YEHOVA M'BUSA WANGA

  Рет қаралды 977,138

Masintha Chitsitsimutso

Masintha Chitsitsimutso

Күн бұрын

Пікірлер: 273
@patrickgwedeza2802
@patrickgwedeza2802 Жыл бұрын
Nyimbo yaimbidwa bwino kwambiri ngati siyomwe ija yotchuka timaidziwa ija. Well done azimayi
@chikondichisenga112
@chikondichisenga112 Жыл бұрын
Komatu zoonaaaa
@JonesMajiya
@JonesMajiya 10 ай бұрын
Proud to be a Presbyterian
@YozmanSamuel
@YozmanSamuel Жыл бұрын
Ambuye akudalitsen mumatitsitsimutsa kwambili amen nyimbo imeney aaaaaa ndilibe mau🙏🙏
@NyashaNyalugwe-su9sb
@NyashaNyalugwe-su9sb Жыл бұрын
Ambuye azikudalitsani Azimayi mumaimba nyimbo zotitsitsimutsa mu Uzimu😭😭🔥🔥🔥❤️❤️❤️
@CidrickCosmas
@CidrickCosmas Жыл бұрын
I almost listen to every song of this choir. Well composed, with deep spiritual message. May God keep blessing these women and choir abanduntly
@SOLOMON-GRANT
@SOLOMON-GRANT 7 ай бұрын
If I may see heaven, this choir will have a 70 percent contribution to my holiness. God continue blessing these mothers.
@nellyjeruto8488
@nellyjeruto8488 7 ай бұрын
💃💃💃🥰🥰🥰God bless these songs
@pemphero-fo9en
@pemphero-fo9en 5 ай бұрын
Ndidzabwezela yehova chiyani
@DerrickMwape-u6p
@DerrickMwape-u6p 2 ай бұрын
True my brother 😊
@MercyZulu-k4y
@MercyZulu-k4y 2 ай бұрын
Beautiful singing
@emmanuelkhwelenje7980
@emmanuelkhwelenje7980 11 ай бұрын
This song dedicated to my mom and dad. If there's phone in heaven please I want to sing this song with mom and dad
@MemoryChatambalala-tq7yy
@MemoryChatambalala-tq7yy 11 ай бұрын
Continue resting in peace dad
@andersonmsosa6266
@andersonmsosa6266 6 ай бұрын
Great , melodious ,sentimental, and spiritual !
@governorchirindi1922
@governorchirindi1922 Жыл бұрын
The best version ever, the backing vocals sweet and calm. Glory be to God. Makes me proud to be a member of C.C.A.P
@TiyamikeChiromo
@TiyamikeChiromo 10 ай бұрын
Mulungu apitilize kukusogoleran kufalisa uthenga wake kuzera ku nyimbo zokoma zopasa tanthauzo amen
@florencechabwera9291
@florencechabwera9291 10 ай бұрын
This was mum's best song, every time I hear it I remember my mum.
@FranciscoLimitedeBarroso
@FranciscoLimitedeBarroso Жыл бұрын
Much love and blessings from Vila-ulongue Angonia- Mozambique.
@FelisterMvula-i6f
@FelisterMvula-i6f 10 ай бұрын
Mumandivetsa kukoma nyimbo zanu azimayi ngati ndafika kale kumwambako ❤❤❤❤❤
@EdwardChisembe-hh9gw
@EdwardChisembe-hh9gw Жыл бұрын
Much love from Kenya East Africa
@tamaJanuary
@tamaJanuary 9 күн бұрын
Agogo anga angazikonda kwambilii nyimboo zanu ❤ bwezii iyiiso atailoweza ,😢❤ ,,, Keep on resting well agogo angaa❤
@stewardmbele7385
@stewardmbele7385 4 ай бұрын
I feel strengthened with this song. May God almighty bless these ladies in Christ our Lord
@beatricemtonga2085
@beatricemtonga2085 11 ай бұрын
So touching and inspiring song.Well composed with spiritual maturity 🙌 🙏 ❤❤. God bless you all beautiful women ❤️ watching from zambia 🇿🇲 ❤️
@beatricemtonga2085
@beatricemtonga2085 11 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤
@SostinMatchado-z2o
@SostinMatchado-z2o 4 ай бұрын
Wow l want to sing this song in heaven, my lord you are my protector gide me right way to pass through
@EdithChimphamba
@EdithChimphamba 8 ай бұрын
I feel like heaven is hear on earth with these women. Their singing heals my broken heart. God bless you mamas
@mikechiwaya9284
@mikechiwaya9284 6 ай бұрын
Azimai awawa amatha..I was once a church elder for their ward in Lilongwe kawale 3 under masintha CCAP.
@YohaneYona-qn6el
@YohaneYona-qn6el 5 ай бұрын
Honestly,I feel so deeply blessed whenever am listening to this song.Ooooh Jehovah you are my God.
@harrisonbrownchikadza3390
@harrisonbrownchikadza3390 Жыл бұрын
Kumwamba kuzilemekezeka. This is so amazing
@TrizaTalandira
@TrizaTalandira 8 ай бұрын
Mulungu azikudalitsani azimayi nthawi zonse pitilizani kuyimba bwino nyimbo zotsitsimutsa GOD bless you all Amen
@MoreenMakwinja
@MoreenMakwinja 8 күн бұрын
I always see my late Dad when I hear this song.imandikumbusa zambir
@CHIKOPABC
@CHIKOPABC 10 ай бұрын
❤ this song was well cooked May God continue giving you wisdom and more talent🎉
@ednamagwaya1107
@ednamagwaya1107 Жыл бұрын
On repeat and getting blessed, so grateful to YAHWEH ❤❤
@HabrilMalaya
@HabrilMalaya 2 ай бұрын
Pali nyimbo zina ngat wafika kale kumwamba ukamaimba kapena kuvera mulungu azikusogolelan mukundidalitsa kwambili azimai
@Zigawooking99
@Zigawooking99 10 ай бұрын
Azimai inuyo Mulungu akupatseni miyoyo yaitali mumandidalitsa ndisaname 😭❤❤❤❤❤🔥
@nixykansinjiro9602
@nixykansinjiro9602 2 ай бұрын
Nyimbo koma iyiiiii,, achmanyamata munayilingalira iyi, Ambuye apitirize kukutetezerani muutumiki wamayimbidweu. Zoona dziko lapansi limadana ndi chilungamo ❤
@WinforeMwakabaghe
@WinforeMwakabaghe 18 күн бұрын
Very inspiring indeed Yehova ndi mbusa wanga
@RachealGulitsa
@RachealGulitsa Жыл бұрын
May God enlarge your territory mamas i always blessed with your songs
@RachelMathandalizwe
@RachelMathandalizwe 5 ай бұрын
Amen nyimbo zanu ndidalitso wanga nthawi zonse mulunugu adzikudalitsani ❤❤😊
@RachelMathandalizwe
@RachelMathandalizwe Жыл бұрын
I miss this church alot azimai ndimakunyadilani kwambili ndi kawale two pafupi ndi mrs Chadewa
@charitykaiche3828
@charitykaiche3828 3 ай бұрын
Powerful massage 🙏🙏 the lord is my shepherd well composed song may God bless you all for preaching through singing lam listening from Zambia
@IsaacNjati
@IsaacNjati 5 ай бұрын
Azimai amatha kuimba pitlizani timadalitsika ndi nyimbo zanu amen
@HarrietChiwambo
@HarrietChiwambo 10 ай бұрын
This is a nice song keep it up dear mamas you are the best
@joycebamusi6164
@joycebamusi6164 11 ай бұрын
Psalm 23 v1-6 delivered & Simplified ❤ To DE PUBLIC for Edification !! I like it ,Kp De Fire Burning Masintha CCAP Chotsitsimutso Choir !! U R Indeed Another Tool /Arm to Revival to The Nation & Society!! Kp on Igniting De Flame !! May God Anoint & Equip U more 4ExtraOrdinary Service !! UP! UP JESUS !!❤❤💪🙏🙏🙏🙏
@PhilemonGondwe
@PhilemonGondwe 9 ай бұрын
Mmm this is really owesome may the almigty God richly bless you my Mothers
@FaithBwalya-x2p
@FaithBwalya-x2p 9 ай бұрын
The blessed woman's of God I love this spiritual songs.
@ChikumbusoMawindoh
@ChikumbusoMawindoh 11 ай бұрын
Keep on nice singing our Mothers listening from SA
@GraceUmali-t2l
@GraceUmali-t2l Ай бұрын
Tikutsitsimuka kobasi kuno ku Capetown south Africa ambuye akudaliseni nomse azimayi ❤❤
@petrokasokomera1926
@petrokasokomera1926 4 ай бұрын
May Lord bless this choir ndipo amayimba bwino kwambil
@andyliponda5377
@andyliponda5377 11 ай бұрын
My dad and mom, grannies inclusive I think you are in the house of the Lord!
@annakatungwe6775
@annakatungwe6775 Жыл бұрын
Beautiful singing with encouraging message. Keep it up mamas n stay blessed
@EstherKanthambi
@EstherKanthambi 5 ай бұрын
Nyimbo imeneyi 👆 imandipanga ine kukhulupila Yehova koposa chinthu chilichonse Amen
@AmnestyBanda
@AmnestyBanda 8 ай бұрын
Amai Chikaphonya ku Dowa atsogoleri achigwilizano anatsogolerapo nyimbo iyi mu Limbikani choir Mulungu anawadalitsa ndimau abwno❤
@sarahnamwera586
@sarahnamwera586 6 ай бұрын
She has a good voice indeed.my mom is a former limbikani choir member.We transferred out od Dowa
@hopembendela
@hopembendela Жыл бұрын
Thank you our mother for the sweetest song am here in south Africa proud of you
@MagieNgomo
@MagieNgomo 11 ай бұрын
May God the almighty bless the wemen of this choir
@SteveChayaluka
@SteveChayaluka 8 ай бұрын
@RonaldMkwalura
@RonaldMkwalura 9 ай бұрын
I'm proud about this spiritual song,God be you masintha women
@towelamngoma540
@towelamngoma540 Жыл бұрын
Masitha , am always blessed with your songs ,amen
@ezrasofasiphiri7266
@ezrasofasiphiri7266 26 күн бұрын
This direct from phsams 23 i always love this verse it inspires me
@PhillipMakonyola-ub6ec
@PhillipMakonyola-ub6ec Жыл бұрын
Always am blessed with your songs, keep it up
@Wongani-jg7nr
@Wongani-jg7nr 7 ай бұрын
Your music blesses me 🎉🎉
@MonicaMathumba
@MonicaMathumba Жыл бұрын
Just in love with the song keep up ladies its my every day morning song
@donaldogot9568
@donaldogot9568 9 ай бұрын
Yehova mbusa......wangadi....................wandigonesa!..................mumsipu x2 Yehova mbusa wanga di, ndiribe kusowa, wandigonesa bwinodi mumsipu okoma x2 Kumadzi ake..........odikha.............ndimoyowanga!...............wofoka x2 Kumadzi ake odikha anditsogolera, ndimoyo wanga wofoka waulimbikitsa x2 Mwazodza mutu...........mafuta...............mwadzadza chikho!....................changadi x2 Mwazodza mutu wanga ndi mafuta okoma, mwadzadza chikho changadi ine chisefuka x2 Kumadzi ake...........odikha.............ndimoyo wanga!................wofoka x2 Kumadzi ake odikha anditsogolera, ndimoyo wanga wofoka waulimbikitsa x2 Zokoma ndiza...........zakuyanja........ndikhala nyumba!............ya Mlungu x2 Zokoma ndizakuyanja zizanditsatako ndikhala mnyumba ya Mlungu ku nthawi zonsezo x2 mm mm mmm.............mmm mm mmm..........mm mm mmm.........mmm mm mmm x2 mm mmm mm mmm mm mm mmm mm mm mm mm mmm mm mmm mm mmmm x2 Oyera oyera oyera Yehova Mlungu wathu tikuyamikani Yehova chifukwa cha zokoma zonse mumatichitila pa myoyo yathu, zoonadi tilibe kusowa, paliponse mumati tsogolera, ndipo sitikhala ndi mantha popeza inuyo mumatipelekeza kuli konse komwe tipita, ndipo Zikomo Yehova chifukwa cha moyo wathu, ukapooka mumatilimbikitsa ndipo tikulonjeza Yehova tizakhala kunyumba yanu kunthawi zonse.... amen Zokoma ndiza........zakuyanja..........................ndikhala nyumba!.........ya Mlungu x2 Zokoma ndizakuyanja zizanditsatako ndikhala mnyumba ya Mlungu ku nthawi zonsezo x2
@misheckdaka9745
@misheckdaka9745 9 ай бұрын
I love the creativity, the content of the song, powerful song
@HarrietMakina
@HarrietMakina 9 ай бұрын
Azimayi inuyo mumatha. God bless you all.
@marthakanyangalazi-bd6qg
@marthakanyangalazi-bd6qg Жыл бұрын
More than a blessing may the good Lord enlarge your territories
@bernaphiri
@bernaphiri 8 ай бұрын
I dedicate this song to my sick grandmother wishing you a quick and speedy recovery ❤
@HebrewMichelo
@HebrewMichelo Күн бұрын
This song is my favorite to me I thank God 🙏 💕
@ChimwemweZiwande-hx1zl
@ChimwemweZiwande-hx1zl 11 ай бұрын
I remember my dad...he likes gospel songs
@khatazamalewezi4249
@khatazamalewezi4249 Жыл бұрын
Praise the lord, i feel so blessed,hallelujah
@phirimacdonald8638
@phirimacdonald8638 10 ай бұрын
Ilike the song,is international song keep it up mums
@rhodahmtambo-jx4dj
@rhodahmtambo-jx4dj 6 ай бұрын
Mukuimba bwino zedi azimayi, keep on❤
@hildankhata3169
@hildankhata3169 8 ай бұрын
Amayi mumandidalitsa. Ambuye akutsogolereni tikayimbe ndi Angelo pakutha pa zonsezi. Koma kukakhala chimwemwe chosatha. Ambuye ndisadzatsale ine nkayimbe nanu nyimbozi
@clarakafumba2398
@clarakafumba2398 Ай бұрын
Ambuye sataya wakeeee❤❤🎉
@JoeNjikho
@JoeNjikho Жыл бұрын
Amen Amen azimayi kuyimba mwalutso.
@MosesChapotera
@MosesChapotera 14 күн бұрын
Nice one. Proud of you
@madalitsokamphambe8517
@madalitsokamphambe8517 3 ай бұрын
This is very powerful..amen
@PromiseChimtengo-qy5qu
@PromiseChimtengo-qy5qu Ай бұрын
This is my prayer this night 🌃psalms 23 vs 1 to 6🙏
@MphatsoMiti
@MphatsoMiti 5 күн бұрын
This song is dedicated to my late grandfather Reverand Hamilton Hb Nyemba may his soul continue resting in internal peace 🕊️🕊️🙌🙏
@gamielymoyo2957
@gamielymoyo2957 Жыл бұрын
Well done Women of God Madintha uko ku Kaware2
@chikondimalowa1566
@chikondimalowa1566 Жыл бұрын
Best song , i like the bass ladies, l miss that bass lady, may her soul continue resting in peace
@chifunirokachingwe3700
@chifunirokachingwe3700 Жыл бұрын
I'm saying Mrs chigwani, May her soul rest in peace 😢
@Joy-in-chaos-rc9ff
@Joy-in-chaos-rc9ff 11 ай бұрын
Which one😞
@chikondimalowa1566
@chikondimalowa1566 11 ай бұрын
@@Joy-in-chaos-rc9ff Mrs Chingwani
@AndrewChasauka
@AndrewChasauka 4 ай бұрын
Nice
@LemianChikwera
@LemianChikwera 11 ай бұрын
A very beautiful song so spiritual and touching
@GreyAlfred-g2y
@GreyAlfred-g2y Жыл бұрын
Azimai mumathaaa ambuye akudalitseni
@HillaryBanda-k8r
@HillaryBanda-k8r 11 ай бұрын
This song reminds my young brother THEODORE may his soul rest in peace 😢😢😢
@AngellahMwanza
@AngellahMwanza 10 ай бұрын
A nice song God bless you mama
@IsaacNjati
@IsaacNjati 5 ай бұрын
That's powerful song glory to be God
@AlufeyoKamoto
@AlufeyoKamoto 5 ай бұрын
Good song form masitnha !
@AmosLapuwa
@AmosLapuwa 9 ай бұрын
Amayi a Masintha amanditsitsi mula maimbidwe awo. Mulungu aptrize kukutsogolerani
@RICHMANCHIMWAZA
@RICHMANCHIMWAZA 5 ай бұрын
It's amazing song , praise God
@JudyMaya-d5k
@JudyMaya-d5k 17 күн бұрын
Wow this song is Nice
@MirriamNamwai
@MirriamNamwai 6 ай бұрын
Powerful may God bless you
@TracySoko-k4o
@TracySoko-k4o 2 ай бұрын
Nice and well composed
@FloridaKamunthu
@FloridaKamunthu 6 күн бұрын
Very encouraging Masintha
@Chikumbutsojimu
@Chikumbutsojimu 2 ай бұрын
Inali nyimbo yoyamba imene inaimbidwa pamene agogo anga amanyamuka rest well my lovely grand father
@josephmkwanda6833
@josephmkwanda6833 8 ай бұрын
Mulungu ndiye chikondi..Amen
@BaxtonBanda
@BaxtonBanda Ай бұрын
Ndimakumbuka nayo akazinga tiimba titakhala pampando
@MasterMwanakhu
@MasterMwanakhu 2 ай бұрын
This is powerful song ❤
@TakondwarexSalamba-ln9qf
@TakondwarexSalamba-ln9qf 7 ай бұрын
Amen, am really blessed
@EssauChimangeni
@EssauChimangeni 3 ай бұрын
Ndikavera nyimbo iyi moyo wang umasinthik kwambr🙏
@hendrixkatanje8835
@hendrixkatanje8835 Жыл бұрын
Thank you for the song 🙏
@chrissymbewe4564
@chrissymbewe4564 Жыл бұрын
This is amazingly beautiful.
@MAVISMITI
@MAVISMITI Жыл бұрын
May the name of the lord be glorified
@MoreenSalim
@MoreenSalim 9 ай бұрын
Mumaimba bwino azimai pitilizani ❤❤❤❤
@KondwaniRichardNkhongoza
@KondwaniRichardNkhongoza 9 ай бұрын
Nyimbo zanu zimanditsitsimutsa Ambuye akuze malire a choir yanu
@CatherineMatiki
@CatherineMatiki Жыл бұрын
Inde Yehova ndi Musa wanga Amen
@evelyndaniel4641
@evelyndaniel4641 Жыл бұрын
Andigonetsa😊
@GetrudeUseni
@GetrudeUseni 8 ай бұрын
Always reminds me me of my dad,, hope he is in God's hands resting
@LilianNamfukwe-m8u
@LilianNamfukwe-m8u Жыл бұрын
I love the song n glory be to God
@MilikaNgulube
@MilikaNgulube Жыл бұрын
Mey God bless you and your family😊❤
@purityhare6436
@purityhare6436 Жыл бұрын
I love the sound 🔥🔥
BAYGUYSTAN | 1 СЕРИЯ | bayGUYS
36:55
bayGUYS
Рет қаралды 1,9 МЛН
人是不能做到吗?#火影忍者 #家人  #佐助
00:20
火影忍者一家
Рет қаралды 20 МЛН
It works #beatbox #tiktok
00:34
BeatboxJCOP
Рет қаралды 41 МЛН
You are Holy_ Malawian Worship 🔥🔥
26:11
Jr2³ Update
Рет қаралды 840 М.
Yehova M'busa Wanga
9:00
Eu Kay
Рет қаралды 642 М.
SULI WEKHA
5:39
Masintha Chitsitsimutso
Рет қаралды 514 М.
KUPEMPHERA KWANGA
6:43
Masintha Chitsitsimutso
Рет қаралды 217 М.
Nyimbo Zolambira with          Natural Favour _ track1 (MalawiWorship 🇲🇼)
26:11
MALAWI UPPER ROOM WORSHIP
Рет қаралды 721 М.
Ndirande Anglican voices Malawi Gospel
17:14
MsTaque
Рет қаралды 552 М.
PARADAIZO
6:38
Masintha Chitsitsimutso
Рет қаралды 158 М.
Rev Alexander Kambiri preaching the SIDE B of the funeral service at Malomo Ntchisi
19:11
CLARA NGULUBE NDIKONDA MULUNGU OFFICIAL VIDEO HD
5:39
Darlington Matabwa
Рет қаралды 1,3 МЛН
BAYGUYSTAN | 1 СЕРИЯ | bayGUYS
36:55
bayGUYS
Рет қаралды 1,9 МЛН