Amen good wafunsa funso labwino mkazi wa mkulu mahule wa ndi anthu oyipa wake kunalibe
@MeltonMumba-rn9mf5 ай бұрын
Exactly
@patrisiobinalison84764 ай бұрын
Uyutu sihule ,mkazi wamkulu pomwe analakwila ndi kuvomeleza mitala
@GiftCMlangeni4 ай бұрын
Mind your tongue remember ngati pali hule ndi abambowo not mkaziyo. Am also aman how can idate wantchito wanga? Mesa amkagwirantchito nde amakapempha banja ngati? Wamkukuyo adavomeleza bwanji mitala nde chitavute nchani kungomugawirako kuti asathe nthawi yaboma? Kungoti ndikupatsa business imodzi or minibus imodzi basi nkhani yatha. Komaso akuiwalakuti chuma chimatha, dzina la abambowo lilindi wamwamunayo, enawo mawanja akakavuta adzamufuna nchimwene wawoyo?? Nanga mayiwa akadzakalamba akaziwa adzakwanitsa zonse zomwe zimafunika mamuna akhalepo?? Mmmmh kuipamtima kukuoneka apa
@MakhumboNyasuluАй бұрын
Shaaaaa
@MadalitsoBokosi-j3u5 ай бұрын
Na ngati wakulu adavomera kt ndi mitala ali mwana wa bambo chuma amupase komaso amupase 25% yamwa make 10%nkhani yatha
@sharifujoe76335 ай бұрын
Camera man is 🏃♂️ runner
@ganizanizuze71043 ай бұрын
The second wife is very genius
@AshleyMbewe-k5z4 ай бұрын
I second with you bro,the rulling is very important
@PamelaSumbuleta3 ай бұрын
Koma chigamulo ndie chikuchedwa bwanji kkkkk
@PaulBambe-m3t3 ай бұрын
Where is the ruling. I need it pliz. Give me a link 😂
@FrankNyoni-pm3jz4 ай бұрын
What was the final judgment ?
@MaxwellMagowajmphiri24 күн бұрын
Mmmmmh zowopsa😢😢
@KafelaMwaleАй бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣kutengeka.... mg 2 ndiwe galu.
@TabithahLloyd-z4t4 ай бұрын
I don't think kubeleka mwana wammuna chikhale chitonzo pa anzawo , iwo adakangopempha thandizo la mwana osati mpaka chuma chifukwa mkazi wankulu kuvomeleza mitala sindiye kuti chilichose chomwe ali nacho ndye kuti nkazi wango'ono akhale nazo
@LovenessKathumba-d1m8 күн бұрын
I need to hear the judgement
@hajikasaku60543 ай бұрын
I like second wife she had a good question to first wife
Mxiiiii ndimmene yathera ? No chigamulo kupereka fotseki
@MwaleYankhoKatanga-k3e5 ай бұрын
The first daughter is coming with some juries and want to run away from this as solution
@christopherpetro-pen36784 ай бұрын
Targe me pa chigamulo day🤸🤸🤸
@HenryLaidon-pl9ly4 ай бұрын
1st born wa Dzanja from MG 1 uli ndi umunthu coz pa dziko pano uli ndi brother wako mmodzi from MG 2 komanso ndi mwana musamalire, komano zolinga ZENIZENI za MG 2 PA mlandu wu aaaaaa chabwino tiyeni tione kuti MALAMULO akuti chiyani
@KhalidYusufu10 күн бұрын
CHUMA cha masiye mkazi Ali ndi gawo lake komanso ana Ali ndi gawo lawo Mzimayi uyu she deserves to have her husband property komano timayang'ana chuma chomwe chomwe chapezeka during her time except mwanayo
@giftthexy5 ай бұрын
Next please
@CleemelLucretia4 ай бұрын
Is this acting classes?
@WillardPatrick-h9s3 ай бұрын
Yes but helpful
@DavisonBanda-u8k4 ай бұрын
Kod akumbumba kwa malemuwa akut chan pa nkhaniyi
@MoyendaWBequiet.4 ай бұрын
Zili bwino ndithu keep it up
@vestarmkandawire61385 ай бұрын
Mkazi wa chigololo ameneyo ndi mbuzi,, banja ndi ndalama ndi zinthu ziwiri zosiyana. Mkazi woyamba ayankha bwino kuti adavomereza mwamunayi akhale awose osati chuma. Ndiye huleyo chuma chake ndimwana wamwamunayo. 1 Akumbukire kuti anali wa ntchito wa mayi wamkuluyo 2 wamulakwira kumulanda mwamuna wamwini. Apapa kunena zoona chuma asamugawire ndi wakuba mayiyu. Zikuonesa kuti wapha mwamuna ndiye kufuna chumacho.
@AwufWaria4 ай бұрын
Wolakwisa ndi mayi oyambayo povomereza mitala,chuma chiyenera kugawidwa basi
Vuto lowakhira nkhani pali za uhule apa mesa akuti unali mgwirizano oti ayese zida abambowo amafuna mwana wa mwamuna ndye atafunsidwa amayi akuluwo anavomera kuti vuto palibe atha kukhala pa mitala mwayi uwo mimba mkubwera akabadwe mwana chimphongo ndye kuti mdala Ku khosi mbeeee kuti mission yatheka mwana wa mwamuna wapezeka. Ndye chomuchulira kt ndi hule mumakhala chili chani....?????
@MilwardChanza-mr4yr4 ай бұрын
Mkazi wachiwiri anakakonda anamkagaila ma percentage angat?
@jameswajumpha67904 ай бұрын
Waiting for next part
@alickmphalasa51674 ай бұрын
That's why singazalembe wa tchito wachizimai ine 😅😅
@NedsonKennedy5 ай бұрын
The best way is, write willo b4 pass away 😂
@WilsonPhiri-vl1di4 ай бұрын
Exactly
@McDonaldKanyinji5 ай бұрын
As long as the first wife accepted that they were on polygamy, the worth is suppose to be shared according to how many kids each wife has......... but not equal..... Court should observe this.❤
@marthachapepa67292 ай бұрын
Share the properties, waiting for ruling
@gracejere4524 ай бұрын
Mboni yufanana ndi step mom😂😂😂
@apollochikoza57374 ай бұрын
Ndipo ndendende ndi dzala zomwe😂😂
@PhyllisJiva4 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@HenlyMusisiАй бұрын
Zosezi nkhani yakusatila pamphaso za YEHOVA, akanavomeleza ana akaziwo sibwezi ziliko izi; komaso asikana musamatengeke anayamba kukusalani munthuyu ali moyo; tiyeni tiphuzilepo pankhaniyi.
Amuna akewo anawona kuti zimene amamupangira zinali zomukwanira palibeso chifukwa choti azipitaso kwa mg1 kukafuna chuma chifukwa aliyense anali ndi nyumba yake anthuwa sikuti amakhala nyumba yimozi ayi
@AnnieBilly5 күн бұрын
Zovuta kukaganiran chuma mwini wak wafa
@GiftMoyo-eh8pw4 ай бұрын
Ndipo wamkulu wandisangalatasa koposa asagaile Chuma icho cos mwachoka Patali Mamie hule linagwa mchikondi bcz Chuma I 😂😂😂😂😂😂😊
@ShadreckMtepuka-sj8ue4 ай бұрын
Part 2 ilikuti kodi
@FRANCISLIFFAH3 ай бұрын
odandaulidwa munamvomera kunkhala akazi awiri, kwa m'bambo mozi sono musachuluke mzeru cfk mamunayo wamwalila
@gremmerchris714 ай бұрын
Nkazi wachiwiri uziyamika kuti uyu woyambayu anakulola kulowa m'banja lawo komaso pokutenga kuti uzikamugwilila ntchito chokhacho uzimuyamika...usazitenge wapamwamba kwambili kuti wabeleka mwana wamamuna nzakoyo sikufuna koma zidangochitika.. Komaso iwe nkazi woyamba kuti ufike pomwe ulipo dzidatengela nzakoyo kukhetsa thukuta ndikudzichepetsa kwakwe kuti iweyo ukhale umoyo ofewawo muthokoze pomupatsa shop imodzi over time mudzapeza ina basi simple..mukutelo pokuti iye ndiyemwe wasunga nfunda wanu basi
@LonjezoSingano4 ай бұрын
Vuto ndi mayi mkulu kuvomeleza mitala mgayren nzanuyo bs
@JoeMassamba3 ай бұрын
Koma katundu amakagawa katu wa nyumba yawina eee
@NaomiMagoha-uw7rm5 ай бұрын
Waiting for court ruling
@HevenChiwaya4 ай бұрын
Nkadzi wa chiwiliyo chuma akanapasidwa ndi mamunawakeyo chifukwa chumacho ndi cha kubanja lalikululo mamuna wanzeru satenga wa kwa Nkazi winabkupitisa kwina akanapanga zawo nthawi imene amunawo Ali ndi moyo😢
@KhalidYusufu10 күн бұрын
Mboni imakhala kunja kwa court not kumamvetsera zomwe awiri akufotokoza
@mussammakwinja52155 ай бұрын
Kkkkkkkkk nyumba mwa mkazi wang'ono ndi wa mkulu mungafanane Bwanji mwamunayo samapanga dongosolo aaaaaa palibe kugawana
Iyiyi imakhala Drama koma kuti tiphunzire mmene nkhani amaweluzira mma Court athu, moti muzionera pa MBC TV Monday 5:pm to 18:00. pamakhala nkhani zosiyanasiyana koma anthu ake otenga mbali ndi omwewa. Zikomo