Рет қаралды 794
Mpingo wa Mulungu wa dzikhazikitsa wokha m’maiko 175 okhala ndi mipingo yoposa 7,500.
Mpingo wa Mulungu umaonaanthu padziko lonse lapansi ngati banja limodzi,
ndipo umapereka chikondi cha Mulungu pokhazikitsa mipingo padziko lonse lapansi, kuyambira kumapiri a Himalaya mpaka ku Alaska mpaka ku nkhalango ya Amazon.
“Mpingo wa Mulungu ndi mpingo umene anthu akhala akuuyembekezera.
Mpingo wa Mulungu ndi mpingo wokha umene umatsatira pangano latsopano limeneYesu
anakhazikitsa ndipo Atumwi monga Petulo ndi Paulo analisunga.”
Wa ndile, Attorney
“Ndaphunzira zambiri, kuyang’ana pa Mpingo wa Mulungu.
Nthaŵi zonse amakhala ndi malingaliro okhudza kusunga mtendere panyumba ndi mtendere pakati pa anthu.”
Xiuhan, DGACM wa UN Personal Assistant
“Tonse ndife mbali ya banja lathunthu.
Tili ndi Atate ndi Amayi.
Ndipo izo zimapangitsa Mpingo wa Mulungu kukhala wa padera.
Mpingo wa Mulungu uli wa moyo.”
Michael King, Civil Engineer
#Gulu laUtumikiwaDzikoLonse Lapansi Mpingo wa Mulungu #MpingowaMulungu#Ahnsahnghong#Mulungu Amayi #Amayi Akumwamba #Vidiyo ya Chiyambi
[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]
〖World Mission Society Church of God〗watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 introwmscog.com