UTHENGA OPITA KWA MCP 20 September 2024

  Рет қаралды 5,972

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 51
@ChristopherJohn-u5i
@ChristopherJohn-u5i 2 сағат бұрын
Azatipase mtendele ndi yesu yekha amene samasitha ngati munthu komanso sakhumudwisa Amen
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 3 сағат бұрын
Tiyenazon bg agaluwa atitopesa
@StellaMichael-s4d
@StellaMichael-s4d 3 сағат бұрын
MCP singasithe ndiyamagazi bas akufuna asataniki awo
@AnthonyZuzePhiri
@AnthonyZuzePhiri 2 сағат бұрын
bon 😊 i lov this man
@ChimwemweKamanja
@ChimwemweKamanja 3 сағат бұрын
Umakwana Kalindo
@user-zx3pz2wy1j
@user-zx3pz2wy1j 3 сағат бұрын
Amene mukunena kalindo ndiwe opusa kalindo amanena zowona .
@jacquelineboya9529
@jacquelineboya9529 16 минут бұрын
Inde amanena zoona koma pali zina amanama uyu amatenga zamuutu mwake
@HalimaShafie-q9k
@HalimaShafie-q9k 54 минут бұрын
❤❤❤ the ddccc❤❤❤
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 3 сағат бұрын
Ati agula Dan luu 500 milion,chikhariren athu akudya chitezi mm
@TiamikeMbalati
@TiamikeMbalati Сағат бұрын
You see ndeakuyembekedzera kuti Mulungu akhale chete never
@Ronaldmtonga-j8c
@Ronaldmtonga-j8c 13 минут бұрын
Kalindo ndiwe amene ukufuna kubweresa nkhondo ,why anthu ukuwauza zopoira? Kodi ukati ndiwe president wa anthu osaika adakuvotera ndani ? Iwe yaziyakhura zopusa zakozo.ndipo sudati MCP ❤❤ mpaka 2030 .ndipo mulirabe
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 сағат бұрын
Ananena Chakwera yekha ku conversation kuti mutsogoleri wogula anthu ndikuti utsogoleri mulibe ndichizete
@TiamikeMbalati
@TiamikeMbalati Сағат бұрын
Kd or atamugula Danyo Daniyo ndi Mulungu ndamene atapangise kuti chakwela awineso chakwera akuchokatu pampando or atagula oyimba onse zikomo koma chakwera akumuchosa pampando ndi Mulungu osadera khawa
@JacksonSquare-us4bf
@JacksonSquare-us4bf 2 сағат бұрын
MCP ndi ma vampire 👹👺🦀🦞🐦‍🔥🐞
@YoungsonmSimkonda
@YoungsonmSimkonda 3 сағат бұрын
Kalindo wazionesa kut ndwe wa dpp
@ALEXSUBME67
@ALEXSUBME67 23 минут бұрын
Iwe nde ndani what have you done for Malawiu
@MadalitsoIbrahim
@MadalitsoIbrahim 3 сағат бұрын
Dan Lu akukayimba zokupha chilima
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 2 сағат бұрын
Komanso ndalama ndi tsatana basi.a dan lu mpaka kulowa mcp😢😢komano adzavotera adad mopandanso kukayikira
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 3 сағат бұрын
The Dc 😊
@macksonmkandawire5718
@macksonmkandawire5718 Сағат бұрын
Marry chilima abweleso ndi boza la mamuna wake
@macksonmkandawire5718
@macksonmkandawire5718 Сағат бұрын
Winiko kkkk umphawi wavuta kwambiri
@andreakalambula7723
@andreakalambula7723 Сағат бұрын
iiiiii mcp ndilibe nawo mau
@macksonmkandawire5718
@macksonmkandawire5718 Сағат бұрын
Azilima Ku mpoto bwanji sitidya chitedze
@YoungsonmSimkonda
@YoungsonmSimkonda 3 сағат бұрын
Mkuchedwa ndzimenezo akalindo
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 Сағат бұрын
❤❤❤❤❤❤
@jacquelineboya9529
@jacquelineboya9529 18 минут бұрын
Za mery chilimazo ukunama bon kalindo😅?mery mwini wake anakana kuti sakufuna ndale nde anthu achita kumumanga chingwe? Khalani pheee ku UTM kutuluka mtsogoleli mbambande akazawina mery chilima azamupasa ntchito not kukhala president
@Daniel-cf4tu
@Daniel-cf4tu Сағат бұрын
Akalindo zilakhula zanu sizomanga or athu ena amakhalila kukuombelani m'manja koma zolakhula zanu ndizokhuza khondo wy?
@bysongeorge3243
@bysongeorge3243 20 минут бұрын
500 million kwacha kungoipeza all over sudden! Afufuzidwe and wapeleka ndalamayo ndani , waitenga kuti? Za Mai Chilima itayeni imeneyo. She is not the solution of Malawi issues.
@EusébioLucianoGaiondo
@EusébioLucianoGaiondo 33 минут бұрын
🔥
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 Сағат бұрын
Dan lu ndi ndani so mu ndale achoke kumene
@YoungsonmSimkonda
@YoungsonmSimkonda 3 сағат бұрын
Kod ndwe was dpp
@HalimaShafie-q9k
@HalimaShafie-q9k 52 минут бұрын
Kalindo alibe chipan palibe ku zionesa kuti ndi wa dpp galu iwe
@hantosidira8720
@hantosidira8720 41 минут бұрын
Kalindo ndiwa DPP mukufuna mtinamize
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 2 сағат бұрын
Zipani zaku mabanja zimenezo ndiye mukuonakuti angachite chani Mary chilima angotaya nthu anamuvotera ndindani masewera eti utsogoleri sukusika Mbale pabanjatu ai Koma dziko.Ndiye mukamati Mary chilima mukuona Ngati bank mkhonde dzikoli
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 3 сағат бұрын
Mcp ndalama zomwe Ali nazo ndi zogulira Anthu basi
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 2 сағат бұрын
Nthawi yonseyi ngat mumadziwa kut Dan lu anamugula, munkalekeranji kunena asanalengeze kut walowa MCP? Ndie chifukwa chakuti lero walengeza yekha kut walowa MCP ndie muzikati aaa ai amugula! Aaa ndinunachitsiru. Ndipo zomwe mukuyankhula apazi ndizopanda nzeru, mesa a DPP-wo ndiamene akumayambitsa nsankho kumanena kut MCP isadzapiteso ku kumwera, zomwe a DPP-wo amayankhula ku phalombe zija, bwanj osadzudzula zimenezijazi ukukanena za MCP? Kod basi umafuna kuyambanitsa anthu dziko muno chifukwa chot ndiwe mulomwe wakumwera? Activi wanji okhala ndi mbali chonsecho umati siwe wandale? Mmutu mopanda nzerumo, anakuuza kut Mery Chilima amafuna u president ndindani? Simupindula kanthu baba ndipo muphulika 😅😅😅😅😅😂😂😂
@ALEXSUBME67
@ALEXSUBME67 27 минут бұрын
Za usilu basi inu
@ChisomoNthukwa
@ChisomoNthukwa 2 сағат бұрын
Koma zodabwitsa kut mukupanga izi ndinu alomwe okhaokha bwanji chikukuwawani ndichani asiyeni azani apange mbali yawo kupusa basi kuzikonda
@YoungsonmSimkonda
@YoungsonmSimkonda 3 сағат бұрын
Kod wabwino ndiuti
@YoungsonmSimkonda
@YoungsonmSimkonda 3 сағат бұрын
Zoona zake zit
@TemboHaswell
@TemboHaswell 2 сағат бұрын
Ngati ndichoncho zilibwinotu kt a mcp akachite manyazi akaone anthu mene akazazile ku nsonkhano wa dpp
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td Сағат бұрын
Iwe ndiye wakamba iwe Malonda ndim'aso kumeneko MCP ingotumiza Wana chakwera sapita wakula ndipamene mudziwe Kuti MCP bomaaa ndilomweli gotani chimwendo oladi Musa akwana tambala Ali ndimoto pamutu wina akalira tiyeni konko tikakhomana DPP imadelera muona Ngati muliku mulanje kayiyambeni mudzadutsa Kuti simu Lilongwe tithana mukuchepela nyawu zathu konzekani tinyape alomwe pobwela kumeneko a police pumani tiombane Kaye apa
@CharityMhone-uk9ym
@CharityMhone-uk9ym 4 минут бұрын
Mmmm inu Nanu 😮inu akupanga chan chikangawa wanuyo anthu akuvutika
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 2 сағат бұрын
Mulindi nkhawa mutha munthu wazeru akaona Kuti ukubkwaipa amachoka okha welcome everyone to MCP boma ndilomweli
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma 3 сағат бұрын
Akalindo ndinu openga inu dan Luu sanalakwitse azikayimbila chinkhalamba chija nindani wazelu angayime kukavotela fundudwa ngati imene ija
@AmoTiamo
@AmoTiamo 3 сағат бұрын
Nawe mutu mwakomo uli misala
@GriperZimba-q5g
@GriperZimba-q5g 3 сағат бұрын
Dani lu ndindani kape malawi wafika poyipa
@dalitson3558
@dalitson3558 3 сағат бұрын
Pantumbo pako ndi chikangawa wakoyo panyini pamako
@CliveChikaphonya
@CliveChikaphonya 3 сағат бұрын
Bambo Akonso Ndpo akavotero DPP iweyo ndkupusa kwakoko khala choncho
@AnthonyZuzePhiri
@AnthonyZuzePhiri 2 сағат бұрын
mmulibe agogo kod 😂
@ChristopherJohn-u5i
@ChristopherJohn-u5i 2 сағат бұрын
Mwakangalika ndikupanga zaziko lapasi,soka Kwa iye wobwelesa chokhumudwisa
Why EU’s Tariffs Won’t Stop Chinese EVs
11:55
CNBC
Рет қаралды 339 М.
这三姐弟太会藏了!#小丑#天使#路飞#家庭#搞笑
00:24
家庭搞笑日记
Рет қаралды 125 МЛН
#JH: Marketers Say N950/L Dangote Petrol Will Justify Importation Of Fuel
24:57
Is Higher Education Still Worth It?
57:00
TVO Today
Рет қаралды 1,3 М.
Sky News Press Preview | Thursday 12 September 2024
32:00
Sky News
Рет қаралды 7 М.
Postgres just got even faster
26:42
Hussein Nasser
Рет қаралды 23 М.
Why the Netherlands Wants to Opt Out of the EU’s Migration Pact
9:24