Zifukwa Zimene Anthu agendera Mdipiti wa A President ndi Izi

  Рет қаралды 9,231

Malawian Cameras

Malawian Cameras

Күн бұрын

Пікірлер: 50
@CharlesNdalama-v5b
@CharlesNdalama-v5b Ай бұрын
very good job guys
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc Ай бұрын
Bro, Anthu muno mmalawi tidzingomenyetsana,mitu,koma solution osaipedza,titha,kusankha sogoleli wabwino komaso wa, zelu.koma,akangofika ndi kulumbililitsidwa, zelu zonse zimatha.uyu,titha,kumuchotsa,tiikepo,,a dpp a president olo,a UTM,a president.koma,ngati sachosa,nyasi zomwe za wazungulula, mmalawi ma bvuto sangathe.bvuto,ndi omwe awadzungulilawo.
@HarrentBanda
@HarrentBanda Ай бұрын
Iweso penapake uzilongosola zomweka kodi ngati anthu akukukonda angakugende,,, Wausiru naweso
@PindamalataLajabuchitutu
@PindamalataLajabuchitutu Ай бұрын
Winaaliyese ili ndimunthu amene amakonda sopano a mcp analakwisa pochosa salu za azawo anthu amene amagenda sanalakwise chifukwa amateteza zindu zawo
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Koma achita bwino kuwahenda because anthu ena okonda chipani cha mcp ku lilongwe amaziyesa ngati ziko lose ndilaiwo okha and mcp ngati ndichipani chokhacho tili nacho mumalawi muno. Tikuwadikira kunuso kumupoto matama wose anachimwendo tisisa kampeni ayamba. Mcp si Mulungu kuti tiziwawombera manja. Zipolowe zikhalapo 2025 because police ndi asilikali ena opepera akusiya chilungamo.
@YamieManda
@YamieManda Ай бұрын
Inu mukunapo chiyani pameepa mukhaalila yomweyo yamabodzayo
@WinerdShadreck
@WinerdShadreck Ай бұрын
It's just beginning
@hamiltonndau
@hamiltonndau Ай бұрын
Palibe nzeru apa
@UmaliGunga
@UmaliGunga Ай бұрын
Kumbukirani anthu akudowa pa chankhungu adagenda mudipiti wa peter muthalika sikuyamba kumeneko 😂😂😂😂
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx Ай бұрын
Ndiye ngat athu akumukonda bwanji agenda iweo ukudya za mcp athu asiya kuvela zakozi ndithu mcp ilibe mwai ulionse
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe Ай бұрын
Nanga kunja kwanjala.bwanji chikangawayo osapeleka matumba a chimanga ndi nyemba zake ndi mcere Ndi mafuta ophikira ? Mmene amapsngira kamuzu Banda.? Koma mafuta a galimoto anthu amadya .? Amuchita bwino amugenda.Waidzowa lower states .siifuna masewera ..
@Paul-q2p
@Paul-q2p Ай бұрын
Wadya chibazi iwe munthu omukonda tsagendendwa
@HaleemaAllie
@HaleemaAllie Ай бұрын
Achita bwino pamenepo pang, Ono bola akanachosa diso
@KondwaniGulonyonyo
@KondwaniGulonyonyo Ай бұрын
Ku lower states kulibe mcp wina asaname zonse zomwe anthu amalankhula kaya mafumu , makhansala ndi ena ambili amangomunamiza president pongofuna kumubela kunena zoona anthu amene akuyenda ndi apresident athu samawakonda penpho chonde chonde mamulumuzana athu mukonden nsogoleli wathu pomuuza chilungamo
@EnerstManess
@EnerstManess Ай бұрын
Simunati muziona
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 Ай бұрын
Ufumu wa mcp wagawidwa kale
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo Ай бұрын
Anthu akudana naye kumene koma musaiwale panopa achakwela amayenda ndi anyamata awo ambili anthu akumaiopa kupanda pamenepo ndibwezi mutavakuti ayiotcha
@akilisaidi
@akilisaidi Ай бұрын
Meaning that there is a lack of discipline from the supporters from directors .these scenes are continuously damaging the already damaged name
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Ай бұрын
Iwe nawe tadzi lankhula zomveka , chikangawa sakufunidwa
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe Ай бұрын
Waidziwa lower states ..chikangawa ndipo adzaona zoopsya tsiku lazisankho .ndi ànthu a ku malawi pmwe iye akutizunzafe
@jamessheki4293
@jamessheki4293 Ай бұрын
Kodi ameneyu analikut bambo ake kukhala president akuona ngati Malawi khola la bambo ake
@UneMe-k8v
@UneMe-k8v Ай бұрын
Iwe ndi kape kwambili
@ClifordBwwanali
@ClifordBwwanali Ай бұрын
Pa ma oudio pali munthu akuyankhula koma iwe zoona ungaphe zako.. sono iwe ukufuna kuyankhula chani..ndili kuno kuno s africa ndaziwa chachitika kuposa iwe tangosiya kuyankhula pamenepo ndiwe chitsiru
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t Ай бұрын
Awachita bwno ku ntchewu kunoso tizamupasaso kwinini ameneyo akutinyasa kubisa, malipoti kmas kuba kunama ndi zina zambili ndiposo akazangoti waluza azachoke mziko muno chifuwa uformer president sazawumva kukoma anthu azamuyendela mwa pa dela ameneyo 😂😂😂😂😂
@HusseinBinali-z1s
@HusseinBinali-z1s Ай бұрын
Anchita bwino
@FrancisStima-sc7zs
@FrancisStima-sc7zs Ай бұрын
Nanga akabwela kwathu Kuno ishi azaonatu tibwezela paja kwao amatumatu nyau
@SallahSallah-i3i
@SallahSallah-i3i Ай бұрын
Amamkonda? Agendedwa bwanji munthu oti amamkonda
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
Zifukwazo sizikukwanila kapena sizikukhuzana ndikugendedwa kwa chikangawa , Anthu atopa ndi umbava ndi umbanda , kupha ndikunama ,
@PatrickLigomeka-c8b
@PatrickLigomeka-c8b Ай бұрын
Ziko ndiyandu ngati sakwayendesa bwino andu awo amene anayika papando akundeni basi kkkkk
@Aubreysekeyah
@Aubreysekeyah Ай бұрын
😂😂😂😂
@sarahchikwekwe1813
@sarahchikwekwe1813 Ай бұрын
Eish school ija koma ndiyofunika 2 mins ina yake😂😂😂 a patrick ligomeka 😢😢😢
@MuhammadMalunda-ex4mj
@MuhammadMalunda-ex4mj Ай бұрын
Brother try to tell people the truth plz! If you want money just ask whom you supporting my brother. Ozona zake ndi zakuti anthu sàkumufuna
@samdiverson9733
@samdiverson9733 Ай бұрын
Palibe zifukwa zolakwanira apapa boss nkhani ndi yoti anthu Sali osangalala ndi mmene zinthu zilili
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje Ай бұрын
Ndiwaboza iwe
@MalawianCamera
@MalawianCamera Ай бұрын
Muzinvesetsa word by word Ndati Gerald Chawez Kampanikiza
@AndrewjemesJemes
@AndrewjemesJemes Ай бұрын
Uyenda yenda apule anthu
@victorauwana7258
@victorauwana7258 Ай бұрын
Mcp yamenya munthu mmozi,,, then kwagendedwa chakwela? Ndiye mkumati chakwela amakondedwa kumsanje?😂😂😂😂😂 Mwapengatu achawezi
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi Ай бұрын
Ufulu ukachuluka mudziko zitsatila zimakhala zimenezi.
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Khansara ameneyu anachita bwino.
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Stupid president Mr Chikangawa Fans yatopa nawo and mumuuze abwere kuno ku Ntcheu tamukozekera ifeso zachibwana palibe..
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Anthu samufuna basi inu musamuyikile kumbuyo
@EvanceRazaki
@EvanceRazaki Ай бұрын
Palibe zimenez president ameney sakufuna.musamuyike kumbuyo ameney ndigalu kwabas
@TiongeChirwa-kz1ub
@TiongeChirwa-kz1ub Ай бұрын
Ndiwe wa MCP iwee et useless
@Chikwawa
@Chikwawa Ай бұрын
Zopepera zomwe ukunenazo.
@josephmsyali
@josephmsyali Ай бұрын
Zayambika
@KumbukaniKafatia-cd2hq
@KumbukaniKafatia-cd2hq Ай бұрын
Okay guys😅
@ApsChap
@ApsChap Ай бұрын
Councillor Molotali
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Ай бұрын
It doesnt make any sense bro
@MalawianCamera
@MalawianCamera Ай бұрын
😂😂😂😂
@PatumaMwasama
@PatumaMwasama Ай бұрын
Maganizo anga ndi achita bwino ndipo awachepesa.
Assista na íntegra o Tema Em Debate 07/11/2024
MIRAMAR
Рет қаралды 234
Real Man relocate to Remote Controlled Car 👨🏻➡️🚙🕹️ #builderc
00:24
Não sabe esconder Comida
00:20
DUDU e CAROL
Рет қаралды 67 МЛН
Hosiah Chipanga Padare Rachief Mutasa
19:12
TICHKACH MTV
Рет қаралды 69 М.
mota yotaura paBudiriro
15:36
Drewmas Media
Рет қаралды 929 М.
ZOMWE A KALIATI NDI ANJAWALA AYANKHULA 6 November 2024
31:40
MUIMBI HOSIAH CHIPANGA MUDARE RAMAMBO MUTASA VS LEON MATESVA  KARANGANDA TV KUTORWA KWEMUNDA
18:01
ED Warns Chiwenga: Pachigaro Chemukuru hapamihwe mihwe unochohwa
11:02
Citizens Voice Network
Рет қаралды 159 М.