Beautiful song guyz keep it up. Dpp is my favorite party. Apm my vote. ❤❤❤❤❤❤❤❤
@marryphili54196 сағат бұрын
Nice song keep it up 💯
@PatrickMtira-w9k8 сағат бұрын
Congratulation for this song am watching in south Africa for Cape Town
@FaheemChipojola7 сағат бұрын
Nice music ❤
@DavieAlumenda-u6y4 сағат бұрын
Well done bro DPP my vote
@RuthBeyala8 сағат бұрын
ndipo sitiloladi aaaah
@DoreenSankho-c6v8 сағат бұрын
Yomweyo chikangawa
@RaphaelWinford-t7u8 сағат бұрын
Dpp ❤❤❤❤❤❤❤❤ we will come back again
@Anthonymendos8 сағат бұрын
Nyimbo wayimba bwino sitilola kuvotela wopanda nzelu
@AlexanderTraffick8 сағат бұрын
Ndipo kaya nkhondo ndili ready kukhetsa mwadzi borani Ana omwe azabwere after kutha kwankhoyo Azakhara pa ufulu.
@MdZack-d9z8 сағат бұрын
Umakwana man wayiphika bhoo
@PrinceBlessings-bv5bs8 сағат бұрын
Koma muti ku dpp anthu ake amatha heavy kukunga nyimbo eti ....😂😂😂😂 Eeesh sikukutuluka mbwelera ❤❤❤
@Alice-z7t4z6 сағат бұрын
Ndipo kukuoneka kt kulibe mbwelera kkkkkkk😂😂😂😂😂
@PrinceBlessings-bv5bs6 сағат бұрын
@@Alice-z7t4zUku anthu amakondako heavy..... Even Dan lu ankaimba motsindika nyimbo zake❤
@Alice-z7t4z6 сағат бұрын
@@PrinceBlessings-bv5bs yeah anthu ndi osangalala ndi DPP kkkkkkkkkk nyimbo zao za meaning
@GreyShadreck8 сағат бұрын
❤❤❤❤
@chifundocharles23487 сағат бұрын
😂😂😂😂 ATI chikangawa 😢😂
@JohnWalekana-z2f8 сағат бұрын
Kuipepelela komaso kuipasa moto ife tili pambuyo pa APM basi form south Africa
@patrickmacheso50627 сағат бұрын
Aliyense amene akuyimba nyimbo yosapota DPP kapena APM ikumakhala Bombaaa moti kwinako akumangolira Dan Lu bc,, Viva DPP.
@ShamimuBisani7 сағат бұрын
Or atakhal wadzaka 400 nkhani ndi usogoleri wake kuti ndiotani bola moyo guyz Koz lamawa ndilamwini Mulungu ndye just wait and c
@PrinceBlessings-bv5bs6 сағат бұрын
AMEN ❤
@AlicksonMakata8 сағат бұрын
Ifenso sitilora kuvotera nkhalamba dpp
@robenallie69858 сағат бұрын
Even years ija anali nkhalamba be koma znali bwino
@YusufJafali8 сағат бұрын
Ukuziwa chani iwe iyaaaa bavotera okuba azakowo😅😅
@ShamimuBisani8 сағат бұрын
Bola moyo koz mawa ndilamwini Mulungu modzi yemwe alibwana pachili chonse muli ndi ufulu ovotera yemwe mukufuna so why r u angry for nothing shame
@EmmanuelNtago7 сағат бұрын
Zamanyazi ma comment onse akudana ndi Chakwera koma only one person in support of Chakwera,,,kkkkk zikuperekadi picture inayake Kut kuli Kuvota Lero wina agwa nayo chagada