Osaopa osafooka Suleman, chisiru chamunthu iweyo galu malondera
@MisheckAselo17 күн бұрын
Ababa Malondera panyapanu ndi chipani chanu chomwe cha kuphachi, tsiku likubwera mudzasanza 😂😂😂😂
@WysonChilonga17 күн бұрын
mkulu ameneyu ozelezeka eti😢😢😢
@FisherAction17 күн бұрын
Malondera ukugamula chipepeso chotero ndiwe jadge kodi ndale zophana muzasiya liti agaluinu mcp onse ofunira zabwino mw kt atukuke mongopha chirima ndi sidiki mia simunakhutisidwebe bwana Suleman please God bless you all
@johnkatapeh718216 күн бұрын
Never give up,,, chilungamo chimawawa ndipo sanati amva pain
@mollymasangano47316 күн бұрын
Hahaha 😆 😂 😆 😂 Ababa Malondera adzigopanga za ubaba zo basi Suleman has got the right ✅️ ♥️ 👌 say if he is in DENGER Akufuna ndalamazo❤ MBAVA OBABA ❤Claiming K3000,000 000.00 FOR WHAT???????
@MikochiKazembe-g7h16 күн бұрын
Kuba kumeneko alephera kuba moyo akufuna ndalama
@cmsanyama20016 күн бұрын
Osapepesa honourable Suleiman,fear no body as long as truth is in what you are complaining.
Director wa youth ku MCP ndi chitsiru chopusa kwambiri. Kape wachabechabe. Afuna kusauka kwake athesere kwa Suleman.. makape.. azingoba za anthu osaukafe
@PatsonKumwex17 күн бұрын
Umphawiwangomutopesa akungofuna kubandalama za wanthu.
@MaryJamali-w7t11 күн бұрын
Zazii!! Basi Kuba kumeneko apase ndalama yacha?
@alexjeremanuel254116 күн бұрын
Ndiye akamupatsa ndalamazo ndiye kuti a Suleman akuyeneratu kumapitilidzatu kuyankhula
@JaneMhango-zl6pt15 күн бұрын
Nanga ndizonama? A MCP ndi anthu a kupha. Akhala akumutsatila Suleman, sizabodza ai.
@SoldieNdovie16 күн бұрын
Sakunkhutila ndizomwe akuba mukuwasakadi akulukulu a dpp chilima sakukwanira pamanyi panu onse a mcp ndinu zisilu
@Bernarddavide-e1o16 күн бұрын
Zoona anthu akupha
@JamesBrown-gx8my17 күн бұрын
Walephera kumupha pano ukufuna umubere....mwana wa ng'ona😊
@BrotherLester16 күн бұрын
Baba malondela kuyalukatu uku ukutuma achinyamata mu Lilongwe molakwika ndiye walakwisa kwambili ndiyenso uku demanda ndalama after your mistake tikukuyang'ana ndi chidwi sichifukwa chokuti uli m'boma ndiye uziwatenga anthu ngati ziweto zoti ukhonza kumapanga zonwe ungafune upite kukhothi asakuyiziwa MCP ndindani ndinutu anthu akupha kuyipa mtima amene mwapha aja sanakwane mmaziwa inu ndikupha basi mfundo mulibe 😮😮😮😮😮😮
@HenzelMikolasi16 күн бұрын
They thought akapha Chilima basi athana ndi omwe angawapinge ndi chilungamo boom kwabadwa wina suleman ndipo uyuyu simumupha agalu inu Fire from heaven will always protect him
@DuwaAjissa-k8w16 күн бұрын
A Steve ndi amisala akufuna alemelele pa Suleman zaziii bas,
@ThocoThawan16 күн бұрын
Koma zinthu zake 😊
@CharlesSpencer-sz3rh16 күн бұрын
As long as he has evidence kuti mukufuna kumupha, basitu simungamunyumwitse. You can talk whatever you can, koma Suleiman can not be shaken. Mwamva?😊
@IreenChilingulo16 күн бұрын
Mau mboni alinawo sureman
@InnocentEdasi16 күн бұрын
Iwowoh akufuna kushinjilikiza,,, ife tikuziwa nzikomuno kuti a MCP ngokupha pamodzi ndi chakwera wawoyoh, ndiye asayelekedwe poti maina awo abwela poyele,,, sangabisale olo pang'ono
Ndipo osapeleka ndalama imeneyi ngati kuli kuba ayaluka ndithu
@BernaChauluka16 күн бұрын
Kuyesera zida zosalira kulizira band
@lestainmatenganya985016 күн бұрын
Kkkk koma ku mcp kuli zitsiru zokhazokha bwanji osangotulutsa black box kuti nkhaniyi ithe
@sparkdymon342916 күн бұрын
Zaziii ndiye MCP ndiyokuphadi
@DONNEXKhama-bk1gy16 күн бұрын
Kkkkkk chakuti Chawo kuzolowerera Moyo wakuba bas
@inackiShaibu15 күн бұрын
Mcp ndanyani akupa k
@PetroHerman-z5g16 күн бұрын
Ili ndibodza lochokela kwa bambo amene adamuuza Suleman kuti anthu afuna kuwapha
@JosephBotoman16 күн бұрын
Komano sulenan bwanji osapita ku court popeza umboni ulinawo,
@LastonMmanga-r2u17 күн бұрын
Nde akapanda kukupatsa kupanga chani??? 😂😂😂 Kuzolowera Kuba ndi kupha basi? Iwetu usova, pita ku khothi ukamang'ale koma ndalama sulandira cz MA umboni suleiman alinawo ochuluka😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉
@ChifundoBeston16 күн бұрын
Suleman alipile azitengera ndale zake pogwilitsa ntchito ma propaganda osiyana siyana. Akelo RC Banda naye alipilideso komaso KZ Ng'oma amulipile. DPP ikuona ngati amalawi ndiopusa kuti tizavotera chifukwa choipitsalana mbiri a MCP izi sizitheka. DPP ndi munthalika analephera kale sitingavoteleso.
@courageouslondo198616 күн бұрын
Angopita ku khothi kk mcp kuyaluka bas
@FlengieAustin16 күн бұрын
Kodi dzina mkumati baba😂😂😂
@yunusuPhili16 күн бұрын
Nkhani ndi Peter r
@MaxNanchapah16 күн бұрын
Zaugaru k300 million sapasidwa akasume kulikonse
@HandsomeManford16 күн бұрын
Zovuta kwambiri iZiii 2025 ali 🔥 fire
@ChisomoMkwinda16 күн бұрын
Lawyer I think mutu mwakemonso muli mamina okha okha a MCP anthu okupha ngati awa aaaaah
Ndizopusa zimenezo ndalama zachani akufuna aphe anthu angati katsegule mlandu wakoo mbuzi iwe ndizoona sakunama mukuduna kumupha a mcp nonse ndinu ankhaza mumadana ndi chilungamo dpp my vote mcp get out of my way