NSOKHANO WA UDF KU BLANTYRE 🙌🙌🙌🙌

  Рет қаралды 19,148

HOT 265

HOT 265

19 күн бұрын

Пікірлер: 160
@IsmailNdemanga
@IsmailNdemanga 17 күн бұрын
Guys chonde asakupusiseni amene akuyankhulayo ndiwa mcp akufuna akudaniseni, becareful munthu wa udf sanganyoze DPP never, ife tonse a udf tikusapoter dpp+udf💪🤝🌽
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 17 күн бұрын
A udf musayambe manyi amenewo inuyo mungapikisane ndi dpp timakukodani inuyo a udf ndi dpp koma mukayamba kunena za dpp muyaluka komanso kapeni mulephela inuyo muzinyoza mcp koma wosati dpp mukhale ndi manyazi
@marryphili5419
@marryphili5419 17 күн бұрын
Kagwere wuko iwe wusatinyase ife DPP woyeeee ♥️♥️♥️ no fondo
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 16 күн бұрын
Ndipo kwambiri
@user-lw9su5om5z
@user-lw9su5om5z 16 күн бұрын
Mapwala opanda nzeru mboli yakoso
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 17 күн бұрын
Osusa kumanyozanaso iiiii sithani kaganizidwe,anthu ake ati poti ndikugoona mdima waphiri mukhalike ndi ulemu, respect to each other
@JaneJames-rb6js
@JaneJames-rb6js 17 күн бұрын
Akunama awa Apm my vote
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 16 күн бұрын
Ndipo kwambiri
@jaydee1236
@jaydee1236 16 күн бұрын
Mwayamba kunyozananso nanga
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 15 күн бұрын
Awa ndie masanje awa😂😂😂😂😂wait for DPP the greatest party
@user-kb7gw3tu7r
@user-kb7gw3tu7r 12 күн бұрын
Dpp machine apa palibe chikuveka😂
@SullyBartsony
@SullyBartsony 16 күн бұрын
Tangopangani sonkhano wanuwo ife ngati sitinaziwe sonkano wanuwo
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i 17 күн бұрын
Ife tikufunanilani mafunso abwino A UDF ndi DPP basi
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 14 күн бұрын
Wakufunsa Ndani Fabiano
@zakeskamoga1291
@zakeskamoga1291 17 күн бұрын
Wandinyasatu uyu
@SophieBanda-el8ri
@SophieBanda-el8ri 15 күн бұрын
Anthu ake amakhala kuti ndi omwewotu
@user-ix7pb6hk2w
@user-ix7pb6hk2w 16 күн бұрын
Uchisilu nde umenewo
@user-xp9zd1wk8g
@user-xp9zd1wk8g 17 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂km awawa ase ine sindikuwona gulu apa inuyo ndi ana pa DPP
@user-kh9tw1xx8f
@user-kh9tw1xx8f 17 күн бұрын
Nsokhano wake ocitikila pa khomo pa munthu ? Kkkkkkkkkk piani ki njamba akakuikeni pa sidelo
@LucySandram-mo6uq
@LucySandram-mo6uq 16 күн бұрын
Hedeeee iziso ndiye ziti haaaaa muchedwa nazo iziiiii
@GrecianWyson
@GrecianWyson 17 күн бұрын
Ine nganganga DPP. UDF borani Koma si MCP
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y 17 күн бұрын
Kkkkkk udf mungovomereza nthawi yanu inatha
@WilliamSitolo
@WilliamSitolo 17 күн бұрын
Kodi chindere chimenechi mchakuti
@chikondiSamika
@chikondiSamika 16 күн бұрын
Inu achipongwe eti
@talentfreshfoods4607
@talentfreshfoods4607 13 күн бұрын
Anthu ake ndiye atiwo?
@owenskabazanechiumia3543
@owenskabazanechiumia3543 17 күн бұрын
Tizinena zowona a UDF simungapose Anthu amene anali ku Msonkhano wa DPP
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 16 күн бұрын
Ndipo zoona tu kkk
@Slyvia-uu3wc
@Slyvia-uu3wc 16 күн бұрын
Awa sangawine angowononga ndalama zawo,,
@patricksamson4852
@patricksamson4852 16 күн бұрын
Inu ndi achisiru
@user-zt7hy5lh4r
@user-zt7hy5lh4r 16 күн бұрын
Gulu lake liti sopano abale, just let be united and take down this nonsense government mcp
@user-qe2lz7mx7u
@user-qe2lz7mx7u 16 күн бұрын
There is no leadership awa palibe chimene angasinthe akungolankhula mayi nasibeko
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 14 күн бұрын
Anthu ake ati😂😂😂😂
@user-sr6hc3pv8o
@user-sr6hc3pv8o 16 күн бұрын
APM anthu musegukanaye mmimbatu😅
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 16 күн бұрын
Akunama UDF singanyoze Apm ndi wachipani cha Allience
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 15 күн бұрын
Panalibe anthu apaaa, koma agwilizane zipani zosutsa kuti achose mbuzi ija chakwera
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 17 күн бұрын
Iwe ndiwe galu mbuzi yamunthu zaziii
@ElvisSpesho
@ElvisSpesho 17 күн бұрын
Chipani Changa UDF 2026🔥🔥🔥
@user-hk3hg1to4e
@user-hk3hg1to4e 17 күн бұрын
Please tikufuna fundo zotchakuka osati zonyozazo ayi
@JIMMYWATHONJE
@JIMMYWATHONJE 16 күн бұрын
KOdi nanga ndimpikisano nanga?
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 16 күн бұрын
Kkk koma amayi awa anakoza, akuti nsalu landilani muike pa toilet
@AllanMafelo
@AllanMafelo 17 күн бұрын
Mmm waboza iwe ungonena zulo anthu amachita kusowa poponda
@GreshamKadzembe-tn8cq
@GreshamKadzembe-tn8cq 17 күн бұрын
Yes koma mumakawatenga kutali, sono awawa ndi amu brantyre momo
@vincentbulirani
@vincentbulirani 17 күн бұрын
Zamanyazi UDF mukanakhala ena mukanangozolika ndi manyazi mwa kachetechete
@user-ti4yu6ob1e
@user-ti4yu6ob1e 17 күн бұрын
2025 amene Ali ndi mwana agwilitse🙉
@davidjames679
@davidjames679 16 күн бұрын
msonkhano ngat birthday ukuyankhulawe sunaone kumjamba
@noahtsamdoka1172
@noahtsamdoka1172 16 күн бұрын
Anthu ache ambiri under 17 achuluka 😂😂😂
@loveruthphiri6645
@loveruthphiri6645 17 күн бұрын
Mukupenga
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 17 күн бұрын
Koma iwe ukuziwa chan
@CharlesMillion-bt9su
@CharlesMillion-bt9su 15 күн бұрын
A udf ndi DPP pangani alaance
@user-vp8mr5ot7q
@user-vp8mr5ot7q 17 күн бұрын
Akaka jabalí kachinamwali osati nsonkhano wachipani
@ishmaeldama8906
@ishmaeldama8906 17 күн бұрын
Mbuzi za anthu izi
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i 16 күн бұрын
Wakhuta ambuye ntengeni uyu
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 17 күн бұрын
Dpp singalowezo mboma chifukwa mulandu owukira chipani cha UDF ithink ukadali ku court 😊
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h 15 күн бұрын
Inu khalani limoz ndi dpp panokha sizingatheke
@mollymasangano473
@mollymasangano473 17 күн бұрын
I think the best way muwauze a Malawi chomwe mwapangira nsokhanowo osati mudzinyoza a DPP,DPP pa mnjamba inali Moto,AMP anachoka ku nyumbakwawo kukafika ku Mnjamba anatenga five hours because of MORE FANS,.
@JohminMatick
@JohminMatick 16 күн бұрын
Aaaaaaa zachamba basi😂😂😂😂 anthu akunenawo alikuti apaa? UDF ili under kwa APM
@user-gw4dt9hq9l
@user-gw4dt9hq9l 17 күн бұрын
Ukumama aise palibe anthu pamenepo
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di 16 күн бұрын
Anthu smbiri koma osaipasa moto 🤔. 2025 tiona zinthu
@mafukenimasangwi5487
@mafukenimasangwi5487 12 күн бұрын
Akulu koma ifetu sitikuonap anthu apa kkkkk
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 17 күн бұрын
Kulankhula mwamzeru mama.. Kumanga osati kupasula..
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 17 күн бұрын
Pali anthu apa?🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@AnishaMoosa-ej7yr
@AnishaMoosa-ej7yr 17 күн бұрын
Thank you
@usumanidaudi
@usumanidaudi 17 күн бұрын
Iweyo kuyambira rero usamabwerese nkhani zanu ndinu opandaso zeru
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s 17 күн бұрын
Awa mutu wao sumagwira mukulimbana nokhanokha mbuzi
@RodrickAustin
@RodrickAustin 17 күн бұрын
Akunama ameneyo wanyanayo ameneyo
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 17 күн бұрын
Zangolowa agents bs koma kunena muchoona APA palibe anthu anthu akupeza pata oyala miyendo uja unali wamunthu wamkulu simungafanane naye mwachepa DPP yemweyo
@user-nr2gs3qy6v
@user-nr2gs3qy6v 16 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Pali anthu pamenepo and inu mukhala ngati ndinu a mcp osati udf
@GiftMathewe
@GiftMathewe 17 күн бұрын
Dalezatundu wanjizimene azathu opepelazimenezo
@honourablemcgregorysc97tv
@honourablemcgregorysc97tv 16 күн бұрын
Aaaaa UDF mungozivuta inu, nthawi yanu idatha kale, osamanyoza chipani cholamura bwanji
@tshidikepadisa3148
@tshidikepadisa3148 16 күн бұрын
akulu inu mzeru zakusowani usamaname wa mcp iwe
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 17 күн бұрын
Awawa anabelana boma dpp ndi akathyali anampusisa bakili muluzi
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 16 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂👍
@patiencebanda3085
@patiencebanda3085 16 күн бұрын
I like your point baby gal 😂 u said u met alot of people rushing to mjamba😂😂for DPP😁😁😁😁😁
@AllieKaisi-je6rm
@AllieKaisi-je6rm 17 күн бұрын
Aaa inuyo mukusokoneza mfundo yanji iyi UDF timaikonda koma osanyoza DPP mwamva
@isaaczidana2914
@isaaczidana2914 17 күн бұрын
Mukusewera ndi add Pali anthuso pamenepa kupambana Kwa adad?
@patrickchataika-jt8dc
@patrickchataika-jt8dc 17 күн бұрын
Chisiru chamunthu ndasiyanso kukupanga follow
@amoschataika7440
@amoschataika7440 17 күн бұрын
Pangani zanu osanyoza anzanu.
@KnowxySainet
@KnowxySainet 16 күн бұрын
Pena gyz kumayamikila anthu awa amidzi yoyandikana not kwanyamula anthu madela osiyana ayi naonso a dpp asiye kutenga anthu magalimoto aziwapenza komko komalidza siyeni chilima sanalamule nawo tonse alliance aaaa
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 17 күн бұрын
UDF what? Mmalo mokqmba zanu muli bzy Matama kunyoza azanu,munava Peter akunena za UDF?
@user-qb1ef1xw5d
@user-qb1ef1xw5d 17 күн бұрын
Udf ndi yamphamvu ndipo chipolopolo chomphera mcp chili ndi udf basi
@CalistoRichard-it8ot
@CalistoRichard-it8ot 17 күн бұрын
Nde apa pali a2 kuyelekeza nd dpp? Aaaaaaa guys chilubgamo amalawi chimativuta
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 16 күн бұрын
Ndipo kwambiri
@AlexMthunziChimpeni
@AlexMthunziChimpeni 17 күн бұрын
Ine Atupele yomweyo osati nkhalamba yanuyi ayi
@user-lv3zj4sk5e
@user-lv3zj4sk5e 17 күн бұрын
Kod adawa akukamba chani😂😂😂😂😂😂😂 or Mfundo mulibemo ayiii😅😅😅😅😅😅
@user-rh7ex9ys8f
@user-rh7ex9ys8f 17 күн бұрын
DPP ndi UDF pangani alliance, musazinamize 50+1 simasewera muzalira.
@ChimwemweMagombobanda
@ChimwemweMagombobanda 17 күн бұрын
Kkkkk ukudwala iwe
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 17 күн бұрын
Koma inu AUDF Pali anthu APA ? Dpp idasezera anthu zinggafane ndiizit 😂😂
@DorrahBanda
@DorrahBanda 17 күн бұрын
Apm woyeeeeeee ❤❤❤
@DannieChimenya
@DannieChimenya 16 күн бұрын
😂😂😂
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o 17 күн бұрын
Ohooooo
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 17 күн бұрын
Dpp 🔥🔥🔥🔥🔥🔥awa alibevundo choka kapikeuko
@carolinechiwanda5907
@carolinechiwanda5907 17 күн бұрын
Wasowa choyankhula iwe DDP woyeeee
@user-xp9zd1wk8g
@user-xp9zd1wk8g 17 күн бұрын
Vomelezani inu dpp ndi one bas
@user-yl5gk4od3s
@user-yl5gk4od3s 16 күн бұрын
Osamanyozana limbikirani kuthetsa nkhaza za mcp inu a udf ndi dpp mugwirizane chimodzi
@usumanidaudi
@usumanidaudi 17 күн бұрын
Ndinu amisaraso bwanji kuri andu uku iwe zipangani za mcp basi timakuziwa
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 17 күн бұрын
Ndichinkhoswe kodi kapena sindikuona bwino?
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 17 күн бұрын
Mukunama inu msonkhano wa dpp kunali anthu kuposanso msonkhano wanuwo
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 16 күн бұрын
DPP my vote ✅
@mphatsobwanali5981
@mphatsobwanali5981 16 күн бұрын
Zaziiii 😂😂
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 17 күн бұрын
Inu nanunso mukulimbana ndi anzanu a DDP nonse a opposition m'malo mot mudzi panga zanu
@kotking-jn5us
@kotking-jn5us 17 күн бұрын
kuti pali anthu ambiri apapa koma anthunu osayamika bwanji bwanji ku dpp inamanga town yonse
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j 17 күн бұрын
Pali chan apo ndi DPP kuchikweza
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 17 күн бұрын
Wodwala iwe ukulankhulawe dpp ndi chipani chomwe chikuopedwa Mmalawi
@sthoramexjrsa902
@sthoramexjrsa902 17 күн бұрын
Mmmmm Kom ziliko ATI Napolo l think even napoloyo akuopa winawake mukamufuse akakuuzani
@DennisDonework
@DennisDonework 17 күн бұрын
Mayo bundle yanga ine mundibwezera a UDF inu
@yamikanichinguwo8460
@yamikanichinguwo8460 17 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 uyu ndi otukwanisa
СҰЛТАН СҮЛЕЙМАНДАР | bayGUYS
24:46
bayGUYS
Рет қаралды 713 М.
Giving 1000 Phones Away
00:18
MrBeast
Рет қаралды 24 МЛН
BRUSH ONE’S TEETH WITH A CARDBOARD TOOTHBRUSH!#asmr
00:35
HAYATAKU はやたく
Рет қаралды 32 МЛН
GWEDE-GWEDE YA LERO
21:15
HOT 265
Рет қаралды 1,6 М.
ZOMWE AYANKHULA A NAMIWA
32:47
HOT 265
Рет қаралды 14 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
IZITU NDIZOMWE A BON KALINDO AKAMBA
15:17
HOT 265
Рет қаралды 3 М.
СҰЛТАН СҮЛЕЙМАНДАР | bayGUYS
24:46
bayGUYS
Рет қаралды 713 М.