Ndichifukwa chake a Malawi nyimbo zanu sizipita patali bass ziiiiii kuzichemelera ngat umatha kuimba
@kelly_swiss Жыл бұрын
kodi ka ukali kaja ndinu et
@bruhanumar Жыл бұрын
Umatha aise
@emmanuelalinafemaliro4338 Жыл бұрын
Kodi ndi disi
@johnsonthebwez7191 Жыл бұрын
Mukukulatu koma kaya mukuziwa
@jamesphameya5489 Жыл бұрын
Ichi chokha wakwapula kwabasi
@migoraychimutu863 Жыл бұрын
Sounds like Young D penapake.... Komaso nyimboyi ndiyobhowa
@fundoworld2023 Жыл бұрын
WAKUKAKAMIZANI KUTI MUMVELE NDANI, TIKUZIWA KUTI YAKUWAWANI YOMUDISSA HENRY CZAR, YA UKALI.. KOMA OSAZITENGELA MPACHIBALE ANTHUWA.... CONGRATS SAME CRIS,,, YOUR STYLE IS ON ANOTHER LEVEL...
@blessingslyton1178 Жыл бұрын
Uli bho
@MisheckJonasi-v4b9 ай бұрын
Dolo😊
@harlodmakawa7587 Жыл бұрын
Nice style 🔥
@kenamapiri Жыл бұрын
Kugwetsa
@bmbboymstyles5894 Жыл бұрын
Utalimbikila chonchi utha kufika pena pake breda rather than kumangochulutsa kuimba zako zako zija,, I like ma verse omwe unaika mu nyimbo ya moyo *Joe kellz zobhebha 🎉🎉❤
@vardytheegoat Жыл бұрын
Same cris umamuvelatu nkaz wako mpaka model osamugwilako thako😂 Same to the 🌎 BIG S/O to benieeee🔥🤞🏾