Zaululika, Iyi Ikuzizimusani, Msilikali Winanso Kulongosola Zonse Mene Zinakonzedwela

  Рет қаралды 309,419

Mukuziwa?

Mukuziwa?

Күн бұрын

#chilima #skc #chakwera #mcp #utm #malawi #trending #viral

Пікірлер: 335
@idrussosman1346
@idrussosman1346 3 ай бұрын
Our Ibrahim Toare the likes of Bokinafaso President. Thanks my Fellow Wasili
@RejoiceKamanga
@RejoiceKamanga 3 ай бұрын
❤❤❤ zilibwino kumayankhula chillungamo tchimo ndilachakwera yekha. Mulungu akudaliseni bro 😢😢
@mosesjnrnyamyola9149
@mosesjnrnyamyola9149 3 ай бұрын
May God protect you brother man till chilungamo chifike pa ground
@JohnAsendi
@JohnAsendi 3 ай бұрын
Ulemu wanu munthu wankulu ndiinu nzelu mukuimila amalawi asati zinazo zikungozinenepela ngati njovu chilungamo kumachiona koma kuchibisa akufuna udindo Allah adzakukhaulisani tsiku Lakiyama lnshaallh 🙏🙏🙏🙏
@ExweloMsukwa
@ExweloMsukwa 7 күн бұрын
Chilugamo chimawawa
@CalvinTonyWaluma
@CalvinTonyWaluma 3 ай бұрын
mumaziwa ndiye simudaiteteze ndege bwanji ........inuso mwapha nawo chief
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 3 ай бұрын
Mbwerera za anthu aku Malawi ndi zimenezo akufuna kuoneka anzeru pano.
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 3 ай бұрын
The son of MCP stupid
@SaidDayton
@SaidDayton 3 ай бұрын
😢😢😢😢 mlungu simuthu chilungamo chiziwika Soon in sha Allah . allah Akbar 😮😮
@idreesahzaneer5769
@idreesahzaneer5769 3 ай бұрын
Inshallah
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 3 ай бұрын
Ukutsutsawe do your audio dzitchule dzina nafeso tikumve fundo zako on public. Simple.
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 ай бұрын
Big up to you brother may almighty God protect you
@murraykaliwo6638
@murraykaliwo6638 3 ай бұрын
Aaa koma ndiyetu asilikali ake ndiopoilatu, ndiye kuti apha nao ngati anachita kuphedwadi
@IsaacKachala-ny9km
@IsaacKachala-ny9km 3 ай бұрын
Commando wathu iweye big up kuyimila chilungamu
@EuritaDeric-fz3ds
@EuritaDeric-fz3ds 3 ай бұрын
Big God bless you 🙏
@rexakalua-dd2qg
@rexakalua-dd2qg 3 ай бұрын
A Malawi ndinu oputsa osandipsetsa mtima mwamva ngati ndizoona bwanji osamunyanyalira Chakwerayo kuti atule udindo 😢
@AbraoEliseuJone
@AbraoEliseuJone 3 ай бұрын
Zimawawa kwa wina aliyense zoona kwa obadwa ndiponso wobhereka@❤
@WilliamNyirenda-xq4km
@WilliamNyirenda-xq4km 3 ай бұрын
Ndipo inu inu
@HajeerahBeib
@HajeerahBeib 3 ай бұрын
Inshallah mulungu akutetezani mpaka chilungamo xhiziweke
@samueljuly8129
@samueljuly8129 3 ай бұрын
Thanks so much our good brother . We really need the truth on this matter .
@AndyWilliams-b3x
@AndyWilliams-b3x 3 ай бұрын
we are behind you comrade, we don't fear anyone.
@AdamMwale-y3y
@AdamMwale-y3y 3 ай бұрын
Sitikufuna kuvaso zimenezo ayi zilibe tchito ikakwana yakwana basi Mulungu analemba anafa atumiki amene amalankhulisana ndi Mulungu ndye mukanene achilima
@samueldiston
@samueldiston Ай бұрын
❤❤❤❤❤thanks😢😢😢😢😢😢
@InnocentCcij
@InnocentCcij 3 ай бұрын
God bless you and protect you 😢😢😢😢
@abrahammalunga5132
@abrahammalunga5132 3 ай бұрын
Kodi ulikuti ukuoneka bwanj😂😂
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 ай бұрын
Thanks alot my brother good Messnge Chakwela you mast go
@IshumaelGama
@IshumaelGama Ай бұрын
Undiolotse ndikakudye kutali 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 Ufuti wachakwera
@corretabanda7685
@corretabanda7685 3 ай бұрын
Thanks so much. More fire osawopa
@chancychikoko-ns5nl
@chancychikoko-ns5nl 3 ай бұрын
Mvuto Malawi timankhulipira social media 😅
@LTTechnician-xp2zs
@LTTechnician-xp2zs 3 ай бұрын
Timakhulupilira ndikumene cz sizonse zimakhala zabodza. Kachilungamo kamakhala in one way or the other
@MaryMsiska-mq8em
@MaryMsiska-mq8em Ай бұрын
Mhuh continue Resting in peace 😢
@nickmzozodo4163
@nickmzozodo4163 3 ай бұрын
Good job sir
@faithmwanga6078
@faithmwanga6078 3 ай бұрын
Bwana kunyansa zoona, you're heartless chakwela
@saulosjeque8115
@saulosjeque8115 3 ай бұрын
Thank you very much???
@PreciousMakuluni-b2s
@PreciousMakuluni-b2s Ай бұрын
Mcp chakwera mfiti galu chilima tizamulila mpaka kale kale chilima anali tsogolo la amalawi
@JUNIORMAXWELL-le2mc
@JUNIORMAXWELL-le2mc 3 ай бұрын
God bless you 🙏🙏
@WillySocrates
@WillySocrates 3 ай бұрын
Or utafa ukaona ufumu wa Mulungu pot kulibe wambeu ku dziko lapansi God bless u soldier 🙏🙏🙏
@KelvinPhiri750
@KelvinPhiri750 3 ай бұрын
Mpaka pano mu chaka cha 2024 ,tikanaganizabe kuti Otilamulira ndi milungu, kuti iwowo imfa singawakhudze.😢 whether assasinated or not its all death😢
@AchinaKellz
@AchinaKellz 3 ай бұрын
Guy's let's work up fighting for chakwera go
@murraykaliwo6638
@murraykaliwo6638 3 ай бұрын
Ndipo munthu akuyankhulani bodza limene kaya mukuti ndindani, koma ndi opusa kwambiri! Bwanji samanena asanakwele ndegeyo
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 3 ай бұрын
Ndipo ndi galu kwabasi ameneyu
@PeaceMaker-p6j
@PeaceMaker-p6j 3 ай бұрын
Respect
@RaymondKaumba
@RaymondKaumba 3 ай бұрын
Kubisala ku South Africa mkumati wabisala akupeza
@MimuGeorge
@MimuGeorge Ай бұрын
God bless you
@NahwaalPalmer
@NahwaalPalmer 3 ай бұрын
Ulemu wanu m'fumu ❤
@GanizaniKachigulu
@GanizaniKachigulu 3 ай бұрын
Umbuliu ndimatenda pena.kodi who chose the plane as veep transport to mzuzu
@petrochimutu7037
@petrochimutu7037 3 ай бұрын
umbuli ovesa chison tu
@janetchinga695
@janetchinga695 3 ай бұрын
😢😢😢 mulungu alipo sakumangani ndithu
@MarriumMubarak-r4n
@MarriumMubarak-r4n 3 ай бұрын
Mulungu sateteza anthu amabodza ngati uyu!
@AtupereMwenefumbo
@AtupereMwenefumbo 3 ай бұрын
Aaaaah thank God chilungamo chixiwike
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 3 ай бұрын
Ndipo olo kumuuza mwana wazaka 7 akhoza kudziwilatu kt ndi bodza ili aaa mkayidi ndiye kt chiyani
@NescotNyamwela
@NescotNyamwela 3 ай бұрын
Ine phe ku capetown za Malawi ndinayiwalako
@Deborahjimu-xf5dk
@Deborahjimu-xf5dk 2 ай бұрын
God protect you
@ActiveChembe
@ActiveChembe 2 ай бұрын
Anthu for aja ndiAmene anapanga kokupha avice prsdnt
@KachiluweWilimoti-t6u
@KachiluweWilimoti-t6u 2 ай бұрын
Ndiwe munthu otani udatani kunena chilima asanafe kmnso chilima ndiye mwini network bwanji osanyamuka
@eliasmatewere1403
@eliasmatewere1403 3 ай бұрын
God be with you brother
@MarriumMubarak-r4n
@MarriumMubarak-r4n 3 ай бұрын
God could not be with this brother!
@olipamaseko2693
@olipamaseko2693 2 ай бұрын
Uyuyu ndi wabodza weniweni ine ndili kuno ku Mzuzu abale kunali mvula inayamba Sunday koma inagwa kwambiri tsiku la Monday komanso onse akuti ndege ku LL inanyamuka 9:17 am Ife tikulira nanu limodzi sogolo lowala lathu lapita koma mmm ma boza satithandiza kuno kunali chifunga
@ChikondiGlibert
@ChikondiGlibert 3 ай бұрын
Iwe ndiye chitsilu chothelatu udziwe. Komwe uliko
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 3 ай бұрын
Zikomo m'bale chilungamo chidziwike, komaso a Mbuye akhale mbaliyanu
@harrispheleni2205
@harrispheleni2205 3 ай бұрын
Iwe ndi kape video ya momwe inanyakukira mpaka kugwa? Anakanika president Raisi kapusitse ana a utm azako
@sammyjonnes
@sammyjonnes 4 күн бұрын
ETI NDI ZOONA NSILIKALIYU ANAPEDWA ???
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
@KelvinJpchimphepo-sh6nc 3 ай бұрын
Apa sipakuyenera kuwopa chifukwa zikatero mawa zizachitikira kwayena ndiye tizivomeleza zimenez mpaka liti apha anthu asogoro lawo angat pangani zomwezo bwana anthu ali pambuyo panu, tima dikira anthu ngat inu ndipo izi zowawa kwabasi, titeteze dziko osat kuphana tokha tokha ngat ndife anthu ndife obwera zoona
@YobuSatinphiri
@YobuSatinphiri 3 ай бұрын
WHY ANACHOSA BLACK BOX?
@GarkiThom
@GarkiThom Ай бұрын
..nkhan za ndale..IZI
@PriscaChapsa
@PriscaChapsa 2 ай бұрын
Iwe ndi opusa iwe ngat umaziwa chilunga umakeka kuulula chilima asanafe bwanji
@JoeMwandira-tq9rs
@JoeMwandira-tq9rs 3 ай бұрын
Mno mu Malawi ngatimli anthu ngati awawa bwedzi dzikolathu likanakhala lachilungamo tsangakuphe mdzanga amalawi ose akuimililani bwana opepela okha ndi amene adzvotera mbuziyi
@leoleonard2103
@leoleonard2103 3 ай бұрын
Izii ndiye zowona osati zomwe akunama chakwela
@NafeAlie
@NafeAlie 3 ай бұрын
Imeneyo singozi ai masewera
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 3 ай бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose adziwa yekha chochita nximu wanu uuse mumtendere bwana chilima
@AaronJaccob-us7xn
@AaronJaccob-us7xn 3 ай бұрын
zabodza izi umbon mwadziwa bwanji kut fuel anali ochepa osatinamiza apa ayi asilamu pajad mtopola vuto mulowetsa ndale
@alai-er1cp
@alai-er1cp 3 ай бұрын
Ku joni ko mumafatsatu 😂😂😂😂😂😂 msilikali wa army osadziwa kusiyanitsa pakati pa blackbox ndi blackboard 😂
@BrianBanda-mr2iu
@BrianBanda-mr2iu 3 ай бұрын
Kkkkkkkki, Galu wachabeee Uyu
@JosephChimangeni-x1b
@JosephChimangeni-x1b 2 ай бұрын
it is well
@LegendLandlord-cq6cw
@LegendLandlord-cq6cw 2 ай бұрын
😢😢 zosayenda konse
@LabKazembe
@LabKazembe 3 ай бұрын
Panyini pamake chakwelayo ndipo imfa yake idzankhala yogendedwa ndi miyala ameneyo
@GeorgeTembo-v6i
@GeorgeTembo-v6i 3 ай бұрын
Good job
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 3 ай бұрын
Uyuyu ndi chitsilu ndipo ineyo nditakhala wakubanja nditha kumutukwana chifukwa olo awulule munthu atafa kale ndi chitsilu kwambili ndipo ndimunthu wodanitsa kwambili aziuza zitsilunu iyaa
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 3 ай бұрын
Chitsiru choyamba ndiwe galu mwana wa MCP 😢
@mphatsokuwali6389
@mphatsokuwali6389 21 күн бұрын
kkkkkkkkkk dpp oyee
@TrichetSawa-u3x
@TrichetSawa-u3x 9 күн бұрын
Whaspp
@AlinafePhiri-g5k
@AlinafePhiri-g5k 3 ай бұрын
Komaso zikuchita kuoneka kuti ndibodza inu mumadziwa bwanji kuti athu amakuwa chosecho inu munali ku lilongwe nanga pomwe athu akakasokoneza ndege inu munatani kuwauza achirima kuti asakwere muligulu limodzi lakupharo
@BrendahKamwana
@BrendahKamwana 3 ай бұрын
Inu anthu ena nngodabwitsadi
@CHIKUMBUTSOSENDEZA
@CHIKUMBUTSOSENDEZA Ай бұрын
Ulemu wanu bwana tidikila inu zinazo
@FlorenceKaposa
@FlorenceKaposa 9 күн бұрын
😢😢😢
@benjaminmitala9877
@benjaminmitala9877 3 ай бұрын
No comment
@ChilangizoKajiyabanda
@ChilangizoKajiyabanda 21 күн бұрын
But to be honest why u tell as today after we lost people
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 3 ай бұрын
Give him bakili muluzi TV KZbin channel here thats we can understand what's going on here 🫵🫵🫵🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🤔🤔🤔🤔
@RajanaBaluwesi
@RajanaBaluwesi 3 ай бұрын
Uyuyu amutuma ndipo amutumawo ali chete. Satana akafuna kusokoneza dziko amalisokoneza. Muganiza kuti anthu akulionera kukondwa ndikoli? Olo mutasintha atsogoleri ambili mbili muganiza kuti zinthu zidzasintha? Poti wina pamenepa akumenya campaign kuti adzadyerenso aMalawi, tsegukani mmaso watumidwa uyu. Munthu wachilungamo sabisala apite direct akafotokoze kuti aMalawi asiye chiwewe.
@BrianBanda-mr2iu
@BrianBanda-mr2iu 3 ай бұрын
Chambaaa chakwera ameneyu
@JoyceMoyo-y6w
@JoyceMoyo-y6w 3 ай бұрын
God bless you 🙏🙏
@ActiveChembe
@ActiveChembe 2 ай бұрын
Anthu for aja ndiAmene anapanga kokupha avice prsdnt
@ShelingtonMtemula
@ShelingtonMtemula 3 ай бұрын
Ulemu wanu munthu wankulu apa ofunika audio muilengeze mu English kuti imveke ziko lonse lapansi
@ernesthkaunda7902
@ernesthkaunda7902 3 ай бұрын
This sounds fake to me. How could the crew members not notice that before starting off from Lilongwe. Tulutsani bodza lanulo .......kodi ngozi yayambira ku Malawi?
@DOLOTHYMAKINA
@DOLOTHYMAKINA 3 ай бұрын
Mulungu awulula ndithu
@DOLOTHYMAKINA
@DOLOTHYMAKINA 3 ай бұрын
Ukulesa chani umuuziletu chakwera wakoyo zonse zimene wachita ziululika
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 3 ай бұрын
Kodi nanga ndichifukwa chani munalibe nduna iliyose ya MCP akanakhala m, bale wanu amene waphedwa sibwezi mukuyakhula chochi mulungu akulangeni nose
@spargomw
@spargomw 3 ай бұрын
Ambuye agugude pa chifuwa chako ndikusawelengera mwano wayankhulawu, coz Mulungu atati awelengere potha masiku 30 ukhoza kuona zoooopsa kwambiri pamoyo wako
@RusselleStanley
@RusselleStanley 3 ай бұрын
​@@spargomwosatchula dzina la mulungu pa chabe ungatenge tsoka
@SteinAustineSakala
@SteinAustineSakala 3 ай бұрын
Bwanji simunaulure Ngozi isanachitike . Tipinduranji panopa a Vice president athu Ali Mmanda . Mkanaulura Ali Moyo bolani
@RusselleStanley
@RusselleStanley 3 ай бұрын
Propaganda otherwise u do nothing
@JohnChikoti-e6f
@JohnChikoti-e6f 2 күн бұрын
Chabwino zavekadi tingoti tionana 2025 chilungamo chizaziwika
@ChimmsRichardOrden
@ChimmsRichardOrden 3 ай бұрын
Mulungu akutetezeni Big man
@mayamikozimanyeta8633
@mayamikozimanyeta8633 3 ай бұрын
Ooowooo ngat mukufufuzabe nde mukutiwuzilanji maumboni okwanilira musanapeze why phuma nanga
@RejoiceKamanga
@RejoiceKamanga 3 ай бұрын
❤❤❤❤ sangakuchoseni ntchito bwana 😢😢😢. Tilinanu pamozi
@ChikondiPhilimon
@ChikondiPhilimon 3 күн бұрын
Mulungu Ali painu ndi kwa onse omenyera ufulu wa chilungamo
@murraykaliwo6638
@murraykaliwo6638 3 ай бұрын
Nanga bwanji samauulula zisanachitike
@bostonbanda4774
@bostonbanda4774 3 ай бұрын
Zabodza izi unatani kunena zisanachitike
@BenPhillip-fw8hi
@BenPhillip-fw8hi 3 ай бұрын
Eti eti
@Hellenistic109
@Hellenistic109 3 ай бұрын
Its Bwana Mumandinyasa ndisakubiseni 😂😂 for me
@mariajonasse9792
@mariajonasse9792 2 ай бұрын
😂😂😂
@ClementKamtedza
@ClementKamtedza Ай бұрын
God bless you bwana
@JudithAbinaele
@JudithAbinaele 2 ай бұрын
U guys u are really taking us for granted..busy making up stories..bring the videos u iditots. Ma phone ama camera amapezeka even kwathu ku Tukombo ..osajambulako bwa? Akwa minyu biiii
@barnettbmphanda108
@barnettbmphanda108 Ай бұрын
Ndiye kunkhalangoko anachita kuyinyamula kukaponyako ndipo video imeneyo umajambula ndiwe? In your statement mwati ndege sinagwe tafotokozani bwino timve? Iweyo unali kuti?
@TWINKIDDMARSECOAL
@TWINKIDDMARSECOAL 3 ай бұрын
Nde mwati mundege kuchotsamo mafuta??? APA mwanamatu and zambri seems bodza coz even galimoto imaonetsa level yamafuta so u mean ma pilot sankaona zamafuta??? Nde analolela kuyendetsa kuti afe???? And video mukuti yochoka ku airport mpaka kumene inagwa munkajambula munadziwa kuti zitere??? Bodza ili
@milanzichikondi7330
@milanzichikondi7330 3 ай бұрын
Black board??, Benzene (this is just a small component in gasoline) how did they suck it? , Every pilot before flight makes a check list. We need real facts gents. We are with you but we need facts.
@koncyk7138
@koncyk7138 3 ай бұрын
Olo ngati driver amapanga check ma tyres, engine coolant, engine oil. Galimoto likalila amaonso all warning ⚠️ lights pa dash board and levels of fuel. Should we say gage ya fuel mu ndege inali yokufa. If at all they use a dip stick, sanapange zimenezo? Facts are really supposed to be laid osati trying to trigger unnecessary riots.
@petrochimutu7037
@petrochimutu7037 3 ай бұрын
wekha ukunena kut ndege sinagwe wekhaso ukuti anachosamo mafuta kut ikayenda ingogwa,, kmaso barracks mwanenayo kulibe dzina lamsilikali mwanenaro
@Gwithcapital
@Gwithcapital 3 ай бұрын
Make a video let us see you ,you think we stupid?panga video anthu akuone anthu olimbikisa mikangano inu
@joshuankata6967
@joshuankata6967 3 ай бұрын
Palibepo chomveka chilichonse chimene wanenapo apa galu iwe
@CliffordMwalwanda-r8p
@CliffordMwalwanda-r8p Ай бұрын
Chilima anali tsogoleri wa mahala ngati computer
@VincentChipwere
@VincentChipwere 3 ай бұрын
Akanakhalapo asilikali onga inu 10 zinthu zikanatha kulongosoka Lazaro ndi wakuphadi
@AustinchikondiMpiphira
@AustinchikondiMpiphira Ай бұрын
Muzeni galu ameyo aonanga zikoli lamake aamandinyasa kwambiri galu😂😂😂😂😂
@JosephySaid-n6m
@JosephySaid-n6m 2 ай бұрын
Ngat ukhava kukuwa iweyo unatan kukawaombola iweyoso unaphanawo
@HopesonHarry
@HopesonHarry Күн бұрын
R I P chilima
Nigeria Billionaire Dangote on Fuel Subsidy, Oil Prices, Football
26:00
Bloomberg Television
Рет қаралды 302 М.
GIANT Gummy Worm Pt.6 #shorts
00:46
Mr DegrEE
Рет қаралды 91 МЛН
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Piksy TV
Рет қаралды 217 М.
🔴LIVE: Benjamin Netanyahu gives speech at UN General Assembly
36:32
AFP News Agency
Рет қаралды 29 М.
Dr Hlophe blocked from JSC processes
8:51
SABC News
Рет қаралды 15 М.
Tikuferanji 25 May 2024
26:23
Edson Gunsalu
Рет қаралды 59 М.
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 129 М.