Chifukwa Chomwe Nankhumwa Akusalidwira Ndi Zipani Zina!

  Рет қаралды 19,679

Sam Malvitha

Sam Malvitha

Күн бұрын

Пікірлер: 57
@ThokozaniBondo-em9fr
@ThokozaniBondo-em9fr Күн бұрын
Kkkkkk aziwona ameneyo thira kuwiri anzakewo akumudziwa
@ThomasSalaka
@ThomasSalaka 3 күн бұрын
Keep on fighting Nankhumwa you are going to make it.Rome was not built in a day
@CharlesNdalama-q2w
@CharlesNdalama-q2w 3 күн бұрын
Nankhumwa ndiwa mcp
@IslamMapepa
@IslamMapepa Күн бұрын
Pita simuthu wadyela abwelele akamulandila ndimtima onse
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 3 күн бұрын
Am speechless Malawi why why
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 күн бұрын
Mesa mukati amamutuma ndi chakwera mwazindikira kuti chakwera mumamunamizira
@katalamajames4947
@katalamajames4947 Күн бұрын
nankhumwayo ndisilu asachiloleso ku dpp chipite ku m.c.p chifukwa ndiamene akamupopa kuti azipanga manyi ake aja akapanga aja
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 2 күн бұрын
Sakumusala Nankhumwa akunati azayenda yekha
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 3 күн бұрын
Chilima musamufanizile ndi munthu wina wa ndale kumalawi chilima anali katundu
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 күн бұрын
Ndipo zoonadi
@Sofi-p1v
@Sofi-p1v 3 күн бұрын
Snake in the glass we don't need him ku dpp
@ThomasMkweza
@ThomasMkweza 2 күн бұрын
Nankhumwa nkhuni zasuluka kuipa kwankhuni mkumeneko azidalila kumwamba
@peterwadi1774
@peterwadi1774 2 күн бұрын
Nkhumba iyi ndi mthira kuwiri mbuli
@YusufRphiri
@YusufRphiri 2 күн бұрын
Abwerere ku dpp
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 3 күн бұрын
Nankhumwa ndimwana owukilq ndi nthila kuwili ngati manganya
@WillyZuze
@WillyZuze 2 күн бұрын
Ndizotheka kondwani nankhumwa kubwelera kwa ADADI ndipo azalandilidwa monga mwana wolowelera
@DaitonMmola
@DaitonMmola 2 күн бұрын
Asabwelelemo Ndi.osokoneza.nankhumwai.ku
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 3 күн бұрын
Aaaa wa mcp uyo mutsyeni
@ElickBanda
@ElickBanda 3 күн бұрын
Nakhumwa ananyoza kholo lake pajat amat mwana onyoza kholo ayenela afe ndithu😅
@FosterTonnex
@FosterTonnex 3 күн бұрын
😂😂😂
@BrightonChidzalo
@BrightonChidzalo 3 күн бұрын
Nankumwatu akuyenera kubwerera kwa bamboo are osati zamisara anapangazo komanso anpupuluma kwambili akanaganixa pafika Peter uja bwenzi atadutsa money abwerere akamulandila Peter ndiwa ntendele
@GiftMusorola-l2o
@GiftMusorola-l2o 2 күн бұрын
Zaboza ukunenazo sukuziwa zomwe zikuchitika mkati uzapusa
@shustahdagii
@shustahdagii 2 күн бұрын
ndiwowukira ameneyo
@xinalungu9616
@xinalungu9616 3 күн бұрын
Ndi kagulu kaja ka tsankho kajaaa!!!
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 2 күн бұрын
Ndiwe wabodza iwe nanga chipani cha prophet mbewe komaso chipani cha kuwani bwanji sukunenapo
@DadTshepo
@DadTshepo 3 күн бұрын
Iwe Nankhumwa Chipani chake chikuthandizidwa ndi MCP where else can he Go akumusupa ndalama daily
@xinalungu9616
@xinalungu9616 3 күн бұрын
Kabambe nayenso akhala ndi vuto lomwero. Tsankhoooo!!!!
@BillyChisale-m1z
@BillyChisale-m1z 3 күн бұрын
Munthu uzizichepesako pa gulu osati Kuti udziwike Kut ndiye odziwa kuyankhula chitsanzo Omani kaliati lelo
@SmartGowani
@SmartGowani 3 күн бұрын
Anapanga zopoila aziwona
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 3 күн бұрын
😂😂😂😂 koma iwe ada
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 күн бұрын
Apite ku utm akamulandila
@JamesYusufu-m4r
@JamesYusufu-m4r 3 күн бұрын
abwelele bass chiseko ndichosegula
@FladielMwase
@FladielMwase 3 күн бұрын
abwelere ku dpp bas nankhumwa😂😂😂😂
@ScentVisual-ke3zw
@ScentVisual-ke3zw 3 күн бұрын
Anangoziyamba😢
@ChineduNyika
@ChineduNyika 3 күн бұрын
Utm yatha nayo anthu akukomokera u president
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 күн бұрын
Mbolo yake😂
@IvyChithyoka
@IvyChithyoka 3 күн бұрын
Ndi wa mcp
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi 3 күн бұрын
Iwe ndimunthu opusakwambiri
@DaitonMmola
@DaitonMmola 2 күн бұрын
Matukutuku.akanangokhala Ku.dpp.osachoka.
@MariaMlanganiza
@MariaMlanganiza 3 күн бұрын
Akabambe tukuthokozani pazimene mwawonetsa pitilizani kukhala ndi ntima ngati wa saulos chilima osaopa asafooka tili pa mbuyo panu 2025 boma
@SandikondaIsaac
@SandikondaIsaac 3 күн бұрын
Nankhumwa anazilakwira
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 3 күн бұрын
Nankhumwa anapanga mwano kwa dad ndiye mulungu a ati mwana wa mwano alangidwe akulangidwa amene yo ankamutuma aja aku mutsika bwanji mutayeni wonse a mwano a ziona chaka chake ndi chino akwni bwa agwa chaganaso bwa
@LisaChiutira
@LisaChiutira 3 күн бұрын
Abwele basi😅
@VeronicaSekobi-is6dk
@VeronicaSekobi-is6dk 3 күн бұрын
❤🎉
@alibwana4452
@alibwana4452 3 күн бұрын
😢😢😢
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 3 күн бұрын
Ngati inuyo a udf ,pp,inuyo amai na Atupele mupita nokha ku mcpko ifeee amalawi tooonse ambiri sitikusatana aiiiiiiiii
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 3 күн бұрын
Wacepa nazo amkaziputilanji vuto la dyela ndilimenelo akungotaya nthawi ngati angafune abwelele ku dpp adad akamulandila, ngati sakufuna akhale dpp singalephele kuwina cifukwa ca iyeyo.
@NyangwaKoma
@NyangwaKoma 3 күн бұрын
Abwele timulandila
@MangulenjeTwangu
@MangulenjeTwangu 3 күн бұрын
Wachipongwe uyu
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 3 күн бұрын
Muthira kuwiri, amakhala oipa kwambiri
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 3 күн бұрын
Zamuvuta uyu basi
@AlesAlesi-p3w
@AlesAlesi-p3w 3 күн бұрын
Abwerelenso NAnkhumwe kuDPP
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 3 күн бұрын
Sililimba pokhapokha apite ku utm
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 күн бұрын
Ndipo timulandila
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 3 күн бұрын
Dpp nayo yatha
@FelixNyirenda-c4y
@FelixNyirenda-c4y 3 күн бұрын
Waboza iwe wakhuta eti?.
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 3 күн бұрын
Zina umangoona waziyamba 😢😢😢
Новости дня | 29 ноября - утренний выпуск
11:40
Euronews по-русски
Рет қаралды 22 М.
Из какого города смотришь? 😃
00:34
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 2,7 МЛН
Мама у нас строгая
00:20
VAVAN
Рет қаралды 11 МЛН
За кого болели?😂
00:18
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 3,3 МЛН
Ching'aning'ani comedy, ft Ngiringande
6:53
Malawi Page
Рет қаралды 370 М.
VN Ya Lero Andale Ambiri Adananane - Ken Msonda
29:04
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 9 М.
Ticheze Nawo Lero- With Dan Lu
17:45
Nkhwachi Peter Mhango
Рет қаралды 241 М.
Kabambe Si Wa UTM ... Ichi Ndifukwa Chomwe Anthu Akumuukira...
5:44
Debunking the Gandhi Myth: Arundhati Roy
25:38
Laura Flanders & Friends
Рет қаралды 777 М.