Рет қаралды 66
Mîsta Kozmik - Mwai Simbota (Mwamwa) Lyrics
Producer : CHAWABEATS
Off "LOVE & EMOJI IS EP"
intro
kings we are, family,
mista kozmik,
I just want a girl like mwamwa,
eyo chawa
HOOK
Nane ndimafuna nkazi ooneka bo //
Azizandifilisaa ngati ndiku show //
Osamongosuta ngati nigga joe//
Osachitisa manyazi pa video call//
I just want a girl like mwamwa,x2//
Azizagwila ntchito ngati mwamwa/
Slim girl ,wa mawu abo ngati mwamwa //
Verse 1
Sindikufuna nkazi, olowelera//
Oti kupanga naye date pompo kusochera//
Sindikufuna nkazi,omangovuta//
Otikuyenda naye kugulu nkumakasuta///
Sindikufuna oti azindipasa thensi//
Ngati pa mic kukanika kuyika verse//
Ine ayi, nkazi omangolira //
Obwera kwaine,kuzandithesera career//
Nkazi waine azizagwila ntchito //
Ananga azavutike iyeyo alipo//
Azakhale business woman, Kaya journalist//
Kaya teacher Kaya azakhala wapolice//
BRIDGE
Ndikufuna wa indipendent, oyima payeka//
Osadalira ine zinthu nkupanga payekha//
Ndikufuna okhala Paden osati shabini//
Wokongola , wakhalidwe,osangowalira Min//
Back To Hook......
VERSE 2
Anzanu,ozisata amaphusha Kaye geli//
Sapanga phuma nkumapangano za usleyi//
Amalimbikira Kuti azakhale paboo//
Ndimamuma Dola azizapanga chi collabo//
Lero Ndikuuzen,
Asamakunamizeni//
Zoti muzagwidwa ndimwamuna wazidollar//
Ndati Ndikuwuzeni, asamakupusiseni//
Inu nkusiya geli busy ndikumakabola//
Mamuna amavuta Ngati ulibe Zi kheeshi,(cash)/
Atha kukutuluka ndikukuyika pa bench//
Osaphunzira amazasowa mtendele//
Amakuvutisaa heavy Ngati ulikundende//
BRIDGE
Ndikufuna wa indipendent, oyima payeka//
Osadalira ine zinthu nkupanga payekha//
Ndikufuna okhala Paden osati shabini//
Wokongola , wakhalidwe,osangowalira Min//
back to hook.......