UTM Kung'alula Lazarus Chakwera (Mr Chikangawa) Ku Mangochi Lelo Pa 17 August

  Рет қаралды 18,925

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Khalani nafe pano pamene tizikupatsirani nkhani mwatsatanetsatane zomwe zikuchitika mudziko la Malawi

Пікірлер: 72
@HarryKandani
@HarryKandani 23 күн бұрын
Koma abusa a chikangawa avutikatu
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 25 күн бұрын
Utm bomaa 2025
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju 25 күн бұрын
Kwavuta mku mangochi lero🔥🔥🔥🔥🔥
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 24 күн бұрын
More fire 🔥 guys all the way from cape Town pa boma moto kuti buuuu soon see you kuzakupasani my vote❤❤❤❤
@PaulChaleka-lb4vx
@PaulChaleka-lb4vx 22 күн бұрын
Kwayaka moto chikangawa a choke munthu oipa and sadzalamulaso Malawi
@kondwanichiwanda
@kondwanichiwanda 25 күн бұрын
Utm 🔥🔥🔥 my vote
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 25 күн бұрын
That's wonderful
@MemoryKamanga-jv4jh
@MemoryKamanga-jv4jh 25 күн бұрын
Utm oheee
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly 24 күн бұрын
Iwe Chikangawa, unamupheranji Chilima uli ndi tsoka
@FelixChikapa-z1d
@FelixChikapa-z1d 21 күн бұрын
Anapoyira ma guys amene aja
@victorauwana7258
@victorauwana7258 24 күн бұрын
So sweet
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 25 күн бұрын
UTM number one ❤
@TonyMhone
@TonyMhone 25 күн бұрын
Mr. Chikangawa kumene aliko kaya akumva bwanji. Nyekhweeee!!!
@elijahmsesa8048
@elijahmsesa8048 24 күн бұрын
Aluta continue aluta continue 🔥 🔥
@ArnoldKhandeya
@ArnoldKhandeya 24 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 24 күн бұрын
Rest well SKC.Anapha thupi koma kuuzimu mulinafe nthawi zonse.
@PatienceMphuche
@PatienceMphuche 25 күн бұрын
Mukamati chipani Cha ana ndiye mukunamatu ,Cha ana chomwecho ndichonwe chinakukhazikani pampando
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 24 күн бұрын
Chipani Cha ana ichi
@user-go2ov9xu1s
@user-go2ov9xu1s 25 күн бұрын
Xamphavu musafoke pamane tikuona chitsogolo kumpha chilima ntima umawawa ngat wandigila pabala
@elijahmsesa8048
@elijahmsesa8048 24 күн бұрын
Akongelesi chaka chamawa musaza chilima akanyimbi zafiti ☠☠❌❌
@ArnoldKhandeya
@ArnoldKhandeya 24 күн бұрын
eya ndchaana kmabe chidakurawitsani boma, cnanga chirengedwereni dziko cmunawinekotu mwina cmudziwayi
@NthambiInvestment
@NthambiInvestment 24 күн бұрын
SKC enjoy your rest we are here to prove that UTM is alive
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 24 күн бұрын
Kkkkkkk UTM woyeeeeee rest well skc😭
@SiyasiyaManda
@SiyasiyaManda 22 күн бұрын
Kom inu mwamupasa kale zina
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e 25 күн бұрын
❤❤❤ mwana ndi mwana 😂😂
@elijahmsesa8048
@elijahmsesa8048 24 күн бұрын
🔥 🔥 🔥 Comrade
@RabeccaMkandawire-i9j
@RabeccaMkandawire-i9j 24 күн бұрын
My President
@Lingstone-r3z
@Lingstone-r3z 25 күн бұрын
To👍🔥🔥🔥
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 25 күн бұрын
Kkklkl chikangawa koma wayalukatu
@blessingschisaka7911
@blessingschisaka7911 24 күн бұрын
How? Ife tili pamangochi pomwepanotu, makape awa
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 23 күн бұрын
Ku nabebatu
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 24 күн бұрын
Uku kuli uhule basi okhaokha
@isaaczuze
@isaaczuze 24 күн бұрын
Nchewa simunthu wabwino ndipo amakhala ndi jelous osati masewela .....chakwera wakoyo zikobwalilephela .....tiona agalu mukudya ndalama zokuba zachakwerazo .....agalu inu
@elijahmsesa8048
@elijahmsesa8048 24 күн бұрын
Viva viva viva fire 🔥 🔥🔥🔥🔥
@isaaczuze
@isaaczuze 24 күн бұрын
Chakwera kungobera mavoti ayi ndithu ziko lizayaka moto .....nkhondo paliponse ........chimwendo banda machende amako ndi galu mzakoyo
@giftkanjuchi-qm8hf
@giftkanjuchi-qm8hf 25 күн бұрын
Chakwera basooop
@augustMag
@augustMag 24 күн бұрын
Mangochi wooooyeeeee 🔥🔥🔥
@Fatima-f5c
@Fatima-f5c 25 күн бұрын
Chakwela Ali m,mazii 2025😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@harrietmkusangombe
@harrietmkusangombe 24 күн бұрын
Rest well My president
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 25 күн бұрын
Aluta indeed 🔥
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 25 күн бұрын
Chikangawaziiii nyekwested
@JamesManjawira-yz4ji
@JamesManjawira-yz4ji 25 күн бұрын
😂😂😂
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 25 күн бұрын
@@JamesManjawira-yz4ji 😂😂😂😂 chilingamo nanga tibanike ife aMalawi nkhalango imeneija mitengo tikagwetsa
@user-rx1dj7kg8k
@user-rx1dj7kg8k 25 күн бұрын
My vote 🔥
@user-ei2yt3kf4x
@user-ei2yt3kf4x 22 күн бұрын
Kodi aluta kutathaudza kuti chani
@KamizaElizabeth
@KamizaElizabeth 24 күн бұрын
Anthu inu chonde musakhale alitima chosani chikangawa mugwirizane ND Dpp
@isaaczuze
@isaaczuze 24 күн бұрын
Chakwera achoke basi munthu woyipa .....galu uja
@DaisonAgripa
@DaisonAgripa 24 күн бұрын
Mmalawi sadzatheka anthu ake ndi womwewa amakhala mmisonkhano ya zipani zonse andale nkhani bola apeze yachakudya chalero mawa voti yawo ndikukapatsa awo. Inu ndikumadzajama ija ya atibela mavoti mudzakhalanso mmisewu nawo mademo anuwo. Ndipo m'bale chilima adakapumula komachiweluzo sichanu ndichake Yehova timawelenga mawu amulungu "ndinachimwa poganiza ndi polankhulanso" zinazi muchimwa nazo chilungamo cha imfa ya bwana Chilima chili mmanja amulungu. Siyani chiweluzo chikhale chake cha Mulungu. Zinazi muchimwa nazo.
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 24 күн бұрын
Anthu ovina gule angakhale abwino?
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r 25 күн бұрын
Mr Chikangawa Munthu woipa
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h 25 күн бұрын
Chikangawa zamuvuta komwe ali
@ArnoldKhandeya
@ArnoldKhandeya 24 күн бұрын
kma wina athawa ndthu
@RajMass-nr3uy
@RajMass-nr3uy 24 күн бұрын
😂😂😂 chikangawa Ali madzi😂😂😂
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 24 күн бұрын
Chipani Cha pa sociol media ichi ulendo uja munali ndi ma mp 4 chakachino kaya mukhala ndi ma mp olo mozi I dout
@ArmandosebastiaoLano-yw5iv
@ArmandosebastiaoLano-yw5iv 25 күн бұрын
A luta continua
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 25 күн бұрын
Zinazi zoziyambadala.... Zimayachontchi koma mpang'ono pang'ono kkkkkkk
@emmanueljelemani4203
@emmanueljelemani4203 24 күн бұрын
Rest well SKC
@KhumboMunthali-jx5me
@KhumboMunthali-jx5me 25 күн бұрын
Koma chikhwima chipanichi
@ChristinaSimwaka
@ChristinaSimwaka 24 күн бұрын
Çhikangawa
@BensonJere-i9k
@BensonJere-i9k 23 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@PiusMpando
@PiusMpando 25 күн бұрын
Eeeeee zoooo yawina kale basi
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa 25 күн бұрын
Chipani cha ana
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 25 күн бұрын
Eya bola kusiyana ndi nganga zanuzo zogona zitakhala kuli kukula 😂😂😂😂😂
@user-rx1dj7kg8k
@user-rx1dj7kg8k 25 күн бұрын
​@@user-qp8kh2hj9otauzeni awa 😂
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 25 күн бұрын
Masapots awa kkkkkk
@user-lp2sd7lt8b
@user-lp2sd7lt8b 24 күн бұрын
Zopanda ntchito izi
@davietimothybanda665
@davietimothybanda665 24 күн бұрын
Iwe mchombo wako ndi okhwima? Eeeeee oboola T shirt, vote yanga kwa anawo
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 25 күн бұрын
Chipani cha ana ichi osakhwima pachombo
@user-zo4ox7bn6s
@user-zo4ox7bn6s 25 күн бұрын
Uzakhumudwa
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x 25 күн бұрын
Ana omweo akukokerani ku una muona
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 25 күн бұрын
Aaa lindani madzi aduse muzakhumudwa inu mulungu simunthu utm my vote ❤❤❤❤
@elijahmsesa8048
@elijahmsesa8048 24 күн бұрын
Aluta continue aluta continue 🔥 🔥
ПРИКОЛЫ НАД БРАТОМ #shorts
00:23
Паша Осадчий
Рет қаралды 4,4 МЛН
When you discover a family secret
00:59
im_siowei
Рет қаралды 35 МЛН
Electric Flying Bird with Hanging Wire Automatic for Ceiling Parrot
00:15
11 SEPTEMBER 2024 PROGRAM
1:11:50
THE CHANGE RADIO
Рет қаралды 4,8 М.
YO MAPS LIVE PERFORMANCE IN MALAWI LILONGWE (Mingoli Bash)
19:50
Alobo Vibes
Рет қаралды 151 М.
Record Label Ya Ku Malawi, ipindula?
13:59
Sam Malvitha
Рет қаралды 11 М.
NKHANGA ZAONA NDI COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM
29:00
Malawi Extra
Рет қаралды 279
ПРИКОЛЫ НАД БРАТОМ #shorts
00:23
Паша Осадчий
Рет қаралды 4,4 МЛН