ZOMWE WAULURA LAYTON MANGOCHI KUTI AMAMUCHITA PAMENE WATULUSIDWA KU POLICE PA BAIL

  Рет қаралды 32,399

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 90
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 8 күн бұрын
Kuswakuswa bas keep it up good work 😇💪💪💪💪
@Ruthgomonda
@Ruthgomonda 7 күн бұрын
Mmmm abweze ndalamayo paka kuba 50 pin mumakwana big💪💪👏👏👏
@AbdulrashidPhiri-c6k
@AbdulrashidPhiri-c6k 6 күн бұрын
Kuswa kuswa basii🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@DysonDube
@DysonDube 7 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅 kweni Layton aaaaa wamubela 50pin yake kkkkkkkkk
@lilianprince661
@lilianprince661 8 күн бұрын
Welcome back big man osaopa osafowoka ndiposo osatopa
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 7 күн бұрын
Kubela. Kaidi😂😂😂kulakwa Apereke..ulemu wanu Comrade
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman 7 күн бұрын
😂😂😂😂 mpaka 3 pin apolice musatichitise manyazi chonde yesesani 😂😂
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i Күн бұрын
Machine osaopa
@FlorenceNyirenda-y4l
@FlorenceNyirenda-y4l 3 күн бұрын
ALozen Asiyekuba
@MussahShamiunasugar
@MussahShamiunasugar 7 күн бұрын
Zoona zake amangochi
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 7 күн бұрын
Welcome back lyton❤
@mphatsosadiki4983
@mphatsosadiki4983 7 күн бұрын
😂😂😂😂😂koma Layton adha,munthu akamangidwa kwambiri amasiya kuopako kufika pozolowera ku Ndendeko 😂😂😂😂😂
@maxwelljuwaophiri
@maxwelljuwaophiri 7 күн бұрын
We are praying for you Bwana Lyton Mangochi and i wish you well
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 7 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 7 күн бұрын
Kkkkk koma mangochi umakhwana zoona anamizila moto wakuamerica
@PatrickMwizozo-ep3vg
@PatrickMwizozo-ep3vg 6 күн бұрын
Kkkk abwenze 50 pin
@RaheemMoosaraheem
@RaheemMoosaraheem 8 күн бұрын
Kuukano kwa akufa Mr MH😂😂😂😂😂😂
@lilianprince661
@lilianprince661 8 күн бұрын
Mwayiwala oopa mulungu ndife amalawi gulu la chikangawa saopa mulungu popeza agalu amenewa siamalawi
@GeraldBonongwe
@GeraldBonongwe 8 күн бұрын
Kkkkkkk mumakwana 💪 big
@vincentkamoto
@vincentkamoto 7 күн бұрын
Kkkkkkk Biggy
@JudithMaida-ug4oi
@JudithMaida-ug4oi 7 күн бұрын
Mpaka kuba 3pin iiih kkkk a police muyaluka Mangochi wake uti oho
@KelvinMandelaChirwa
@KelvinMandelaChirwa 7 күн бұрын
Sanabe agwilitsa ntchito zina
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 8 күн бұрын
Welkom back comrade 50.000 yapita a polisi akuba, zosadabwitsa atengela chikangaw
@MariaSoza-e1m
@MariaSoza-e1m 6 күн бұрын
Abweze kkkkk
@Nelsonmatenda
@Nelsonmatenda 7 күн бұрын
Lyton mangochi mumatimenyela ufulu osaukafe..No more mcp in 2025
@AllanChabwela
@AllanChabwela 7 күн бұрын
yokuba yokhayo ndiyoona,inenso anandibela zinthu zanga apoli apa area 3 atandigwila breatherisers,anthuwa amabadi mwa akaid
@WilsonChiona
@WilsonChiona 8 күн бұрын
Tiye nawoni
@FreddieNkhoma
@FreddieNkhoma 7 күн бұрын
Triple O OSAOPA OSATOPA osafoooka come on Malawi
@planBfore
@planBfore 8 күн бұрын
Mpaka kuba ka 50 pin agalu kkkkkk 😅😅😅😅😅😅 mukukandad et
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 Mkayidi wabeledwa
@GreciousNkhoma
@GreciousNkhoma 7 күн бұрын
😅😅😅
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 7 күн бұрын
😂😂😂😂
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 7 күн бұрын
Si mavuto awo nanga kumubela mkaidi ndalama chonsecho akukutumaniwo alemela koopsa, zitsiru!
@AmosMizeck
@AmosMizeck 7 күн бұрын
Aaaaaa wadya chamba iweee manvwa ako
@MemoryLaisi-h7y
@MemoryLaisi-h7y 7 күн бұрын
Very shameful kkkk
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 7 күн бұрын
Zoonadi brother Mangochi chilungamo chioneke basi
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 8 күн бұрын
Ulemu wanu CHAKWELA ndi MCP yakeyi anthu oyipa dzedi
@JuniorSamalia
@JuniorSamalia 8 күн бұрын
😂 amuna!
@JosterLeman
@JosterLeman 7 күн бұрын
Chiphazi ndindani kod😂😂😂😂😂
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 7 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@LazarusMkandapachuma
@LazarusMkandapachuma 8 күн бұрын
Naoso azamangidwa achiphazi awo siku likubwela osafooka lyton
@fannyzimba149
@fannyzimba149 7 күн бұрын
Osawopa Mr Layton mu kubwera bwino agalu awaatitopetsa mizimu yaku chikangawa Belezebulu ikukanthani misanati achimphazi kkkkk
@omarajibu860
@omarajibu860 7 күн бұрын
Mangochi now
@PriscillaMangata
@PriscillaMangata 7 күн бұрын
Chiphazi ndindani abale 🤣🤣🤣
@Khadija-q9r
@Khadija-q9r 8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 aba ya nkaidi Akuti yaine mubwedza kkkkkkkk
@DavieDulani
@DavieDulani 8 күн бұрын
Big Layton welcome back tiuzeni zinalibwanji
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 7 күн бұрын
Awa ma arv awazunguza bongo ,a mangochi mulibe kenakalikonse mungamenyere ufulu a Malawi inu a chitsiru inu
@BerthaFriday
@BerthaFriday 7 күн бұрын
Iwe chiphanzi ndazako mzatengeni koma guys ati boma ndilomweli oky
@TadalaBirsonkanjanga
@TadalaBirsonkanjanga 7 күн бұрын
Bwezani 50pn gyz
@AllanMwakalenga-wn5ib
@AllanMwakalenga-wn5ib 8 күн бұрын
Nkayidi waberedwa,mupaseni zake
@YassenYasin-v6o
@YassenYasin-v6o 7 күн бұрын
🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
@GraceMlauziNkhoma-ml7tv
@GraceMlauziNkhoma-ml7tv 7 күн бұрын
Kkkkkkkkkk awapasa mphamvu zuchulika kkkkk
@MartinMajola
@MartinMajola 7 күн бұрын
Chikangawa mbuzi yamuthu
@CharlesMlenga-k4m
@CharlesMlenga-k4m 8 күн бұрын
Walila mkaidi kkkkkkk dont do it again this is mcp mphwanga
@SiyasiyaManda
@SiyasiyaManda 7 күн бұрын
Kod chipadz ndi ndani
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 7 күн бұрын
Chimwendo
@AlfordJuwa
@AlfordJuwa 7 күн бұрын
kkkkkkk
@SylvesterSululu
@SylvesterSululu 8 күн бұрын
Zinazi mukumango kakamidzatu apa ndikuvamfundongati yakuwawatu yomangidwayo kkkkkkkkk koma
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 7 күн бұрын
Ma activists a muziko muno mukunva kuwawa ndipo mukamba mutopa mpaka 2030 woooo mukhalila yolila yomweyi
@DannyKalumbaWaBanda-q7o
@DannyKalumbaWaBanda-q7o 7 күн бұрын
Kod mwava inu akantengeni?🤣🤣
@AllanChabwela
@AllanChabwela 7 күн бұрын
auzeni kkkkkk anyapapiwa
@NelsonMalija
@NelsonMalija 8 күн бұрын
Wopusa uyu cadert
@ChristopherCk-s4w
@ChristopherCk-s4w 7 күн бұрын
Omenyera ufulu mwa umbuli anyamula makaka achipani ndikumatukwana 50 pin yokupasa a Dpp zaziii munthu mkulukuluwe adzukulu Ali phweeee manyazi bwanji
@RuthBeyala
@RuthBeyala 7 күн бұрын
Ingobwezani 50 pin inuyo muliperekere bomalo kaa😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@ShillaShamil-v2y
@ShillaShamil-v2y 7 күн бұрын
Zizukuluzo ndi zache ndiye yakuwawa
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 7 күн бұрын
Ku chikamwako chikangawa son
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 7 күн бұрын
Ayamba misala ausufu mangochi
@EvansEgra
@EvansEgra 8 күн бұрын
Nchifukwa adzikumanga, ndiwe nchisiru ,umalankhula za umbuli? Ukupalamulanso pamenepo, ukunyoxa munthu kuti Chiphazi,Chavuta ndi umbuli mmutu mwakomo
@ishmaelimedi7363
@ishmaelimedi7363 8 күн бұрын
Ku malawi pafika zithupa pakufunika makani kuti zikuyendele, zavuta malawi wathu
@GreciousNkhoma
@GreciousNkhoma 7 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 8 күн бұрын
Apolisi ku Malawi kuno ndi akuba too much
@CharlesBanda-v8k
@CharlesBanda-v8k 7 күн бұрын
Anyamata mwagwedeza mcp 😂😂😂😂😂😂
@PempheroMoleni
@PempheroMoleni 8 күн бұрын
Kkkkkkkk chafika😂😂😂
@mailos.laisoni7001
@mailos.laisoni7001 8 күн бұрын
Abatu 😂😂😂
@EnerstMwitha
@EnerstMwitha 8 күн бұрын
Wakulu wafika tsopano
@FulumensioTembo
@FulumensioTembo 8 күн бұрын
Munthu wakulu watulukila
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 8 күн бұрын
Auzeni agalu awa amcp mbuzi za anthu
@EvansEgra
@EvansEgra 8 күн бұрын
Alibenso ndi mfundo yomwe, agawane video ndindani? Zopusanzo
@giftsululu4274
@giftsululu4274 8 күн бұрын
Kodi Ada awa mga dpp
@Christopherchapeta-q2j
@Christopherchapeta-q2j 8 күн бұрын
Ameneyu ndi M'malawi nanga owe ndi ndani?
@solomonmunthali610
@solomonmunthali610 7 күн бұрын
😂😂😂
@CharityPhiri-q1c
@CharityPhiri-q1c 8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@Openjkick
@Openjkick 8 күн бұрын
kzbin.info/www/bejne/pWHKZGiObrKCe5Ifeature=shared
@TenganiObety
@TenganiObety 8 күн бұрын
Ndiwe wemwe unathandiza kuononga dzikolino galu iwe
@AchinaKellz
@AchinaKellz 8 күн бұрын
Mulira achikangawa opusa ndi mbuyewako yemweyo
@EvansEgra
@EvansEgra 8 күн бұрын
Galu uyu , Layton
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 7 күн бұрын
I hope he is not violating court bail Conditions . Adangomva kuti ukafuna kutchuka koma kudya galu pagulu .
@AchinaKellz
@AchinaKellz 8 күн бұрын
Tizule mbeu yakaufiti pa September malengeni machaka manja ziwandazi zili ndi mifuti
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 7 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@AlfordJuwa
@AlfordJuwa 7 күн бұрын
😂😂😂
BON KALINDO LERO PA 06 FEBRUARY
19:03
Makosana
Рет қаралды 18 М.
СИНИЙ ИНЕЙ УЖЕ ВЫШЕЛ!❄️
01:01
DO$HIK
Рет қаралды 3,3 МЛН
What's Really Behind the M23 Conflict and Who's Involved? PLO Lumumba
31:59
Ndan Yemwe Wapopa Manganya Kuyambisa Chipani?
4:09
Sam Malvitha
Рет қаралды 38 М.
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34