Waphedwa ku Lebanon; Nkhondo yafika povuta ku Israel.

  Рет қаралды 32,141

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

6 ай бұрын

Пікірлер: 162
@user-qq3ip1od6i
@user-qq3ip1od6i 6 ай бұрын
Big up bakili,, I wish one day you became ministry of information,,
@GeorgeGeorge-bu6cy
@GeorgeGeorge-bu6cy 6 ай бұрын
Ulemu wanu brother
@SinsaKachale
@SinsaKachale 6 ай бұрын
Following frm south Africa..inuyo ndi hero wathu osaopa pachilungamo ❤❤❤❤❤
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 6 ай бұрын
Ukamakumbila amzako mayenje olowamo iwenso tsiku Lina izalowamo this Palestinians should stop ISIS and JIHAD
@user-rl5zq1qr4d
@user-rl5zq1qr4d 6 ай бұрын
Ulemu wanu bwana its a sad story dziko lonse la pansi lingoyang'anira kuphatikipo maiko onse a chislamu osapangapo kanthu pamene maiko achikhrsitu onse akuthandiza Ayuda inna li llah wa inna ilaih rajooon
@BenissoneErnesto-eh6zs
@BenissoneErnesto-eh6zs 6 ай бұрын
2024 kalikonse kobisika tikaona watching from Mozambique never give up bg brother ❤❤❤
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 6 ай бұрын
Big up!!!! Thanks for the information, proud of you always brother Man
@johnkamwana3154
@johnkamwana3154 6 ай бұрын
Komano Hamas anaziyamba okhatu. Nkhonya yobwezera kuwawa
@Shaabann
@Shaabann 6 ай бұрын
Thanks my brother God bless you and your family
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 6 ай бұрын
Oyenda ndi lupanga nayenso adzamphedwa ndi lupanga..ndipo sizodabwitsa kumphedwa kwa munthu ameneyu..ntchito zake zampangila umboni..panopa alinso ku gehena..
@DicksonMvula-vd6rb
@DicksonMvula-vd6rb 2 ай бұрын
0pll
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 6 ай бұрын
Ayuda sakulakwa coz Hamas Nd imene inayamba zithu zimene singamalize
@user-lu4cu2td4i
@user-lu4cu2td4i 6 ай бұрын
Watching you direct from Lusaka Zambia 🇿🇲🇿🇲
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 6 ай бұрын
Zikachitika ine ndimavera ku Bakili muluzi TV kp it up
@wilsonsawasawa3794
@wilsonsawasawa3794 6 ай бұрын
Thus great! continue giving us the updates
@hezekiayelemia
@hezekiayelemia 6 ай бұрын
Thank you so much to bring news to us ,I hope you daily update it's so importance to us
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 6 ай бұрын
Ife monga anthu opephela sitingaime nkuchemelela ayi koma tiziwapepherela anzanthu
@isaacschamatwa3596
@isaacschamatwa3596 6 ай бұрын
Israel osamapanga nayo zibwana
@GiftMalawian-kc4cy
@GiftMalawian-kc4cy 6 ай бұрын
Ndamva aisee
@JamusMigo-tk4mk
@JamusMigo-tk4mk 6 ай бұрын
Thank you big boss
@madalitsochitekwe7786
@madalitsochitekwe7786 6 ай бұрын
We are behind you israel
@cephasnkhoma2301
@cephasnkhoma2301 6 ай бұрын
We are following
@user-le6jk3td6t
@user-le6jk3td6t 6 ай бұрын
thank you my brother
@fraserluwemba6364
@fraserluwemba6364 6 ай бұрын
Sindimafuna kuphonya news pa tv iyi. Luwemba from Mulanje
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 6 ай бұрын
My best Chanel ❤❤❤
@paulvimbamvula9508
@paulvimbamvula9508 6 ай бұрын
Apa palibe mbali . enemy wako sungakhale naye pafupi
@user-yt4so1hx7y
@user-yt4so1hx7y 6 ай бұрын
Thank you so much to bring this news to
@ishakatimbe7341
@ishakatimbe7341 6 ай бұрын
Koma ndiye kuvutatu
@johndaka6368
@johndaka6368 4 ай бұрын
Big man🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
@user-nn9mx5tt6d
@user-nn9mx5tt6d 6 ай бұрын
Best TV in Malawi
@joemlelemba6572
@joemlelemba6572 6 ай бұрын
Iwe ndi one
@user-jb6rq4mh2d
@user-jb6rq4mh2d 6 ай бұрын
Respect bg man
@user-lp3zx3yt5l
@user-lp3zx3yt5l 6 ай бұрын
I was waiting for this one.i wish to work with you
@OSSAMADaUDIE
@OSSAMADaUDIE 6 ай бұрын
Thanks you very much to bring news to everyone Allah blessings you sir
@wilsonali7890
@wilsonali7890 6 ай бұрын
We really appreciate he really gave us the good information but he must stop talking side as a good journalist. Kufunika asiye kumanena kuti "HAMAS ndi zigawenga" it's not good ndi anthu amene akumenyera ufuru mu dziko lawo inunso mukudziwa
@shinezenda5513
@shinezenda5513 6 ай бұрын
Ummm zoti kuno ndife akapolo ndizaboza. Tikukhala bhbh ku israel
@user-pn7cj9hb3t
@user-pn7cj9hb3t 6 ай бұрын
Yanu ija fadah
@AbuMussah-wi7gb
@AbuMussah-wi7gb 6 ай бұрын
Alhamdullah you are welcome
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 6 ай бұрын
May Allah almighty protect Palestinians
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 6 ай бұрын
Don't waste your time with this. Prayer 😂😂😂
@zeckbmalawi8017
@zeckbmalawi8017 6 ай бұрын
Best tv
@user-iq3iv8tp8t
@user-iq3iv8tp8t 6 ай бұрын
Watching from capetown
@kubengovender6996
@kubengovender6996 6 ай бұрын
Big respect !!
@ThomsonMusowa
@ThomsonMusowa 6 ай бұрын
Ndimakunyadilani bro❤
@user-iq3iv8tp8t
@user-iq3iv8tp8t 6 ай бұрын
Your the number 1❤❤❤❤❤❤
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 6 ай бұрын
Why cant they go to Lebanon
@user-mz4tk1pw3f
@user-mz4tk1pw3f 6 ай бұрын
Ulemu wanu big
@successngoma
@successngoma 6 ай бұрын
Ana osankhidwawo ma Israel ma type yake nde
@ZONKEMASEKO-rm5fn
@ZONKEMASEKO-rm5fn 6 ай бұрын
Big up
@josuahkachali1489
@josuahkachali1489 6 ай бұрын
Mr keep it up
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 6 ай бұрын
We appreciate
@user-hn9dt6tv4h
@user-hn9dt6tv4h 6 ай бұрын
watching Live from canberra city
@user-cy1vf5vz8y
@user-cy1vf5vz8y 6 ай бұрын
Thanks ❤❤❤
@austinharawa720
@austinharawa720 6 ай бұрын
Chakwela alora izizi....mapale kumpanje
@kondwanisimiton-lr6un
@kondwanisimiton-lr6un 6 ай бұрын
Ulemu wanu bro
@user-cy5ko2qw5d
@user-cy5ko2qw5d 6 ай бұрын
best Tv
@innocentchirombo2073
@innocentchirombo2073 6 ай бұрын
Kodi Ku Africa nde kotaila zoipa zonse??😢
@ibrahimmeemzy9754
@ibrahimmeemzy9754 6 ай бұрын
Allah Akbar ☝️……😢
@joemapiri4050
@joemapiri4050 6 ай бұрын
Zikachitika timvera kwa inuyo bro🤜🤛💯
@user-qf4sd1xy4h
@user-qf4sd1xy4h 6 ай бұрын
mumakwana abwana big
@christophermkhize1991
@christophermkhize1991 6 ай бұрын
Koma inuyo ndiye basi mulungu must protect you big
@abisalomchunga6695
@abisalomchunga6695 6 ай бұрын
Good good bother
@user-ps9nu6se9k
@user-ps9nu6se9k 6 ай бұрын
Mumakwana boss ndipo tikudikira mutiuze nkhondo ya Russian ndi Ukraine ili pati
@daudimatolano1715
@daudimatolano1715 6 ай бұрын
Great
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 6 ай бұрын
Asilamu anayiyamba okha nkhondo,,aimalizetu,, asilam mwano,akwapulidwe asilam anthu amwano,,
@user-mz8nw6nx6p
@user-mz8nw6nx6p 6 ай бұрын
Example wapeleka kale kuti,,,Zimbabwe ibwele kumalawi ndikumalanda Malo a Malawi,,,kodi mungakhale Chite poti inu Achristu mulibe mwano?Nanga patapezeka gulu losakondwa ndizimenezo ku Malawi,,,,,Kodi gululo likhoza kukhala la zigawengaso?kapena poti ndigulu la Chisilam?
@user-mh9se5to6k
@user-mh9se5to6k 6 ай бұрын
Ku Gaza sikuli asilamu okha big
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 6 ай бұрын
Asilamu ndi anyani. Machende awo onse. Pamtumbo pawo onse.
@user-mh9se5to6k
@user-mh9se5to6k 6 ай бұрын
Free Palestin
@IssaKakowa
@IssaKakowa 6 ай бұрын
Eish
@user-oz1ts3yi7d
@user-oz1ts3yi7d 6 ай бұрын
Well done Israel
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 6 ай бұрын
Komatu kwavutatu
@ChrispinTaombe
@ChrispinTaombe 6 ай бұрын
Our b lvd tv❤
@matembamadadada8291
@matembamadadada8291 6 ай бұрын
Ulemu captain❤
@milajimussa4120
@milajimussa4120 6 ай бұрын
Mavuto
@paulvimbamvula9508
@paulvimbamvula9508 6 ай бұрын
akufuna kusamusa anthuwa chifukwa ndi amtopola
@basheerkachelenga9198
@basheerkachelenga9198 6 ай бұрын
Watch from Durban
@user-rv8gi4ro6r
@user-rv8gi4ro6r 6 ай бұрын
👂👂👂timakusatilani abwana
@victormaulika6523
@victormaulika6523 6 ай бұрын
Best tv ever
@user-frasernamaona14
@user-frasernamaona14 6 ай бұрын
One thing chomwe chimandidabwitsa ndichakuti ku Israel kuli president komano munthu wamphavu ndi Prime Minister why?
@alfredbanda1693
@alfredbanda1693 6 ай бұрын
Ndimene structure ya government yawo ilili sizidabwitsa mayiko ambili ena amapanganso choncho mwachitsanzo iran kuli prezident komano supreme ruler ayatollah ndi amene ali pa mwamba pa zonse
@user-frasernamaona14
@user-frasernamaona14 6 ай бұрын
@@alfredbanda1693 Ndakumvetsani boss; olo ku England kuja heard kuti Prince Charles has no power to interfere ndi za politics komano zamipingo or ma charity activities and sangalamule dziko kuti lilowelele nkhondo only Prime Minister ndi amene amapanga ziganizo. It's crazy.
@abdulmalikissah6979
@abdulmalikissah6979 6 ай бұрын
Exactly, Pakistan is like that as well ​@@user-frasernamaona14
@alfredbanda1693
@alfredbanda1693 6 ай бұрын
@@user-frasernamaona14 paja don't forget kuti prince or queen amakhala nkulu wakhonda like mene alili chakwera but yes mphamvu zimapatsidwa kwa pm koma prince akhoza kupanga declare but not implementing it. Only pm can both declare and implementing it
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 6 ай бұрын
That's why it is reach. Malawi cannot be rich because the president is more powerful.
@user-nx9tj5ho2c
@user-nx9tj5ho2c 6 ай бұрын
🖖 respect
@FrancisDay-br7xb
@FrancisDay-br7xb 6 ай бұрын
Zilimakola
@rodglae6657
@rodglae6657 6 ай бұрын
@user-xh1ve5ym3l
@user-xh1ve5ym3l 6 ай бұрын
Ulemu wanu munthu wamkulu kwambiri
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 6 ай бұрын
Mmmm
@paulvimbamvula9508
@paulvimbamvula9508 6 ай бұрын
Israel inagwilitsa ntchito drone ya militaly nkuitumiza ku Beirut Lebanon mkatikati mwa dzikoli ndipo Israel intelligence Monsad inkamuwerenga ma movement Ake...mpaka anamupenza drone inalowa pa window nkuphulika nkupha onse mchipindamo..ndipo Israel inati onse Adani Ake ndi oyenda akufa..kumbukilani Israel Ili ndi most intelligence in the world
@molicieeosama8877
@molicieeosama8877 6 ай бұрын
❤❤❤❤
@CleverlyKanthyos-ds5sg
@CleverlyKanthyos-ds5sg 6 ай бұрын
Super power bambo 🇮🇱🇮🇱🇮🇱🇮🇱
@farmupmalawi
@farmupmalawi 6 ай бұрын
Ambuli
@austinvincent1264
@austinvincent1264 6 ай бұрын
Tafikatu
@user-to4lf5cr5v
@user-to4lf5cr5v 6 ай бұрын
Allah bless plaster
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r 6 ай бұрын
Tipephe mwini moyo kuti alowelelepo kuti khondo yinthe khondo simanga mudzi ambuye mnanena kuti mzatimenyela khondo ife tili chete
@AllieKaisi-je6rm
@AllieKaisi-je6rm 6 ай бұрын
Ina lillah waina lillahr rajiona
@JemiMangani-if6wt
@JemiMangani-if6wt 6 ай бұрын
aise koma iweyo mulungu anakudalisa tungodikira agalu akutilamulirawa tikawachosa pampando tizakuoneni boss
@Goliath461
@Goliath461 6 ай бұрын
Koma akangobwera kumalawi timenyananso tokhatokha 😂😂😂
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d 6 ай бұрын
Hidira amazindikira kuipa kwaayuda
@emmanuelkapelula6142
@emmanuelkapelula6142 6 ай бұрын
islael stop the war
@user-qp3ie7nl9y
@user-qp3ie7nl9y 6 ай бұрын
deal imeneyo ikangofika kwachakwera itheka paja ndiwadyeratu angowona kuchedwa kuti alandile 60 pin ina😂😂😂😂
@staubioxygensensor559
@staubioxygensensor559 6 ай бұрын
Dolo
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w 6 ай бұрын
Mumatiimilira inuyo💪
@paulvimbamvula9508
@paulvimbamvula9508 6 ай бұрын
Sanatunize ndege ya fighter jet..koma anatumiza drone
@user-nt4fr2le3f
@user-nt4fr2le3f 6 ай бұрын
Mungopanga yanu page muzitipasila nkhani zanu,zosusazo ayi
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 6 ай бұрын
Kuchema
@amidubanda079
@amidubanda079 6 ай бұрын
Kodi amene anayamba chiwembuchi ndi ndani Kuti mukanenene Kuti ayuda ndi ankhaza Mesa ma pelestina ndi amene anachita chiwembu ?
@user-mh9se5to6k
@user-mh9se5to6k 6 ай бұрын
Ma pale anapita kukabwezela big nkhondo inayamba kalekale ma Israel analanda malo ama palastine eeetu wakulu
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 6 ай бұрын
Zoonadi. Anaziyamba dala. Ayuda si a nkhanza.
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 6 ай бұрын
Andale ayambapo kukhwima now ready for 2025
@user-pd1lm4vb8n
@user-pd1lm4vb8n 6 ай бұрын
No koment for this story, because to gather us one
@AbdullahKenneth
@AbdullahKenneth 6 ай бұрын
😢
@derekkhawoleya3591
@derekkhawoleya3591 6 ай бұрын
❤🇲🇼💪💪💪💪💪 mukumveka¹⁰⁰% wakulu
Дарю Самокат Скейтеру !
00:42
Vlad Samokatchik
Рет қаралды 8 МЛН
Sigma Kid Hair #funny #sigma #comedy
00:33
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 29 МЛН
Does size matter? BEACH EDITION
00:32
Mini Katana
Рет қаралды 19 МЛН
Trump Accepts Nomination | News on The 700 Club - July 19, 2024
15:29
26 November tinanena izi koma ena anatsutsa. Mawu aakulu akoma akagonera
15:23
How to win a argument
9:28
ajaxkmr
Рет қаралды 381 М.