Пікірлер
@user-tl8pe5ge6l
@user-tl8pe5ge6l Күн бұрын
Amunyanyiwa ntchito simuiziwa ayi mukulephera kumfusa mafuso mwaonongatu ndalama ulele
@XolaMzebetshana
@XolaMzebetshana Күн бұрын
Komaso dzilikooooo
@RanneckKapata
@RanneckKapata 4 күн бұрын
nice one
@FatimaSande-lb1hd
@FatimaSande-lb1hd 4 күн бұрын
Chithandizo cho iye ndalama amapeza koma mowa aaaa..... Tazikhalani serious kuzolowera kupempha eti? 🤔
@FatimaSande-lb1hd
@FatimaSande-lb1hd 4 күн бұрын
Kuyembekezera kuti ndimva funso loti joe ali ndi Ana angati? Ationetsa madam a joe ayi ndithu za ziiiii..... 🤭
@KilionSphiri
@KilionSphiri 6 күн бұрын
Mfundo zikuwoneka zikuwoneka mulibe next time. Zafuseni zazeru . Komaso gwaladi mwatichitisa Mandyazi asa asa hiya
@LukaSpoko-i3l
@LukaSpoko-i3l 26 күн бұрын
Akomaamakana ndipotimawanyadila
@EdisonNakulenga
@EdisonNakulenga 27 күн бұрын
Akamunaamenewo amativesakukoma jo
@RittoKei
@RittoKei 29 күн бұрын
Is this comedy 😅😅😅😅
@LonelyKhoma
@LonelyKhoma Ай бұрын
Gwaradi sakufunika kumupasa ndarama ayi kuthandiza kwake kuimirire ndi munthu wina azimupangira kaya ndi nyumba iyeyo akapeze yomanga kare ndikumuikamo mmmm zokhudza bwanji kuntchuka koseku 🤔
@SadguruPrernaTrust
@SadguruPrernaTrust Ай бұрын
Jumping Jack !
@user-iv6iw1ck8s
@user-iv6iw1ck8s Ай бұрын
Zopanda ntchito izi, anthu akuvutika kwambiri kumudzi, okalamba, aumphawi, olumala, amasiye, odwala, osamalankhula mwachibwana kut Mulungu Ali mbari yanu yet zinthu sizili bwino, kulankhula ngati anthu opanda mzeru, palibe chanzeru chomwe mukuchita chopindulira Malawi kuposa kumangomanga wanthu ndi kusintha maina azipatala zoti simudamange ndinu, 4 years just for nothing, shame on you guys, mzipatala mankhwala mulibe, chitetezo taaa, ma school Nde mwakweza ma fees, anthu akumudzi omwe alibiletu chiyembekezo ndipo alibe chilichose akwanitsa bwanji kulipilira Ana awo ma school, chakudya Nde kulibiletu, chomwe mukuganiza mkuti tidzadzitsa bwanji matumba wathu kuti tidzabele zisankho, AGALATIYA opusa, oyamba ndi zabwino kutsiliza ndi zoipa, When I said amalawi akuvutika I mean it, mukamadya bwino kumitundako musamati aliyese a kudya, go to the villages and see how life is, you will cry, anthu a kugona ndi njala and you are expecting those people to go and vote for you this coming 2025 nonsense, MAY The Soul of SKC continue to Rest well and hope he is watching you all,
@user-qf7ko2dd5g
@user-qf7ko2dd5g Ай бұрын
Ufiti
@JaytuSaisi
@JaytuSaisi Ай бұрын
amapanga sewero
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Kuyankhula koputsa kwambili,Kodi moyo ndi wanu??? Inu anthu omvetsa chisoni kwambili
@Cathy-oc7vd
@Cathy-oc7vd Ай бұрын
It is supposed to happen.. MCP is a big party sangalore kuberekedwa
@KimuEmmanuel-lv9wt
@KimuEmmanuel-lv9wt Ай бұрын
Chakwera ndi mbudzi yamunthu
@PercyTrading
@PercyTrading Ай бұрын
Koma malawi kodi mukhalabwamji? monga azomba ndi azisuzo mumamwalila apanda kanthu kalikose.
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Ай бұрын
Mwagwanayo UTM yakutulukani forever Chakwela kwamai ako
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Ай бұрын
chisankho chabwino koma osanyoza adzanu ayi
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Chakwera ndi munthu olephela ....mkazi olanda amavuta
@PercyTrading
@PercyTrading Ай бұрын
Anamangindwa chifukwa chani
@mannersaint
@mannersaint Ай бұрын
Ayi ndth anthu matha kuvina eeeee😄
@OsmanOsher-sh6gp
@OsmanOsher-sh6gp Ай бұрын
Osayiwala chipande ndipowomola
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Tso pali chimene wapanga chakwera success! Agalu achabe chabe.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
Za ziiiiiiii! Chakwera ndi MCP yake akagwere uko
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 Ай бұрын
Zakuvutani bas
@victorauwana7258
@victorauwana7258 Ай бұрын
2025 president wanu chakwela? Is so sad for Chilima 😢 rest well
@victorauwana7258
@victorauwana7258 Ай бұрын
Ubwino simuvota nokha
@user-xe1so5xj2w
@user-xe1so5xj2w Ай бұрын
Anthu akuba akugawana ndalama za boma
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i Ай бұрын
Mbudzi ya mdzimayi mulungu dzikusunga ndi moyo wawutali pomzunza anthu
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo Ай бұрын
Oloko akupaseni ndalama koma dziko lilingati galimoto ngati siiwe dilaiva sungakwanise kuyendesa achakwela alephela
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi Ай бұрын
Mcp we no need it again yatizuza mokwana
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r Ай бұрын
Chakwela Galu wohipaa
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu Ай бұрын
2025votiyo yakuba chani musayi namize fiti yanuyo bozaa Galu lwe
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu Ай бұрын
Agalu lnumuzaziona mungotiphe ndinyani wanuyo agalu lnu
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma Ай бұрын
Mbuzi iweeeeee meeeee 😂
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Ай бұрын
Ameneyo ndi neneli wakale nanga watsopano watipo chani
@Masturdthepoet
@Masturdthepoet Ай бұрын
Kuzinamiza pamenrpo😢😢😢
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 Ай бұрын
Fack you all you taken advantage our country fack you all amcp
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 Ай бұрын
Ohhhhh amenewo nde ma results aifa yachirima inuyo Malawian okuzidwa?
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo Ай бұрын
Pamsana pako iwe, koma ukuliona dziko, chamba et kuyankhulila kumaliseche kt pant adzimva kapena pakamwa
@danielmuriya8675
@danielmuriya8675 Ай бұрын
Oooooh yes, chakwera emweyo mukudya naye bwino
@OrtonKabbichi
@OrtonKabbichi Ай бұрын
Wandevu ameneyi sanasochere Wakuda angapezeke kwao
@yusufbakali
@yusufbakali Ай бұрын
Ndi chimene chinamupha chilima
@user-dn3gp6yi4y
@user-dn3gp6yi4y Ай бұрын
Kuyankhula komaliza mawu anuwo sumuzayankhulaso 2025 mukugwa
@user-xm3zl5cg6x
@user-xm3zl5cg6x Ай бұрын
Kd mcp ndichan pamalawi
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r Ай бұрын
Emusipi idziwe kuti kunja kuno kuli Mulungu ndipo Mulungu sangalole Kuti Amalawi tipitirize kuvutika
@user-bg7ur1gw1q
@user-bg7ur1gw1q Ай бұрын
Chakwela ndiye chani
@AbdullCassim
@AbdullCassim Ай бұрын
Fundo sinakhazikike amtolakhaniwa