Nancy vs Che Nkope - Boma ndi lomweli

  Рет қаралды 9,594

CHE NKOPE

CHE NKOPE

Күн бұрын

Пікірлер: 56
@grantnailuwa
@grantnailuwa 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 boma loyenda ngati chizumbazumba big up Nancy chenkope
@FaziaSindi-fp1ll
@FaziaSindi-fp1ll 3 ай бұрын
Koma naaaa iweyo ❤❤❤❤
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 3 ай бұрын
Ineo like this guy plz phepo tayesesa kumapanga daily
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 3 ай бұрын
Kutikitatu Nancy kungopanga zakuti Ena azidziwe 😂😂😂😂😂❤
@GraceBatumeyo-u8d
@GraceBatumeyo-u8d 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 Nancy please usandikomole ine boma ndilomweli mpaka tife
@AlexNachuma
@AlexNachuma 3 ай бұрын
More fire na ❤❤❤❤
@georgesmart3791
@georgesmart3791 3 ай бұрын
More fire Nancy 🔥 🔥 😂😂😂😂😂
@williammenard48
@williammenard48 3 ай бұрын
First to like and comment 😅😅😅
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 3 ай бұрын
Wozaaa Nancy 😂😂😂❤
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 3 ай бұрын
More 🔥🔥🔥 Nancy
@DAVIEPelete-of3dr
@DAVIEPelete-of3dr 3 ай бұрын
I was waiting you Nancy ❤❤
@mosesmvula5437
@mosesmvula5437 3 ай бұрын
Nancy osamangolankhura koma kumadziwanso kubisala ngati muja apangira wa bakili muluzi tv, otherwise akutengapo masanasana😊
@veronicamalisero2671
@veronicamalisero2671 3 ай бұрын
Bomadi ndi lomweli,,,sikutinso pangakhale kusintha ataaa 😊
@SteveNdhlovu-r2x
@SteveNdhlovu-r2x 15 күн бұрын
Koma munthu wanzeru zake angama vote kuti nkhondo ipitilire ku Israel koma akuti ndi mbusa mmmmm. The almighty gwirani ntchito yanu
@stanleynamatcherenga4698
@stanleynamatcherenga4698 3 ай бұрын
Nancy sangadye bans 😂😂😂... ndi dolo kwambir 😂
@khaleedsaidi6232
@khaleedsaidi6232 3 ай бұрын
😂😂😂😂 chekhope azakunyengelele Nancy ali ndi chibwezi ameneyo ndi mr taonani taonani 😂😂😂
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Ай бұрын
Koma ndiyedi ndi panja
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 3 ай бұрын
Nancy yomweyo galu iwe nawensoo😂😂😂
@emmanuelroben162
@emmanuelroben162 3 ай бұрын
Wadya Bazi iwe😂😂😂😂
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Ай бұрын
😂😂😂😂❤
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug 3 ай бұрын
Nancy pola Moyo 😂😂😂😂😂
@KondwaniNguleti-o9o
@KondwaniNguleti-o9o 3 ай бұрын
Nancy I like u will u marry me? 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Umandiwaza kooooophya neweenso! Kkkkkkk
@StephenPrinceScale
@StephenPrinceScale 3 ай бұрын
😂😂😂😂Nancy kubwera ndikachilungamo😂
@AngellaMkwamba
@AngellaMkwamba 3 ай бұрын
😅
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 3 ай бұрын
Koma Nancy ndiwe mwamba zoonad tingoyang'anizana😂😂😂😂😂
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 ай бұрын
😂😂😂 Amalawi muli ndi vuto mukatenge munthu oti wachinda chinda agalu mmizimu inu mukuti akhale president
@KachingweNkhoma
@KachingweNkhoma 3 ай бұрын
😂😂more 🔥🔥che Nkope!!
@HassanJabuhkhayiroo
@HassanJabuhkhayiroo 3 ай бұрын
Nancy ndi yemweyu situsinthanso nayenso😅
@OlayjerempondahMponda
@OlayjerempondahMponda 3 ай бұрын
Ma hope a Chiwamba😂😂😂😂
@Princephiri1999
@Princephiri1999 3 ай бұрын
Nancy aaaa iweyo
@lusolawo73
@lusolawo73 3 ай бұрын
Kkkkkk km nase 😊
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 3 ай бұрын
Tikudya katatu boma lake liti lomweli😂😂😂
@YoxyJay
@YoxyJay 3 ай бұрын
😂😂😂Amen Nancy
@LM-gz5pk
@LM-gz5pk 2 ай бұрын
Kungotopa kuing'alula bas
@ModesterChigaya
@ModesterChigaya 3 ай бұрын
😅😅😅😅km Nancy suzatheka.!
@HendrickBanda
@HendrickBanda 3 ай бұрын
😂😂😂😂🔥🔥♥️♥️♥️
@MarriamShakira
@MarriamShakira 3 ай бұрын
❤❤
@ShertmanChikoja
@ShertmanChikoja 3 ай бұрын
Naneso
@CathrineRamseyJafaal
@CathrineRamseyJafaal 3 ай бұрын
Akuti boma la chizumbazumba iwe akusakaditu kkkkk
@StewardKapoto-u7k
@StewardKapoto-u7k 3 ай бұрын
Kkkkkk koma Nancy kodi mesa unali ndi mr taonani
@BoleroAirtelmoney
@BoleroAirtelmoney 3 ай бұрын
Koma Nancy Boma lake litilo lokuphalo , kapena kubwelera Ku 1 party system
@VincentPhiri-iv5fw
@VincentPhiri-iv5fw 3 ай бұрын
😂 😂 😂 😂
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 ай бұрын
Inenso ndikuti boma ndi lomweli lakhanzali
@EdgarKB-x5r
@EdgarKB-x5r 3 ай бұрын
Nancy umakwana
@kasupeowenpaul
@kasupeowenpaul 3 ай бұрын
😅😅😅
@YamikanOffman
@YamikanOffman 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂
@SlageChambo
@SlageChambo 3 ай бұрын
Nancy 😂😂😂
@ArronBenson-g6d
@ArronBenson-g6d 3 ай бұрын
😂😂
@MynessChirwa
@MynessChirwa 3 ай бұрын
😂
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 3 ай бұрын
Boma la chizumbazumba😂😂😂 😂
@EstherManda-ex3bc
@EstherManda-ex3bc 3 ай бұрын
🤣🤣🤣
@EsetaGerate
@EsetaGerate 3 ай бұрын
😂😂😂😂 koma Nancy ayi taa boma luyenda ngati chizumbazumba😂😂😂😂
@GuliwaGixious
@GuliwaGixious 3 ай бұрын
❤❤
@vincentchimawochavula2354
@vincentchimawochavula2354 3 ай бұрын
😂😂😂
@TownEngcobo
@TownEngcobo 3 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
Nancy  Vs Che Nkope - USI sumafuka  opanda moto
24:15
CHE NKOPE
Рет қаралды 13 М.
NANCY VS CHE-NKOPE AKUTI KOMRADE MITAMBO ASATIBOWE
13:52
Kwagwanji?
Рет қаралды 635
IL'HAN - Qalqam | Official Music Video
03:17
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 700 М.
99.9% IMPOSSIBLE
00:24
STORROR
Рет қаралды 31 МЛН
Мен атып көрмегенмін ! | Qalam | 5 серия
25:41
Nancy vs Che Nkope -Trump
11:43
CHE NKOPE
Рет қаралды 6 М.
ABWANA BODZA LONSE LIJA CHOMWE CHINAPANGITSA CHAFOTOKOZEDWA LERO
6:52
Malawi Trends TV
Рет қаралды 6 М.
sateh nding kairama episode 171
21:27
Team Kitabu D Comedian
Рет қаралды 10 М.
Nancy vs Che Nkope - Nkutula khomo
14:10
CHE NKOPE
Рет қаралды 6 М.
NDALE BY NANCY VS CHE-NKOPE
15:06
Kwagwanji?
Рет қаралды 2,4 М.
Nancy vs Che Nkope - Bokosi kunga
17:20
CHE NKOPE
Рет қаралды 13 М.
Mr Jokes/ Kulakatula Baibulo, Genesis to Chibvumbulutso!
20:16
Nancy vs Che Nkope - Ankhutukumve Inu
19:30
CHE NKOPE
Рет қаралды 9 М.
Nancy vs Che Nkope Two Paki 2
16:47
CHE NKOPE
Рет қаралды 9 М.