Njala yokhayo anaenerad kuchitapo lsnthu mm so sizili bwn Nancy umakwana
@Thokozani-n6d4 күн бұрын
Nancy umakwana iweyo kk
@EstherManda-ex3bc4 күн бұрын
😄😄😄
@DigleDafter4 күн бұрын
Nancy mpaka kulira 😂😂😂😂😂waonekadi kuti iwe umakonda dziko lako ❤ live form boksburg north SA 🇿🇦
@AlexKaunda-w7l4 күн бұрын
Boma ndi lomweri tidye nyemba kulibe kuti ndi mpongozi wa President or wa Dan lu tidya ntchunga
@CarolineJohn-ue3tr4 күн бұрын
😂😂😂😂❤ koma lero Nancy unali serious eeeeeee mpaka kulira ayidi koma zithu sidziri pa bwino ai
@douglastholo3904 күн бұрын
Koma Nancy amazitsata zinthu. Indeed amayi pakhomo ndiye amaona za njala pakhomo. Tinasintha koma ndiyedi tikuvutika. Amalawi tili ku Bagamoyo instead of Canan??
@JimmyIsaac-xd4ef4 күн бұрын
More 🔥 Nancy
@RilJacksy-w5t4 күн бұрын
Kkkkkk koma Nacy
@DanielHolla-v9s4 күн бұрын
Za passport mmmm koma bwezi athu awa atachitako manyazi kutipasa ma passport athu asale ndi ziko lawoli aaa
@DokotalaPhungu-lk4kn4 күн бұрын
Muli bho che Nkope. Muzibwerabwera.
@SabinaNkhoma-o1h4 күн бұрын
Nancy mpaka kufika polira😭
@AnnieZiba4 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@yamichadzunda61484 күн бұрын
La masanje
@ZinenaniSiyaya4 күн бұрын
Iponde Nancy wachiponyeponye❤❤
@ZinenaniSiyaya4 күн бұрын
Kkkkkkk
@rashidkandulu2904 күн бұрын
Mulape kkk
@OptimumFoundation4 күн бұрын
😢😢😢
@DOLADAUSI4 күн бұрын
Nancy mpaka kulira?😅😅😅😅😅 Kudya kwake katatu amatanthauza uku tikungochulukana😅😅😅😅😅
@ZinenaniSiyaya4 күн бұрын
Imwa madzi chemwa Nancy❤
@ThutsanBridgetteMonet4 күн бұрын
Likanakhalà boma lamakutu bwenzi litasintha pa 5 years ndipo ukulira zoona nanse
@preciouskuntindi-du1xw4 күн бұрын
2:53 😂😂😂 koma uyu
@JamesRoben-dy7bx4 күн бұрын
Well cm chekope
@ZinenaniSiyaya4 күн бұрын
Milakuliiiiiii..Nancy😂😂
@AllieBenimwema4 күн бұрын
NANCY PAKHA KULIRA LERO KWAVUTHA
@ZinenaniSiyaya4 күн бұрын
BP yakwera Nancy ❤😢
@ZinenaniSiyaya4 күн бұрын
Ipatse Moto Nancy tikubvutika koooophya❤😢
@AdmiringBabyOctopus-mw5eh4 күн бұрын
Koma che nkope ndiwachabe ngat wa mcp koma ai xikom