa nayo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@AmisiDytoni
@AmisiDytoni 14 күн бұрын
Ndimakunyadilan Mr chisale
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s 14 күн бұрын
Achinyamata nonse ku opposition gwirizanani kuti ziyende bwino APM ndi amuna pa utsogoleri,Ntandire kudzakhale Technical Colleges.
@Jonas-v8y
@Jonas-v8y 14 күн бұрын
Boma iilooooooooo, APM 2025 bomaaaa, APM my vote
@MichaelPotan-y5y
@MichaelPotan-y5y 14 күн бұрын
Chisale uyu ndi pangolin waboma #Hervey duty
@vintefelisbertoRosário
@vintefelisbertoRosário 10 күн бұрын
Malawi viva
@VincentBorrah-f9z
@VincentBorrah-f9z 14 күн бұрын
Adha chisale iwe umatha
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 13 күн бұрын
Ulemu wanu big man
@MadaMw-j3u
@MadaMw-j3u 13 күн бұрын
I once thought APM will win but mmm unless they partner with someone strong
@dreetosh8502
@dreetosh8502 13 күн бұрын
We need changes
@TinasheKamanga-p9c
@TinasheKamanga-p9c 14 күн бұрын
Long live adad my own trump❤❤❤💙💙💙
@jonathanchigundeni-i3r
@jonathanchigundeni-i3r 13 күн бұрын
Keep on
@MenfordZimba
@MenfordZimba 12 күн бұрын
😅 police imeneyo inalipo nthawi ya DPP, ndiye apa mukulubwalubwa zichani??
@LuwizaChika
@LuwizaChika 14 күн бұрын
😂😂😂😂 yomweyo bwela bwela my vote Dpp oyeee 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 14 күн бұрын
Boma ilo 🔥🔥🔥🔥
@TisopeMkozo-h8t
@TisopeMkozo-h8t 14 күн бұрын
Apm my Vote
@ValerieSteward-m8i
@ValerieSteward-m8i 13 күн бұрын
My vote Dpp
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 14 күн бұрын
Osaopa osatopa osafooka comrade
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 13 күн бұрын
Amuna amenewo omanga ndi mawadi.
@fabianogama5447
@fabianogama5447 13 күн бұрын
Malayawo alembedwa kuti chani?😂😂😂
@ENOCKSEVISON
@ENOCKSEVISON 14 күн бұрын
Chisare ari ndi mkwiyo, fundo aribe
@TisopeMkozo-h8t
@TisopeMkozo-h8t 14 күн бұрын
Chisale asakhale ndi mfundo nanga Iweyo wasiilanji kulankhuea za mfundo
@PrinceNyirenda-w8d
@PrinceNyirenda-w8d 14 күн бұрын
Norman Chisale m'matiyimilira ku Dpp .Dpp 2025 nd Boma kale osanamizana abale
@LastonKuseka
@LastonKuseka 14 күн бұрын
DPP yan ga
@GeraldChilundu-e3v
@GeraldChilundu-e3v 13 күн бұрын
Vote yanga APM. DPP woyeeeee
@JamesGondwe-q7w
@JamesGondwe-q7w 13 күн бұрын
Mulibe mfundo inu Peter anali kale pampando womwewo tikudziwa kale mesa ndalama amadya ndi inu Achisale
@WilliamMisoya-g3z
@WilliamMisoya-g3z 14 күн бұрын
❤❤❤dp
@pauljosephmakaula6835
@pauljosephmakaula6835 14 күн бұрын
Zaubusazo AYIIIII...Zitayeni za church zisakukhuzeni
@TiyamikeSibale
@TiyamikeSibale 9 күн бұрын
Chisale umakwanira ndipo ndli pambuyo panu
@Jonas-v8y
@Jonas-v8y 14 күн бұрын
Wina aziwona pa September pano, pompo-pompo kumangidwa basi palibe kunva chisoni
@AchinaKellz
@AchinaKellz 14 күн бұрын
auzeni makapewo ana anawalakwira kkkkkkkkk gogo pa I'd
@GiftZuze-ge1ne
@GiftZuze-ge1ne 14 күн бұрын
Tikupepha mumwakwanisa kulamula bomanu chonde 1Boma palokha lizipanga business ulime wathililayo athu ena amena angakwanise asengere makapena awo awo arembe antchito bomaso lisengere makapani awo ena ngati omweyo ine aziona kodi uku tingapengako chn kuli kwana kuli malo okongara maganiko kuzibwara athu akunja malo ochuluka ndi abweno zikoratu 2 ku ojezara mphavu zamagesa athu ku wamanger manyumba amena sangakwanisa wa boma kumamudura akukwara ntchito pakapani kumamudula magesa pose pose mukhara mwabwezeresa chirengegwe chifukwa athu ambire azigura magese misenje yatu kuimaga thaka osamakokoloka ndichito yazeka ziweli oro dzitat 3 miseu yathu ikhare wabweno ndi yochuluka magari moto a police kusitha komaso kuwachilukesa a police a traffic athu azigwara chito yachilungamo komaso magaremoto abweno osati yomweyo police yomweyo traffic ay zipatara zathu zomwezo zomwezo kumagozesitha maina magani .zanu zamakono mamgwara pose pose ogwara ntchito abweno ... Ndipo bomalimenelo silizachoka paka paka
@VickMuluwera
@VickMuluwera 13 күн бұрын
Mavote kuti bweeee guys inu palibetso
@VickMuluwera
@VickMuluwera 13 күн бұрын
Achisale nduna ya zanyamata 2025 16th September pano
@MemoryZiyaya
@MemoryZiyaya 14 күн бұрын
🧢🧢🧢🧢🧢💙💙💙
@wesleykamwendo5063
@wesleykamwendo5063 14 күн бұрын
DPP ndi MCP zanu ndi zimodzi musaoneke ngat abwino chifukwa muli Ku opposition inunso mukapanga zomwezo nthawi yanu ija
@MonijaKataika
@MonijaKataika 14 күн бұрын
Koma soya pieces timagula 50kwacha..ndipo timadya by choice not chance..Lero 600 bola tibwerere ku DPP komweko
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka 14 күн бұрын
Bola dpp km mcp ili we si aaaa mudzisiyanitsa zithu zina
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w 14 күн бұрын
Boma.boma.add❤
@InnocentMtafya-c6b
@InnocentMtafya-c6b 13 күн бұрын
This is what you were doing, no wonder you are preaching ,osalembetsa ana kutyolo,mulanje ndi phalombe ana a 13 to 17 years old amavota chaka ndi chaka we have lomwe friends who boats about it....
@AndileZondi-b1u
@AndileZondi-b1u 14 күн бұрын
Amalawi tipwetekedwa dihandu monga hawa
@masianobrighton
@masianobrighton 14 күн бұрын
Akumva kuwawa uyu wachalira kubwezera uyu kodi tizikhalira tit for tat za zii Kuzunza agogo kufuna kumuuser
@ModestaMlamba
@ModestaMlamba 14 күн бұрын
Lazalo pawulendo
@EvanceMwambakuluEva
@EvanceMwambakuluEva 14 күн бұрын
Mbamva iyi ikufuna izidzamuberanso Muntharika. Guard mumakhala ndi magalimoto mpaka 40 chonsecho anali Londa kungoti Ku DPP kuli Nkhumba zokhazokha. Komatu sizitheka kutha Kwa DPP kuli pa September. Wat u should know is dat: Bingu ndiye adali mwini wake wa Dpp kufa Kwa Bingu Dpp idathera pompo. Peter sangalamulirenso dziko lino ngati mukuganiza zimenezo mukutaya nthawi. Ife sitingalore kuti Londa ndi Getrude plus Talandira kuti azidzalamulira dziko lino mwina azidzalamulira Ku Thyolo koma Kuno Ku Central Region sitingalore zopusazo.
@IssacMateyo
@IssacMateyo 14 күн бұрын
Koma inu kkkkk😂😂😂😂
@IssacMateyo
@IssacMateyo 14 күн бұрын
Koma inu kkkkk😂😂😂😂
@UseniMailosi
@UseniMailosi 14 күн бұрын
Tachuluka amene tikufutika chifukwa Cha boma lanuli
@PeterKainga-e3h
@PeterKainga-e3h 14 күн бұрын
Komatu ine ndikazapeza mwayi wayankhula ndi Brian Banda iiiiiiiii nzamuuza zakukhosi
@GiftZuze-ge1ne
@GiftZuze-ge1ne 14 күн бұрын
Chaka chinu muwina koma ife tikufuna mukalowa mutikozera ziko rathu osati muzikozera chuma chinu. chonde, ziko ratu lizioneka lokongala lachisamalilo miseu,misika zomanga zabamwaba nanga zaka zose muzingo oneka mukafuna ma vot atu sichocho inuyo nokha makamabwera kupangesa sokhano muziva kukoma ndi mise yapamwamba misika yathu yosama libwa bweno yomangigwa bweno koma malo opangara sokhano Chaka choyandi kira vot.ndi omweo zomanga zaka zosazewika bweno .bwanji kd ziko rathu?? bwana mukalowa mutimangare ziko rathu chonde bwana tisamasirir kupita kunja bwana
@duncainjimmy
@duncainjimmy 13 күн бұрын
Komatu please musamathe Mawu, 200 kwacha passport?
@eliasgondwe
@eliasgondwe 14 күн бұрын
Ndiyetu a Chaponda sakufunika pa utsogoleri
@eliasgondwe
@eliasgondwe 14 күн бұрын
Gangata anthu awuzeni zochita palibe Chimene mukuyankhula , mimba ya Chisale yatani, nkhani anthu adzakuvoteleni chifukwa Chiani?
@AmoTiamo
@AmoTiamo 14 күн бұрын
Comment ya chikangawa kuzolowera kuthuzula zithupya
@TisopeMkozo-h8t
@TisopeMkozo-h8t 14 күн бұрын
Wa Mcp iwe nthawi yako yatha
@kenmasta
@kenmasta 14 күн бұрын
Tiwavotera popanda chifukwa
@eliasgondwe
@eliasgondwe 14 күн бұрын
@kenmasta kkkkk, musayiwale kuti fuel adzakhala pa 650prliter, pomwe ku Tanzania ndi 3000malawi kwacha bola Dpp
@moyowrobert3331
@moyowrobert3331 13 күн бұрын
❤❤❤😂❤❤❤❤
@briannkhata6111
@briannkhata6111 14 күн бұрын
😂😂
@CharlieChirwa
@CharlieChirwa 14 күн бұрын
Zoonadi chisale sakupanga ma licence
@IssacMateyo
@IssacMateyo 14 күн бұрын
Palibe ukufuna udzikabaso mudzina lamuthalika galu iwe chisale
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 14 күн бұрын
Km muzina la chakwera eti
@Jonas-v8y
@Jonas-v8y 14 күн бұрын
Wina aziwona pa September pano, pompo-pompo kumangidwa basi palibe kunva chisoni
БОЙКАЛАР| bayGUYS | 27 шығарылым
28:49
bayGUYS
Рет қаралды 1,1 МЛН
Every team from the Bracket Buster! Who ya got? 😏
0:53
FailArmy Shorts
Рет қаралды 13 МЛН
OCCUPIED #shortssprintbrasil
0:37
Natan por Aí
Рет қаралды 131 МЛН
УЛИЧНЫЕ МУЗЫКАНТЫ В СОЧИ 🤘🏻
0:33
РОК ЗАВОД
Рет қаралды 7 МЛН
Orlando Pirate VS Kaizer Chiefs - Betway Premiership match 01 February 2025
17:08
БОЙКАЛАР| bayGUYS | 27 шығарылым
28:49
bayGUYS
Рет қаралды 1,1 МЛН