ZILI KUSERIKU/ KWAGWANJI KU MALAWI

  Рет қаралды 135,118

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 203
@cadohjabu5565
@cadohjabu5565 8 ай бұрын
Achedwa nayo nkhani Mr president
@StevenLeoJana
@StevenLeoJana 8 ай бұрын
Not a Malawi but few chosen people.
@AustenBestonChimombo
@AustenBestonChimombo 8 ай бұрын
Atolankhaniwa akuthandiza anthu komaso achakwerawo
@XasankaalibeeyNuur
@XasankaalibeeyNuur 8 ай бұрын
Zimene mukamba inuyozo simukuziwa mene president chakwera akuzuzira anthu malawi muli bzzy kukamba za vise president kambani za anthu omwe akuvutika mutero chifukwa zanu zili pabwino chani 😢😢😢
@Nulunulu634
@Nulunulu634 8 ай бұрын
Ndilowese ndikakutafune
@collingsmkandawire4688
@collingsmkandawire4688 8 ай бұрын
Mr president chakwera hell is waiting for you, mwatikwana
@AbdulEliaskalonga
@AbdulEliaskalonga 8 ай бұрын
Azimayiwosoamamujedatu
@andsenJeke
@andsenJeke 8 ай бұрын
Ife timadziwa kuti awa achilimawa ndi makwelero awa ife ana adad tili phee!!!!
@collingsmkandawire4688
@collingsmkandawire4688 8 ай бұрын
And on his last day, hell is waiting for him
@RaffiqRaphael
@RaffiqRaphael 8 ай бұрын
Chakwela umuthu ulibe
@patriciap.bandah3385
@patriciap.bandah3385 8 ай бұрын
APM my Vote
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 8 ай бұрын
Olo lero utamwalira lero i think nkovuta kukukumbukila , mavuto okhaokha bsi, munthu no 100% koma iweyo chakwela wa nyanya kuipa ntima and okuyamikila iweyo kuyambila pano azifufuze yekha, ngati samugaila cash yaulere . Koma na amene amadya thukuta lake aah akhoza kugwilizana nane kuti ulamuliro uyu wa chakwela akumva nayo ululu, koma ngati umadya cash ya ntukula pa khomo or za kovid ah mpake kumuyamikila nkulu ameneyu. Koma kwa okhesa thukuta aah chakwela ndi empty brain 🧠 sure wanzelu na pamachitidwe ankulu ameneyu sangaonese mano believe me.
@jamessingini-fh1bz
@jamessingini-fh1bz 8 ай бұрын
Za bodza izi kkkk Chilima sangapusisikenso
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 8 ай бұрын
Chilichose kuonela pa pepa president wantunduwanji uyu go tuck ur self mr president I don't like u anymore.
@JamesjKanjuchi
@JamesjKanjuchi 8 ай бұрын
Dzilibhooo kubwela kumeneko
@MoosaSame
@MoosaSame 8 ай бұрын
Mr president are you reading poime
@PizoZopi-w2g
@PizoZopi-w2g 8 ай бұрын
Stetemantete mukulakhulayo yemwe walembayo akupusisani akulu
@madalitsomakawa9708
@madalitsomakawa9708 8 ай бұрын
Background music it's so annoying too loud very disturbing. Please change if you take time reading comments
@KapepuzaFernandos-bd6nv
@KapepuzaFernandos-bd6nv 8 ай бұрын
Mukupangaso campaign wachiwili abrian
@KapepuzaFernandos-bd6nv
@KapepuzaFernandos-bd6nv 8 ай бұрын
Wamulembela zoyankhulazakezo ndani ngati may onse wayankhulawo Ali amutima make.poti akuwelenga zonsexi
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 8 ай бұрын
Analodza malawi anatilakwira
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 8 ай бұрын
Malawi kozeka ndikulamulidwa ndi Afana oganiza bhobho heavy mulandu ukuthetsedwa kupanda kuthetsedwa chitedze chiyabwa wamkulu tsogolo kabwino lowala layandikila
@yohanedaudi1740
@yohanedaudi1740 8 ай бұрын
Zoyankhula idzi zikakhale Za mtsogoleri wadziko????
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 8 ай бұрын
Simupanga zoyambana ndi anthu koma kuba
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 8 ай бұрын
Malawi anadzukatu akulu musapusise anthu akulu inu
@hamischikalimba6626
@hamischikalimba6626 8 ай бұрын
Apapa kulibwino asiyane chilima sakupatsidwa ulemu wake ngati vice president. Ma governer kumachita kukhala ndi mphavu kuposa vp wadziko this is very sad. Utm contributed alot during 2020 presidential election and majority who voted were because of the confidence they had in Chilima. Today chilima can not even become a minister, his contribution has gone unnoticed, may God help Malawi. Good people politics pa Malawi ayi ndithu
@JosephElliam
@JosephElliam 8 ай бұрын
Open ur eyes
@FelistasNkasalaMakumbo
@FelistasNkasalaMakumbo 8 ай бұрын
Mawu achiphimba maso izi mukananena four years ago
@petrooverton6643
@petrooverton6643 8 ай бұрын
ine ndikuona kuti CHAKWELA akudikirila mlandu uthe kae and akuziwa kuti CHILIMA awina mlandu adakakhala kuti CHILIMA akugwilabe tnchito yake kwaio zikanakhala ngati zosenzo akupangila limozi, nde dikilani kae mlandu uthe CHAKWELA ampasanso CHILIMA maudindo ake then 2025 CHILIMA aimila u president nonga mwa phangano enao akukuwao ku mamitingi onse omwe CHAKWELA ndi CHILIMA kumene anka kumana kunalibe nde asieni azi kuwa ngati galu wa chiwewe ( sungani mau anga ) chete wa A CHILIMA sikupusa ai ndifana oganiza booh heve ameyo
@EdgarKaronga
@EdgarKaronga 8 ай бұрын
Mr president let them talk when God has open the door for you no one can shut❤
@collingsmkandawire4688
@collingsmkandawire4688 8 ай бұрын
Which god???
@jamesmsonkho4830
@jamesmsonkho4830 8 ай бұрын
He don't know what is he saying
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 8 ай бұрын
Achitsilu inu
@EllenMapata-x9v
@EllenMapata-x9v 8 ай бұрын
A chakwera angovomeleza zomwe anagwirizana ndi chilima basi nkhani yatha 5 yrs achakwera yawo yatha turn ya 5 yrs yinayi alamulile chilima chifukwa pangano yinadulitsa mutu wa yohane
@AllanBamusi-jw5fy
@AllanBamusi-jw5fy 8 ай бұрын
Tiyezeke kaye iyi sidandipeze ili munjira
@InnocentMalimusi
@InnocentMalimusi 8 ай бұрын
Braaa achedwa akafuna chilima 2025 pamwamba chakwera vc Apo ndiye azasunga mawu awo Apo biiiiiii plastic smile😂😂😂
@robayami-xz2wg
@robayami-xz2wg 8 ай бұрын
Brian Banda sanganene zabwino za Dr Chakwera and MCP cause he is a UTM member.
@RhodwellMpinganjira
@RhodwellMpinganjira 8 ай бұрын
Bodza iri, zaudani zinadziwika pama speech achina mkaka ndi Gotan hara
@ellahmvula
@ellahmvula 7 ай бұрын
Bodza😂😂😂😂😂
@rabsonsikelo-pu1qu
@rabsonsikelo-pu1qu 8 ай бұрын
Zoona a president
@augustMag
@augustMag 8 ай бұрын
Mmmmmhu a Chakwera mwaona kuti nthawi ya chisankho yayandikira mwayamba kuwanyengerera a vice Anu a Chilima kuti akuwoloseninso? Koma abale dziko ndilozungulira 🙌🙌🤣🤣
@fraserbereck2269
@fraserbereck2269 8 ай бұрын
Chimenechi ndie chimayamikira anzawo?
@lupakishomalangaelix6606
@lupakishomalangaelix6606 8 ай бұрын
Kkkk
@AllieKaisi-je6rm
@AllieKaisi-je6rm 8 ай бұрын
😂😂😂😂 natseka imwe ngati akwayambanisa ena ngati sakufuna kuyambana zomwe munagwirizana zichitike inuyo chakwela mukhale vp nkhani yatha. Ngati mungawinenso chifukwa nonsenu atsogoleli wanu wankha
@AllieKaisi-je6rm
@AllieKaisi-je6rm 8 ай бұрын
Utsogoleli wanu nonse wanukha nanjinso chilima u vp ma term awiri akwana palibe chaoneka ngati chaoneka mwalemera nokha
@MadalisoKaujole
@MadalisoKaujole 8 ай бұрын
Amp my vote
@HappyCookingApron-cr3tu
@HappyCookingApron-cr3tu 8 ай бұрын
Koma akunama kod
@thomasyohane987
@thomasyohane987 8 ай бұрын
Apm my vote
@Regrand-malawiLilongwe25
@Regrand-malawiLilongwe25 8 ай бұрын
Quote from Lucious Banda * nthawi ndikachisilu* mr president indeed he is on edges of his Seat!
@prettytambala5687
@prettytambala5687 8 ай бұрын
Asowa choyankhula
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 8 ай бұрын
Mbuli yophuzila ai zikomo
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 8 ай бұрын
Na m'busa uyu ai sizau-Mulungu izi , satana wen wen uyu
@Johnfrank-gi5uc
@Johnfrank-gi5uc 8 ай бұрын
aMalawi anakusakhani chifukwa mumati musisa mtengo wa fertilizer komanso 1million job do it anthu akukondan, palibe angakuyambaniseni chifukwa mgwirizano ndi wa anthu awiri
@EnockSikoti
@EnockSikoti 8 ай бұрын
Next time put up your opinion on the matter osangotumiza video clip yonse
@BrightMbengo-h1v
@BrightMbengo-h1v 8 ай бұрын
Chilima wafinyidwa ndipo asapusitsike ndi zomwe akulankhulazi
@NothandoNyathi-r6h
@NothandoNyathi-r6h 8 ай бұрын
Mbudzi yachabe chabee
@MarcyMakhala
@MarcyMakhala 8 ай бұрын
Amkaka ndi amene salibwino
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 8 ай бұрын
Mukuithatu guys auzeni basi Chilimanso saangaimvetu yoti asala
@leonardzchavula3139
@leonardzchavula3139 8 ай бұрын
Very good advice ...however an issue on the removal of delegated/ministrial position of V/P....KHEZI MSUKWA was delayed to be removed from being a minister ....Malawians cried out why the delay...... your comment please
@Edwardtolo
@Edwardtolo 3 ай бұрын
Lero mpeni wanu mwawutulusa ndipo mwacheka nawo azanu eeeee ayi 😢😢😢
@allenahkanziza2706
@allenahkanziza2706 3 ай бұрын
Ndipo inu eeeee
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 3 ай бұрын
I concur with you HE.Keep it up and don't renege.
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 8 ай бұрын
Achakwela tikuwonani kt chaka chino asogola chilima panja pali 5yrs wina inayoso wina😂😂. Pomwe tiziwe kt inu ndi busa
@ErnestMaloya-dt2sl
@ErnestMaloya-dt2sl 8 ай бұрын
Zadala izi akufuna akamulimitse kachikena akawine chaka chamawa coz awona kt nthaw yatha
@CostantinoChirwa-t3r
@CostantinoChirwa-t3r 7 ай бұрын
😂🎉
@ShahidMia-j6j
@ShahidMia-j6j 7 ай бұрын
Mabodza amenewo anaononga kale ekha ubale wake ndichirima usatipusitse chakwera 2025 kulibe kuwina aise
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 8 ай бұрын
I can see kut mfundo zawo sizochokera pans pa mtima koma achita kuuzilidwa kut ayankhule. Cos zikanakhala kut nzaiwo wokha, sibwenzi lemba lililonse akuchita kuwelenga. Kapena mkulanda mfundo kokhakokhako? Palibe munthu uyu analankhula zondigwila mtima.
@georgednthala-wh3pf
@georgednthala-wh3pf 8 ай бұрын
Misecheyo sikuti inachokela mbiri imodzi ayi, mbali ya president komaso mbari ya VP konseku kuli anthu amene akufuna kuti anthu awa aziyambana
@RichardBondwe
@RichardBondwe 8 ай бұрын
Yawa nawo akadadikira kaye?? Misalatu iwe Brian Banda ndi UTM yako malamulo akuyenera kugwira ntchito for there is no smoke without fire.
@ConfusedAtv-bs4gc
@ConfusedAtv-bs4gc 8 ай бұрын
Chakwela zotizungulila Ife ayi mkaka uja Amati chani ndi brain Banda Amati kalata yangwilizano sinafike npaka pano Koma mwina ili munjila zaka 4 China tamufunsani chakwela Kuti 2025 iye ayimilanso kapena ayimile ndichilima zimene ayankha ndizimene ndizimene zipase mayankho azonsezi APA osamachedwa ndizokamba kamba ayi takamufunsani basi
@wanangwamwafulirwa8839
@wanangwamwafulirwa8839 8 ай бұрын
Ngat iweee mwini unakoza kut zitele lero chavuta ndichani.....
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 7 ай бұрын
Za ziiiiiiii! Boma lalephera kale apa, palibe kumene chimene mukuchita.
@StewartGoma
@StewartGoma 3 ай бұрын
By this time u showed to colours u killed ur voice president Chilima b
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 3 ай бұрын
Tiuzeni what happened with chilima in chikangawa is what we want nothing else.
@leveltrapper4322
@leveltrapper4322 8 ай бұрын
Ayamba kumufuna tsopano tima fake speech tochakwera utu. Akuziwa kt ukuku kukubweraku ziwavutaaa
@GiftWysonKatemangu
@GiftWysonKatemangu 8 ай бұрын
Chakwera kuyankhula ngat wabwino kufuna kunyengelera chilima kut akuwoloseni kachikena kulokuno muzimunyosazo
@Biath-m4b
@Biath-m4b 22 күн бұрын
Koma unapha nzakoyo unamusungila mpeni APM my vote
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc 7 ай бұрын
Zuchitika zopusa mziko muno pomwe iwe president ndiye uzikamba manyi ako wooo asiile amzako ulibe msogolo muuzeso mzako chilima mapazi anu nonse inuso opepela muli apa
@ShaibuMwawa
@ShaibuMwawa 2 ай бұрын
koma zosakhara bwino zomwe zikuchitka Ku malawi 😢😢😢
@AdamNakonya
@AdamNakonya 7 ай бұрын
Koma chakwela mulibe iliyose ndikape samathaso kuyakhula
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 8 ай бұрын
Sangalorerane olo zitavuta motani...ali yense wasungira mpeni nzake kumphasa
@owenbrightkamwaza2429
@owenbrightkamwaza2429 7 ай бұрын
nanga si mipeniyo mwasunga ndinu
@DonaldPonda-p2q
@DonaldPonda-p2q 8 ай бұрын
Iweyo palibe kutumikira amalawi koma kuzunza ndi kupha
@GidionLufani
@GidionLufani 2 ай бұрын
Iweyo unamusungila chilima mpeni kuphasa
@MACDONADLITIA
@MACDONADLITIA 8 ай бұрын
Bwanji sanadikile kukuchotsa iwe brain
@blessingsmzomela1944
@blessingsmzomela1944 3 ай бұрын
Juman being who as sense can not vote to Mcp again 😊
@ellahmvula
@ellahmvula 7 ай бұрын
Tikudikira mgwirizano wawo wa 5 yrs ine chete
@johnkambala692
@johnkambala692 8 ай бұрын
Pamenepa tele kupanda kufotokoza bwino ndikuyambanitsa
@imranhabibu1743
@imranhabibu1743 8 ай бұрын
Iwe unayamba wamuyamikilapo APM?
@godfreysingini1508
@godfreysingini1508 8 ай бұрын
Ngati momwe iweyo umayambanisila nankhumwa ndi peeter Ukutumikila amalawi ati?
@godfreysingini1508
@godfreysingini1508 8 ай бұрын
Wadziwa liti zimenezi Uka dzudzule chimwendo kaye
@mikeasmachine4581
@mikeasmachine4581 7 ай бұрын
Utumikira ndani koma iwe msete zako wava chakwera
@alicehananiya
@alicehananiya 8 ай бұрын
Iweyo zoyambana sufuna koma zokuba ndie mbali yako
@blessingsmzomela1944
@blessingsmzomela1944 3 ай бұрын
I know u don't want someone to say the truth
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc 7 ай бұрын
Achitsilu awa oipa mtima mulibe tsogolo inu
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 3 ай бұрын
Inuyo munasungira mpheni mwana ku mphasa?
@WilliamGama-w8m
@WilliamGama-w8m 8 ай бұрын
Udaniwo anauyambitsa ekha ameneyu ndi galu kwabasi
@harrykalenga915
@harrykalenga915 8 ай бұрын
Onama
@JalalShaike-lh6bi
@JalalShaike-lh6bi 3 ай бұрын
Pamene uli chingawenga chachikulu
@RichardBandaRichk
@RichardBandaRichk 3 ай бұрын
Palibezimenemunapangapomumalawi
@InnocentNakhuwa
@InnocentNakhuwa 6 ай бұрын
Kutha ma plan kwa apresident
@grangerphiri7625
@grangerphiri7625 8 ай бұрын
Mau
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 8 ай бұрын
Chilima asalole kumunyengeleledwa
@RichardBondwe
@RichardBondwe 8 ай бұрын
He can not 21:57 stand 2025 as presidential candidate
@MarshalBanda
@MarshalBanda 6 ай бұрын
Ndi mtsekelera nkudyele uyu
@ElubeMisoya
@ElubeMisoya 2 ай бұрын
Ndizomwe munachitazi
@DonaldPonda-p2q
@DonaldPonda-p2q 8 ай бұрын
Brian banda
@SteveFote
@SteveFote 7 ай бұрын
Tikavote mwanzeru
@thesocietynews3181
@thesocietynews3181 8 ай бұрын
Wawononga MALAWI ndi mnzako CHILIMA
@PhynexMw
@PhynexMw 7 ай бұрын
Zaboza ndiopusa ameneyo
@TeniyapoQuefassiCadiwa-sz6iz
@TeniyapoQuefassiCadiwa-sz6iz 3 ай бұрын
Que L
@KeniusSanderson
@KeniusSanderson 6 ай бұрын
We are not fools
Electric Flying Bird with Hanging Wire Automatic for Ceiling Parrot
00:15
when you have plan B 😂
00:11
Andrey Grechka
Рет қаралды 67 МЛН
Inside Out 2: ENVY & DISGUST STOLE JOY's DRINKS!!
00:32
AnythingAlexia
Рет қаралды 12 МЛН
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 49 М.
BON KALINDO LERO PA 1 October 2024
17:37
HOT 265
Рет қаралды 8 М.
CYCLONE FREDDY FUNDRAISING DRAMA #malawi
1:31:45
Kanema Online
Рет қаралды 489 М.
Electric Flying Bird with Hanging Wire Automatic for Ceiling Parrot
00:15