SAMEER SULEMAN WAYAMBISA KHALIDWE ILI NDE ANYAMATA ANALOWA MU GROUND KUTIBULANA

  Рет қаралды 12,463

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 37
@MaxwellKapalamula
@MaxwellKapalamula 18 сағат бұрын
Waganyu waku chipiku ndi ndani? Chakwera.
@SamzyFrank
@SamzyFrank 19 сағат бұрын
Let's gather here watch in Cape town great job 😂my vote
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa 15 сағат бұрын
Busa wanji? Ophaa khosa zake.zamanyazitu
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 19 сағат бұрын
MALAWI WATOPA NDI KHALIDWE LA CHAKWERA CHIKANGAWA KKKKKKKK ANTHU KUSWA KUSWA
@paulbanda9638
@paulbanda9638 9 сағат бұрын
Wanjala samamulowesa mu nkhokwe,mistake mwalowesa munkhokwe onyamula matumba ku chipiku
@RichardAlick-o8k
@RichardAlick-o8k 18 сағат бұрын
APM my vote 2025 Boma
@PatienceMphuche
@PatienceMphuche 9 сағат бұрын
Ukamaseweretsa mkazi wa mwini osamachedwa ndi mikanda😂😂ku Malawi nkokoma
@adeNuramo
@adeNuramo 12 сағат бұрын
Apm my vote😅😅😅😅😮 yomweyo chiksngawa iwe😄😂😂😂😂😊😊
@MonijaKataika
@MonijaKataika 16 сағат бұрын
Pangolin 💙💙💙💙
@masianobrighton
@masianobrighton 29 минут бұрын
Osakagula mafuta athire ma filling station kumati azigula a dpp okha bwaa tonse tikukhalira limozi pamzere ndipo njala kummwera osagula chimanga muzigawa kuti amalawi athandizike koma kutukwanana za ziii kaperekeni ndalama kumalampani opanga zithu zichipe kuti tionedi kuti mumakonda anthu kufuna kukaba poti mukuziwa mmene mumabera kubomako ovutika ndamalawi iwowo azapita kunja ife tikukhapana muno za ziii
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 19 сағат бұрын
Ndalamazo munakagula chimanga nkugawila anthuwo zinakakhala bwino kwambiri, izi zimafunika anthu atakhuta osati atagonela mango.
@Mmajayzet
@Mmajayzet 18 сағат бұрын
Iwe mbudzi kwambiri
@IbrahimMatola-k9p
@IbrahimMatola-k9p 16 сағат бұрын
Ndi mbudzidi imeneyo osakayiwuza nkhande ija bwanji yochedwa chikangawa ija kulu wakudambwe uja
@DoreenSankho-c6v
@DoreenSankho-c6v 8 сағат бұрын
Yomweyo chipiku
@OwenNyangu-nv1yt
@OwenNyangu-nv1yt 7 сағат бұрын
Nkhondo ija ndimeneyi sure
@MosesNHLANE-c2e
@MosesNHLANE-c2e 18 сағат бұрын
Ndale zaumve,mpaka kutukwana,ndale zakale ,chakufwa sandapange ndale zimenezo ,mmalo mopeleka mfundo mzingotukwanapo apa za zii
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 18 сағат бұрын
Maka Chimwendo ndi jersey kabwira eeeeish ndilibe nawo m'nunkhira😂😂😂
@masianobrighton
@masianobrighton 38 минут бұрын
Ndipo kutukwanako kusonyeza kusowa chikhalidwe ndipo ngati akutukwana munthu oti sakuwayakha ndiye apinduranji
@FundoNdeketeya
@FundoNdeketeya 19 сағат бұрын
Koma chakwera ndi president ovetsa chison ndithu akutichitsa manyazi kwambili
@KingsleyJambo
@KingsleyJambo 11 сағат бұрын
Anthu obwera awa asatisokoneze kuzolowera kuba basi
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 13 сағат бұрын
Kkkk ndizoona cikangawa amaseza matumba ku cipiku akatero akolope lero ndi pule ndicifukwa angoba
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 10 сағат бұрын
Nyimbo yoopyaaaaaa
@CorneliusSande
@CorneliusSande 10 сағат бұрын
Kakambani nfundo asatimbwererazi ayi inuyo zimba ngakhale wanthu ovotera inuwo adziwiratu kuti iyi ndi hade yeniyeni yasulufule.kusekana nzikundu anyani kkkkkkk.
@AmosPhilemon-y5e
@AmosPhilemon-y5e 14 сағат бұрын
Or Chakwera azakavotera peter kukana kupitiliza zamuthina
@MaxwellChabwera-y7x
@MaxwellChabwera-y7x 15 сағат бұрын
Mbambande APM my vote chakwera waganyu Ku chipiku azikhale ng'oma driver Ku Coca-Cola company kkkkkkk
@VincentAndrew-p8l
@VincentAndrew-p8l 14 сағат бұрын
Pangani zoti mudzawine mucheni nazo
@EmmanuelPoison-n5n
@EmmanuelPoison-n5n 12 сағат бұрын
Anthu apwetekana wina afandimtima
@HillstoneKabwazi-q9b
@HillstoneKabwazi-q9b 10 сағат бұрын
Tidzapnana pa tsiku lovoter
@AmosPhilemon-y5e
@AmosPhilemon-y5e 13 сағат бұрын
Suleman nd mwamuna
@EmmanuelkpPraise
@EmmanuelkpPraise 13 сағат бұрын
1:42
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 12 сағат бұрын
😂walankhula zowona zake
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 19 сағат бұрын
Yomweyo 😂😂😂😂😂😂 dpp woyeeeeee
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 19 сағат бұрын
Eeee km kuswakuswatu 😂😂😂😂😂😂
@HappyBirchForest-zy8nq
@HappyBirchForest-zy8nq 17 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 suleman ayayayaya iweyo km
@HolinessThindwa-pz5hw
@HolinessThindwa-pz5hw 11 сағат бұрын
Izi ndi mfundo izziiii aaaaaa Malawi iiiiiiii otsekerera mmmm
@HillstoneKabwazi-q9b
@HillstoneKabwazi-q9b 10 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@CharlesBanda-kv8bh
@CharlesBanda-kv8bh 13 сағат бұрын
Makaladi awa angayese kwawo kuno
Tsvangirai addresses crowds as Parliament sits to impeach Mugabe
8:06
Noodles Eating Challenge, So Magical! So Much Fun#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:33
Who's spending her birthday with Harley Quinn on halloween?#Harley Quinn #joker
01:00
Harley Quinn with the Joker
Рет қаралды 27 МЛН
Car Bubble vs Lamborghini
00:33
Stokes Twins
Рет қаралды 45 МЛН
MALAWI VS BURKINA FASO (NOV 18, 2024) HIGHLIGHTS
12:40
Kwagwanji?
Рет қаралды 12 М.
Michael Manganya Usi - Odya Zache Alibe Mlandu
5:09
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 41 М.
Noodles Eating Challenge, So Magical! So Much Fun#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:33