RICHARD CHIMWENDO NDI SAVAGE - LYTON MANGOCHI KUGWIRIZANA NDI NAMIWA.

  Рет қаралды 8,482

Mpungwe-Pungwe mw

Mpungwe-Pungwe mw

Күн бұрын

Пікірлер: 47
@WilsonFelix-y7z
@WilsonFelix-y7z 4 күн бұрын
Mangochi apatu mutu wayamba kugwila wasia fodya uja eti?
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 4 күн бұрын
Very strong speech
@TonyMhone
@TonyMhone 4 күн бұрын
Tikanakhala ndi anthu 10 wonga awa dziko lino likanakhala penapake. Bravo bravo Namiwa and Lyton. Keep the fire burning
@Drmuhammadchiwona
@Drmuhammadchiwona 4 күн бұрын
We love you sir layton mangochi and we need more power
@beakab2378
@beakab2378 4 күн бұрын
Well said 👏👏👏👏
@AndrewMdala
@AndrewMdala 4 күн бұрын
Lyton mangochi apande wabwelamo amalawi akulila kuchikangawa ndipo chilima anachita kuphedwa koma a mcp mmmmm zikomo😢😢😢😢😢
@lyiemax
@lyiemax 4 күн бұрын
Powerful speech ❤❤❤❤
@EverlantNdeule-w6t
@EverlantNdeule-w6t 4 күн бұрын
Chikangawa mbunzi ya president
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 4 күн бұрын
Uku nde kubwera Comrade mangochi
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx 4 күн бұрын
Welspoken our comrade
@PATRICKTHlMZY
@PATRICKTHlMZY 4 күн бұрын
Kwayambazenizeni amangochi😂😂
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 4 күн бұрын
Ulemu wanu Mr mangochi we love you lots ❤❤❤
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo 4 күн бұрын
Panopa ndiye mwabwela madala mumachedwa pati😂😂😂😂auzenu
@FaheemChipojola
@FaheemChipojola 4 күн бұрын
😂😂😂😂 ndemwati aikidwa botolo ishiiiiii osati naoso adyetsedwa chibazi😢😢
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 4 күн бұрын
Bola osatembenuka🙏itatu timakudaliranitu bwana
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 4 күн бұрын
Mangochi apatu wabwela takulandila usapangetso za utsilu mcp ndi yokhupha osayiyimila ayi
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 4 күн бұрын
🙏🙏🙏🙏🙏Mangochi
@CatherineDesire
@CatherineDesire 4 күн бұрын
Iyeyo chakwera NDI big crocodile Male 🐊
@HarryKandani
@HarryKandani 3 күн бұрын
Mangochi ndalama za abusa a chikangawa zija zinatha eti? Mesa pakatipa unali busy kuyamikila zi anthu zokuphazi
@GrecianWyson
@GrecianWyson 4 күн бұрын
Welcome back Mr mangochi
@PetrusTlhokwane
@PetrusTlhokwane 4 күн бұрын
Apapa ndakupasa ulemu kuti utiyimila mcp yatikwana kwambiri kupha anthu osalakwa tiyeni a Malawi tizuke
@FrankKambwani
@FrankKambwani 4 күн бұрын
MCP ndiyamagazi zoonadi
@JoelKacheche-x6i
@JoelKacheche-x6i 4 күн бұрын
Iwe takhala pansi,pakati pa iweyo ndi akubanja la chilima amene akuyenera kulira mowonadi ndindani?musasewelese imfa ya chilima inu a dpp,kuti anthu akukondeni,mulibe mfundo yomveka kutula ziko la malawi.Mimba zanu mukhuta manyazi 2025 palibe kulowanso mmboma 😂😂😂😂😂
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 3 күн бұрын
Zatha ndalama anakupatsani zija?
@rodgersbotha2458
@rodgersbotha2458 4 күн бұрын
Wayambano u Malawian keep it up
@UncleShopRite
@UncleShopRite 4 күн бұрын
Apatu amangochi mukuimilano amalawi keep it up
@braveglorymwanzagolah4899
@braveglorymwanzagolah4899 4 күн бұрын
Wakabazadi uyu watikwana
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 4 күн бұрын
Ndulo ndiyankhula zomwezo zokhudza a PAC. Dzitsilu zawanthu zimenezi
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 4 күн бұрын
Ndege yokwanira anthu 18 akuti inadzadza mutalowa anthu 9👈MCP kills people.
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 4 күн бұрын
Wanenawanena basi osamva ndizake akomoka yekha
@JafarAustin
@JafarAustin 4 күн бұрын
Anamunamiza ndalama uyu
@EnockCosmas-x5x
@EnockCosmas-x5x 2 күн бұрын
Koma amangochi zayamba kukuyendelani tsopano eti
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 4 күн бұрын
Hahahaha Mangochi Layton 😂😂😂 tears master
@CatherineDesire
@CatherineDesire 4 күн бұрын
Chakwelatu salibwino mmutu kapita 😇👺😈basi
@davidkaduya6407
@davidkaduya6407 4 күн бұрын
MKAKA WANTHA MWATELO
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 4 күн бұрын
Amongochi muzingogwirizana ndi achina bon kalindo osadana ayi chifukwa boma LA chakwera siloti muzidana ayi inuyo muzingotiimilira A MCP tu ndi agalu achiwewe anamuluma mbuye ache chilima awa siathu
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 4 күн бұрын
Kkkkk kabaza man
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 4 күн бұрын
Zoonadi tiyeni a Malawi tigwilane manja pothanizana ndi anamiwa atiyambila chimwendo atiuze bwinobwino amene anamuuza kuti ndege asakwele ndani
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 4 күн бұрын
More fire a mangochi awuzeni chilungamo. chipani chakupha ichi kuba, kumanga omwe akunena chilungamo ; eish kom Ambuye atithandizani ndithu mdima ungakule bwanji? Kunja kumacha bas etu
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 4 күн бұрын
Kodi nkhani imakhala choncho uchisilu okhaokha munthu wanzelu angavere zimenezo
@GeraldGomati
@GeraldGomati 4 күн бұрын
Iweyo ulibe nzeru siwamvera nawo
@ChristopherKawilam
@ChristopherKawilam 4 күн бұрын
Iweso ndi kape eeeti
@Wisdommhango7dj
@Wisdommhango7dj 4 күн бұрын
Kma wayankhula bwino kwambili
@ChristopherKawilam
@ChristopherKawilam 4 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan 4 күн бұрын
Mangochi yemweo uleremuwako
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 4 күн бұрын
Crocodile 🐊 🐊 🐊 🐊 🐊 🐊 hahahahahaha
@LungoAli
@LungoAli 4 күн бұрын
😂😂😂😂😂
NKHONDO YAPAKAMWA - MORTON BAGHAYA KUBWENZERA JB
1:35:14
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 3,2 М.
Пришёл к другу на ночёвку 😂
01:00
Cadrol&Fatich
Рет қаралды 9 МЛН
LIMPOPO FM - TIKUKUONANI
36:34
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 6 М.
KUNAVUTA LERO ANYAMATA AWA 🔥🔥🔥🔥
1:17:11
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 3,6 М.