ZIKUULULIKA KU CONVENTION YA MCP KU LILONGWE - BRIAN BANDA NDI CATHY MAULIDI🙌🙌🔥🔥

  Рет қаралды 39,008

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 57
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 2 ай бұрын
Zoti atemani simukuziwa kd. Kulibe tendele kumeneko aphana amenewo. Ngati akulanda ma card pali bwino
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 2 ай бұрын
Eti eti wina nkono uli lende aukhapa ena akulira panja pa hotel akuti card lawo laperekedwa kwa non delegate kkkkk mtendere uli pati?
@LaitoneJefitala
@LaitoneJefitala 2 ай бұрын
Bwanji Kodi anthu abodza
@ayamijackson1443
@ayamijackson1443 2 ай бұрын
Magaz magaz party chikangawa club
@vincentmpighu1080
@vincentmpighu1080 2 ай бұрын
Umangoziwilatu
@modestamhango7737
@modestamhango7737 2 ай бұрын
Cathy Maulidi umatha kwambiri.
@Tawina0101
@Tawina0101 2 ай бұрын
Second Comment 🔥
@VictorChelewani-uy8pg
@VictorChelewani-uy8pg 2 ай бұрын
Respect to cathy maulidi amatha iweyo
@modestamhango7737
@modestamhango7737 2 ай бұрын
Zoona
@yassinn5634
@yassinn5634 2 ай бұрын
A Brian Banda angosaka ma negative okha okha paja ndi mdani wa MCP analowa ku DPP nanga pajatu anathamangitsidwa ku STATE HOUSE
@WillardMasika-yf3dw
@WillardMasika-yf3dw 2 ай бұрын
Nde zopereka ma card kwa anthu ena omwe asali ma delighte Brian Banda zikumukhuza bwa😅
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 ай бұрын
Chikangawa I always saying mcp ndi gulu la zigawenga mwawona akukhapana wokha wokha
@TroubleMuthala
@TroubleMuthala 2 ай бұрын
Mr chunga u r # 1, good speak mwaiimilila 🙏
@SmithYvonne-s9z
@SmithYvonne-s9z 2 ай бұрын
Ineyo ada awawa this is my first time kumuva akuyankhura mwalutha
@MercyMithie
@MercyMithie 2 ай бұрын
First comment
@leoleonard2103
@leoleonard2103 2 ай бұрын
Mcp singawineso this time mupakila your door is open to go with peace 😊
@JollyPaul-m1y
@JollyPaul-m1y 2 ай бұрын
Live from south africa
@PaulBexter-c4g
@PaulBexter-c4g 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 zilikotu ziliko
@MoosaSame
@MoosaSame 2 ай бұрын
Tionana 2025 mbolo zamanu mu beletu ndrama za misokho yanthu
@ChikondiKammaluwa
@ChikondiKammaluwa 2 ай бұрын
Chinyengo chokhachokha makadi apatsilanji anthu osayenela?
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 2 ай бұрын
Chikangawa imeneyo 😂😂😂😂😂chipani cha magazi
@felixmakwinja-o9f
@felixmakwinja-o9f 2 ай бұрын
Wayana Mchunga, kuyankhula kwabwino
@josephgabriel5941
@josephgabriel5941 2 ай бұрын
All ambassadors are MCP members
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 2 ай бұрын
Is everyone working in Embassies belongs to MCP? Why being called to attend MCP convention yet others belong to various political parties? Eish ndalama ndi satana kuteroku gulu la a Callista lasintha thabwa kkkkk koma ziliko
@johnkambala692
@johnkambala692 2 ай бұрын
Palibe watemedwa. Angodzipaka paint ngati magazi
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 2 ай бұрын
Chikangawa party chipani cha nkhanza
@mathewssiliya574
@mathewssiliya574 2 ай бұрын
Bava zamba mwokwana zipite
@TensonChawinga
@TensonChawinga 2 ай бұрын
Zonse tingozisiya mu manja mwa mulungu
@PatrickRodgersKalumo
@PatrickRodgersKalumo 2 ай бұрын
Maudindo amene akukanganiranao ndinso kuhonga anthu ndindalama ,,,,,,nzoti akudziwa chomwe chinsinsi chilikuchipani kuti mavoti aberedwa kale awina kale ,,,,akuziwa chomwe chikuchitika
@ganizanimanyamba
@ganizanimanyamba 2 ай бұрын
Kodi lipoti zikutibwanji thawitu litulukaliti kuchikangawa tikudikilatu????
@AishaOsman-m8x
@AishaOsman-m8x 2 ай бұрын
Mumpaseko moni zikhaa
@SandfordBanda-gk2dp
@SandfordBanda-gk2dp 2 ай бұрын
Brian wayipa lero Koma dzulo anali dolo
@JumaGadaff
@JumaGadaff 2 ай бұрын
Mulungu chotsani onse amwano
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 2 ай бұрын
Boma ili tizalichosa by fire by force
@HamzaMasuwa
@HamzaMasuwa 2 ай бұрын
Azolowela Kuba mpaka Kuba ndalana za tambala night kkkk chikangawa
@leoleonard2103
@leoleonard2103 2 ай бұрын
Mcp yayamba kubela 😂
@JasonMailos
@JasonMailos 2 ай бұрын
Koma akuziba ndalama zambili bungwe la auntie corruption Bureau Lili chetee! Mene ndunazimenezi zikubela
@dilmayankam4052
@dilmayankam4052 2 ай бұрын
Naweso unaiwala bwanji camera 😅
@gradsonmayira9336
@gradsonmayira9336 2 ай бұрын
Brian adzapandidwa ndithu 😂😂😂😂😂😂
@ManuelMalunga-j3l
@ManuelMalunga-j3l 2 ай бұрын
Following up
@FebbyPhiri-n7j
@FebbyPhiri-n7j 2 ай бұрын
Second
@LucyKumwenda-ti5yc
@LucyKumwenda-ti5yc 2 ай бұрын
Mtendere uli pati anthu akhapidwawo
@ApostleDJoaquim
@ApostleDJoaquim 2 ай бұрын
Zooona?
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 2 ай бұрын
Divided kingdom 😂
@SmithYvonne-s9z
@SmithYvonne-s9z 2 ай бұрын
Wayana mwayankhurako zanzeru lero
@EmmanuelMoyo-hy5ni
@EmmanuelMoyo-hy5ni 2 ай бұрын
Chikangawa party mavuto osatha
@pauljosephmakaula6835
@pauljosephmakaula6835 2 ай бұрын
Atulutse ma national ID and tally up
@atusayemwandelile8307
@atusayemwandelile8307 2 ай бұрын
Chikangawa party to much noise
@HendrickBanda
@HendrickBanda 2 ай бұрын
Following
@johnkambala692
@johnkambala692 2 ай бұрын
O Chunga zinazi mwaonjeza.
@CostasChirwa
@CostasChirwa 2 ай бұрын
Km zithu zake
@KimChisola-gm7yw
@KimChisola-gm7yw 2 ай бұрын
Zoona wayana pazikhala kusiyanisa za chipani ndi za boma kodi a ku embassy abwara pa tikiti ya boma kapena chipani?fufuzani tiziwe
@AustinBornface
@AustinBornface 2 ай бұрын
Tidzaonana
@jomochirwa
@jomochirwa 2 ай бұрын
Iyi ndi convetion ya amawo,wosati za dpp ndi utm izo zawana a pa facebook .
@kondwanimperiwa
@kondwanimperiwa 2 ай бұрын
Muphana
@robenallie6985
@robenallie6985 2 ай бұрын
Ku mcp komweko
@CharlesChimphamba
@CharlesChimphamba 2 ай бұрын
Following
NZE SIFERA NGAKO HAJJI MUTEBI NJAGALA KIMU JUSTICE KU MWANA WANGE
52:58
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 275 #shorts
00:29
Osman Kalyoncu
Рет қаралды 3,7 МЛН
My Daughter's Dumplings Are Filled With Coins #funny #cute #comedy
00:18
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 36 МЛН
Ouch.. 🤕⚽️
00:25
Celine Dept
Рет қаралды 22 МЛН
Bobi Wine ne Mickie Wine bayingidewo. Olumbe Lwona Lukyankalanye
14:19
Mukunja atasera
Рет қаралды 61 М.
Grace Chinga - Udzaimba Nyimbo.(360p)
6:53
Steve Spesho
Рет қаралды 171 М.
EXCLUSIF - Moments de vérité - Gbagbo dit tout
1:06:47
Alain Foka Officiel
Рет қаралды 1,4 МЛН