Corruption inunso mukuhuzidwa nawo ku Reserve Bank of Malawi under Mutharika
@Elizabethmanda-es7se2 күн бұрын
bweresani umboni, poyera
@jameswajumpha67902 күн бұрын
Muthu wamkulu kuyakhura moveka bwino DK my vote
@TinasheKamanga-p9c2 күн бұрын
Akabambe sangakhale president lero adikire kaye akhazikike mundale osati lerondilero vuuuuu ayi dzikoli Lili pamoto ndizomwe zimavutanso abwana chilima akanavomeleza kuluza first elections bwenzi pano atakhala apre koma coz anaona kuti alliance ndiyomwe ingawatengere kukhala pre onani lero ndiawooo anatisiya nde awo mmmm l dout kuti sangapite patali ndiphumali afatse azipatse nthawi kutsogoloku azakhala not now.
@josephmwamlima23772 күн бұрын
Malawi has no good candidate for presidency
@SallyMwalrMusicКүн бұрын
the simple fact
@markmatimati2 күн бұрын
dziko la malawi likufunika asongoleli ngati awa osati kwantele
@banetmtungama60472 күн бұрын
Malawians indeed turned to be Lazaro's.
@FiskaniLungu-z8r2 күн бұрын
I can see something in DK
@GodfreyMurambiwaZhuwaki2 күн бұрын
IThe dude thinks All Malawians foolish like him...... He was a governor and just helped DPP to robe the poor country....and someone with straight mind is busy listening to the lies.....
@LawrenceNdala2 күн бұрын
Uyu alepheretsa chipani cha UTM. ...kulalata za ziii ngati Kaliati
@CharityBandaa2 күн бұрын
Wakuba chipani uyu
@Elizabethmanda-es7se2 күн бұрын
sanabe wagopasidwa usogoleli basi ndipo chipani ndi cha a nthu, sicha family.... ndipo BIYENI anananaso
@VeraVermaakКүн бұрын
Bwana 😂 mudzayenda wa pasi ndinu wa bodza simudzawina
@Jermah51kennias2 күн бұрын
This is Dpp reserve not UTM
@LawrenceNdala2 күн бұрын
No knowledge of Climate change, I can confirm the speech....too pathetic for a aspiring president!
@FrankPotipher2 күн бұрын
Wachamba iwe
@ChoopsyaLloyd2 күн бұрын
Cadet wa DPP uyu ndani angamuvotere
@TsArKhaii2 күн бұрын
Mazira anu bwana
@LawrenceNdala2 күн бұрын
Koma ngongole zaboma muzapereka? Maloto achumbatu awa
@gomezthera5352 күн бұрын
Anali kale mumuboma ameneyu akathandizila kupanga ma looking figure ndiwakuba
@LawrenceNdala2 күн бұрын
Kabambe, explain where you got the abundant monies dished during the convention while you accuse your fellow politicians. Iwenso wakuba yemwe ndi Mutharika
@chimwemwebwanausi95212 күн бұрын
True Economist🎉ulemu wako ntchana
@LawrenceNdala2 күн бұрын
He assisted plundering in Government resources in Mutharika's while Reserve Bank of Malawi governor.Kabambe was equally a failure as Mutharika..Big as him professionally failing to comprehend the law of supply and demand for maize....ndakomoka!.Hungry for power thus the poor child speech.Set your house clean Kabambe. Speech yosakhwima similar to Kaliati