BON KALINDO LERO PA 6 SEPTEMBER 2024 |
16:10
NKHANI MADZULO APA 5 SEPTEMBER 2024 |
20:05
KUCHAPA INTERVIEW BON KALINDO MBAMBANDE |
43:34
GWEDEGWEDE LERO PA 5 SEPTEMBER  2024 |
30:28
BON KALINDO LERO PA  4 SEPTEMBER 2024 |
18:03
NKHANI ZA MADZULO APA 3 SEPTEMBER 2024 |
21:04
GEORGE  KASAKULA  MUSIYENI PRESIDENT AYENDE |
44:41
BON KALINDO LERO PA 3 SEPTEMBER 2024 |
17:33
KU UDF KWACHEMA ZOMWE ALANKHULA ZIVERENI |
28:19
BON KALINDO LERO PA 2 SEPTEMBER 2024 |
18:39
KANDIVELERE MPOKOSO LOCHEPA NKHANI ZAMBIRI |
31:31
NKHANI MADZULO APA  1 SEPTEMBER 2024 |
18:01
12 сағат бұрын
HOT CURRENT LERO PA 1 SEPTEMBER 2024 |
46:34
FROD UKU NDE WANG'ALURA  KUMSONKHANO UKO |
9:07
MUKHALE NDI UMUNTHU POMWE REPORT LATULUKA |
18:51
Пікірлер
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah Сағат бұрын
Ineyo monga mMalawi yemwe ndikuyidziwa MCP bwino bwino, ndikuti anachita choyinkoza ngozi imeneyi . Mchifukwa chake report labwera monama chomchi. MCP imapha anthu onse amayidzudzula komanso owoneka kuti azatenga ma udindo . Ndipo simacheza pokhapo. Anapha Sidick Miya , lero aphanso Chilima ndi ena aja. Ndiyokupha basi ziziwika zambiri ikachoka mboma
@kadijachilwan967
@kadijachilwan967 2 сағат бұрын
Mpunga mpaka kukagulaso ku Japan komweko 😂😂 osagula malawi momwemobwanji?
@kennymwanyongo8165
@kennymwanyongo8165 2 сағат бұрын
Apa ndiye mukunama mwankukunika. Bwanji osangosiya maboza anuwa. Apa mwaonesa kuti media yimanamadi mopanda manyazi.
@BesterDaude
@BesterDaude 3 сағат бұрын
Komano chipani chimenechi chawononga zithu kwazaka 5 watambauti atadutsaso apapa amalawi tidzakhala paumasiye wochuluka
@MakabaBauleni-c2i
@MakabaBauleni-c2i 3 сағат бұрын
Msogoleri wanji omaima pachulu mkumati ndinagwetsa kwacha iwe okhala mtsogoleri sukudziwa kuipa kogwetsa kwacha ???? Lero ukaime mopanda mmanyaz mkomwe kumauza ife zimenezo mwina vuto ndikusayenda ndikuona maiko ena mmene amayendetsela chuma chawo upite maiko ena ukapedza kt ndalama yao idaima njiii Malo amodzi ndipo sipanga nawo zomwe mukuipanga kwacha yanuyo kumangomvela mabungwe bax tapitani even pa south Africa pomwepa mukapedza kt Rand yao samalora zopusa kt mabungwe ndi ena otelo ailamulire kuyambira 1994 pomwe analandila ufulu ozilamulira okha mpaka pano mukapedza kt olo 10 cent ikugwilabe ntcito,nde iwe ulibe manyaz
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 4 сағат бұрын
Dziko lathu likugulisidwadi,😂😂😂😂
@NactonMwale
@NactonMwale 4 сағат бұрын
Koma A Joyce Banda analuza kubwela mpaka no 3 koma Ali m'boma akufuna akutinamiza awa angapeze mavoti kuposa dpp aime awona polekela
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 5 сағат бұрын
Mzimayi uyu wachikondi kuposa chakwera even mfundo zake
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 5 сағат бұрын
Ndisaononge data yanga ndi Joyce banda
@JamesLuke-f5d
@JamesLuke-f5d 5 сағат бұрын
Bwana kalindo mumakwana
@mphatsomalenga
@mphatsomalenga 5 сағат бұрын
Awaso 😢 komatu Ali m,Boma momwemo
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 5 сағат бұрын
Nsimai opanda manyaasi uyu be careful a Malawi anzanga. Munthu wa satanic wachabechabe.
@LatifBeni-e6z
@LatifBeni-e6z 5 сағат бұрын
❤❤❤❤❤
@ManganiStanley
@ManganiStanley 6 сағат бұрын
MCP party iwe
@AishaJafali-h3b
@AishaJafali-h3b 6 сағат бұрын
111
@lezawawal
@lezawawal 6 сағат бұрын
This is not even an interview ,but rather interrogation.
@FiskaniTonymahone-vl3og
@FiskaniTonymahone-vl3og 6 сағат бұрын
Sakufuna kuleka kanthu kalikonse 😅 iiiih 😢Koma Chakwera akufunika Kuganiza bwino kwambiri, chifukwa ana Ake kapena zidzikulu zakenso zilinao pamoto umene tiliwu..
@FiskaniTonymahone-vl3og
@FiskaniTonymahone-vl3og 7 сағат бұрын
This presidency takes responsibilities as a slave but not Chakwera, the problem is that the people portrays him as Bwana or Boss..
@ADHASAPONYILENDA
@ADHASAPONYILENDA 7 сағат бұрын
Zazi
@user-ox4dh3ey6b
@user-ox4dh3ey6b 7 сағат бұрын
Amayi awa mfundo zimawasowa.
@juliussamson6212
@juliussamson6212 7 сағат бұрын
KUNALITU BWINO MAI KUZISIYA ZANDALE CHIFUKWA ZIKUVUTANI KWAMBILI NOSE INU MUDZATHELA PAKAMPENI NOSE MUNACHITA CHIPONGWE MR CHILIMA MUZILAPILATU MUSANAWONANE NDI MULUNGU
@juliussamson6212
@juliussamson6212 7 сағат бұрын
AJOYISI BANDA MUNAPANGA NAWO NJILA YOPHERA MR CHILIMA IFE TITIFUNASO MUZITIDUTSA MASO PAMODZI NDI AZABU ONSE
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 8 сағат бұрын
Mbunzi yachabe chabe iyi unaphanawo chilima iwe ndani sakukuziwa
@user-ug3bf4pr9p
@user-ug3bf4pr9p 8 сағат бұрын
Great words amai ndinu amaidi
@giftsululu4274
@giftsululu4274 8 сағат бұрын
Pomwe jb a amanga manyumba ndi Bakili Muluzi... APM anali busy kugona
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 8 сағат бұрын
Kugwesa kwacha siudolo mai inu tikulira chifukwa cha chakwera kugwesa kwachako aaa
@user-dt5bd7ou3t
@user-dt5bd7ou3t 8 сағат бұрын
Ok ok guys ine ndangomva mawu oti kuli kampeni yowoohya kusogoluka Ali ndi mwana agulise kkkkkk
@user-hn8sr9oc7k
@user-hn8sr9oc7k 8 сағат бұрын
Iyi ndiye ngamo ngamo,ngati achakwera sakudziwapo kanthu za IMFA imeneyi bwanji uyo anawanamizayo sanamuchotse ntchito?achakwera mulandu umenewu muyankha ndipo mudzayankha
@BesterChaima
@BesterChaima 8 сағат бұрын
Umatha dc
@CharlesFalakeza
@CharlesFalakeza 8 сағат бұрын
Galu iwe ufuna kuwagulitsaso amalawi ku chigawenga mbuzi ya mayi
@AndySymon
@AndySymon 8 сағат бұрын
❤ Captain
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 8 сағат бұрын
This woman encouraged Chilima to go into alliance with Chakwera but when Chilima died, she went silent
@victorbanda9039
@victorbanda9039 7 сағат бұрын
Nkhani izingokhala yachilima Kodi
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 6 сағат бұрын
Mai ameneyu ndi oopsya zedi
@austinvincent773
@austinvincent773 6 сағат бұрын
YAkwanadi bwanji mose tayambila​@@victorbanda9039
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 4 сағат бұрын
Inu mmafuna tikambe yandani​@@victorbanda9039
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d 8 сағат бұрын
Awa ndi maganizo achizimayi kugwesa Kwacha ndizo zobwelesa mavuto . IMF ndi bungwe lobwelesa mavuto. Amayi awa asazalamulilenso . IMF ndi mdani wathu . Denis Mahata ndamene angabwelese chitukuko
@JohnTimbenao
@JohnTimbenao 8 сағат бұрын
Koma guys you are too careless.
@LenardJames-j1n
@LenardJames-j1n 9 сағат бұрын
😂😂🫵
@petermasenti2084
@petermasenti2084 9 сағат бұрын
Useless opposition
@yusufbakali
@yusufbakali 9 сағат бұрын
We are together guys
@ShadreckEliya
@ShadreckEliya 9 сағат бұрын
True
@BillyBentryMunthali
@BillyBentryMunthali 9 сағат бұрын
Chipan ichitso ndi cha sankho nanga chifukwa chian sapangira convention ku mpoto?
@EstherMbisa
@EstherMbisa 10 сағат бұрын
Koma mwati sitili m'botolo abale😓😓😓, nanga bwanji sitipanga act 😭😭😭
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 10 сағат бұрын
akungotaya nthawi yawo ameneo adatikwana ndi chakwela wakeyo mr and mrs chikangawa
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 10 сағат бұрын
Zitavuta motani simungawine nokha
@user-ux9ik4zr5x
@user-ux9ik4zr5x 11 сағат бұрын
Osowa zochita uyu,anasankhidwa pa WhatsApp 😂😂 kodi ndi a Malawi angati omwe ali pa WhatsApp?zachamba basi
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 11 сағат бұрын
Mankhwala mu zipatala mulibe president ndalama akungochindira mahule uku kasakula akuti vuto palibe mulungu amuyendera mwapadera
@user-zj1xx1ic2m
@user-zj1xx1ic2m 11 сағат бұрын
Chitsuro chanji, Dangerous Child, good interview.. ❤❤❤
@DominiqueChitimbe
@DominiqueChitimbe 12 сағат бұрын
❤❤❤❤❤ 0 pa 10 yomweyo I love you my dear dc
@RodgerChaula-r5z
@RodgerChaula-r5z 12 сағат бұрын
The D C
@GiftKananji
@GiftKananji 12 сағат бұрын
you are better than achina ndevu za mwayi
@GiftKananji
@GiftKananji 12 сағат бұрын
You are representing us very well, gys
@user-js6xn9qj1r
@user-js6xn9qj1r 12 сағат бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥