Tisadzave Kuti Chakwera Wawina Mu 2025 - Jonathan Phiri

  Рет қаралды 1,546

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

Пікірлер: 24
@kimukamawe1591
@kimukamawe1591 4 күн бұрын
Inu ndiye kwanukuti kod mmaona ngati malawi ndiwa achewa? Zopusa basi kuzolowera tsangobasi, panopa amene akuvutika ndi amitundu Ina inuyo achewa ayi? Kuganiza mopeperabasi ngati zakukanikani vomerezani mumkaona ngati kulankhula chizungu ndiye utsogoleri lero ndizimenezi mwaolesa dziko kuwola kweni kweni pambiri yadziko lamalawi ndikoyambatu aka. Bwelerani kacharichi basi musakakamile manyi sapimpha timaonera ntchentche ntchentche.
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 5 күн бұрын
Mwasinthana lelo mwaonekela ndanamalomba ndanzanuwo muzitinamiza
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 5 күн бұрын
Chakwera sangawine aise,😂😂😂😂uyu DPP ilanga yokha
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 5 күн бұрын
Kupepelatu Joyce Banda adapangaso kafukufuku koma adanama mu 2019 adanamaso ndiye ukuti bwanji chisilu ndiwe opposition yongona
@robsontyg3928
@robsontyg3928 3 күн бұрын
Mufune musafune chakwela wawina kale ndi 60% , alomwe kwanu ku Mozambique dzipitan
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 5 күн бұрын
Lelo mwatifuna ayawo akumangochi nsewo a. D. P. P, udakukanikani wamakanjila munkatinamiza tisanaiwale
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 5 күн бұрын
Muzinamiza amene sakukuziwa kumakanjila ife tinkafuna msewo wabwino kumakanjila ukumangidwa ndipo kwasinthika a,. D. P. P. Amkantinamiza zansewo lelo. M, C. P, zikutheka boma ndilomweli sitisintha,
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 4 күн бұрын
Nde akaxawina muzapanga chani
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 4 күн бұрын
Alomwe muzazimangilila chifukwa ntundu umene ukulila kwambiri Malawi ndi wachilomwe chonde tapitani kwanu ku mozambique
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 5 күн бұрын
Kupha munthu akapanga zosokoneza osaopa kuti ndi president or ndani
@JohnYoweli
@JohnYoweli 5 күн бұрын
Kodi afrobrometer yo idzavota kunganiza mo pusa mukanalira musanati kanyozani basi
@symoldicky
@symoldicky 5 күн бұрын
Iweso nde uchitsiluwo cuz nkhale Ali kalosela chabe koma amapangidwa kuchoka pa ground and whats on the ground nizomwe amabwera nazo ndipo mavot amachoka pa ground pompo nde iwe chifukwa Chot zosatira zapa ground sizugwilizana nchisankho chako nde ukalankhule zankutu ngat ndiwe wanzeru nde ugaluwo
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 5 күн бұрын
Mukudzinamiza inu....look at the figures. Ma stronghold mwalembetsa ochepa kkkk game mwayiphonya pamenepo 😂
@AgnesNjikho
@AgnesNjikho 5 күн бұрын
Ndipo wawinadi Iwo amagome momwe amawauza kt musakarembese pano ayambapo boza lakuti awina kale pomwe anthu wawo sana uze kt kalembeseni kkkkkkk amati kukavota ndikutukwana
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 5 күн бұрын
Makasu kalembetseni muzalemeletse zitsilu Malawi dziko la anthu opepela, masausande a anthu kumaopa mwana wa John tembo osamuombela ngati umo tichitila kujoni
@VeraVermaak
@VeraVermaak 5 күн бұрын
Ndipo usakaikire mukafuse JB
@johnkambala692
@johnkambala692 5 күн бұрын
Kuwina kumene. Who is Jonathan. The barrot will tell us.
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 5 күн бұрын
Musatinamize kumangochi udakukanikani msewo wamakanjila lelo achakwela akumanga mufuna mutiuZe chiyani
@simamkelegusha6248
@simamkelegusha6248 5 күн бұрын
A jelasi inu.osusa inu.chakwela wawina kale ufune usafune
@LinlyMathewe
@LinlyMathewe 5 күн бұрын
Hehehe 😂😂😂😂😂
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 5 күн бұрын
Muthalika sankatukwana pakanpeni inuyo anakuuzani nindani zotukwana pansonkhano anthu adziwa kale zaumbavawanu
@YusufMoyo
@YusufMoyo 5 күн бұрын
Makamaka chimwendo anangokula mutu opandanzelu
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 4 күн бұрын
Nde inuyo mukukhulupilila machine muzalila chifukwa afrobometer yanena chakut simungagwese congolese sitifuna alomwe kut atilamulile
@tasmania527
@tasmania527 5 күн бұрын
Chakwera ngowinawina inuyo muzilira basi.
Izindaba zesiZulu @13H00 l 13 December 2024
24:35
SABC Izindaba
Рет қаралды 6 М.
Hon Suleman Vs Mr Sambo: Interview Ndi Chimwemwe Magazi
54:59
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 22 М.
Мен атып көрмегенмін ! | Qalam | 5 серия
25:41
[BEFORE vs AFTER] Incredibox Sprunki - Freaky Song
00:15
Horror Skunx 2
Рет қаралды 20 МЛН
Макрон ищет нового премьер-министра
1:09
Euronews по-русски
Рет қаралды 1,4 М.
Nyimbo Za Ndale  - Sitilola Kuvotela Congress
8:21
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 3,4 М.
Palibe Cha Mzeru Chimene A Chakwera Angaliwuze Dziko - Samuel Lwara
10:22