Moses kunkuyu ndidolo poyankha mafunso Brian waziwaso tisanene kumbali, Moses kunkuyu very accurate,you are really fit to be a minister of information ❤❤❤
@freddzuwalina2 күн бұрын
😊k
@Littlefair7Күн бұрын
Ndi dolo koma lero wagwa nayo.
@JoelKacheche-x6iКүн бұрын
Mafunso onse womwe wafunsa Brian Banda liripo lomwe moses kunkuyu sanayankhe? Moses Kunkuyu wayankha mafunso mwa chindunji,mosapsyatira,komanso mwachisimikizo.Anthu enanu timakuziwani kale kuti mumasankha dala kukhala wogontha mmakutu olo mukuwuzidwa chilungamo.Tilibe nanu mulandu ndi ufulu wanu.
@Danielumodzi23 сағат бұрын
kunkuyu Kaya anakulakwirani chani koma ndi dolo kwambiri udindowu ukumukhala kwambiri aliyese voti mumtima mwake
But the roads are constructed NOT from Chakwera's OWN money. The plan had been there way before Chakwera and the money is a donation/grant/loan from China/Japan.
Aaaaaaaaa munthu ukasowa manyazi udzikhalako ndi umunthu dzonse dzikasowa bola ukhaleko ndi chisoni kma dzonsedzi Kunkuyu ndi Chikangawa alibe dzonsedzi
@Danielumodzi23 сағат бұрын
interview yopanda madzi akumwa
@SnowdenGostenMugagelaКүн бұрын
In case muzalowa nsogolo ino ND 2024 sugar Ali pa 2900 petrol pa 3000
@FortyoneHarwa3 күн бұрын
Koma kunkuyu ndichitsilu kwabasi Chakwera tsanzawinanso
@ShnayzAshraf2 күн бұрын
Nde mwat njanji ija ntchito yake ndi chan? Chifukwa mafuta ajatu nde apanga stack
@PartsonMdezaКүн бұрын
🤣🤣🤣
@AdizzMadizoКүн бұрын
Nzimu wa witika ukudikila don't forget u gonna pay back
@AtupereSadiki2 күн бұрын
Ndi oupusa awa za ziiii zomwe mukuyankhula
@OusieSaeed2 күн бұрын
A minister akuchita kuvetsa chisoni Zthu zakanika next ku maule ndale zachabe 😢😢😢
@shantelngomaКүн бұрын
😂😂😂pa AIP pajapo
@MayesoBissaiКүн бұрын
Akuti mwayakha kuti chani😂😂😂
@sibomasina3302 күн бұрын
😂😂😂😂 Brian muleke nzako.😂😂😂😂😂
@ChiefJustin-l5p3 күн бұрын
Akuona ngati zonse zilibwino
@RuthMkangala2 күн бұрын
Brian Banda uzakomola Muthu mmmmmm
@DavidZimba-pw9ypКүн бұрын
Akunkuyu avomera kuti a Pule anapita ku Eid ku UAE