ndipo ditso lazimayi limeneli khope ya zimayi oti ali pa mpando akudya ndalama eish koma kuli zithu ndithu akuzinyoza okha akuzitukwanisa okha malingana ndi uchisilu wake osati rwara olakwa ayi
@StevenMasamba-y1p17 күн бұрын
Anthu sakuwafuna
@TakalaniGlenda17 күн бұрын
Economic muno mu malawi angayithe ndi Denis mahata ndi kabambe ali bwinonso koma utsogoleri ndi chinthu chochokera kumwamba serious
@MorrisMapiri-o4k20 күн бұрын
Eti! Amakhululukirana ndale
@ElassMunthali-qw3qo20 күн бұрын
Koma sibwino kuti anthu aziwapatsa chimanga, kuli bwino kutsitsa Fertilizer, chifukwa chimangacho sichingakwanile zifuna za wanthu.
Please let's pray to our God, to give us, leaders with spiritual eyes in order to lead this country. Please open your Bible and read Mathews 15:14, Mathew 13:16
@JOSEPHJABULANIMNYAYI20 күн бұрын
Aneneli onyenga mmasiku otsiliza.😢
@AnnahKachidza-e8y20 күн бұрын
Achitsiru Inu nzeru muribe kufuna udindo
@JimmyMhone-b5p20 күн бұрын
Monica Chakwera is handsome
@JoefreyGongoni20 күн бұрын
@@JimmyMhone-b5p chinekewooooooooo😃
@GraceKANYOZA-e3v20 күн бұрын
Kkkkkk❤❤❤❤
@MiracleRose-f9x20 күн бұрын
Chakwera where is chilima and 8 others u must stand for all malawian and say sorry i killed chilima and bring the black box the asss we finish story ife aku ntcheu .mpoto yonse sitizakuvotera😂
@VeronicaChirwa-ct4os20 күн бұрын
Inangokhala mistake pomuyika chakwera pomusankha kukhala President.
@WanangwaMfune20 күн бұрын
Naweso ndiwe ofoila et kkkkkkk
@VeronicaChirwa-ct4os20 күн бұрын
Zoonadi za Mulungu tiziyike apo
@blessmarleystech571220 күн бұрын
Kod iwe wasowa chonena mbuzi iwe iwe ulimbana ndianthu osaesa iweyo bwa