Рет қаралды 307
Kupyolera m'Baibulo, Anthu Ayenera Kudziwa Atate ndi Amayi a Mizimu Yathu
Monga aliyense ali ndi atate ndi amayi omwe adawabereka mwakuthupi, pali Atate wauzimu ndi Amayi auzimu omwe amatipatsa moyo wosatha m'dziko la angelo.
Pokhulupirira zimenezi, tiyenera kusunga Paska wa pangano latsopano, njira yokhayo yokhalira ana a Mulungu.
Dzina la Mulungu mu M'badwo wa Mzimu Woyera Lomwe ana a Mulungu ayenera kudziwa
Ana a Mulungu, omwe adzalamulire mu ufumu wakumwamba kwamuyaya, ayenera kudziwa dzina la Mulungu.
Monga oyera analandira dzina la Yesu ndipo anapulumutsidwa mu m'badwo wa Mwana, mamembala a Mpingo wa Mulungu alandire Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi mu m'badwo wa Mzimu Woyera, kulalikira dzina la Mulungu ku dziko lonse lapansi ndi kupereka uthenga wa chipulumutso.
Ahebri 12:8-9
Koma ngati mukhala opanda chilango, chimene onse
adalawako, pamenepo muli am'thengo, si ana ai.
Komanso, tinali nao atate a thupi lathu akutilanga, ndipo tinawalemekeza;
kodi sitidzagonjera Atate wa mizimu koposa nanga, ndi kukhala ndi moyo?
Masalimo 20:7
Ena atama magaleta, ndi ena akavalo; koma ife
tidzatchula dzina la Yehova Mulungu wathu.
[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]
〖World Mission Society Church of God〗watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 introwmscog.com