Eya zoonjeza anthu, lets build Africa on our tisamadalire america
@AbdulrazaqHussain6 күн бұрын
Like mandela said, "it's impossible until it's done ",l believe in us, so should you, Africa rise!!!!!!!!!!❤❤❤❤❤❤❤
@OssmanAbubaker-v7t7 күн бұрын
Pakufuninika Mahata Dennis alamulire osati enawa
@titosilver73137 күн бұрын
Sakulakwitsa mwakula mwatha, anthu akukhala ku USA komwe achokera uphamwi, we should wake up and create opportunities ourself the best thing we have God.
@osmanmdala-uh7xw7 күн бұрын
Akuchita bwino. Akutiphunzitsa ma Africa kuziimira pa okha
@AbdulrazaqHussain6 күн бұрын
Iook at Burkina faso, can't we learn something from them?if they doing it, so can we. Let's forget about Donald Trump, and focus on standing on our own feet, they just showed us that our lives are doesn't matter, stand up Africa, together we can achieve everything, Africa for Africans
@DaniloDavideRobate-i3u5 күн бұрын
Malawi tiku mu saukinsa tenkha
@OwenMkandawire-j2n7 күн бұрын
Nawoso azunguwo tiwadulisire zithu zathu monga miyala ya Gold,Diamond etc plus Mafuta.kwawo ku American kulibe kalikose kungonyada basi
Ku israel ma scientists anapeza mankhwala ochiritsiratu. HIV fufuzani pa internet and. Connect the dots.
@langsonmndalanga7 күн бұрын
Tiphudzirepo kuzidalira
@SeventeenSosten7 күн бұрын
Uyu atipweteka 🥱
@BlessingsMuheliwa7 күн бұрын
Uyu apha gulu
@Chitani1007 күн бұрын
😂😂😂 Otsamenya bwanji 😮
@MaxonKambazithe7 күн бұрын
Munavotera nkhondo kuti ipitirire ku Israel 🇮🇱 pita konko chakwera ukapephe chithandizo uyu singathe atilephera
@Mohammed-sk1fy7 күн бұрын
Ndeno ""Bingu"" anat chan plz tell me "Sam",,,......
@Riah80916 күн бұрын
Bingu ndi amene anayambitsa zoti adziwike mankhwara a ma A R V anthu amangomwalira chifukwa chakuti tinali tisakudziwa zoti kuli mankhwara otalikitsa moyowa
@Mohammed-sk1fy6 күн бұрын
@Riah8091 Oooowh apa ndakumvan komaso ndaziwaso ""Thanks""
@OmariWasili-hx4cs7 күн бұрын
Mabunkhwa osewa? Komulova osata😏😏
@PempheroAĹLI7 күн бұрын
Athuwa ndi akuba owonekere bas Lazaro
@FilbertKomba-fi2nl7 күн бұрын
Amalawi kudandaula iyi alibe anzao kodi mabungwe ali.kumalawi malawi ilipinduka Chani Olo atatetsa kutandiza ngati ma ARV Tipanga atu a mitengo ya chilengedwe basi