Woow what a good song .. this song deserve to award
@RiteRoderick5 ай бұрын
I'm telling you brother he deserved to get award for this song but you know malawi 😢
@tyrachiumia36815 ай бұрын
Mwalo mwa award amangidwa😭😭💔
@RiteRoderick5 ай бұрын
@@tyrachiumia3681Zoopsa zedi mmm
@WesleyKunjilika-t2y2 күн бұрын
Ichi ndye chilungamo zonsezi ankanena okha ndipakamwa pawo ndye tikakumbutsa azitiophyeza.this is good song
@davidlinerevelation34274 ай бұрын
I cried listening and watching this song 😢 😭 God have mercy on our nation
@YamikaniChataika-ib6dd5 ай бұрын
I have been listening to this song for the whole day
@williamskaudzu35234 ай бұрын
Listening to this song, misozi ikutsika. God is watching from a distance.
@chisonimponda3633 ай бұрын
You can say that again
@AufiThera5 ай бұрын
This song deserves award this year
@eliasmalingamoyo7485 ай бұрын
Kulibeko zosakana apa, this song was composed and recorded before all these assassinations of vp happened and messages in this song are clearly without insulting anybody but facts. We are not scared even afraid of anybody. Special messages to the composer my boy Frances keep it up for your good work.
@RiteRoderick5 ай бұрын
He's my favourite brother ❤❤❤
@WillmotChiuimia-vr6ou5 ай бұрын
Yaa that's great songs , palibe zomalozana zala apa yaaaaa❤
@RiteRoderick5 ай бұрын
@@WillmotChiuimia-vr6ouNdipo koopsa zedi boss
@CyrusGracestone5 ай бұрын
Its all facts only koma poti boma li limadana ndi chilungamo pajatu
@MaharaWuss-kv8rh4 ай бұрын
Very well said brotherman 😍😍
@FelixMachika5 ай бұрын
Ndipo asati mitu gwaa, Atiyankhe basi. 😎😎😎😎😎😎😎😎😎👍👍👍👍👍👍👍
@FunnyFishWaffle-oo7bd5 ай бұрын
❤❤❤❤ mwana wakwathu kuntchewu uyu amayimba zenizeni ndipo ayelekeze kukamumanga akaphwanyidwako uyu nde namalila weniweni proud of fj timakukonda
@kenessmsuku94715 ай бұрын
Wow! What brought me to this song? My time not wasted
@DanielBonfaceadungaz-rx4sm4 ай бұрын
chilombo pogwira ntchito ndimanganyayu
@SolomonNjolomole5 ай бұрын
Beautiful song ❤
@moureenmolesi2 ай бұрын
akumusakawo ndidzitsiru munthu waphuritsa nyimbo uyu God bless you bro
@RiteRoderick5 ай бұрын
Wow!!!! What a sweetest song❤❤❤❤❤❤❤❤ keep it up brother mbambande zedi eeeeee chinyimbotu mmmm❤❤❤
Umakwana brother ndipo mcp sidakawina ndipo live chakwera oipa moyo
@DonaldPonda-p2q5 ай бұрын
My Banda dziko lija ndiye laphulidwa chilima alikuti amayi ?
@EveMawonga-ro2bx5 ай бұрын
Nice song 🔥🔥🔥 Chomusakira ndichani,akufuna amuphenso
@paulphiri-fz9me4 ай бұрын
Tinakunyadilani pa dzana paja poti munapha njobvu ndi buma. Ndipo timaona ngati ndinu munthu opemphera koma za ziiiiiiiii😢
@DicksonMoyo-t5u4 ай бұрын
kkkkkkk komadi bale galu amaneyi
@manditopatricioarmindoju-jx2qf5 ай бұрын
Foram Mozambike the Song is very good.
@Yusuf-w8x9c4 ай бұрын
It's good song 🎵 guys keep it up ❤❤❤❤❤❤ 👌
@RiteRoderick5 ай бұрын
This song need to be given award, song of the year award❤❤❤❤❤❤
@RiteRoderick5 ай бұрын
My favourite song ever❤❤❤ eeeeee guys chilungamo ichi zedi❤❤❤❤❤
@WilliamMatanya5 ай бұрын
Agalatiya mwataya chipangano 😢😢
@RiteRoderick5 ай бұрын
@@WilliamMatanya 😃😃😃😃Ndipo zedi brother
@ChimzyGolden3 ай бұрын
Good song mwanayu amatha kuyimba ndipo nyimbo yonveka bwino
@AliceTwaya5 ай бұрын
Good song l ❤ loved it
@mussachimtendere55554 ай бұрын
This song just made my day,,may the soul of skc rest in internal power
@shayrafernandeslatif95565 ай бұрын
I'm so in love with this song❤❤❤ndipoo ndiyogwira moyo❤❤❤ ndipoo mau a SKC shall forevermore echoi in our hearts n mind MTSRIP 🌹
@petermitambo5 ай бұрын
Anyamata apa town kuyibongetsa
@RodgersNtambalika5 ай бұрын
My local musician Francis jomeka nice song
@ThokohKalonga5 ай бұрын
Kkkk nyimbo yabho kwambili no mantha ayi 💪💪💪🇲🇼
@MasterBlack-r2n5 ай бұрын
Tili mdziko la democracy. No kucheuka . Koma vuto chipan chamagazichi mmmmmmm. Koma God protect him
@daviestsamba96395 ай бұрын
Keep on playing this songs facts are there u can not see pictures of the alliance day. Man 🔥 Malawi yanukha
@BlessingsMadaSiment5 ай бұрын
Eish man
@nonhlanhlanhlanhlo39075 ай бұрын
I like this song its very nice
@PeterRabson-z3wАй бұрын
Very nice song❤
@ChimwemweDemelo5 ай бұрын
Ndaonaso legend Charles nsaku akupereka salute
@KinziWindasoni-h4bАй бұрын
Good song waimba ndendeee ndeee zomwe zinachitika
@MikeChinomba-d8r20 күн бұрын
chomusakila ndichiyani Apapa kuZolowera kumanga anthu DPP yachulidwayo sopano koma Malawi ETI
@RaffiqMahmoud5 ай бұрын
Ndibwino kumamasula chonchi,ndiye olo kumphako apha mpaka liti poti aliyense akudziwa.mbiri yao,Anapha serious man kamba kachilingamo chake koma bwanji sanaphe evance mrleka kamba Ka nyimbo ya thata zanjala
@WillmotChiuimia-vr6ou5 ай бұрын
@@RaffiqMahmoud yes that's true bro
@masausomtonga-kc4et5 ай бұрын
Nice song who produce this this song ❤❤
@FrancisTNdalama5 ай бұрын
Amakwanisa eti?
@bisweckchimphamba84975 ай бұрын
Ndi chilungamo wayimba mu nyimboyi ndiyebwslakwitsa pati,kumangomangana zili zonse,mwasowa zochita
@GilbertKuziona5 ай бұрын
I like this song baibulodi ❤and muli mfundo zothyakuka
@Wmwase97Ай бұрын
Mmmmm great thinking
@nellikkmwenda70875 ай бұрын
Wayimba panthawi yake mulungu amudalise
@ChoiceKapatamoyo5 ай бұрын
Iwetu uhv done great session mulungu akudalitse waphaso njovu ndimwala
@ulemummangisa31505 ай бұрын
Mmmh Ali dele mkulinga utaenda nae bagamoyo life 😢😢😢
@FalidaJames-i6sАй бұрын
Nyimbo yachilimbikitso ku mbali zonse ngakhale ena aluzapo ndalama zawo kuona ngat idzakhalabe ku mbali yawo.
@frigildop.j.riscopereira5 ай бұрын
Irmãos do Malawi, como posso ter esse áudio gostei muito da música.
Mtima wazako ndi sidya Lina, ndiwolose kakutafune 😭😭 a Joyce Banda ndi azimzanu mwamuphesa mwana ndinu amene mumamukopa kuti achite geirizano ndi mbali ya akambukuwa. Enoch chihana ndinu amene munamupangisa chilima kupanga gwilizano ndi afisiwa Lelo mwana ali mmanda pomwe Inu muli kunjoya ndimabanja anu okay Koma mukuyenela kumenya nkhondo kuti uyu nayeso achoke pa mpando a Timothy mtambo mumve komwe muliko
@MasterKikah-cg5fc4 ай бұрын
Nice song. Tingayipeze bwanj nyimbo imeneyi tikayike wap status 😊
@KaungaYawaka4 ай бұрын
Wow❤❤ amazing song
@SenkaBalon5 ай бұрын
Munthuyu ali ndiluso koma amakhomelela
@DumisaniMhango-e4i5 ай бұрын
Nice song
@EsterJackson-v4g5 ай бұрын
Beautiful song❤️
@MagretPhiri-z3b6 күн бұрын
Akumbunse iwe ixikhala pa repeat mwina akumbukula zomwezo anagwilizana😅
@HenryMikithayo5 ай бұрын
Kkkk ndipo waiswadi nyimboyi man wa ndioganiza bho heavy😂😂😂😂
@GreyGwaza5 ай бұрын
Km Jomeca umatha kuzuzur ase kkkkk
@davidnoel5995 ай бұрын
this song deserve an award
@dysonmasiye57365 ай бұрын
Straight
@FosterChinzimuBanda5 ай бұрын
Dyela pa chuma akuluwa ,anabwela kudzatizuza zedi.
@ChirwaMyness5 ай бұрын
Keep it up brother nyimboyi ndiyabwino kwambiri 🎉🎉🎉🎉🎉