The resignation of her honor Madam Nyalonje from doing her work in the current government brings back tears and sorrow over the death of the VP - SKC. Malawians will keep morning for the VP. SO SAD INDEED. May his soul rest in peace.
@EmmanuelNgamuti11 сағат бұрын
She is not the first minister to resign!
@wonderfullomoliwa5380Күн бұрын
The first minister to resign as cabinet minister was Clement Chiwaya, when Bingu dumped UDF and formed DPP in 2005. Nyalonje is not the first one to do so
@tingo3155Күн бұрын
Mulira simunati
@BlessingsMassiКүн бұрын
Bravo madam
@haroldfodya7071Күн бұрын
Bravo mama protecting u CV is very important
@Chikwawa3 күн бұрын
Bravo. Chikondi choonadi. Osati Zakeyu ndi amnzake ena.
@cmsanyama2003 күн бұрын
Great is Nyalonje
@PeterMwakihana2 күн бұрын
Only God fearing person can do that osati ena adyela ife
@AlexanderTraffick3 күн бұрын
Ingokambani zakutura kwake udindo..koma sikuti oyamba ndiiyeyo chiyambireni 1994 . mbuyomuso zimachitika koma Social media kunalibe ..FB ndi UTube taidziwa zaka zapompamo... And Atupele anatura pasi udindo wake zinthu zikukoma .ndambili mufufuze bwino
@felistassumani3 күн бұрын
Which ever. Zakukhudzani mowawa Eti? The political landscape has changed. Dziko lidasintha ili. Anthu otere ndi ochepa. So congratulations to her are on order.
@fahadcade5123 күн бұрын
Komaso boni karindo anaturaso undindo
@GoodsonBilliatkanyoza-e5m3 күн бұрын
Mayi nyalonje ndi munthu yenwe safuna kukonda ndalama kapena udindo koma akuyang, ana komwe wachoka komanso infa ndi ubale omwe unalipo pamgwilizano WA alliance sizinayende bwino mpaka wina kuluza moyo eeiish zachisoni
@MathewKalinkhu3 күн бұрын
Ulemu wa mai Nyalonje. Ndipo akudziwa kuti boma ili palibe chomwe likuchita. Wachita bwino kwambiri mai.
@Austin-b4r3 күн бұрын
Watching from south Africa ❤❤❤👌
@MacleanLungu-q5w3 күн бұрын
President will choose another to take the position
@MaxwellBabarcheWhisky4 сағат бұрын
Well done Agi.
@BlessingsNgomba2 күн бұрын
She is not the first. Austin Atupele Muluzi did it during the era of Dr Joyce Bandai.
@MacleanLungu-q5w3 күн бұрын
Our president don't be shaken you will win the position of mcp
Mmene chakwera ndabali ake anamuphera Chilima mowawa a Nyalonje sangalephere kutula unduna pansi . Kukhalira kuphana basi yoooo!
@ShamimuBisani3 күн бұрын
Bob Khamisa anazatulas pansi udindo osati mayiwa ndi oyamba koma aonesa ukaswiri mu nzeru mzawo mai obereka uyu God bless her and be strong mum we love u
@MussaLenard-s2t3 күн бұрын
🎉🎉🎉 ulemuwanu mama👏
@StanleyMunthali-s1d3 күн бұрын
Uku ndikuyiwonera Game patali . What elderly people can see while sitting down children can't see while standing !
@DalitsoSaidi-zm7yl3 күн бұрын
Inu mu dziko muno, Atupele anatulapo unduna mu nthawi ya JB Late Sidic Mia did the same mu nthawi ya JB towards 2014 elections... Kunena kut nd koyamba nduna kupanga izizi kuchokera mu nthawi ya Bakili muluzi sizoona go and check mbiri iyiyi mukaipeza I forget late goodall gondwe anapanganso izizi mu nthawi ya JB he step down as Minister of Economic planning
@BerthaMuyangwe3 күн бұрын
Aunt Agness may God guide you and protect you in everything
@FloraBanda-l2s3 күн бұрын
She is not a member of parliament
@innocentmtungambera49053 күн бұрын
Nyalonje si MP analuza kwawo. Komanso siwoyamba kutula unduna .Sidiki Mia anatulanso boma la Joice Banda, Henry Phoya anatula nthawi ya Bingu. Mordecai Msiska anakana unduna mboma lomweri komanso Chakufwa Chihana anakanaso unduna nthawi ya Bingu
@HwiwhHahaha3 күн бұрын
Let them learn by action..... More faaa mama
@MarkElia-i7q3 күн бұрын
Nduna yoganiza bwino Dyera alibe Mayiyu We need good Leadership like what nyalonje Does
@ShearstonNyirenda2 күн бұрын
Kunzimba north chao kulibe sangawineso awa palibe chapangap iwowo ku constitutience kwao
@edsonnyasulu53943 күн бұрын
Apa athandize kabambe ndikutukula utm
@RobertChimenya-j7c2 күн бұрын
Akuziwa zambiri zokhuzana ndi imfa ya skc zambiri ziululika wina athawa dziko lokhala lake
@MavutoDuweКүн бұрын
Good wavibekera patali
@BistonMacheso3 күн бұрын
Boma kachakwera ndilokupha chifukwa atula Pasi unduna mai wo APM boma
Atupele muluzi anatulaso pasi unduna thawi ya Joyce banda
@ChembeWaimba3 күн бұрын
Zaka zonsezi kuzatula pansi udindo lero Chaka cha mawa ma vote wadya zingati za ziiiiiiii
@corretabanda76853 күн бұрын
Anatula pasi udindowu mu July koma a Pule ankakana muzimvetsa zinthu
@FredKanyerere3 күн бұрын
Great to her Nyalonje mother of year.
@sichalibosswell77983 күн бұрын
Title ya video ndizomwe zili mu video zosagwirizana, nanga mukuti chifukwa chomwe Agness watulira pansi udindo yet mu video mulibemo zifukwa, inuso simukuziwa, stop kuti wonongela data
@EdiwardPondamali2 күн бұрын
Adakondedwa ndiudindo komso alino muguli limodzi ajera uja amenayu osada
The first minister to resign as cabinet minister was Clement Chiwaya, when Bingu dumped UDF and formed DPP in 2005. Nyalonje is not the first one to do so