The way I love this song ndimachitakuva ngati ndafika kale kumwamba. The bass eish❤❤❤❤❤
@emmakamowa85822 күн бұрын
Ndadalitsika,the uplifting song indeed
@KetDan-o8p15 күн бұрын
Amen ,kuli mtendele
@SamuelLapken-v1e9 ай бұрын
Dzulo munabhebhetsatu ku Mvama CCAP, 🤩
@mayamikomnolo70329 ай бұрын
it was great
@MalindaJohn-h5u18 күн бұрын
Zonyaditsa kwambili Brother
@endtimes-b3h4 ай бұрын
It built my confidence in Christ Jesus from the first day things fell apart in my life and ignited new life that all these shall pass.
@ellenkadammanja7197Ай бұрын
Amen,kuli mtendere
@BakhitaJohn-d2yАй бұрын
Kma kumwamba ndimalo abwino 😊 nyimbo iyi imanditengera kutali
@JohannesMachobane2 ай бұрын
Amen and amen timava nanu kukoma kwambili ❤❤
@EnockNandolo27 күн бұрын
My sis inuyo mumakwana ine nkanakonda titakumana nkuuze umboni wa mbiri Ku chokera mu nyimbo ya mwanakazi thamanga aaaaaaa you are indeed the blessed one
@HerlooneySameerАй бұрын
Ndimaimvera daily nyimbo iyi mwaombola moyo wanga❤
@HelenaSumylaCoimbraАй бұрын
Nyimbo idhakakoma kwambili kukadhakhala kuti tsikana waimba kwachili unja ndiewotsogolela. Nyimbo yabwino zedi
@EnessKapumaManda5 ай бұрын
Ndikuva kukoma kwambili ndinyimbo imeneyi mukandiona ndikusangalala ndiyesuyo basi