Speech - Michael Usi Takes Office as Malawi's New Vice President

  Рет қаралды 62,590

Amuna Misso Tv

Amuna Misso Tv

Күн бұрын

Michael Usi Takes Office as Malawi's New Vice President

Пікірлер: 45
@Richardbanda-hg6pt
@Richardbanda-hg6pt 3 ай бұрын
Welcome Mr.michael ussi u're Agood Governor to the Nation of Malawi all the Best ❤
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 3 ай бұрын
Very sensible speech Vise president usi
@kearabetswemashego3084
@kearabetswemashego3084 3 ай бұрын
Uyu akuziwa. Imfa yachilima
@christieprince6991
@christieprince6991 3 ай бұрын
Very Eloquent. May God enable him serve wuth resounding success.
@EphraimKawinga-tx8tu
@EphraimKawinga-tx8tu 3 ай бұрын
Zazeru kwambiri! justice!
@Okalekale
@Okalekale 3 ай бұрын
We shall hold you accountable should thieves remain in the government atealing from poor Malawians Dr.Usi.Musapusise aMalawi apa.Tazakukumbusani mau amenewa.
@tiwongehojaney5873
@tiwongehojaney5873 3 ай бұрын
Ndipo amalawi simukudziwa kut uyu ndi wa mcp ameneyu munthu oipa uyu asaaa
@IssacMateyo
@IssacMateyo 3 ай бұрын
Iweyo ndiye wabwino ndipo ubwino wako akudziwa ndindani
@IssacMateyo
@IssacMateyo 3 ай бұрын
Iweyo ndiye wabwino ndipo ubwino wako akudziwa ndindani
@AmbronzioKondwani
@AmbronzioKondwani 3 ай бұрын
Sibasi Chakwera akafa week ikubwerayi mr Usi president 😂😂
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 3 ай бұрын
Sangalole mkaka 😂😂😂
@sylvesterfrank4259
@sylvesterfrank4259 3 ай бұрын
dziko lapansi ndilomvuta kwabansi
@jaimeerfassesimango6395
@jaimeerfassesimango6395 3 ай бұрын
Ine ndi wakumozambiqui ndimafuna ndikambe ndi inu amalawi, muphunzile kukonda azitsogoleri wanu, aliyense asakhale woyipa kwayinu. Michael Usi, ali ndi ndale zabwino mutamuthandiza akuthandizani, koma mukamangotsutsa aliyense mudzakhala wovetsa chissoni mpaka kalekale. Aliyense akalowa adzifuna abeletu podziwa Kuti zivute sizavute anthu samukonda pakangodutsa mitezi iwiri.
@DonaldPonda-p2q
@DonaldPonda-p2q 3 ай бұрын
Nfundo zonsangalasa chakwera osati anthu idzi
@ShearstonNyirenda
@ShearstonNyirenda 3 ай бұрын
Good speach ussi congrats
@richiePushie-hq5cy
@richiePushie-hq5cy 3 ай бұрын
Nothing I can say. I'm still recall legend Chilima 😭😭😭
@Dauson-j5i
@Dauson-j5i 3 ай бұрын
Takulandirani a new vice president mwayandikirapo sopano mukwanilise maso mpenya omwe munali nawo musaiwale before thanks
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 3 ай бұрын
Audi anthu akulirabe maliro inu mukusangalala ndikufa Kwa Chilima .
@flourencejamu6455
@flourencejamu6455 3 ай бұрын
Mulungu muthandizileni akwanilitse mawu analankhulawa
@Richardbanda-hg6pt
@Richardbanda-hg6pt 3 ай бұрын
Pliz solve all❤problems and not cause problems Amen
@GeorgeMvula-pc9rg
@GeorgeMvula-pc9rg 3 ай бұрын
Koma Malawi waphweka ndithu, ndipo zafika pomvetsa chisoni. Kulibe chomwe chingasinthe Ku Malawi.
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu 3 ай бұрын
Ukunjoya usi ndi chakwera zoona chilima munamwaliradi tikulira chilima wanthu 😭😭
@krrishinvest4666
@krrishinvest4666 3 ай бұрын
watipatsa hope manganya yuu
@leoleonard2103
@leoleonard2103 3 ай бұрын
Iweyo usi ndi chakwela mudziwana zomwe munapanga pa chilima
@Imraanjafali
@Imraanjafali 3 ай бұрын
Sorry for this malilo anu tiyika soon osadanda mbuzi ndi mbuzi munachitadi tamva ndithu koma chakwera matha ake akuchulukilabe ungaziwe mbuzi iwo usi
@EsnartChipongwe
@EsnartChipongwe 3 ай бұрын
Very sad speech
@takesurenkhoma3031
@takesurenkhoma3031 3 ай бұрын
Anayankhula bwino
@anniekanyenda3016
@anniekanyenda3016 3 ай бұрын
😅😅😅Umangoona wayankhula
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 3 ай бұрын
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😱😱
@sizwekamala9264
@sizwekamala9264 3 ай бұрын
Chitsiru ichi palibe chimene chingapange
@chiyedzoaeverson2336
@chiyedzoaeverson2336 3 ай бұрын
Usi ndi chilima zochita zawo ndizimodzi
@henlyyassin1718
@henlyyassin1718 3 ай бұрын
Is black box plane crush for chilima”s death found??
@stelladabreu1819
@stelladabreu1819 3 ай бұрын
Speech of understanding with wisdom.
@christieprince6991
@christieprince6991 3 ай бұрын
He is strong 😮 Pray for him yo be successful in service
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 3 ай бұрын
Kkkkkkkk avice anthu amenewo kkkkkkkk😅😅😅😅😅😅
@robertkalima874
@robertkalima874 3 ай бұрын
Welcome home Sir.
@leoleonard2103
@leoleonard2103 3 ай бұрын
Vice President wanthabwala
@EsnartChipongwe
@EsnartChipongwe 3 ай бұрын
Uyu muntu sachita mushe mwaandi so
@RobertNyaude
@RobertNyaude 3 ай бұрын
Dolo iwe kkkk
@IssacMateyo
@IssacMateyo 3 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🤟👍
@GiboSunset
@GiboSunset 3 ай бұрын
Ala, mxiiiiiii,zakuntumbo mwapha chilima nde mudziti fwefwefwe,chauta akulangeni
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 ай бұрын
Kakupha aka njoka iyi
@johnarushamasese108
@johnarushamasese108 3 ай бұрын
Ana usawi
@MoosaSame
@MoosaSame 3 ай бұрын
His involved for Chilima death
How Strong is Tin Foil? 💪
00:26
Preston
Рет қаралды 116 МЛН
Cute
00:16
Oyuncak Avı
Рет қаралды 12 МЛН
My daughter is creative when it comes to eating food #funny #comedy #cute #baby#smart girl
00:17
FREDO MASINTHA
12:07
Fredokiss
Рет қаралды 54 М.
Nigeria Billionaire Dangote on Fuel Subsidy, Oil Prices, Football
26:00
Bloomberg Television
Рет қаралды 266 М.
Highlights: FCB Nyasa Big Bullets 3-2 Creck Sporting Club
9:26
Nyasa Big Bullets
Рет қаралды 18 М.
How Strong is Tin Foil? 💪
00:26
Preston
Рет қаралды 116 МЛН