ZA DALITSO KABAMBE NDI CHARLES NSAKU EEEH ~ KUTHEKA SIMUNAMVE ZOMWE WAPANGA CHARLES NSAKU KUSELIKO

  Рет қаралды 44,169

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 216
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 3 күн бұрын
Wow wow nice song from Msaku, Chakwera zolubwalubwa sapanga nawo. Man of integrity ❤
@VictorNyundo
@VictorNyundo 3 күн бұрын
Kabambe is a winner. No body can oppose this.
@EfassyChisi
@EfassyChisi 11 минут бұрын
What a nice song ❤
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 Күн бұрын
Charles nsako u more talented 🎉
@timothymhone2340
@timothymhone2340 3 күн бұрын
Nice song Charles nsaku 🔥🔥🔥🔥
@BensonJere-i9k
@BensonJere-i9k 3 күн бұрын
Kabambe more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@AllanKuthindi-g1h
@AllanKuthindi-g1h Минут бұрын
nice song❤️🔥🔥🔥
@LetshaChirwa
@LetshaChirwa 2 күн бұрын
Garu nsako malawi akuwawilamu
@johnchicoti
@johnchicoti Күн бұрын
More fire 🔥 🔥 🔥 🔥 nsaku
@LonelyNyirenda-u6w
@LonelyNyirenda-u6w 2 күн бұрын
Nsaku more fire I love it❤❤❤❤❤❤
@EnerstBanda-m4s
@EnerstBanda-m4s 3 күн бұрын
Kabambe more fire 🔥
@Milanzi-nb5fv
@Milanzi-nb5fv 3 күн бұрын
Nice song koma akuchemelera team yoluza😄
@mlimolubanda6348
@mlimolubanda6348 3 күн бұрын
Za Charles nsako ndizako ....ife sitingamvele nyimboyo
@christopherphiri8476
@christopherphiri8476 3 күн бұрын
Chitsiru nsaku ndi ndwela chabe gumkumo mmeneyu
@MarthaDeborahMhango-sx8dk
@MarthaDeborahMhango-sx8dk 2 күн бұрын
Nde zikugwirizana bwanji ndi kabambe ndi nyimboyi Pali connection yanji pamenepa zaiiii
@GeoffreyBokosi
@GeoffreyBokosi 3 күн бұрын
Charles umakwana mcp woeeee❤❤❤❤❤❤❤
@Gunde-yo7ew
@Gunde-yo7ew 2 күн бұрын
Charle nsako wopusa kwam biri ndi nyimbo yakeyo
@WillyMajiya
@WillyMajiya 2 күн бұрын
Ndi achitsirutu Kodi maluzi amukwapula
@VuyisekaTukwayo-wt5pn
@VuyisekaTukwayo-wt5pn 12 сағат бұрын
Kodi akati otsutsa ndi dzina lamatenda eti ndidziwa mu 2024
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 3 күн бұрын
Wakwiya ndi mfiti yokupha ma alubino, Msaku nyimbo wakwapula iyi, Chakwera ndi katundu, samayankha ti ana AI. Iye koma chitukuko
@KondwaniGumba
@KondwaniGumba 3 күн бұрын
Mcp 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 , chakwera sakamba za ena ndipo sanyoza aliyense.
@austinvincent1264
@austinvincent1264 2 күн бұрын
Muli kudzudzulatu mumnyimbo iyiyi koma kuinvela uli side ina singakukomele
@ackfordkasambeni3687
@ackfordkasambeni3687 3 күн бұрын
Nsako ndi Musician wabwino 🎉
@austinvincent1264
@austinvincent1264 2 күн бұрын
Muli chilungamo munyimbo iyi dziko losinthasintha utsogoleli silimakhala ndichitukuko ndizoona izi maiko amene samasintha sintha president ndotukuka
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 күн бұрын
Kabambe my vote❤
@IsaacKulongwe-ol5mx
@IsaacKulongwe-ol5mx 3 күн бұрын
Wakwiya ndi Mfwiti ndi nyimbo iyii
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 күн бұрын
Charles Nsaku ndiwa Mcp but you will regrate one day
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 3 күн бұрын
DK MY VOTE❤❤❤
@SaukaniMbiliyawanda-ur7zb
@SaukaniMbiliyawanda-ur7zb 3 күн бұрын
Nsaku umakwana BOMA ndilomweli sitikusintha
@Jane-qb5qf
@Jane-qb5qf 3 күн бұрын
Zaziiiiii angofuna ndalama awo nawo a msaku tayimani pachilungamo basi anthu akuvutika zoona kumayionerera ndalama kumagwa chonchi zikukomera ali kunja akamatumiza ndalama kutumiza yochepa uko yambiri koma nanga alikumeneko akumva bwanji ndalama ikusowa inu osamangoombera manja ayi a Chakwera zoona anapeza ndalama muboma mulibe koma akaneyesesa kupeza njira yobwenzerersera mumalo motero akubizika ndikuhonga oyimba zaziii
@Jane-qb5qf
@Jane-qb5qf 3 күн бұрын
Nyimbo imeneyi a Chakwera mkoyamba kukhala muboma ndi akubwenzera kwa ndani ngati anayamba akhalapo kale ndiye akubwenzera, peter akayankhula izi after zomwe anamuchita mu 2019
@YohaneSteven-v4w
@YohaneSteven-v4w 2 күн бұрын
Palibe nkhonya yobwedzera apa Nsaku,vomeredzani Chakwera ndiolephera komanso ndalama idyani nyimbozi imbani,Kabambe woyeeeeeeee
@AgnesNjikho
@AgnesNjikho 3 күн бұрын
Usalile nkhonya yobwezera kuwawa nchito iyo
@BerthaChisoni2
@BerthaChisoni2 2 күн бұрын
Nsaku wachoka lit kupita ku Malawi ..sianali ku south Africa
@SammyKalebe
@SammyKalebe 3 күн бұрын
More fire
@samuelsamirawjohns2671
@samuelsamirawjohns2671 3 күн бұрын
Kabambe 2025 Boma ndipo osakaikanso ndithu
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 3 күн бұрын
Aku,. D. P. P, amapelekaso ndalama mwaiwala. M. C. P. Iyenela kupelekaso kwawoimba
@ChimwemweMakopa
@ChimwemweMakopa 12 сағат бұрын
Nyimbo ili bwino chabe kuti akutamandila njoka...km nsaku luso lilipobe
@DannyKalumbaWaBanda-q7o
@DannyKalumbaWaBanda-q7o 2 күн бұрын
Kabambe my vote
@CentTiger
@CentTiger 3 күн бұрын
Inu Ansaku kodi kwanuko feteleza ndi chimanga mukugula ndalama zingatiii, nanga sopo osambila, ochapila ndi zina zose zofunikila ndalama zingati, ngat iweyo ukukwanitas ndi zomwe akukuhongazo akukulipilazo uzingowanyela , usatipwetekese mdziko munoooo!! Enafe tilibe dziko lina lopita dziko lathu ndi lino, paja inu muli kunjaa not.............!!
@ShinglaiAli-be3yn
@ShinglaiAli-be3yn 3 күн бұрын
Mboli yake ameneyu....pamtumbo pake munthu wamkulu koma opanda nzeru,,, Maluzi amuthibula akatero
@ChristopherMwase-n7n
@ChristopherMwase-n7n 2 күн бұрын
😂😂😂😂
@TysonMwenye
@TysonMwenye 2 күн бұрын
Aaaa chilekeni chilezelere ichi....chikatero ndiyekut chikufuna yamowa basi😂😂 Charles apa wadzionongera career😢
@TraNcy-f9c
@TraNcy-f9c 2 күн бұрын
Ndipo munthu omvetsa chisoni ngati uyu
@JalaphyBandah-h7n
@JalaphyBandah-h7n 2 күн бұрын
Zinazi Koma Mmmm athunu muziwona njala muziko lathu lamalawi. Osatizitukuko zopanda athukudyazooooo
@ShavickMzula
@ShavickMzula 3 күн бұрын
Kabambe fire
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 3 күн бұрын
Tidzavotela amene akupatsa ndalama oimba achakwela utchaya kugwetsa abambe olo pita
@LynesBanda-r1p
@LynesBanda-r1p 2 күн бұрын
Enawa ndi atidye nawo kuimbaku amafuna ndalama zamsowa Nsaku zoona fertilizer mpaka 107,000 agula anthu angat
@LetshaChirwa
@LetshaChirwa 2 күн бұрын
Nkhan km ya mr president kabambe
@KumbukaniBenala
@KumbukaniBenala 3 күн бұрын
Naye nsako ndi munthu maplan amatha kuyamba kunyika ngat mmene wavikila 😢😢😢😢
@JacksonNamakhwa-jp4mg
@JacksonNamakhwa-jp4mg 2 күн бұрын
Angofuna ndalama awa ndi ndalama za mcp zaphwekazi
@FrankKambwani
@FrankKambwani 2 күн бұрын
Nyimbo ya Nsaku,..ati Chakwera akuyendetsa bwino..fertilizer from k20pin to K110 000 ufiti ulipodi ku Malawi
@CharlesPembaMusaiwale
@CharlesPembaMusaiwale 3 күн бұрын
Nsalu has shown dyera kufuna Dollar
@ChikondiMasebo
@ChikondiMasebo 2 күн бұрын
A nsaku amangokakamira kuyimba koma sadziwa kuyimba bulutu wachabechabe
@salatielmartin9499
@salatielmartin9499 3 күн бұрын
Musanyoze Nsaku wayimba momwe waiverera MCP
@ashankagwa668
@ashankagwa668 3 күн бұрын
U are talented, zinazo sizikundikhudza kkk
@majorsonfrank4324
@majorsonfrank4324 2 күн бұрын
Paja ansaku munazolowera kudya zachipani? Zipatseni ulemu kt anthu asakutukwaneni .mukutha kudya ndalama za MCP zo koma tsiku lina zizakudyani ndalama zachipanizo.
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 күн бұрын
Mufune musafune Kabambe ndi president wa utm adasankhidwa ndi ma deligates
@MatthewKaliyati
@MatthewKaliyati 3 күн бұрын
Naye kufuna kukadya nawo ndalamaza chikangawa maluzi avuta komaso watopa ndikulezela kuno ku south, good luck
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 күн бұрын
Simukudziwa kodi kuti ali ku Malawi kkkkk
@ishmaelimedi7363
@ishmaelimedi7363 3 күн бұрын
Charles ndi njala iyi, angofuna ndalama basi, ali south Africa kufuna ndalama zodyela zoyimba zabwino zija nzeru linatha
@HusseinMofatt
@HusseinMofatt 2 күн бұрын
Zochemelela chitsilu chakwelazo ifetu ayi manyiamenewo sitipanganawo
@BlessingsTomoka
@BlessingsTomoka 2 күн бұрын
Akabambe akumbutsa mau agogo anga ndili mu teenager Anati mamuna akabwera kufunsila banja ngati akunena za ena mutayeni umunthu alibe Khalidwe alibe Ndipo zinandipindulila❤❤❤
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 күн бұрын
Kabambe 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 3 күн бұрын
Guys ngamo ndiyabwino Msuku ndi katundu, Kabambe ndi mwana size yake ndi Kumkuyu
@KumbukaniBenala
@KumbukaniBenala 3 күн бұрын
Mpaka 90min ukufuna sugar tigule 18pin nawe wasowa zoimba eti akupepetula et
@DumiMhango
@DumiMhango 3 күн бұрын
Kabambe❤
@GolosiMalapata
@GolosiMalapata 2 күн бұрын
Wayimba nyimboyi iyeyo akufuna ndalama kuti apaseni osamadela ngawa ndi akapiniwa
@VuyisekaTukwayo-wt5pn
@VuyisekaTukwayo-wt5pn 12 сағат бұрын
Nsaku ndiyetu akutero nsalile
@GiftUlaya
@GiftUlaya 3 күн бұрын
Chinyimbo 🔥🔥🔥🔥🔥
@PaulDaka-dc3re
@PaulDaka-dc3re 3 күн бұрын
Kapekedwe ka nyimboyi kalibwino vuto mkumene ikukamba zotamandira kwinako🙅🏿🙅🏿🙆🙆🙆
@AliNtolera
@AliNtolera 2 күн бұрын
Msaku alibe nyumba umphawi unamukanda adye nawo ndalamazo. Ngati zili choncho asiye anthu avote mwa ufulu opanda kubela anthu technology manually tiwone ngati anthu amuvotere Msaku akufuna ndalama zamagazi ndiye wagwilitsa ntchito luso lake asaphe sogolo LA anthu Ena chifukwa iwo alibe luso kuti Chakwera angawagule amadalila usogoleri kwabwino
@LonelyNyirenda-u6w
@LonelyNyirenda-u6w 2 күн бұрын
UTM will never be in Government
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 3 күн бұрын
Nyimboyo sindivera coz ngat zikoli lili pamot coz mcp
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 3 күн бұрын
Ngat mufuna kulowa m,boma Mujambule azikwanje wina atamupha apapa sizikubeba km chakwela sakuchoka
@Sugerman-tw4do
@Sugerman-tw4do 3 күн бұрын
Bambo wakulu ngati iwe kuithawa joz sikupusa kumeneko achisilu opanda mzelu
@AlicePondani
@AlicePondani 2 күн бұрын
Akufuna ndlama a nsaku,panja Mcp nkomwe kuli mgodi wa ndlama,tadzidyani guys,mcp ikuopa milandu thats why ikungogawa ndlama
@RodgersSaikonde-q6j
@RodgersSaikonde-q6j 3 күн бұрын
Komatu oyimba athu ku Malawi mwakonda ndalama mpaka mwaleka ntchito yanu yolalikira uthenga wabwino ku mtundu wa anthu adziko la pansi
@PaulManyamba
@PaulManyamba 3 күн бұрын
Nsaku ndiwe ndani iweee kape ngati iwee nyumba unagulitsa ukusowa pokhala auze akugule a mcp ungopeza yogula chimanga
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 3 күн бұрын
Sakuchoka chakwela bodzalanulo mufika potopa
@MacfelsonMunthali
@MacfelsonMunthali 3 күн бұрын
Nsaku woye!!!
@Maulana-s2n
@Maulana-s2n 3 күн бұрын
Aliyense ochemelera nunkha manyi chakwera ndi mfiti yopanga chisoni
@PatrickMbenje
@PatrickMbenje 3 күн бұрын
A Nsaku ndinu a chisiru kuimba nyimbo yolimbikisa ziwawa Malo momanga umodzi
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 3 күн бұрын
Team DK
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@mkandawirem610
@mkandawirem610 2 күн бұрын
President of the Malawi
@GiftNkhoma-n2w
@GiftNkhoma-n2w 3 күн бұрын
Ku South kwamvuta ndeno mwati muimbile nyimbo 😂😂😂 or mayaz ulibe ukufuna ndalama 😂😂😂
@abdulsalammkwepu3321
@abdulsalammkwepu3321 2 күн бұрын
Koma mmene zinthu zikuvutira M,Malawi muno mphanvu zoimbira mfiti mmanja anthu akuzitenga kuti,?
@GophineNjikho
@GophineNjikho 3 күн бұрын
Kabambe chonde maso pasogolo pazimene wauza anthu . Anapanga okha campaign kutiuza kuti ndiwe ofunikira anati usi ngoipa nanga wabwino akhala ndani. Mlendo ana amaona kholo mumene akumupasira ulemu pamepa amaziwa kuti mulenduyu ngofunikira nanga ma delicate akanati bwanji. Ma top chairs ndi amene anayamba kumpasa ulemu. Utm motoooooo koma chonde inuyu ntchito Yani yikhale kt munga lumikize bwanji anthu a usi ndi camp yanu . Izi za mademu zikutaisani thawi khalani ndi sogolere wapa round table osatiwaku seu.
@MartinMajola
@MartinMajola 3 күн бұрын
Kabambe anafumdo sologolo la malawi
@ellensambo6323
@ellensambo6323 3 күн бұрын
Voti yili ndi mtima Bola money
@QueneteCatundulo
@QueneteCatundulo 3 күн бұрын
Charles take care.
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 3 күн бұрын
Nsako ndiwe wa nosense, matokoso anakuzerekesa
@SandramValilani
@SandramValilani 3 күн бұрын
koma ndalama zaphweka ku MCP iiii acharles mpaka kuimbila mfiti manja mmm ai zikomo
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 3 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤
@NaomieBanda-t6g
@NaomieBanda-t6g 2 күн бұрын
Ingonwerani kuno ansaku nanu tizakumwesani mowa munthu wopanda plan
@GeoffreyKaluwa-em7eb
@GeoffreyKaluwa-em7eb 3 күн бұрын
Angompasa yoti akagule alomo basi😂😂😂
@miraclejohnphiri7687
@miraclejohnphiri7687 2 күн бұрын
Koma oimba aku malawi uphawi kwambili kupepha mwazeru kumeneko azoons
@lindadzaoneni
@lindadzaoneni 3 күн бұрын
Inu Nsaku amakhala ku Malawi kuno? Sakumva nawo kuwawa uyu
@ShemieMavuto
@ShemieMavuto 3 күн бұрын
Nsaku chitsiru,,,Chakwera akubwenzera Kwa a malawi'fe?chitukuko chake chiti?
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 2 күн бұрын
Kabambe ulendo uno palibe opikisana naye pankhani ya nzeru zoyendesela dziko amene akususa atchule wake timuwone
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 күн бұрын
Viva kabambe 💪💪
@ManuelMuzembe
@ManuelMuzembe 2 күн бұрын
Viva❤❤
@RitaBan-t7c
@RitaBan-t7c 3 күн бұрын
Umphawi wakuphani mwabvumbuluka kufuna chithumba cha Achakwera ayii mudzukira a Nsako
@GilbatChimwaza
@GilbatChimwaza 3 күн бұрын
Kabambe sangakake muyiwale mpikisano ndiwa d p p ndi m c p basi
@MoffatChirwa-z4e
@MoffatChirwa-z4e 3 күн бұрын
Kabambe motto Pauline zobera🎉🎉
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 3 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@MadalitsoIbrahim
@MadalitsoIbrahim 3 күн бұрын
Saku unalibe pofikila ku malawi kuno. Apo ukusaka thandizo tikuziwa
@CharlesChamveka-u6r
@CharlesChamveka-u6r 3 күн бұрын
Chitsilu chitukuko chogawanisa athu uzatipeza Kuno ku mpanje
@AgnesNjikho
@AgnesNjikho 3 күн бұрын
Kumenya kugwesa ❤ boma ndilomweli nchalo ameneyo motooooooo buuuuuuui usalile kkkkkkkkkkk
@frankndawandawa6666
@frankndawandawa6666 2 күн бұрын
Mwamuona DK akulubwa lubwa apa mumsamale ameneyu 2025 wamuboma baxi
A Malawi Kususuka Ndi Ndalama Tidzaphetsa Ana - Bon Kalindo
17:49
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1,6 М.
كم بصير عمركم عام ٢٠٢٥😍 #shorts #hasanandnour
00:27
hasan and nour shorts
Рет қаралды 11 МЛН
Players push long pins through a cardboard box attempting to pop the balloon!
00:31
Lamborghini vs Smoke 😱
00:38
Topper Guild
Рет қаралды 28 МЛН
VN Ya Lero Andale Ambiri Adananane - Ken Msonda
29:04
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 9 М.
GWEDE GWEDE PA MALAWI | 29 NOVEMBER 2024
30:31
Malawi News Update
Рет қаралды 9 М.
TIKUFERANJI? | 17NOVEMBER 2024
25:41
Malawi News Update
Рет қаралды 29 М.
كم بصير عمركم عام ٢٠٢٥😍 #shorts #hasanandnour
00:27
hasan and nour shorts
Рет қаралды 11 МЛН