You are giving out the real facts, your explanation tells the right evidence
@DuncanThambalaКүн бұрын
Amene muli ndikuthheketa chonde perekani chitetezo kwa Mr Namiwa chifukwa galu chakwera sakupuma naye bwino afuna amuphe chifukwa kupha to Mr chakwera it has become his habit,Yehova mtetezeni mkuluyu
@henryphiri6100Күн бұрын
Anali ku state house Namiwa. Chitetezo si vuto ayiii ndiodzidalira
@ShamimuBisaniКүн бұрын
Mulungu pasogolo
@SaidiBanetiКүн бұрын
iweyo namiwa number one ❤❤❤❤
@AtupereSadiki17 сағат бұрын
May the almighty God protect u Mr Namiwa
@MwenekabwekayondoSilumbu-g4x3 сағат бұрын
Amen
@hastingskayangeКүн бұрын
Keep it up mr Namiwa.. Tili pambuyo pano..tikufuna chilungamo basi😭😭
@abwinoamatani4921Күн бұрын
Namiwa couldn't fight from within coz he is intelligent. He knew that the report was already drafted
I didn't know kuti ku 🇲🇼 we have people like you more fire brother man
@DavielangwanMachekeКүн бұрын
inu ndi mkango wa a Malawi ambuye apitilize kukutetezerani Mr Namiwa
@bridgetmajor3646Күн бұрын
Yabaya .....Viva Namiwa ......Anthu oipa ompha Azawo......Azionatu. Ine ndimava kuwawa .....frola......selemani...chemwali wanga kufa....nkhondo ya Abare....😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢zimatiwawa munatenga mzati....Angalu A mcp inu munya 2025
@catherinekadwala3839Күн бұрын
God pls protect Mr Namiwa
@isaaczuzeКүн бұрын
Koma namiwa si munthu wamasewela ayi ndipo amaziwa milandu ......munthuyi ndi mwana wa amfumu a namiwa .......munthu ameneyi zina ili la namiwa kwawo ku thyolo ndi amfumu .....ineyo ndiye namiwa amandisangalasa kwambili chifukwa Ali ndi mfundo zogwilika ......chakwara akuyenela kuchoka ....mbuzi ya munthu iyi
@eunicesaitiКүн бұрын
More 🔥 🔥 🔥🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 Zikomo Mr Namiwa.
@amosbula1249Күн бұрын
Namiwa needs support
@MariaGatomaКүн бұрын
Mr namiwa mulungu akudaliseni,,,ifa ya chilima imandiwawa paka pano
@BenjaminKwerengweКүн бұрын
Inu a opposition,you need to support Namiwa and his team .This is a team with 100% integrity. Thandizo lathu lili m'manja mwa anthu amenewa
@KossimasiMaluwaКүн бұрын
Namiwa anakupanga ayise supanga ma ziyen kuchipinda 😂😂😂😂
@Martha-m6eКүн бұрын
Kuli moto kuti buuuuu❤❤❤❤.
@MagretChitsimeКүн бұрын
Oo yes❤ Namimwa yemweyi
@stephankamyata3862Күн бұрын
Basi skc wangolowa mitima yanthu ochuluka 😂😂😂asowa omuphatu sinanga anthu akuchuluka owapweteketsa mitu
@LucyJoacquimКүн бұрын
😂😂😂😂😂
@LucyKulemekaКүн бұрын
Pafera mwazi ana Mulungu mosamvetsetseka mizimuyi imavuta kwambiri, 😮
@alexsumani6823Күн бұрын
long live Mr Namiwa
@DennisKankhuni-b8lКүн бұрын
Koma namiwa 😂😂😂🎉🎉🎉respect
@GIFTTONY-sw5qhКүн бұрын
Koma funso la Winston kalimira ndy ndilopeperatu😂😂😂
@GivenMvula-k5kКүн бұрын
Eti eti 😂😂😂 ndimaona ngati ineyo ndamene ndikupepera koma atolankhani ena😂😂
@RemitterFlik1130Күн бұрын
Atola nkhani akuchikangawa awa
@MwenekabwekayondoSilumbu-g4x3 сағат бұрын
We are behind you Mr namiwa osawasiya achikangawa awa
@LeyvanSamuel-pe5tcКүн бұрын
Eeeeee namiwa anapasa pakamwa😅 umakwana iweyo
@costerbwino338Күн бұрын
Salute and Stay Safe Namiwa❤
@laurentbutao4084Сағат бұрын
Komatu wamisala anaonadi nkhondo.This is real facts
@DaveMakondetsaКүн бұрын
sure Namiwa ❤❤❤❤❤
@d.chemixjiya540616 сағат бұрын
Chilichonse Mulungu amapanga ndi cholinga. Ntambo uja anamusiira mpando munthu oyenera, wanzeru ndi othandiza kuposa m'mene akanayendetsera zinthu Ntambo. Namiwa uja ndi boma payekha😂
@MaxonKambazitheКүн бұрын
Good of you namiwa tifuna anthu ngati inuyo
@ZephMbeleswa-n8mКүн бұрын
Joseph mazizi iweyo ndi ndikatundu chifukwa takhala maulamuriro ose palibe amene anachotsa ntchito 😂😂😂😂
@CliftonPhiri-m8vКүн бұрын
Zimangovuta koma umayesesa Namix 😅
@Timothy1chipokaКүн бұрын
I salute you Namiwa, i loved chilima more
@VITALISCHIKWENIСағат бұрын
Atolankhani mpaka kugoja kufunsa mafunso?😂😂😂
@DavidKadewereКүн бұрын
❤❤❤❤❤❤ Namiwa
@IigIgfКүн бұрын
Malemia wakumalawi 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@FosterLogeyaКүн бұрын
Ndpo live
@ShamimuBisaniКүн бұрын
Angofunika support
@CharlesChibisaКүн бұрын
Tell us what really happened during the plane crash at chikangawa forest. You are the voice of the voiceless in Malawi.on top of that you are not afraid to climb on top of the mountain fighting for our freedom.
@JulietLizziePhiriКүн бұрын
Koma Namiwa, ayayaya, ulemu wako aise
@0wenNkhambuleКүн бұрын
Good my brother ❤
@ChrispineTemuwaКүн бұрын
kumbali yandale Malawi ndiziko limene Lilibe Luntha pandale Anthu ake Ndi Amzeru Za sukulu koma Alibe kulimba mtima Mbuli ngakhale itakhala yosaphumzira koma ili yolimba mtima imaposa Gulu Lama Degree omwe angozimva sukulu ndi ndalama koma ali ogonaa😢
@RobertChizКүн бұрын
Straight
@EthelBernard-h1mКүн бұрын
The truth will prevail no matter how long
@abwinoamatani4921Күн бұрын
Mtolankhani mene akufunsa kuti bwanji a cidec akugwiritsa report loti apanga condemn akuoneka kuti nzeru zake zili ndi malire
@HarrisonMatick80Күн бұрын
We need people like you namiwa in malawi
@isaaczuzeКүн бұрын
Ndiye pali sisilu zina zikuyankhila zsusilu apa ...akudana ndi namiwa popangisa press briefing .....mbuzi za anthu zomwe zimalandila ndalama zokuba kwa chakwera
@JudieBandaКүн бұрын
Afiti okhaokha
@henryphiri6100Күн бұрын
Namiwa brilliant, u took time to read this report and replied this nosense old people call themselves advocates and lawyers. Ndege yogwa 4.5m singaoneke chonchija. The wreakage was worse
@AkimuKambalameКүн бұрын
Woooooo Mai Malawi wanga
@ThokoMsonkho-hy4ucКүн бұрын
Ife tikuti Namiwa akunena zoona pakuyenera ena amangidwe monga Collin Mzamba,Valitino Phiri,Chimwendo,Londa wa pa Tawa kuti akanene bwino,amene adayimisa kafukufuku ku Chikangawa,ogwira ntchito ku Mzuzu airport ndi a Kunkuyu kuti chilungamo chiziwike osati kuti basi tikhare chete zatha ayi.
@ErnestChigawa-p6yКүн бұрын
Akupatseni ndalama inuyo mufufuze
@JerieWytonTengani-h9qКүн бұрын
Zitsiru nthawi zon se siziganiza .Amene anytime lipotili Lili bwino ndiye chitsirucho.Apresident anytime lipotili liwafikire onse amabanja omwe able awo anamwalira PA ngoziyo kuti alone ndi kuliwelenga bwino.Funso mkumati owerengawo sanakhutile ndi lipotili apanganso komishoni of enquiry Ina?kapena ayenere Kopitar ku ma khoti?
Koma a Namiwa muli ndizochita???? Nthawi ndiyolima iyi, dziko lingatukuke chonchi
@JohnPhiri-t2r6 сағат бұрын
Zoona chirungamochizaziwika bola kusintha.vote yanga sogoro langa
@NikolasNanawe6 сағат бұрын
Kd makanilanja km awa😂😂😂😂😂😂
@PempheroMkusangonbe17 сағат бұрын
Namiwa must protect this is light person who help Malawian to now the truth about the plane crushes which take place on 10June 2024 who killed our Late Vice president Dr Souls Chilima ♥️♥️♥️
@GiftMoyo-k7jКүн бұрын
Ngati iwowo ali ndi umboni wogwirika osapita nawo ku bwalo la milandu bwanji
Akuluwa ali ndinzeru koma nzeru zawo akuzigwiritsa ntchito pachabe why, coz if anthu adakana the investigation not to be public akadadekha kukhala momo bwezi atadziwa zambiri kuposa pano and mwinanso ngodya zofunikirazi bwezi mafunso ambiri ataysnkhidwa .koma apapa aaaaaaaa ndikuona ngati mission yachilungamoyi ivuta plus kumathawa anthu azikwanje atatu okha basi aaaaaaa mbola iyi.
@SolomonMumba-i5nКүн бұрын
Indeed these two deaths have a lot of questions than answers
@GraceShaibu-i9dКүн бұрын
Big up namiwa💪💪💪
@GeorgeYohanePaulКүн бұрын
Namiwa ndinudi obatizidwa mwambwuye
@CLIFORDZAKARIAКүн бұрын
Tiyeni nawo akuphawa adzayamba kunjaira ngati dziko analikenga ndi Iwo!