GWEDEGWEDE SAMAOPADI MUNTHU ETI NDIKUTITU KUNALI. KUNG'ALURA MUSAONA NKHOPE |

  Рет қаралды 65,801

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 306
@MaryNgola
@MaryNgola Ай бұрын
Amen 🙏 izi nde zoona zake ndipo nde mwayankhura zoonatu,anthu akuzitenga zophweka chifukwa anamwalira aja saabale ao
@SailotaSamuel
@SailotaSamuel Ай бұрын
That's why lm in love with this program of gwedegwede bcz kunjakudi kwavuta nde mukamatiyankhulila timakondwwla🎉
@GifLiche
@GifLiche Ай бұрын
Za ndale si mbali yanga but this issue of chilima it is so painful
@Betty-fe9ql
@Betty-fe9ql Ай бұрын
I tell you anamukhiya game yoyipa kwambiri
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka Ай бұрын
Kwambiri olo ine zandale simbali yanga km IMFA ya anthu 9 ija inandipweteka kwambiri, kuphuzitsa mwana school sizophweka anthu amene aja analindimaudindo makwawo ndipo ineyo eish😢😢😢 zinalakwika
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 Ай бұрын
Program iyi lero mwadya good guys,
@mphatsomonjeza4371
@mphatsomonjeza4371 Ай бұрын
True talk guys bravo well spoken
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Ай бұрын
MBC, singapange nawo zoterezi, bravo MIBAWA TV
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka Ай бұрын
Bolatu lero mwalankhula za nzeru 🔥🔥🔥💪💪💪
@bornface4786
@bornface4786 Ай бұрын
Tandifunsirani kwa anthu amene amayang,ana zoulutsa ndi kutera ndege kuti Kodi nthawi imene ndege inapita ku mzuzu koyamba siinkawoneka pa radar coz tikumva inapita koyamba then kachiwili
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 Ай бұрын
Koma chakwela Mr chikangawa alindi zelu anthu wosewo kupita nawo ku China 🇨🇳 apo ku machinga anthu akugona ndi njala
@HaliJana
@HaliJana Ай бұрын
Inu chakwera machende wake tamufusani kuti wachita chani kuno Ku Malawi galu ameneyu kupha basi Mr chikangawa
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule Ай бұрын
Zoona chakwela you mast go watikwana
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Ай бұрын
Steve apa wankhula bwino zed kusiyana ndi mbuyomu umaopa boma pano ulibho zed❤
@EmmanuelNtago
@EmmanuelNtago Ай бұрын
Ukuku nde kuyankhura,, yemwe zikumuwawa ndi mfiti yotheratu,,,osafuna kusintha zinthu
@KondaniPhiri
@KondaniPhiri Ай бұрын
Ndipo zikutiwawa. Za ifa imene inja. tapangani pls. Ndipo adulidwe mutu chakwela
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 Ай бұрын
Pamenepa ndiye mwang'aluradi zenizeni kuwayankhulira amalawi Otsuka mwatisangalasa zedi❤
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Ndi munthu oyipa mtima osamva chisoni anthu akufa ndi njala. Mpaka afika pokudya chidze ndi deya owawa. Ubusa uli pati Lazarus Chakwera iweeeeeeeee!!!!
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko Ай бұрын
ndipo ine Banda umandiwaza ndisaname umayima pachirungamo tithandizeni abanda timakukonda muri worimba mtima l love you
@FlorenceKamtambo
@FlorenceKamtambo Ай бұрын
I don't agree with commission of inquiry thing because of what commission of inquiry has been yielding. Better if we can constitute public inquiry like we did with presidential elections where we used parliamentary special committee, those who failed to replace expired battery in 2004 should be questioned because that affected counter-turbulance navigation AIDS of the fated plane.
@JonesChilonga
@JonesChilonga Ай бұрын
This program is so educative,,may God bless you guys,,Anthu akudya chitedze BOMA Lili duu! Nkumayembekeza kuti anthu awavotere,,,mcp you are joking
@SandraChibaka
@SandraChibaka Ай бұрын
Bravo bravo to you guys...osaopaa
@Betty-fe9ql
@Betty-fe9ql Ай бұрын
Kodi zoti ndege sinafike ku mzuzu ndi zoonadi
@JECKYGREY
@JECKYGREY Ай бұрын
Eya mn
@HassanMussah-i9j
@HassanMussah-i9j Ай бұрын
Powerfully gwede gwede osaopa komaso osasekelelaso munthu dzikoli ndilanthu ili 💪💪💪💪
@TimexKaufa
@TimexKaufa Ай бұрын
Tsiku langozi akuti Tawa idali yozima. Idaizimitsiranji? Kuchotsa Recoder, kuzimitsa Tawa zonsezi amkafuna kut mafoniawo as angwiretchito. Pakungofunika Madomo akulu
@mikesangano6624
@mikesangano6624 Ай бұрын
Big up guyz, I'm following you with interest. This is the truth you are updating us
@kelvinjumbe1526
@kelvinjumbe1526 Ай бұрын
I personally was of a view kuti inali ngozi monga momwe ngozi zimachitikira ...komano from the preliminary report that have recently been released, I am left out on the corner in disbelief... trying to connect probable dots of facts but all seems not to add up...I think we really need special commission of enquiry to bring relevant authority to answer questions that we are unable to get the tangible answers... Thats what we call transparency and accountability
@franciscophiri2855
@franciscophiri2855 Ай бұрын
Congratulations guys for this one
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri Ай бұрын
Mwadza inuyo ma guys more fire
@WysonLipende
@WysonLipende Ай бұрын
Well come gwedegwede
@Vincentmandota
@Vincentmandota Ай бұрын
Big up guys kumeneko nde kuyakhula
@lyiemax
@lyiemax Ай бұрын
Powerful, big up guys
@ManzyNgoleka
@ManzyNgoleka Ай бұрын
Chiyambileni kutsatira ma program anu iyi yokha nde 100% ena onse aja mbola
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
❤❤❤ this is totally true we need balck box tikumufuna chakwela abwele
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Ай бұрын
TAKUTHOKOZANI LERO MWAYANKHULA ZANZERU MUPITIRIZE , ABUSA AMALIRAO ANAWACHITA BWINO KUWAZUZULA PA GULU CHIFUKWA ANAONETSA NTIMA WA DYERA , OSAMAWASEKERERA ABUSA OTEREWA NDAMENE AKUPANGITSA KUTI DZIKO ANTHU AZIZUNZIKA CHIFUKWA CHA DYERA , ATSAKANSO ENA TIWAYALUTSA
@JosephyKambalu
@JosephyKambalu Ай бұрын
The fact that ma batile anatha 2004 it's a sign yosonyeza kuti we didn't have leadership yazelu. Don't forget ndegezi zinagulidwa ndi Kamuzu/MCP.
@BlessingsManyamba-e6o
@BlessingsManyamba-e6o Ай бұрын
Keep your heards ringing we need anthu ngati inu mumatv station
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg Ай бұрын
Mwalakhula mosaona mbali guys 🔥
@RachealKumwenda-j6d
@RachealKumwenda-j6d Ай бұрын
Mwayowoya mwawanthu ,yifwa yikutiwawa chomene yila ,unenesko uoneke ,ndicho tikukhumba,yowoyani chomene Charu nchithu ichi ,topenge chiuta no munthu munyithu yayi,chikutiwawa chomene,chilungamo chioneke
@NathanLubangaKaunda
@NathanLubangaKaunda Ай бұрын
Ndipo ulemu wanu mwayankhula mfundu zothyakuka kwambiri .ndipo amene wakwiya ndi mfuti 🙏🙏
@DoricaGoweka
@DoricaGoweka Ай бұрын
Ulemu wanu awulutsi athu Chakwera anachita kokonza chiwembu ichi abale athu 9 anachita kuphedwa.Chawera ndi chilengwalengwa cha president. Akungoyendayenda kuwononga misokho yathu pomwe amalawi tikuvutika kusowa makhwala mzipatala.
@KondaniPhiri
@KondaniPhiri Ай бұрын
Zipangike mwachangu pls tisamangolankhula pls achoke
@EsetaGerate
@EsetaGerate Ай бұрын
Anthu amenewa amasewera padiwa awona kovalira 2025 ngat amaona ngati athana ndichilima anyera
@MoMoses-g9u
@MoMoses-g9u Ай бұрын
Nice
@dytonkaphwanya5167
@dytonkaphwanya5167 Ай бұрын
Out of 9 People lost their lives present 9 family lost their relatives life finally how large number of people missing and suffer out of this 9 People
@SueWahna
@SueWahna Ай бұрын
Busa ameneyo amafunika pagulu kumene galimoto yamupengesa misala sakumvaso zonena za anthu awo
@SolomonMumba-i5n
@SolomonMumba-i5n Ай бұрын
He is not and hasn't been ready to govern. His only interest is the well being of his family and friends.
@lameckmajiga5426
@lameckmajiga5426 Ай бұрын
Koditu tisamanene kuti ndi athu 9 omwe anatisiya pangozi ijayi koma tiziyikaponso malemu kasambala,cidic mia nawonso aligulu lachikangawa😢😢
@StephanolucianoLuciano
@StephanolucianoLuciano Ай бұрын
Osamangolawitsa timaprogram tanuti chonde, muzitibweletserako full program please.
@talandilabenedicto
@talandilabenedicto Ай бұрын
Akuzitengeratu chibwana kobasi akubomaku, ndipo wina adzayesere kunena mwachibwana amvekere boma ndilomweri ndili pomwepo, m'dzamuwomba khofu zedi
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Ай бұрын
Steve wanena zoona. Uwuze mabilimangwe aku mbc opanda zeru. Iwe Steve upite ku mbc ukaziphuzitse mbewa zingo limbana ndi dpp ndi utm osaziwa kuti ife amalawi tikufuna chani pa report
@MADALITSOMISHEC
@MADALITSOMISHEC Ай бұрын
Muzitumiza full program osat kumaidula .. Program ya 30min inu mukaika ya 20 min
@laston-rj2qs
@laston-rj2qs Ай бұрын
Kwin munthu uyo wakwenda kwenda mmm
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu Ай бұрын
Mr. Banda ndi Selina mukutilankhulila bwino kwambiri. Kunena zoona ku Malawi tilibe mtsogoleri, akudziwa kuti ajuchoka 2025 ndiye akuseselatu kandalama konse m'boma.
@ToweraChisanga
@ToweraChisanga Ай бұрын
Well speak guys
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t Ай бұрын
Alizungulizunguli koma anthu akufa ndinjara koma iye akungoononga misonkho yathu kuendera
@HajiraMustapher
@HajiraMustapher Ай бұрын
Iyi ndiye ngamo ngamo,ngati achakwera sakudziwapo kanthu za IMFA imeneyi bwanji uyo anawanamizayo sanamuchotse ntchito?achakwera mulandu umenewu muyankha ndipo mudzayankha
@kingSoko-wf4pe
@kingSoko-wf4pe Ай бұрын
Kodi achakwera mbuyomu amagwirisa ntchito box ikunenrdwayi mulibe akafukufukuwo atifufuzire zambuyonso
@glochilangwe936
@glochilangwe936 Ай бұрын
Womwalirayu ndi vice president! Plus anthu ena 8, nkhaniyi siingathe popanda wina kumangidwa. Panali ma negligence from different individuals apa
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l Ай бұрын
Abusawoso anatopakaya,ndebwinoooo,wamung'alulira pagulu
@SsBakali
@SsBakali Ай бұрын
Silute guys ur doing well Truth is painful
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 Ай бұрын
Apapande izizi ndi fundo zeni zeni ,thandizani amalawi fe ndikutiziwisa zowona
@AmosShadreck
@AmosShadreck Ай бұрын
Kodi akudya chitedzewa muembekezera adzachongeso padzina lanuuuu?
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx Ай бұрын
Chakwera you must go chikangawa ameneyo Chakwera
@MolosonMisitala
@MolosonMisitala Ай бұрын
Chakwela samava pleese akufuna kuononga dziko,chingofunika mkupeza ginito timugwetse bs mkusasava kwakeko
@FelistasNkasalaMakumbo
@FelistasNkasalaMakumbo Ай бұрын
Bravo mibawa
@Jonas-v8y
@Jonas-v8y Ай бұрын
Program yabwino, tinvedi zenizeni za brack box
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Ай бұрын
Inuyo ndi achipongwe chikangawa amayiziwa zoom?
@graceofgodlivingchurch.
@graceofgodlivingchurch. Ай бұрын
komadi chidachitika ndi chiyani mkati mwa ndenge?
@ChristinaStambuli-q3e
@ChristinaStambuli-q3e Ай бұрын
Mwangonena kut kuli msonkhamo ku America but the way this guy isI flying from òne country to the other definitely he is going I'm sure of that..coz za mavuto a Malawi 20 million iye sakulabada ..apart from family yake cabinet yake ndi amudzi wakwao ndi omwe akudyelera. But God is watching .
@MoosaSame
@MoosaSame Ай бұрын
Well done guy's ❤❤❤❤❤🎉🎉
@ApostleAmoskampetewu6321
@ApostleAmoskampetewu6321 Ай бұрын
Ine ndungofuna yemwe analamula kuti ndege inyamuke koma akudziwa kuti kuli chifunga,,,ndipo asatiyese ife amalawi oputsa,,,,ndipo ilala nayo mutikonzere mwachangu ife kumudzi kwanthu ku new salawe kulibeko misewu ndipo sikumafika galimoto Oro njinga zakapalasa,,timadalira ilala yomweyo nde chonde imvani mavuto anthu nafe ndamalawi,,, zikomo mibawa mwatiyankhulira
@IssahAluba
@IssahAluba Ай бұрын
Inu just imagine Aku Germany akuti black box munalibe kukhuyu akuti black box, ilipo chakwera akuti ndege inafika kuzuzu Aku Germany akuti munalibe zipagizo zolumikizirana ndi control traffic nsete zenizeni
@Dan44-x5b
@Dan44-x5b Ай бұрын
Osati malaoya koma achibale awowo koma otseguka mmaso. Komanso kodi ngati ma commission of enquiry wa ayoenera kuti ayankhe mafunso enei enei osatingati omangidwa kwa Anti corruption beraeu
@peternashyo9850
@peternashyo9850 Ай бұрын
Straight talk
@fridaymwenje1346
@fridaymwenje1346 Ай бұрын
Kkkkk akutsonya et kkk
@FranciscoFabiano-ed6sj
@FranciscoFabiano-ed6sj Ай бұрын
Steve ukunera kupeza ku times ukuyakhura zazeru hvy sukuopayi
@blessingsmaganga7399
@blessingsmaganga7399 Ай бұрын
Ngati sakupereka zoona zenizeni nde kuti a bayeni munawephera dala
@HopesonChembekezo
@HopesonChembekezo Ай бұрын
🎉big up
@emilynthite6545
@emilynthite6545 Ай бұрын
Asalimbane ndi chakwera koma apange mwaokha akuchipani komanso akubanja zakafukufukuzo koma simungauze muthuokuba kuti akasake wakuba amupezakuti?? Poti mbava ndiyomweyo chakwerayo
@GLADYSCHIDOTHI
@GLADYSCHIDOTHI Ай бұрын
Mumakwana mr banda
@HarryMakwale
@HarryMakwale Ай бұрын
Bravo guys ❤❤❤
@richardmahata5523
@richardmahata5523 Ай бұрын
Viva guys straight talk
@JanuaryGwere
@JanuaryGwere Ай бұрын
Utsogoleli uwu tilibe nawo mawu
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l Ай бұрын
Mokupemphani,tapitilizani,ife kunva kukoma ndipo zose zemene akupanga achakwera ndi chipanichawo,kungoti,,,.ndingatukwane
@EFRIDALINDE
@EFRIDALINDE Ай бұрын
Zandele so mbale yanga koma na apapa inuyo mwayamkhula kwambiri ndithu ndipo inuyo mumakwana this is srs talk guys
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t Ай бұрын
Chikangawa ndi amene anapha mesa akuziwona kuti anapha ndi iyeo koditu u former wake iyeo sazaumva kukoma cnanga akathela ku police ndi apolice azizakewo opha nawowo koditu ifeo tikuziwona opha zake nayeso aphedwe chikangawa ndi azizake onse azamangidwa ndikuwapgaso basi atikwana opanda mphindu owo Chikangawa ndi kunkuyu mai nyolamu gonani ndi ena onsewo
@yusufbakali
@yusufbakali Ай бұрын
We are together guys
@ChristopherSankhani
@ChristopherSankhani Ай бұрын
This very true
@Fanny-h9r
@Fanny-h9r Ай бұрын
Zoona zake anthu akudya chiteze,ndizovuta kut azavoteleso boma lomwe lawadyesa zosaenela kudya 😢😢😢zomvesa chison
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi Ай бұрын
Mr chikangawa chifunga adapha chilima basi full stop Paja ndi congeresitu abale osaiwala
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k Ай бұрын
Inu Lazaro askhaleko mugulu losankha anthu ofifuuza zangoziyo chifukwa iyeyo ndi chigawenga chachikulu
@WinerdShadreck
@WinerdShadreck Ай бұрын
We love u🎉
@eunicesaiti
@eunicesaiti Ай бұрын
Mau mau 🙏
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k Ай бұрын
Ali momwemo chakwela oyipa ameneyi.Munthu wamagazi uyu
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Ай бұрын
Chilungamo ndani angazavotele Chakwerayu akudyesa anthu chiteze? Iyeyu kumayenda ngati zose zilibwino
@JossamKamanga
@JossamKamanga Ай бұрын
Gwedegwedeyu..ndamkonda kwambiri. Koma ndikutsuseni pa nkhani yoti mubusa wina samalira. Kuchokera pa nkhani yomweyo ..momwe mwanena yoti anapita kwa purezideti.. ," POKHAPO"POOKHAPO" kulirako nkochepa.. bola kuachotserathu.. komanso abweze ndalama zomwe anayendera kudutsa luwerezi, CHIKAngawa, kasungu mpaka kwa puleko. Dziko likufunika anthu odzudzula layivi ..azibusa ambili amakona ndalama zakuda
@JossamKamanga
@JossamKamanga Ай бұрын
A tv musafoketse ozuzula..pafikadzikopa
@jamessheki4293
@jamessheki4293 Ай бұрын
Tinamva kale kuti iwo sakuchoka 1, kuiwala kut boma linali logawsna,2 Mkaka ananena kut wayedzeka... Ndale zawo amapanga usiku.. 3, mareport okha okha a MCP akukamba zosiyana,inenso ku MCP ayi....😢
@ShadreckEliya
@ShadreckEliya Ай бұрын
True
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t Ай бұрын
Chikangawa you must go 😂😂😂 ukaphele kutali basi
@akimchigaga3441
@akimchigaga3441 Ай бұрын
Ngati black box ilipo aibwesetsetu nrnga, nkhani itepo akuisunga chifukwa chani
@EnockMithi
@EnockMithi Ай бұрын
Ineyo ndine driver koma ndi kamayendetsa galimoto ngati ndilibe nyali ya brake amandigwila kusonyeza kut sindikuloledwa kuyenda pa nsewu ndiye kuli bwanji ndege
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms Ай бұрын
Amaziwa kuti ma battery munalibe kapena anatha and black box chifukwa chiyani kwa anthu wofunikila amawakwezamo
KWAVUTA GWEDEGWEDE ANG'ALURA UKU |
27:22
DZIWE TV
Рет қаралды 11 М.
BON KALINDO LERO PA 2 NOVEMBER 2024 |
14:35
DZIWE TV
Рет қаралды 4,6 М.
When mom gets home, but you're in rollerblades.
00:40
Daniel LaBelle
Рет қаралды 122 МЛН
Sigma baby, you've conquered soap! 😲😮‍💨 LeoNata family #shorts
00:37
Will A Basketball Boat Hold My Weight?
00:30
MrBeast
Рет қаралды 136 МЛН
Wait for it 😂
00:19
ILYA BORZOV
Рет қаралды 10 МЛН
BRIAN BANDA VS KEN NSONDA NTHAWI IMENEYO
7:39
WAMACHIGWE MEDIA
Рет қаралды 14 М.
Senzo Meyiwa Trial: Calls Between Mncube & Ntuli
30:38
Sthembiso Mngoma
Рет қаралды 7 М.
Bobi Wine Ne Ba Celeb Balaze Fresh Kid Love.
12:02
Rock Minem
Рет қаралды 1,2 М.
November 2, 2024
37:25
Eswatini Politics
Рет қаралды 6 М.
When mom gets home, but you're in rollerblades.
00:40
Daniel LaBelle
Рет қаралды 122 МЛН