Komanso ndamva ena akukuwa akuti dpp oyee! Mumvesele bwino×2 mumumva basi mcp no chance mwatizunza kwakwana.
@DennisTobias-b4r4 күн бұрын
Ine ndavanso
@isaaczuze8 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkkkk kugwa Kwa babulo ....anthu ngati sakukufunani bola kuvomeleza mcp anthu sakuyofunanso ayi .. .chipani choyendesedwa ndi zisilu
@MandalaChaona5 күн бұрын
Ndipo Zitsiru zake zokumwa Mwazi, mikodzo ndi Malobvu, opanda zimenezo mphamvu Chipani chilibe 🤣🤣
@LuwizaChika8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 zochitisa manyazi Kwambili my vote Dpp oyeee 💙🔥🔥🔥
@eliffagondewe82145 күн бұрын
Kkkkkkk koma pls eesh 🔥🔥🔥🔥
@JafarWiati8 күн бұрын
Ayankhe kabwila 😂😂😂😂
@chrissyamanda55108 күн бұрын
😂😂😂😂muchimva chikuyankha chikangotha kubwila fodya wa mphuno
@thokozanindalama8 күн бұрын
😮😮😮😮😮
@HappyAbyssinianCat-xt2bm7 күн бұрын
Ndpo hule limenelija liyankha manyazi alibe
@MandalaChaona5 күн бұрын
Even the Devil himself is angry with Chakwera and MCP Party 🤣🤣
@MemoryZiyaya5 күн бұрын
😂😂😂😂😂eeissh!@@MandalaChaona
@ShukuraniTonex8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂kkkkkk
@YamikanBanda-z7z4 күн бұрын
Kma abale,eeee anthu akumasuka ndithu😊
@FytonRichard-t3w8 күн бұрын
Kkkkk Dpp my vote 😅😅
@ChristopherJohn-z5z8 күн бұрын
Timati zayang'ana ku thazi bomu 😂😂😂 soya wa chita mpapapa kkkk
@JohnWame-u3l8 күн бұрын
😂😂😂😂😂koma zina zikati zichitike😂
@DONNEXKhama-bk1gy8 күн бұрын
Kukhala WA MCP ndi kulimba mtima 😂😂😂
@Amiduj5 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 moti mpaka pamenepo?
@TimothyKumwenda-z4m5 күн бұрын
Eya chifukwa ndimmene zinalili pamenepa mmm ine Bp kukwereratu
@OdettaLowrence6 күн бұрын
Ndei zicsni ziiiiiiii 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@georgeaiwa86618 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 iwe DJ umandiwaza koopsa ndimmene umatambasulira nkhani. Ndiwe wanga WA nambala one
@bridgetmajor36468 күн бұрын
Apm my vote
@MillieMalakam5 күн бұрын
😂😂😂zamanyazi kwambili
@JJ-in-the-hut4 күн бұрын
Koma mpaka DPP woyeee! Kuma Lacoste camp🐊🐊🐊?🤣🤣🤣🤣
@ReadsonChisaga8 күн бұрын
Apa zaoneseratu kuti anthu ku Lilongwe sankufuna Razaro ndi chipani chake cha mcp.
@KhadijaMsosa-d7z7 күн бұрын
Shaaaaa😂😂😂😂🙌
@phalysbanda24315 күн бұрын
Agalu amenewa adzipita 😂😂😂
@zimmekapachika67848 күн бұрын
😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂yomweyo Chikangawa party
@fannyzimba1498 күн бұрын
Akhaula a wachita bwino agalu amenewa
@Lizzie-h1k5 күн бұрын
Malawi trends ndaikonda....pena imabweretsa zinthu zoti ena saangadzipeze😅😅😅😅...awatu zawo zada...kkkkk...MP wanzeru apitiletu ku DPP...akapange nao ma primaries!
@rashidadan25338 күн бұрын
No chance for the wicked
@BirzetScott8 күн бұрын
😂😂😂😂😂 madzi apanga katondo.
@AlexKaunda-w7l5 күн бұрын
Tilibe ntchito ndi mcp akuchinda kwambili too much kupakula nyemba
@HenryKatopola7 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂mcp yatha , chikangawa😂😂😂😂😂😂😂
@daviechikopa-r6w8 күн бұрын
a geruge zulu kunoooo😅😅😅😅😅
@JamesALLi-m8i5 күн бұрын
Yes chala mwambad Adad woyeeeeee dpp is my vote 🗳 😀 👍 2025 boma and Apm boma we love Malawi 🇲🇼 guys 🇲🇼 💙 🔥
@GiftBello-v1i8 күн бұрын
Esh chapanadi chitseko apa😮😮😮
@YounusWabullah8 күн бұрын
Ndie ena akukomenta kut dpp ku opposition mukhalitsako 😂😂😂😂😂😂😂 zikugwirizana manyazi bwanji muoneramu😂😂😂😂😂
@MathewKalinkhu8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 zamanyazi , MP wa MCP, koma anthu akuti chala m'mwamba , meaning DPP! Eshi! Manyazi basi.😅😅
@MaxwellMangamba8 күн бұрын
zikutheka. APM my vote❤
@MayesoBikefa5 күн бұрын
APM 💙 akubwera komweko
@jacquelinemphwere8948 күн бұрын
Zaulendo uno😂😂😂
@JohnmjigoMalinda8 күн бұрын
Zovuta kwambiri kkķ
@SymonJowabe-y1q5 күн бұрын
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂
@MarthaGama-q1o8 күн бұрын
😂😂😂😂😂 komandiye apa yalimbadi nkandilo olo kuthila madzi sitheka , kukhala WA mcp nkulimba mtima
@LukaSamson-w5h8 күн бұрын
Chipani cha mcp chantha chifukwa cha anthu awa, zikhaleng'oma, chimwendo Banda, Moses kumkuyu ndi Jessy kabwira ayipisa dzina la Chakwera
@HenryKasiyama8 күн бұрын
Malawi Trends ndikukunyadirani mukuitha
@OwenJambo-g4m5 күн бұрын
Kkkkkk koma Adah
@LeonardJere-h8s8 күн бұрын
Kkkk anthu atopa ndikunamizidwa
@ChristinaMdeza8 күн бұрын
Pajatu Jesse akuti boma ndilomweli bas mzimu wa chilima wakwiya nawo bas chakwera munthu wakupha uja,Kuba, mkati, kumanga anthu osalakwa ddp boma bas mu September mu chakwera azipita bas ndi chipani chake cha mcp
@EstherChimombo8 күн бұрын
My Malawi 😂😂
@trifoniachilunda62638 күн бұрын
Yakwiya Mizimu ya chilima
@trifoniachilunda62638 күн бұрын
Chakwela paulendo pakilani
@MrArif-tc2cu8 күн бұрын
Ine ndi mnyamata wa 31 yrs, bambo Anga amkandiuza Kuti mcp ndi yakupha, Kuba kuononga, But now l trust my dad, in our district, area, and my village we don't want mcp party
@spargomw8 күн бұрын
Zavuta kumpanda, kuchipinda kwa MCP😂😂😂😂😂 Adachita mistake kupha Chilima coz ndie anali Joka wawo😂😂😂 Long live APM❤❤❤
@WisdomKapawo8 күн бұрын
It's was big mistake brother ndipo awona zinthu
@ShamimuBisani8 күн бұрын
Mwadzi wamunthu ndi wa nkhuku ndi osiyana
@FracksonMadani6 күн бұрын
E, pa infa ya Chilima yokhayo hmmmm anadzionongera heavy, kudzionongera kwamunthu wankulu kumavuta kukonza 😂😂😂😂anthu amangoseka basi lero siiziiii😅😅
@isaaczuze8 күн бұрын
My vote is for Apm osati chisilu ichi akuti chakwera mbuzi yeniyeni ya munthu olephela .....sindingavotelenso chisilu ine ayi
Amenewo amamudziwitsa kuti akalowe chipani cha Dpp
@ShamimuBisani8 күн бұрын
Malawi Trends aaaa ungabwerese nkhni yokoma chonchi apa moyo umenewu mawa ubwereses zina til pano koz iweyo
@jamessheki42938 күн бұрын
MCP anthu akutopelani
@MussaAli-h4i8 күн бұрын
😂😂😂
@FracksonMadani6 күн бұрын
Gangata ndi Kabambe alikuti kodi?😂😂😂😂
@PaulMwachande8 күн бұрын
Kkkkkkkkkk koma anthu atopa eti mmmmmm mcp yathapo bassss mmmmmm manyadzi alibe koma
@Lizzie-h1k5 күн бұрын
Nkhani ndi DPP....I think even Chakwera is planning to join DPP , there is no question about that!
@WarriorKB-l3i4 күн бұрын
@@Lizzie-h1k kkkkk ndi choncho kumene
@LookmanAdamu8 күн бұрын
😂😂🎉😂😂😂
@PatrickChagaka8 күн бұрын
Kkkkkkk koma zinthu zake zosayendatu
@LilianKachala-yz2xf8 күн бұрын
MCP akunyozeka kwambili Chifukwa Cha njala ndi fertilizer sizinayende bwino.
@AlwayneH8 күн бұрын
😂😂😂 komatu malawi trends
@AustinNangwale8 күн бұрын
😂😂😂 Ndimanena kale Kuti Chakwaela apangitsa chipani cha MCP kuthelatu ndipo palibe yemwe angakhaledo busy kumvesela boza la bwana chakwela😂😂😂
@VdbdbxDvv2 күн бұрын
Makape awa a mcp sadziwa chilichose koma kumba ungule basi
@WilsonNedi-s6t8 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkkk zuchita kuwonekeratu
@TelezaManyera5 күн бұрын
Mkumanama kumati Lilongwe ndi chipinda cha MCP zamanyazi,chawo palibepo gangata kumeneko ndikwake basi.
@ChisomoSaiti8 күн бұрын
Chikangawa Chala mwamba
@WarriorKB-l3i6 күн бұрын
Kkkkk chala mmwamba ndi dpp apapa anthu amayiwuza mbuzi ya mcp kuti kunoku sinu olandilidwa koma ndi kwa dpp dzosaowa kufunsa ichi ndichitsimikizo choti anthu chikangawa sitikumufuna, muwone olo a zimayi avala za mcp ali ndi manyazi 💙💙💙💙💙💙💙💙boma! Mcp ifune, isafune APM boma!
@AlieNkalapwagaNkalapwaga8 күн бұрын
Sanger konde and
@SherifaG.Mlelemba8 күн бұрын
Iiiii! Aziona anzathu a boma ndilomweli😮
@hanifahmponda87115 күн бұрын
Kkkkk a MCP anyanayo game DZIKO LATILUKA ANGOKAKAMIDZA ANTHU KOMA ANTHU ATHANA NAYO MCP MUDZINGODALIA MACHINE OBELA CHITSANKHO BASI OSATI VOTE YACHILUNGAMO SUMUNGAWINE NDINTHU
@ChifundoNinje5 күн бұрын
Mmmmmmm😂😂😂😂😂
@ChriOffice5 күн бұрын
Ndie one koma chala mwamba
@RosinaPatel7 күн бұрын
Chala mwambaaaaaaaaa
@chirwaellace10934 күн бұрын
😅😅😅😅😅
@VictorSiwale-e4v5 күн бұрын
Chakwela anabwela kupha a Malawi ndi Chipani cha mcp, ndeno mcp wake up rise against chakwela he has to resign otherwise no mp will win elections the whole country