you prolly dont give a shit but if you guys are bored like me during the covid times then you can watch all the new series on instaflixxer. Have been watching with my gf recently =)
@harrylouie79553 жыл бұрын
@Jerome Uriah Yup, have been watching on InstaFlixxer for years myself :)
@homeremedys3748 Жыл бұрын
Kamuzu ankayankhuranso chichewa, Ankawakoza chichewa ma interpreters nthawi zina pa nsokhano
@medsonboti19843 жыл бұрын
Mutipatse mbiri ya Kamuzu wathu weniweniyo tiyidziwe.
Ine chomwe ndisakumvesa ndichoti why mama kadzamila sakufuna kulemba book la life ya kamuzu banda ngati iye munthu mmodzi yemwe akumudziwa dr banda kuposa wina aliyense
@g_deonm57933 жыл бұрын
Chifukwa ntchito anthu akhoza kukuukila mama pothandiza kubetsa dziko...ichi ndi chinsisi chomwe adzalowe nacho mmanda pofuna mtendele. Koma boma litafuna kuti anthu adziwe izi akhoza kufufuza ndikulemba mwatsanetsatane chilungamo chomwe..but they choose the easier path: " pretending not to know".
@EBBOY-nl7gr Жыл бұрын
Ine munthu uyu sindimawonanso chifukwa chake chomwe amamuyikira pa pepala la ndalama
Nkona amapha anthu ozindikira????zoopsa And how come mpaka kumakanika kuyankhula language yakwawo.hmmmm
@kalimawandale7161 Жыл бұрын
Those that know Kamuzu's Tumbuka and Chewa ascent know that he was a real Malawian, if you talk about him killing people you will find that in those days politics was about killing opponents all over the world
@majiyabanda45103 жыл бұрын
You're the best bigman
@allanmakwiti51453 жыл бұрын
This is good history worth listening to 🙏🏼
@shabbanusuf50963 жыл бұрын
We love you brother keep it up
@bobkenneth29479 ай бұрын
This's real history,ulemu wanu Bigman pitilizani kupanga expose anthu amenewa
@alexanderkaunda95543 жыл бұрын
Nanga asilikali ndi apolice anagonabwanji
@twisimwaighogha1822 Жыл бұрын
The British Government should now declassify Kamuzu's file.
@giftmingo9293 Жыл бұрын
Kojo Botsio
@martinnyirenda30962 жыл бұрын
So lovely and very true story
@memoryfrancisco65583 жыл бұрын
Anali obwera uyu.
@williammaseko85423 жыл бұрын
This guy knows how to dig deep with investigations based on facts. I enjoy watching and listening to your videos. Keep the fire burning for us to see the flames. You rock.
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
@@ishmaelchiponda5471 iweyo ukuchita kudziwa kuti a MCP ankaletsa wina aliyense kulemba history ya Kamuzu. Mabukhu ambiri anachitidwa ban Ku Malawi kuno. Iweyo ukunena zopusa zakozo potengera history yabodza imene ankakuphunzitsa a MCP. But the truth is that there are many books that said Kamuzu Banda's real name was Richard Armstrong. Go and read the book titled post colonials in Africa.
@johndulla77053 жыл бұрын
@@ishmaelchiponda5471 ndie tiuze iweyo kuti ndi chifukwa chani mnthawi ya ulamuliro wa kamuzu tinkaphunzira Ashanti kingdom ya ku Ghana mu syllabus ya Malawi? What great was Ashanti kingdom to be in our syllabus instead of other tribes near us?
@johndulla77053 жыл бұрын
@@ishmaelchiponda5471 of course it is true kuti mnthawi ya kamuzu kunalibe chilungamo and Ana sankadziwa zoona zenizeni zokhudza history chifukwa zambiri ankangonyepula, komanso mabukhu ambiri amene ankalemba chilungamo ankaletsedwa kuwerengedwa ndi Ana mmasukulu. Ndikupatse chitsanzo cha bukhu la Norman Lowe limene linaletsedwa kuwerengedwa ndi Ana mmasukulu mnthawi ya kamuzu. If you know history of the world you can understand that Norman Lowe books are one of the best history books in the world. And mcp govt banned those books, do you think Ana akanadziwa bwanji history yabwino without reading those books? .
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
@@ishmaelchiponda5471 iwe anthu anachangamuka nthawi ya Muluzi. Ana ozindikira anayamba kupezeka nthawi ya Muluzi. Nthawi ya Kamuzu Banda kunali mbuzi zokhazokha zodziwa ma types of grasshopper. Nthawi ya Bakili Muluzi ana ankawerenga mabukhu enieni okhudza mbiri za dziko lapansi. Even syllabus ya Malawi anayisintha tinkaphunzira world history 1 and 2. Mnthawi ya Kamuzu Banda kunalibe zimenezo.
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
@@ishmaelchiponda5471 iwetu ukuonekeratu kuti ndiwe mbuli. Mnthawi ya Kamuzu Banda mu syllabus kunalibe cold war, world war 1, world war 2, Vietnam war, even Cabinet crisis 1964 sanayikemo. Ma history akuluakulu okhudza dziko lapansi kunalibe mu syllabus ya mcp
@lamecknyadani190510 ай бұрын
Tisazamve kamuzu Banda stadium.... Sanamangepo stadium mkulu wa ku Ghanayi
@frasernamaona65263 жыл бұрын
Sanali mmalawi uyu ada Kamuzu
@chelseajackson32003 жыл бұрын
The government should take Kadzamila, Kazombo, Mzaza family to courts on supporting Kamuzu. They leave on the stolen money that kamuzu store from taxpayers.
@lamecknyadani190510 ай бұрын
Kamuzu Banda tamuchosa mu history ya Malawians kkkkk
@bobkenneth29479 ай бұрын
He was not a Malawian citizen
@frankcholimbirapo2623 жыл бұрын
Tikuziwa zambr via pa phone
@lamecklipenga855 Жыл бұрын
At least Kamuzu helped those who may say they are real Malawians yet stealing and stealing.
@giftmingo9293 Жыл бұрын
You're a genius Comrade
@georgeamosi9931 Жыл бұрын
Very good!
@leonardmchiela6533 Жыл бұрын
That is his original home country
@chelseajackson32003 жыл бұрын
He could easily be Kwame's cousin even brother.
@wizahsimbeye32273 жыл бұрын
Kodi bwanji osafusa za Cecilia Kadzamila za Kamuzu Banda Mesa she is alive you are now too much on Kamuzu Banda. Kwame Ncluma was a nationalist nde why Kamuzu Banda was if he Kamuzu was supporting azungu a Ku RSA?
@memoryfrancisco65583 жыл бұрын
Cecilia kadzamira sanganene chilungamo. Ndi magulu okhaokhawo amene anakhala akubisa chilungamo for 31 years. So don't expect any truth from that evil woman. Everything she can speak out on her mouth can be all lies
@shabbanusuf50963 жыл бұрын
This is really Ghanaian we don't have these faces in Malawi
@osamabinraden93913 жыл бұрын
Adali wa Ku Ghana sadali m'malawi
@jkfodya9997 Жыл бұрын
Ndavula kachisoti bwana
@basiliojeremias62002 жыл бұрын
Ndipo kwamenkruma akufana khope ndi Kamuzu banda
@yaissah45183 жыл бұрын
Za chipumi is true
@osamabinraden93913 жыл бұрын
😁😁😁😁Dzaka 31 lokomwana Ku Malawian adali chumba m'dalawu😁😁😁😁😁😁😁😁😕😕
@johnchavula3282 Жыл бұрын
nice
@dastahchikwekwe78643 жыл бұрын
Who can say the trueth about kamuzu banda ok it seems like he was not amalawan by his language mama may be can know if he was not a malawian it's so shame to malawian
@dorikakamwendo69703 жыл бұрын
Anali Foreigner uyu
@edwingondwe28603 жыл бұрын
Pitirizani kutiuza za mbiri zobisika
@stevenchirwa5028Ай бұрын
Straight to jail
@emmainvestmentgroupofcompa33553 жыл бұрын
Kukafukla kumumenya ndikupanga deported. Gana or kungomutaya ku shire
@Sikhakhane210 ай бұрын
He was really devil 😈 this man
@peterarvaszulu50692 жыл бұрын
Why was kamuzu Banda not arrested posthumously for the evils he caused on innocent people
@peteruko3 жыл бұрын
Zipumi? Lol !😂
@umaliisah69203 жыл бұрын
We follow u
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
What you are talking is making sense somehow. Analephera bwanji kulankhula chilankhulo cha makolo ake for the rest of his life.
@eltonmpiro87383 жыл бұрын
Samalakhula even chichewa?
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
@@eltonmpiro8738 inde kaya sankalankhula Chichewa. Anangolankhula kamodzi komanso chochita kuwerenga choonera pa bukhu
@@ishmaelchiponda5471 ndie unamuona Mandela atalemba ntchito interpretor omasulira chizulu pa msonkhano wake? Kapena unamuona Mugabe atalemba ntchito interpretor omasulira Chishona? Mandela and Mugabe were speaking English poyenera kulankhula English, koma ankapanga communicate ndi anthu a kumidzi mchilankhulo chawo. Not this Kamuzu Banda who was speaking English to the rural masses where there was more uneducated people
@duncankamanga34613 жыл бұрын
Kodi tikungomva kuti kale kunali ulamulilo wa chipani chimodzi,ngakhale munthawi ya atsamunda,koma tikamamva mbiri tikumvamo kuti zipani zina zinaliko.ziwona zenizeni ndi ziti?
Amalawi ndi kuwudzeni vuto ndilakuti amalawi tulo (1)kuopa kwambili asilikari ndi apolice ndi chifukwa mbudzi dzikakhala pampando dzimagwilisa ntchito asilikali ndi apolice kuophyedza anthu ( tithokodze asilikali apano chifukwa akuona m'mene dziko likuyendela pomalidza chakwera ndi chilima musamale
@alexanderkaunda9554 Жыл бұрын
That is point kuopa kwambili apolice ndi asilikali komaso naonso ndi osauka
@piperharder74363 жыл бұрын
Kamuzu analidi jabulosi koma za nkazi wake panopo zli pati
@tonyomondi26833 жыл бұрын
Please narrate in English so that others can understand
@chelseajackson32003 жыл бұрын
The reporter needs to go to Ghana and dig out Kamuzu village, his relatives & friends on identity issues. I for one believed that kamuzu was never a malawian.
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
@@rickchipo4140 it's true story kungoti amalawi ambiri anapusitsidwa mu ulamuliro wa MCP. Kamuzu Banda was not a Malawian.
@chelseajackson32003 жыл бұрын
People in the clan of Kazombo, JZT, Kadzamila, Mzengereza know the truth but love of money/benefits they keep quite. If Muluzi had genuine love for the country, he could have challenged Kamuzu on this but alas, kuba basi.
@louiskagona2 жыл бұрын
Zinachitika basi. He ruled Malawi with integrity Than enawa
@drjoetheu3 жыл бұрын
The more the narrator points to Kamuzu's background as a Ghanaian, the more he is losing credibility because he is using very lame arguments. For example, he uses the similarity of foreheads in Kamuzu's picture and that of Kwame Nkruma's. This is a very weak argument which may not stand serious critical examination . He keeps referring to knowledge of a foreign language and failure to speak one's mother tongue as another very strong proof that one is not from his claimed motherland; again another weak argument. As he continues to use such weak arguments, he begins to lose followers who may have been convinced in earlier episodes. For one, I have followed the few times that Kamuzu spoke Chichewa and Chitumbuka and on all occasions I was convinced beyond doubt that his accent was that of one from Kasungu-for example; he pronounced "weni weni" as "wene wene". In Malawi, this kind of pronunciation is common in Kasungu. People from Kasungu are usually very good at Chitumbuka as well. He seemed to speak very good Chitumbuka. This to me more than pin points his home village, right in Kasungu. Please revisit these points and reconsider your points when making arguments on Kamuzu's Malawian origin and other historical arguments in general. Otherwise, this is a good initiative with so far reasonable output.
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
Kamuzu Banda was not speaking Chichewa or even chitumbuka. Don't cheat people here. Even me I can teach someone chizulu just by reading like the way Kamuzu was reading at the podium. That doesn't mean he was speaking Chichewa or chitumbuka. Where in the world Kamuzu Banda spoke Chichewa or chitumbuka without reading on the paper? Inu mukunena zoonera pa likasa lochita kulemberedwa?
@g_deonm57933 жыл бұрын
The narrator posses a good argument a good point. I like his points, even if they may not stand to prove his point beyond reasonable doubt in the court of law but they provoke ones thinking and provide alternative reasoning. We are enjoying this...!
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
@@qonttransportltd7027 olo mutsutse Kona zomwe akunena munthuyu ndi zoona. Amfumu a Mwase ake ati amene ankalemberana makalata ndi Kamuzu? Iweyo ukunena zimenezo potengera mabodza amene unkanamizidwa ndi a MCP koma choti udziwe nchakuti Kamuzu Banda anayamba kudziwika ndi anthu Ku Malawi kuno mzaka za man 1950s. Zina zonse zimene umamva zokhudza Kamuzu it's just a makeup by MCP gurus for you to believe that he was indeed a Malawian. Zoti ziliro mumba ankadziwana ndi Kamuzu ndi zabodzanso, don't believe those lies. Ziliro mumba died in 1945 and he don't know Kamuzu. Zomwe ukunenazo ukunena potengera information imene ankakunamiza a Kamuzu Banda was not a Malawian and that's why he was making sure to block everyone to write his biography. Mnthawi yake kunali ulamuliro wa chipani chimodzi and he denied access to information regarding his biography. He was not even speaking Chichewa don't cheat us here. Tell us that Kamuzu was just reading Chichewa chimene ankachita kulemberedwa ndi ma advisors ake. We have the videos and there was nothing like speaking Chichewa.
@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
@@qonttransportltd7027 iwe ngombwambwanadi eti. Unayamba utayiona degree ya Kamuzu Banda kuti inali ndi dzina la Kamuzu Banda? Degree yake ya za udokotala anapangira mdziko la United States of America not Britain. And ankalephera kuwaonetsa anthu. In 1959 MP Mr Whitewick anamuuza kuti aonetse macertificate ake ngati anali ndi dzina la Kamuzu Banda, Kona Kamuzu sanaonetse. Komanso atangobwera kumene able ake adamukana Ku kasungu ponena kuti amene uja sanali Kamuzu. And you know kuti anthu amenewa anachita kutsekedwa pakamwa ndi ndalama at that time. There was an old woman there who claim that Kamuzu anali ndi chipsera Kunkhope kwake pomwe uyuyu analibe. Ngakhale pomwe anali president, he detained alot of people amene anali able ake Ku kasungu ngati njira imodzi yowaopseza kuti asaulure.
@memoryfrancisco65583 жыл бұрын
@@qonttransportltd7027 mmmh, palibepo za u cadet apa nanu. Kuzolowera kudana ndi chilungamo basi. Instead of bringing real argument basi waganiza kuti uzitchula macadet. Kungosonyezeratu kuti cadet ndi iweyo amene ukufuna kumanamiza anthu pano kuti Kamuzu anali mmalawi