Tisamanyozane zikhulupiliro ayi ndizopanda pake zimenezo,Kodi njira yophera mbewa kapena nsomba ndi imodzi? Ine so mkatolika koma tinapachika zotozana,konzani njira yanu kt mukakumane naye maso ndi maso,basi, leave it, just take what spoken he is also image of God,not so? Amen man of God,true
@MacxwellStuarts-h9r6 күн бұрын
Ndizoonadi chakwera wauma mtima kuchita zoipa pa usogoleri wake ngati farawo koma ukulu was mulungu uzaoneka
@ZellesChimaimba-y1g2 күн бұрын
Amen!!!!! Mau achilimbikitso
@GranceChirhwa11 күн бұрын
Tanthokoza father potilimbikisa kuti tiziyendabe ngakhare tarefuka 🙏🙏🙏
@Josephiriillovo11 күн бұрын
Komatu nde kunali kucheza asaaaa nice. Glory Be To God
@FelinaMasesa4 күн бұрын
God bless you father i follow you
@LovelyJkamangaKamanga11 күн бұрын
Thank you Father for Mau aUzimu atsiku ndi tsiku.
@EdsonSingano8 күн бұрын
Amen pastor god bless you
@bensonmanda23511 күн бұрын
Tayamika kwabasi ndi mau achilimbikitso. Akuti tisabwenzere choipa.
Powerful... What a friend we have in Jesus. He is our only hope
@AkweniHafule11 күн бұрын
🙏🙏 Amen abusa kumwamba kuremekezeke
@JumaEriya11 күн бұрын
Mau otsitsimutsa wasembe osafooketsa uyu ndimakunyadira bambo mutharika murungu odziwa kutsekura mwayi wa atsogoreri adziko atsekure dzikorathu ramarawi zikomo
@ThandiBinali11 күн бұрын
F R inuyo mulungu akupaseni moyo wa utali mu kugwira nchito ya yikulu Yehova akuva kulira kwa malawi
@AndsonMlambala6 күн бұрын
Powerful.amen
@ReyonAndrewBanda11 күн бұрын
Tizingocheza ndi ambuye apa bas 😂😂 ilibwino zed
@TriciaMalikebu11 күн бұрын
Beautifully delivered 🙏🏽
@RuthTimothyChirwa11 күн бұрын
Amen watching you from Cape Town men of god keep it up ❤
@JaLHSavers11 күн бұрын
Wish!!! Uthenga opotsera nsembe
@josephyheans717911 күн бұрын
Amem
@Fanie-i7z11 күн бұрын
Amen n amen Father
@GetrudeGogoda6 күн бұрын
Ai father mwayendako bwino kocheza ndi ambuye ndipo atilimbikitsa muzacheze nawonso tsiku lina
@AleiphurMwamadi10 күн бұрын
Amen and amen
@LovemoreKutsamba11 күн бұрын
Zofunikad kumacheza ndambuye 😂
@MaggieMasiano11 күн бұрын
Amen tuvutika ife ambuye tipulumutseni
@WarriorKB-l3i11 күн бұрын
Koma apa nde mwalasadi dziko lino tikufuna anthu inu mtumiki osati awa akuzitcha kuti mapolofeti za ziii angoti cikangawa 2025 boma, boma lake la mawo? Dzikoli anthu tikuvutika nde wina adzikamba za kutchini kwazaza anthu inu mukuti ma prophert inu mukhale cete palibe ca mzeru mukulankhula.
@GraceKondwan-v2k11 күн бұрын
Very encouraged words
@PeterRabson-z3w11 күн бұрын
Amen father
@RuthMtambe11 күн бұрын
Amen mulungu atitulutsa mavuto
@giftmakoyo144111 күн бұрын
Amen very powerful
@ShamimuBisani11 күн бұрын
Wansembe uyu ndi mchosa nkhawa thesa BP Mulungu akudalisen baba