Richard Chimwendo Banda Waphula Scandal yochititsa manyazi mmmh (Tinaiwala kuponya usiku video yi)

  Рет қаралды 22,012

Malawian Cameras

Malawian Cameras

Күн бұрын

Пікірлер: 337
@tingamasi106
@tingamasi106 3 күн бұрын
watsala pang'ono kuika chithunzi cha chilima mkulembapo kuti "Ntchito za manja anga kuikira umboni" kenako mkuzati " boma ndilomweli la chikangawali..........God you make them confess soon
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow 10 сағат бұрын
kkkkkk koma big eeee mwamulankhulatu kkk
@amoschataika7440
@amoschataika7440 3 күн бұрын
Ntanyiwa akamakuwuzani kuti this is not 1964 this is 2024. Shame on you foolish Minister.
@lightwellsilumbu
@lightwellsilumbu 3 күн бұрын
Kani abambo awa ndi achitsiru chonchi?. Ndeno nkumati ndi atsogoleri athu?. Mumalo mopanga chtikuko busy kumanama. Munthu olepkhera amaonekera patali. Kuzindikilaa yekha kuti ngolephera. Dziko ndi aanthu ngati awa silingasinthe zero. Mumutu mulibe nzeru. Tili pamavuto amalawi. Tichotse dziwanthu ngati izi.
@AubreyWilson-j8w
@AubreyWilson-j8w 3 күн бұрын
Umbuli too much
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 3 күн бұрын
Achimwendo banda stop nonsense 😒 😑 🙄 😤 pls you most know this government 🙄 is going 2025 Apm is coming soon to be president of this country Malawi 🇲🇼 😉 🙄 😒 manyizi bwaaaaa dpp is my vote 🗳 boma 2025
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 3 күн бұрын
Koma nduna iyi imandibowa ndikamuona ndimaziwa kuti ndawona nduna yopanda zeru yozikweza yozitukumula or Chakwera ali pasi
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms Күн бұрын
Muli ngati ine big azayambe kumanga iye
@AubreyMatress
@AubreyMatress 3 күн бұрын
Ng'ona party manjenje plus ziphwisi nde chomwe awona ndikumaba zinthu za ku India kumafuna kunamidza a malawi koma akuchepa,, malawi wa lero si omunamidza_ anthu awa akudziwa kuti coming 2025 sanunkha kanthu tsano angoganidza zomanamidza anthu😂😂 konseku kuyetsera kut asatulule m'boma koma achedwa atalawira,,, 2025 timanga timbava tonse ta emusipi_just wait and see Angels of God are busy sweeping off and restoring things for 2025
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 3 күн бұрын
Njanji inamangidwa ndi boma la Mozambique koma a Chakwera akuti amanga ndi iwowo. Bodza la MCP ndi loyipa kwambiri.
@michaelamon9691
@michaelamon9691 2 күн бұрын
Lier
@ManganiStanley
@ManganiStanley 3 күн бұрын
Mutiuzileko chimwendoyo macende ake munthu opusa kwambiri
@MarthaChigonero
@MarthaChigonero 3 күн бұрын
Mulungu pitilidzani kubweresa chilungamo poyela kuti tisukike maso
@IbrahimMatola-h4i
@IbrahimMatola-h4i 2 күн бұрын
Mbuzi yamunthu chimwendo Banda
@GeophuliesHarry
@GeophuliesHarry 3 күн бұрын
Koma chimwendoyi makolo ake ndi abale alipo... Munthu wochitisa manyazi ndithu
@SanudiTchuma
@SanudiTchuma 3 күн бұрын
Kalekale anthu ambir asakuziwa internet bodza ilili likanagwira km nowdayz mm apa ndye mwayaluka achi leg
@FelixAaron-jm3ui
@FelixAaron-jm3ui 3 күн бұрын
Actually this guy is a really GOAT
@dalitsohealthchartcorner5498
@dalitsohealthchartcorner5498 Күн бұрын
😂😂😂😂😂
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 3 күн бұрын
Boma la asatan okha okha okuba, kupha ndikunama Zitsirutso ndi zomwe zimazitembelera pomati boma ndilomweri Mulungu akuikani poyera ndipo mukuonanso ulamuliro uchititsa manyadzi Nanga izizi nzichani Malawi di wa 1964 uyu very shame
@FrankKambwani
@FrankKambwani 4 сағат бұрын
Chipani cha wanthu amagazi angapezeke bwanji ndi kunena zoona?
@ThomasMGamah
@ThomasMGamah 3 күн бұрын
That's imeneyo ndikuti you are second Bakili muluzi tv look how explanation well understood listening from Capetown
@HanifiYaumu
@HanifiYaumu 3 күн бұрын
Tikangositha boma mu September 2025 tikukandani madazio achina chimwendo musaza zomwe mwadyazo
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 2 күн бұрын
Zamanyazi, kuika zithunzi za ku India😂😂😂😂😂😂😂 Boma la bodza kuyambila President chakwera mpaka nduna zonse, eish! Malawi ili pa vuto kobasi.
@IsaiahMiSheck
@IsaiahMiSheck 18 сағат бұрын
Basi boma loseli kumangoveka athu amoxi moxi achimwendo xikhale ng,oma basi
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje Сағат бұрын
Uuuuuuuuuu manyazi bwanji ndi chimutucho simunati munya
@IsaiahMiSheck
@IsaiahMiSheck 18 сағат бұрын
Nduna zadyela basi kkkkkk km awa boma ndilomweli lachani lonamali inewo sixoti sanama km boma ili lawojexa
@FidesChandama
@FidesChandama 7 сағат бұрын
Machende ake amenewo akuitenga Malawi ngati 1954
@DennisMdezq
@DennisMdezq 2 күн бұрын
Munthu osapangitsa manyaz uyu kapolo kobasi ukuona Ngati 1964 eti Ife ndi ama 1990
@hassanrasheed1379
@hassanrasheed1379 2 күн бұрын
chimwendo iwe ndi galu mutu ngati chibazi savage iwe ukuwona ngati amalaei ndife wopepela Ndondotcha ya Achskwera iwe ''zoona'' shaaa 🤔 wadya manyi aise
@DigleDafter
@DigleDafter 2 күн бұрын
Chimwendo uyu 2025 azangothawa bas chifkwa azafera mmanja mwawathu
@WiliWili-y2d
@WiliWili-y2d 16 сағат бұрын
kkkkkkkkk km, chikangawa kuchenjela kkkkkkk
@thokojames5231
@thokojames5231 2 күн бұрын
Nduna yochitisa manyazi mbudzi chimutu,mphuno, milomo,kukulako ndimaona ngti ndi nzeru ,
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 күн бұрын
Mutu ngati nguli chimwendo 😂😂😂😂😂😂😂 malawi wa leroli oloko mutatani simungati namize hahaha
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 күн бұрын
Apm deserve to be the president of the republic of Malawi achimwendo shame on you
@hassanrasheed1379
@hassanrasheed1379 2 күн бұрын
iwe chimwendo nzeru ulibe bolo yako aise iwe ndi muthu wopangitsa manyazi galu 😡 moti mukamapita mayiko enawa simumachita manyazi agalu
@FidesChandama
@FidesChandama 7 сағат бұрын
ang'ona party mwationjeza kwambiri
@juliochiwalo
@juliochiwalo 2 күн бұрын
Dziko la malawi liribe utsogoleri nchifukwa kuli mavuto opsa
@FrytonKampira
@FrytonKampira 3 күн бұрын
Mcp ndiyaboza , a chakwela atinamiza za njanji ku nsanje a chimwendo banda kutinamiza za nsewu amalawi tinapanga mistake kuvotera mcp
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow 10 сағат бұрын
Ndale za chitsiru zoona minister?
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje 2 күн бұрын
Minister ochitisa manyazi, muthu wakulukulu kufasa kumalemba zithu zimene akuziwa kt sizakumalawi shame on you
@MandalaChaona
@MandalaChaona 3 күн бұрын
Chimwendo Banda Chimodzi mwa Zitserekwete za Ku MCP. Ukulitenga ngati Dzikoli ndi lako. Changokula ichi koma ndichopanda mzeru. Nthawi mkachitsiru tidzakuonera ndi Nyansi zakozo.
@GEORGESITOLO
@GEORGESITOLO 3 күн бұрын
This is not propaganda I checked pa google it's true ndi nsewudi wa ku India 😂😂😂😂😂
@BillyKalambo-jx3vf
@BillyKalambo-jx3vf 2 күн бұрын
Vuto ndiloti ku mcp kuli agalu okhokha iyeyu chimwendo ndi mutu wakewo akuzimva udolo aziwanamiza anyau konko
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 2 күн бұрын
Kkkkkkkkk koma chimwendo wangokura chimutu chopanda manyazi
@ChicoBanda-kq7py
@ChicoBanda-kq7py 3 күн бұрын
Ntchito yabho mumakwana petrizani kuti onesa zomwe achisilu angumanamiza anthu
@UneMe-k8v
@UneMe-k8v 3 күн бұрын
Koma mulungu amayika poyera nzisilu ngati chimwendo b galu wachabe chabe athu akufa kumabgonamabe
@Jabilumatendewu
@Jabilumatendewu Күн бұрын
Mutumidźile Dan lu
@juliussamson6212
@juliussamson6212 3 күн бұрын
SAMALA CHIMWENDO NTHAWI ZINA KUDZACHE NGATI MMENE AMALAWIAN S AKUVERA NDIPO NTHAWI IDZAKHALA YAKO ANY CHIPANI UDZAROWE TIDZAKUTSA NDIKUPATSA MAKOFI OCHULUKA IWE CHIMWENDO BANDA TAKE CARE
@AubreyChiyaya-ty8ge
@AubreyChiyaya-ty8ge 2 күн бұрын
Achimwendo Banda ni mbuli nyani .... pamodzi ndi makolo ake
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 2 күн бұрын
Ndizoba ameneyi
@AbdulNyambi
@AbdulNyambi 2 күн бұрын
Nduna anasankha chakwera ndi mbuli zosaziwa chomwe akuchita
@MayesoBikefa
@MayesoBikefa 3 күн бұрын
Shame on you Richard chimwendo banda
@phillipkazembe7281
@phillipkazembe7281 3 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 koma yaaaaaaa MCP muli pa ntchito never ever again
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 3 күн бұрын
Umbuli wangokula chimutucho koma mulibemo kanthu komanso umbuli akuyesa a Malawi ndi osazindikila amalawi panopa amazisata za technology sungawapusise iweyo chimutu
@gmxplayboy6559
@gmxplayboy6559 2 күн бұрын
Kodi a Malawi tidzadzuka liti? Kodi anthu amenewa azingotidoda mpaka liti? Can't we do something together to eliminate this nonsense before 2025 Election? Anthufe ndiye tikutoledwa kupusa ndithu. Vuto lomwe tiri nalo ku Malawi kuno ndi lakuti tiri ndi Opposition Parties yogona. Anyway, who knows? Maybe Otsutsawa akumawoneka kuti ndi otsutsa kumbaliko, but in actual sense they are together with these ruling party fooling poor Malawians
@SungeniKameja
@SungeniKameja 2 күн бұрын
Mcp yamangaso Malawi lowan kulilongwe muesa ngat muli kuja
@emilynthite6545
@emilynthite6545 2 күн бұрын
Kkkkkkk agwanayo chimwendo bandayo
@emilynthite6545
@emilynthite6545 2 күн бұрын
Chimutu ngati basi
@MalawianCamera
@MalawianCamera 2 күн бұрын
@@emilynthite6545 😂🤣🤣🤣🤣🤣
@alexandermwandira2376
@alexandermwandira2376 3 күн бұрын
Gentleman ku india uku
@WatsonMalanga
@WatsonMalanga 3 күн бұрын
Ndi mbava kwambiri ndunayo
@juliussamson6212
@juliussamson6212 3 күн бұрын
ANTHU ANGADYE MISEWU MIMBA ZANU IWE CHIMWENDO SAMALA ZIMENE UKUCHITAZI MAWA ZIKUBWERERA POYERA
@partmaulidiPatrick
@partmaulidiPatrick 2 күн бұрын
boma likuyendetsedwa ndi atambwari okhaokha ili
@MussaRafael-d4q
@MussaRafael-d4q 2 күн бұрын
Chimwendo ndiwa Tchende et asamatiwone kuphusa
@EviChio
@EviChio 3 күн бұрын
Chimwendo Banda iweee, udzikanamiza ana ako ndi amako wanva? Tatopa nalo bodza lanulo
@HajjiFreza
@HajjiFreza 3 күн бұрын
Kkkkkkk bas palibe kumene angathawile amalawi ana chenjela pano 😂😂😂😂😂
@FrankMkwala
@FrankMkwala Күн бұрын
Akutenga a Malawi ngat zisilu eti 😂😂😂😂
@TendaihMwenefumbo
@TendaihMwenefumbo 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 chimutu chachikulu ngati cha junda 😂😂😂😂
@KhalifabwanadoSaidi
@KhalifabwanadoSaidi 3 күн бұрын
Ndizaku lndia zimenezo inenso ndalowa ndawona ndi maso angawa koma guys ok ndiwonana popano
@PreciousChisale
@PreciousChisale 3 күн бұрын
amalawi adadzindikira panopa si malawi wa ma 1990s ai adzinamidza akumudzi omwewo
@PeterChombo-f5r
@PeterChombo-f5r 3 күн бұрын
Wabodza uyu ndipo asayembekezele kulowanso m,boma awa, zamanyazi
@LindaMalikita
@LindaMalikita 2 күн бұрын
Kukula mutu sizeru ay zamanyaz ine naziwa kale kt sikumalawi ay
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 18 сағат бұрын
Mbutuma iyi
@wedissonelitete2454
@wedissonelitete2454 3 күн бұрын
Evil that men do leave with them and leave after them
@Mickeykasambula265
@Mickeykasambula265 2 күн бұрын
Hahahahahahaha koma nawe zoyambana sukudandaula😂😂
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 күн бұрын
Afiti a satanic awa Chakwera ndi nduna zake zonse.
@ThoccoChimbali-h6g
@ThoccoChimbali-h6g 3 күн бұрын
Mbuzi ili inakulira ku mudzi, wakula akunyenga Mbuzi uyu
@ollensmsonda3686
@ollensmsonda3686 3 күн бұрын
Shameful
@JamesKamanja
@JamesKamanja 3 күн бұрын
Kkkkkk
@JamesMkomela-k3f
@JamesMkomela-k3f 20 сағат бұрын
Kkkkkkkkk
@ChisomocaxstonStima
@ChisomocaxstonStima 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂 komatu abale koma tipuma?😂😂😂😂😂😂
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 2 күн бұрын
Nduna zosaphunzira izi akachita chimutu
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 2 күн бұрын
CHIMWENDO BANDA NDI MBUZI KWAMBIRI ETI
@junaidibrahimishaaq
@junaidibrahimishaaq 3 күн бұрын
Zochita eni kupembeza mafano.
@RoseThindwa
@RoseThindwa 3 күн бұрын
It's really ridiculous 😂
@timothymphwina
@timothymphwina 3 күн бұрын
Koma uyu midzimu yakwiya chikangawa basi
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 Күн бұрын
Kkkkkkk fodya
@Kelvinbanda-c3x
@Kelvinbanda-c3x 3 күн бұрын
Chitsilu chamunthu ameneyu anamiza ndani
@etiennenyandwi058
@etiennenyandwi058 7 сағат бұрын
vuto ndi chimutucho
@AdamAhamad-k2i
@AdamAhamad-k2i 2 күн бұрын
Kumtumbo kwawo agalu a MCP anthu okupha awa
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 18 сағат бұрын
Nduna imandinyasa kwambiri
@LukwesaKamanga
@LukwesaKamanga 2 күн бұрын
Zomvesa chisoni😢Malawi wanga
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 3 күн бұрын
Ndiposo tikanangovota pompano tatopa nazo izi
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga 3 күн бұрын
Malawi camera mumakwana 😂😂😂😂😂 Koma bodza lake iiiii iii amalawi
@MalawianCamera
@MalawianCamera 3 күн бұрын
😂😂Zank yuu🎉😂
@IssahBannet
@IssahBannet 3 күн бұрын
Mbolo wako chimwendo chakwela ma pwala ako
@AliNtolera
@AliNtolera 3 күн бұрын
Kkkkkkkk amalawi
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 күн бұрын
Anyulatu ndipo kwambiri kkk
@EsetaGerate
@EsetaGerate 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂 machete chimwendo Banda 😂😂
@frankcassim
@frankcassim 3 күн бұрын
Chimwendo Banda ndichitsilu
@StewardKapoto-u7k
@StewardKapoto-u7k 3 күн бұрын
😅😅😅😅😅 nduna za MCP eeee ndinkhan zina
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 3 күн бұрын
Mcp yonse kuli makape okhaokha 😡
@WatsonMalanga
@WatsonMalanga 3 күн бұрын
Azolowera kuba kwambiri a mcp
@harrymicah6140
@harrymicah6140 2 күн бұрын
😂😂😂😂😂 aaaa koma adah
@SamNkhomo
@SamNkhomo 3 күн бұрын
Koma amalawi anazuka simungawa namize
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 күн бұрын
Mapolo yako chimwendo
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 күн бұрын
Chimwendo usandichimwitse
UMBONI WA PASTOR CHIWANDA - ANANDIUZA KUTI NDINAFA KALEKALE
34:49
Charles Shonga
Рет қаралды 2,5 М.
WORLD BEST MAGIC SECRETS
00:50
MasomkaMagic
Рет қаралды 54 МЛН
Офицер, я всё объясню
01:00
История одного вокалиста
Рет қаралды 3,5 МЛН
Inside Out 2: BABY JOY VS SHIN SONIC 3
00:19
AnythingAlexia
Рет қаралды 9 МЛН
MFUMUKAZI 25 SEPTEMBER 2024 pa Times TV
28:10
MALAWI 265
Рет қаралды 7 М.
Elizeo Bambo Nthalika: Tu quoque Brute.
27:58
Ndine Mkatolika
Рет қаралды 4 М.
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 43 М.
RESERVE BANK - Episode 171
9:15
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 22 М.
Sendera Sisters - A Peter Yo Yo Yo (Nyimbo Za Ndale)
4:11
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 15 М.
Amalawi tidzameta maliro a Chilima 2025
7:57
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 56 М.
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Senior Prophet Rodrick Mtupa SC
Рет қаралды 47 М.
Mfumukazi comedy series 25 September 2024
28:10
Grant Bandah
Рет қаралды 9 М.
WORLD BEST MAGIC SECRETS
00:50
MasomkaMagic
Рет қаралды 54 МЛН