amalawi mudakhala bwanji tayambani ndi chichewa kut muthu wakunuziave koyambirila so mukangoyamba ndi chizugu muthu wakumuzi amangotseka osavelaso or mubwele ndi chichewa kumapeto iye amakhal kut wayamba nchito
@MussaChilembwe2 ай бұрын
Zipani pano zonse utm dpp ndi zina agwilizane apange chimozi amuchose chilangawa pamozi ndi manganya mwana oyipa kwambi athu amewa ndi athu amagazi koma zuzika pano kwambili mulungu athana nawo pompano
@kingsleyhopematchaya51842 ай бұрын
Dpp inatipanga chipongwe ife a udf sitingaloleso kt itipangeso chipongwe dpp ife a udf sitidzayiwala
@SamboMaria2 ай бұрын
Tili pambuyo panu
@RemaniNkhoma2 ай бұрын
Koma prz gyz osayerekeza kuti mupangeso mgwirzano ndi mcp uko ndikuputsa ngat mukufuna kupanga mgwirzano pangani ndi DPP prz gyz kusogoroku boma rizakhara ranu tikuvankhani zoti akugureni musavomere Apolo ndiye kuti mukuzigurisa ng'onazi ndizoyipa zizakudyanisoni