Nzinvereni nokha Samuel Lwara kuseliku😂 😂

  Рет қаралды 15,336

Malawian Cameras

Malawian Cameras

Күн бұрын

Пікірлер: 46
@vincentmalaulo4046
@vincentmalaulo4046 3 ай бұрын
Sitikuopa! Stikubwerera m'mbuyo ndpo stifooka🇲🇼!!!
@BensonChilundu
@BensonChilundu 3 ай бұрын
Komatu tisazamve kuti Chakwera wawina,mudzayaka muno
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
More 🔥🔥 💯 kulira salesana ngati wina zikumunyasa akakolope nyanja
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 ай бұрын
Samuel lwara Auzeni achakwela ndi mbuzi ya kupha
@MikeKanyaza-bm5tp
@MikeKanyaza-bm5tp 3 ай бұрын
I agree with you mr lwara,we don't have government here
@MosesKalenge
@MosesKalenge 2 ай бұрын
R.I.P SKC and 8 familys💔💔😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani 3 ай бұрын
Dzoona zake izi Timalemphera kumvomeleza kuno Kumalawi
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 3 ай бұрын
Muuzeni Chakwera ndi kawadi mfiti ya munthu ndipo sitikuchifuna chichoke mbusa okuba ndalama zaamphawi iyeyo nkumasangalala Amalawi tikuvutika asamadalire kumanga kumangakotu ndikutiwopa bwera poyera opanda otimanga uwona uthere mmanja mwa Malawi 🇲🇼
@hawardmkandawire673
@hawardmkandawire673 3 ай бұрын
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 ай бұрын
Ndipo chakwera adalankhula yekha pa campaign kuti akadzalephela kusintha dziko adzatula pansi udindo, koma akulephela.
@BrightPhiri-bt6ev
@BrightPhiri-bt6ev 3 ай бұрын
Koma iweyo i think anakakupasa u vice president chifukwa zikuwoneka kuti u gardener waku state house siunakusangalase.pamene umadya nawo unali zii siumatisokosela panopa munanyelana uko wayamba kutisokosela kuzimva inu kumakuvutani.lwara unasuzgo yambula kwamba uwongenge kuti uli kugwilapo ntchito ku state house bcoz of chakwela not chilima.
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 3 ай бұрын
Tamuuzen amvetse ameneyu chidebe chopanda madzi mmesa adakaona ku state chifukwa cha Chakwera not chilima, komanso adakhoza kumulemba as gardener adaona kt mulibe umunthu weniwen
@NthambiInvestment
@NthambiInvestment 3 ай бұрын
Chakwela mbuzi yeni yeni kupanda chilima bwenzi Ali ndani ,,lero anaiwala mpaka kumuphanso timuona kuti kampeni yaulendo uno aziti chani
@ChipiliroSmart
@ChipiliroSmart 3 ай бұрын
❤❤❤❤❤
@BrightPhiri-bt6ev
@BrightPhiri-bt6ev 3 ай бұрын
Muja wayambila kulalata mphindu ndichan? Attention seaker!!!!
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 3 ай бұрын
Anakalira nawonso maliro a saulosi zisomo ndi okwanilaso za chilima
@chikondimapondera954
@chikondimapondera954 3 ай бұрын
There is sense
@RitaBan-t7c
@RitaBan-t7c 2 ай бұрын
Nzeru zamuthera chakwera m'malo moti azimitse moto ndiye akuponyanso zinyalalapo kuti moto uyake kwambiri Achakwera imvani kaye kuti anthu akulira bwanji
@GiftSoko-i3s
@GiftSoko-i3s 2 ай бұрын
Tilipamanyuma pinu mudala no matha we love broz truth must be come out chakwera must go walephela apite
@BeatriceProfessor
@BeatriceProfessor 2 ай бұрын
Yowoya dada mtumbuka simunthu wamba respect 😅😅😅
@MosesKalenge
@MosesKalenge 2 ай бұрын
MAU AMPHAMVU BROTHER ♥️ 💪💪💪💪💪💪🫂
@AlexGomani-ss5nj
@AlexGomani-ss5nj 3 ай бұрын
Pitiruzani kuwauza anthu osamvawa uthenga omveka bwino ngati umeneu, cholinga mawa asadzaname kuti samauzidwa, samadziwa. Ndi agontha nkutu 🤝🤝
@BeatriceProfessor
@BeatriceProfessor 2 ай бұрын
Tell them nonses Government
@ChiefJustin-cl8jl
@ChiefJustin-cl8jl 3 ай бұрын
Auze alephela komanso kumakulakula mtima
@MosesKalenge
@MosesKalenge 2 ай бұрын
💪💪
@MikeMwale-bw1xw
@MikeMwale-bw1xw 3 ай бұрын
Campaign ya ulendo uno agalu amenewa iwavuta adzatiuza chani chachilendo,bodza lonse talionalo?
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 3 ай бұрын
Kkkkk paja Muluzi adakulonjezan nsapato bwana kaa adakuguliran
@ChipiliroSpencer
@ChipiliroSpencer 3 ай бұрын
Muthuyi akuyakhula zoona koma kuti vuto amalawi ife tidakalibe ndi tu
@OwenNyangu-nv1yt
@OwenNyangu-nv1yt 3 ай бұрын
Mulungu anapanga ifa ndipo ifa imabwela kwamunthu ndizollinga zake tingopezelapo uchimo chifukwa akudziwa chilichonse chimachitika akuchidzowa ndimulungu
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 3 ай бұрын
Nde iwe osakhala chete bwanji , kusonyeza kuti ulikumbuyo kwa okupha.
@DjFiquickTech
@DjFiquickTech 2 ай бұрын
Mbava iwe
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 3 ай бұрын
Musiyeni munthu arankhure phindu riripo ndirot chakwera akanva aziwa kt kunjaku anthu sakundifuna kusiyana ndikukhara chete akhoza kumawona ngat anthu akukondwa ndiwuramuriro wake ndakuyankha phindu rake osamafusa anthu mafuso opanda mutu apa ngat ndinu anzeru kwambiri
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 3 ай бұрын
Nawenso openga kwambr ukuona ngt voice ya Lwara ingasinthe support ya Chakwera? Support weniwen sasunthika ngakhale Lwara atachezera kulankhula akungovutika chabe siziphula kantha zimenezo
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 ай бұрын
AAAAAA IWE AMENE UKUTI MULUNGU ANAPANGA IMFA NDIPO IMFA IMABWERA NDI CHOLONGA UKUTANTHAUZA CHANI? IMFA YAKE NDIYE SI YACHILIMA IYI IMFAYI MUSAIKEPO MULUNGU UTENGEREPO TCHIMO NDIWEYO IMFA IYI SIYOCHOKA KWA MULUNGU INACHIKA KWA CHAKWERA NDI NDUNAZAKE IWE UNAONAPO NGOZI YA CHITIKA ANTHU NKUPEZEKA MALISECHE OLO NSAPATO KUPHAZI NGOZI YAKE YOTANI , MPAKA MA FONI KUSOWA TIZITI NDENGE NDI YOMWE INATENGA MA FONI AWANTHU AJA ? MUSAKWIITSE ANTHU NANU
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 3 ай бұрын
Arwala atifumbireniko ku boma uko ka minda ya press wakuguriska ninja and uyo wakuguriska iyo wakagura kwanja? Fukwa ine pa mayano yano yane nge minda ya press walekere wanthu awo kamuzu wakapokako malo iye wakagura cha wakapoka wawezgereso kuwanthu
@sanuhabdullah5998
@sanuhabdullah5998 3 ай бұрын
Talk n dont fear only fear God
@MikeManyamba
@MikeManyamba 3 ай бұрын
Akunena zoona
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 3 ай бұрын
Keep on talking Lwara wina achire Kaya a mwa panadol
@YassinAssima
@YassinAssima 3 ай бұрын
Kuimbila ufiti mmanja phuno salota
@HendrickBanda
@HendrickBanda 3 ай бұрын
🔥🔥🔥💪
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani 3 ай бұрын
16:33 💪💪💪
@jamesgama5489
@jamesgama5489 3 ай бұрын
We need people like you more fire rwala
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 3 ай бұрын
Kuchikamwa uku kudzachita manyazi one day mulibe ndiumunthu maliro tinaika Koma andedwa ndiye mwawazuza ukanati kunena zayesu bolani Koma akulu ndale Mwai pa maliro Pola Moto peza Ina nkhani adaaa usaonekele utsilu wako
Mai Mary Chilima report la Ku Germany lija.............................
5:51
ZOMWE WAONA CHIKANGAWA KU UNGA BASI SADZAKHUMBILAKOSO AMUONETSA
18:08
Malawi Trends TV
Рет қаралды 28 М.
Running With Bigger And Bigger Lunchlys
00:18
MrBeast
Рет қаралды 107 МЛН
HAH Chaos in the Bathroom 🚽✨ Smart Tools for the Throne 😜
00:49
123 GO! Kevin
Рет қаралды 15 МЛН
Hot Current ya Lero
12:04
Malawian Cameras
Рет қаралды 3,2 М.
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 43 М.
Full Gwamba interview
10:10
PAKAYA TV
Рет қаралды 9 М.
Wakatolika uyuyu Amutapa posachedwapa😂😂🤣😂😂
14:40
Malawian Cameras
Рет қаралды 72 М.
TAMVANI ZA IMFA YA CHILIMA IJA
10:10
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 255 М.
M'busa yu mumulanguze apiteso ku Church  asamakambeso chilichose chandale.
9:02
MIYAMBI YA NANCY VS CHE-NKOPE
8:52
Kwagwanji?
Рет қаралды 350